- 40
- 429 730
NKHANI TV
Приєднався 17 лис 2022
Takulandirani pano pa NKHANI TV. pangani SUBSCRIBE .
Ntchito yathu ndikukufikitsirani nkhani zosiyanasiyana zochitika mmalawi komanso mayiko Ena.
Ntchito yathu ndikukufikitsirani nkhani zosiyanasiyana zochitika mmalawi komanso mayiko Ena.
KULANKHULA MWANZERU PAKUMANGIDWA KWA KALIYATI //BONI KALINDO
#malawipolitics #nkhanitv #Bonikalindo #kaliyati #MCP #UTM #DPP
Переглядів: 184
Відео
ZOMWE A DPP ALANKHULA DZULO PA 23 OCTOBER 2024
Переглядів 257Місяць тому
ZOMWE A DPP ALANKHULA DZULO PA 23 OCTOBER 2024
TANVANI ZOMWE BONI KALINDO WALANKHULA LERO
Переглядів 107Місяць тому
TANVANI ZOMWE BONI KALINDO WALANKHULA LERO
THE D.C BON KALINDO , Phone yanga idasweka ku malawi first
Переглядів 94610 місяців тому
THE D.C BON KALINDO , Phone yanga idasweka ku malawi first
anthu awa ayambana pompano sikaleso ay
Переглядів 1,6 тис.11 місяців тому
anthu awa ayambana pompano sikaleso ay
WAKWIYA BONI KALINDO PAZOMWE A BWANA CHAKWERA ALANKHULA KU MTUNDU WA AMALAWI
Переглядів 50 тис.Рік тому
#chakwera #president #malawi #Nkhanitv
KWAVUTA KU NYUMBA YAMALAMULO UKU // PRESIDENT CHAKWERA
Переглядів 32 тис.Рік тому
#Malawi #chakwera #Nkhanitv #parliament
KODI APHULE DZIKO LA MALAWI NDI NDANI ? //BENI LONGWE
Переглядів 10 тис.Рік тому
#Malawi #Nkhanitv #chakwera #chilima
A PAC PALIBE ZODZADZA MATUMBA ULENDO UNO WATERO //BENI LONGWE
Переглядів 7 тис.Рік тому
#pac #malawi #chamwera #chilima #Nkhani
NGATI NDIWE M'MALAWI UKUYENERA KUNVERERA IZ //MR GAME CHANGER
Переглядів 22 тис.Рік тому
#Malawi #Nkhanitv #Chakwera #Chilima
MONDAY PA NSEWU NGATI CHAKWERA SALANKHULAPO KALIKONSE MASIKU ATSALAWA //BONI KALINDO
Переглядів 21 тис.Рік тому
#nkhanitv #malawi #chakwera #chilima #bonikalindo
KHALANI OKONZEKA PA 23 NOVEMBER PANSEWU BASI, CHAKWERA ACHOKE
Переглядів 32 тис.Рік тому
KHALANI OKONZEKA PA 23 NOVEMBER PANSEWU BASI, CHAKWERA ACHOKE
KODI IFE NGATI AMALAWI TITANI KUT TITETEZE DZIKO LANTHU LA MALAWI ? // BEN LONGWE
Переглядів 7 тис.Рік тому
KODI IFE NGATI AMALAWI TITANI KUT TITETEZE DZIKO LANTHU LA MALAWI ? // BEN LONGWE
THE D.C ... MALAWI WATHA CHOFUNIKA APA MDIKUGWIRANA MANJA BASI // BON KALINDO
Переглядів 28 тис.Рік тому
THE D.C ... MALAWI WATHA CHOFUNIKA APA MDIKUGWIRANA MANJA BASI // BON KALINDO
CHIFUKWA CHIMENE CHAKWERA WAPITIRA KU SAUD ARABIA KOMANSO ZOONA ZENIZENI ZAKUTSIKA KWA KWACHA
Переглядів 23 тис.Рік тому
CHIFUKWA CHIMENE CHAKWERA WAPITIRA KU SAUD ARABIA KOMANSO ZOONA ZENIZENI ZAKUTSIKA KWA KWACHA
TIYENI TIPHERERE DZIKO LATHU LA MALAWI 🇲🇼, LIKUFUNIKIRA MAPEMPHERO APADEREDERA
Переглядів 3,4 тис.Рік тому
TIYENI TIPHERERE DZIKO LATHU LA MALAWI 🇲🇼, LIKUFUNIKIRA MAPEMPHERO APADEREDERA
KWACHA KUTHERATU UKU ,, TANVAN KULIRA KWA AMALAWI UKU
Переглядів 18 тис.Рік тому
KWACHA KUTHERATU UKU ,, TANVAN KULIRA KWA AMALAWI UKU
BONI KALINDO WACHOTSEDWA PA U PRESIDENT WA MALAWI FIRST //Redson Munlo //Bon Kalindo
Переглядів 8 тис.Рік тому
BONI KALINDO WACHOTSEDWA PA U PRESIDENT WA MALAWI FIRST //Redson Munlo //Bon Kalindo
Ben Longwe kulankhulako zokhudza anthu omwe akumenyera ufulu mimba zawo
Переглядів 2,2 тис.Рік тому
Ben Longwe kulankhulako zokhudza anthu omwe akumenyera ufulu mimba zawo
Anthu awa aphana ndithu , Tanveran chilungomo chenicheni
Переглядів 14 тис.Рік тому
Anthu awa aphana ndithu , Tanveran chilungomo chenicheni
Nkhondo iyi ivuta kwambiri , tanvani chilima uku
Переглядів 82 тис.Рік тому
Nkhondo iyi ivuta kwambiri , tanvani chilima uku
nkhani yakuphedwa kwa anthu M'malawi yavuta uku , tanvan izi
Переглядів 4,4 тис.Рік тому
nkhani yakuphedwa kwa anthu M'malawi yavuta uku , tanvan izi
Lips 💋 Service , Abwana Atupele muluzi akuti There's no real action to fight Corruption
Переглядів 3,6 тис.Рік тому
Lips 💋 Service , Abwana Atupele muluzi akuti There's no real action to fight Corruption
Uthengawu special ukupita kwa abwana a Bakili Muluzi tv
Переглядів 3,9 тис.Рік тому
Uthengawu special ukupita kwa abwana a Bakili Muluzi tv
NKHONDO IKADAPITILIRABE PAKAT PA ISRAEL 🇮🇱 AND PALESTINE 🇵🇸
Переглядів 663Рік тому
NKHONDO IKADAPITILIRABE PAKAT PA ISRAEL 🇮🇱 AND PALESTINE 🇵🇸
Amalawi don't repeat the same mistake, osavoteraso chakwera ay.
Переглядів 7 тис.Рік тому
Amalawi don't repeat the same mistake, osavoteraso chakwera ay.
D.C Bon Kalindo , ndalama zavuta ku M.C.P
Переглядів 5 тис.Рік тому
D.C Bon Kalindo , ndalama zavuta ku M.C.P
Malawi agulisidwe bola andipase gawo langa
Kwao kwaboma ndilomweri hehehehe ayi chikangawa wandikwan msaname
❤ Viva Kalindo Vivaaaa. Ife Kalindo motooooo
Fotseki iwe iwe ndi mwarabu wokuda ngati iwe. Iwe ndi mu Africa zikukukhuza Pati a anena bwino zigawenga zachisilamu chifukwa chisilamu ndi chobwera fitseki
U speaking true brother my Allah protecte ameni
Ndimene amanenela okha polankula kut athu adziwe athuonse
Gyz taganizani azungu amamenyana ndiathu achilunga km simungaone akubwela kno ku African kuzamenya khodo amaziwa kt ndife zisilu
Km uyu akukamba chulungamo
Koma chakwera uyu a kuononga dziko tonse tikuona,,,, maiko azathu ngati Kuno ku south Africa sangapange manyi akewo mpaka atapilikitsa,,
Mulungu azakhala mpomp siku limeneli
Kalindo woyeeee
Listi imeneyo ubweletsela anawako galuiwe ulindi msanje zopusa nkhumba
Machendeako ndi Ben longwe wakoyo
Akugulaiwe nkhumba
A iwe usokosa ndiwe opusa iwe redson
Viva kalindo reason achoke
Bon kalindo woyeeee
Well done Mr. Kalindo
ben longwe sometimes voice yako imatha kumukhudza kwambiri the listener but vuto lake ndi kusaima professionally in one part osamakhara mbar ziwiri munthu mmoz ai ai otherwise muzaoneka sageousness later
Achitsiluwa alowa MCP
Ben longwe lero atukana Nakhumwa Za mu Panti mawa akumuyamikira umusatu nyaope Ben ? Miserable Ben think We are stupid
😅 good
Inu ndi ogulidwa ndi andale, ndimu makape, mumawona ngat amalawi ndife opusa et? Mafuso opusa sitimawafuna ay. Umphawi ndiwathu bas.
Mukuchita kufusa bwana, Inu simukuziwa kut Malawi yose ikut chakwela BOMA, mcp moto kut buuuuuuuuh! 2025
Kalindo ndi 1 more fire basi chakwera ndi panja basi
God bless you boni kalindo🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏
Mukadangosiya
Chisilu cha munthu eeeechii kwabasi akubvutisa anthu anthu kumalawi ine sindikadabvomeleza zopusa izeeeee akumufuna Chakwera simunthu wa satanic uyu asamatisokoneze akufuna magazi basi makolo onse azintha ndikumwalira
Ben longwe umangolimbana ndi Bon Kalindo that's being stupid. You are doing stupid things
umakwana
❤❤❤❤
Atulu atikwana bwanawa ndinachoka ku Malawi pano nduvutika ku rsa kuthawa kwathu komwe
Ndipo zoona
Abwana awa abwere kuno asamangolankhula kunja bwelani abwana
Bwana wanga mumadziwa ndithu kulankhula mfundo komanso kuunikila bwino. Koma ndikadakondwanso inu mukadamabwera ndi ma reaction anu osamangoloza ena
Had it been this people are going to Russia mukanaona reaction ya USA 😂😂😂😂
Akasintha zinthu ndiye vuto likhala pati
Tangomusiye bone karindo ngati chakwera akhoza kusintha zinthu ndiye vuto riripati
A Malawi 🇲🇼 osapusa ndi Anthu awa sangakuthandizenu sure tanganizani ngati akulimbana okhaokha omenyera ma ufulu mukuganiza kuti ndi za nzelu
DPP oyee bonirongwe ndichisiru
Fakiyu onamaiwe
I think bwana Longwe , you have lost the direction, what you are doing is just a confirmation of what MCP has done to you activists, devide and rule,that's what MCP has done you, you are still busy tearing each other amongst yourselves,why ? I think you need to put your house in order,and start all over again
Big man ndimakusatani kwambili koma ndakhala ndikufuna kupempha chithu ichi Kod sizingatheke kut mugwirane manja muzichita zimozi ndi a bon kalindo ? Kuphatikizapo a munlo komanso ndi ma member nonse a malawi first ? Please ndipempho chabe koma ifeyo amalawi mmayenela kut mutithandize Please Ndili kutali kwambili kot ndingakufikileni kut ndizagwade pamaso panu kupempha please help us bwana Charles Ben longwe
Galu ya munthu
Uyudi ndioputsa bwanji akulimbana ndi munthu wankulu bon kalindo
Ine ndibwere iyii ngati chakwela akukakamila udindo komanso ngati zisankho zitalephereke 2024 muyembekezere zithu izi kwa majaji tizayamba kuphulitsa ndi petrol bom manyumba awo kapena magalimoto ao petrol bom siyifunija training ndiye muyembekenzere zoopsya zomwe zingabwere
Mokupephani muziyakhula muchizungu chifukwa khaningatizimenezi zikupita pazikolose kutibomali liyaluke ndikuikapo mbedela yamalawi chifukwa timakusatani pokuziwani Sono Muchizungu zifalikila ulemuwanu🙏
Paja mupita dark liti?
Kodi nkhani ya online banking timaidziwa?
Ngati mumakhala ndi information, mumaphonyetsa bwanji? Eh dzulo ndinalakwitsa, eh ulendo wachiwiri or wachitatu.
Munthu akamuchita tocha magazi amasanduka drag !! Ehh!!
Mchifukwa chake ambiri tikuti tiyeni tilimbabe nao anyani atonse amenewa adzipita tikufuna zisankho zikhale 2024 osati 2025 zolimbikila ndidzimenezi komano otimenyela ufuluake akumakayikitsanso osagwirizana kutukwanizana ndiye amalawi aomboledwa bwanji