KULANKHULA KWA ABWANA A BENI LONGWE

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 8 гру 2024

КОМЕНТАРІ • 37

  • @OmegaChingamuka
    @OmegaChingamuka Рік тому

    Abwana awa abwere kuno asamangolankhula kunja bwelani abwana

  • @mbaliehaward947
    @mbaliehaward947 Рік тому

    Mukadangosiya

  • @christopherstosherchimbuwi676
    @christopherstosherchimbuwi676 Рік тому +1

    To be honest Bon Kalindo sakuti Chakwera asachoke nooooo mu malamulo a Malawi sitimachonsa president term yake isananthe Bon Kalindo kunena kuti Chakwera akodze zinthu sakulakwitsa he doing the same job opposition can do 💪💪💪💪

    • @neemahkapatamoyo9563
      @neemahkapatamoyo9563 Рік тому

      Kwanu Kuno kulibe zimenezo inutu mukunama pajatu chakwela ananena yekha Kut ngt sakwanitsa adzatula pansi undindowo nde vuto ndife anthu munthu uyu Atha kuchoka mosavuta titati tonse tatengana nsanje to chitipa ndukuuza uyu Atha kuchoka mosavuta vuto ndife tokha timasiila anthu amodzimodzi Kut azitimenyela nkhondo

  • @SelinaLuhanga
    @SelinaLuhanga Рік тому +2

    M cp siyikufuna anthu osusa don't bleam D PP we must bleam our self cozy ubuli sitiziwa chabwino kwanthu kususa basi to saute we. Fall

  • @ritchardchakuma5725
    @ritchardchakuma5725 Рік тому

    Mokupephani muziyakhula muchizungu chifukwa khaningatizimenezi zikupita pazikolose kutibomali liyaluke ndikuikapo mbedela yamalawi chifukwa timakusatani pokuziwani Sono
    Muchizungu zifalikila ulemuwanu🙏

  • @beakab2378
    @beakab2378 Рік тому +3

    DPP ikulamula munkalimbana nayo, pano ili ku opposition mukulimbanana nayo, daily DPP this n that. Activism yanu ikakhala focused on DPP palibe muphule mpaka 2025!! Iwe ndi Munlo mimadzimva a nzeru kuposa aliyense mmalawi muno. I hate MCP too koma ur approach is wrong. DPP has a right to choose their own strategy, inuyo spread ur net wide, pomwe palilipa u can write convincing proposals to international organizations to give you funding for ur activities, osati daily decampaignimg DPP. If Chakwera wins again in 2025 it's you plus all Malawians who will continue to suffer, not DPP as a party.

  • @DaudBonomali
    @DaudBonomali Рік тому +1

    Mchifukwa chake ambiri tikuti tiyeni tilimbabe nao anyani atonse amenewa adzipita tikufuna zisankho zikhale 2024 osati 2025 zolimbikila ndidzimenezi komano otimenyela ufuluake akumakayikitsanso osagwirizana kutukwanizana ndiye amalawi aomboledwa bwanji

  • @DaudBonomali
    @DaudBonomali Рік тому

    Ine ndibwere iyii ngati chakwela akukakamila udindo komanso ngati zisankho zitalephereke 2024 muyembekezere zithu izi kwa majaji tizayamba kuphulitsa ndi petrol bom manyumba awo kapena magalimoto ao petrol bom siyifunija training ndiye muyembekenzere zoopsya zomwe zingabwere

  • @ChisomoYakweyakwe
    @ChisomoYakweyakwe Рік тому +1

    Big man ndimakusatani kwambili koma ndakhala ndikufuna kupempha chithu ichi
    Kod sizingatheke kut mugwirane manja muzichita zimozi ndi a bon kalindo ?
    Kuphatikizapo a munlo komanso ndi ma member nonse a malawi first ?
    Please ndipempho chabe koma ifeyo amalawi mmayenela kut mutithandize
    Please
    Ndili kutali kwambili kot ndingakufikileni kut ndizagwade pamaso panu kupempha please help us bwana Charles Ben longwe

  • @AliAli.aliheassim
    @AliAli.aliheassim Рік тому

    Ulemu wanu abwana❤❤❤

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj Рік тому

    A Malawi 🇲🇼 osapusa ndi Anthu awa sangakuthandizenu sure tanganizani ngati akulimbana okhaokha omenyera ma ufulu mukuganiza kuti ndi za nzelu

  • @SamukLungu-zg7fl
    @SamukLungu-zg7fl Рік тому

    Tangomusiye bone karindo ngati chakwera akhoza kusintha zinthu ndiye vuto riripati

  • @VictoriaNyirongo
    @VictoriaNyirongo Рік тому

    Muli bho man ife timakunyadilan mumatiimilila

  • @tonemuyaya6284
    @tonemuyaya6284 Рік тому

    Chko galu iwe 😂😂😂😂😂 zikuvuto bas iwe 😂😂😂

  • @YNOTGEORGE8
    @YNOTGEORGE8 Рік тому

    Akasintha zinthu ndiye vuto likhala pati

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 Рік тому

    Awa afika potisenda chikopa tikuona ndi maso 😭😭😭

  • @CosmasChikwindi
    @CosmasChikwindi Рік тому

    Now you are talking Sir

  • @obedlanken
    @obedlanken Рік тому

    Bwana wanga mumadziwa ndithu kulankhula mfundo komanso kuunikila bwino. Koma ndikadakondwanso inu mukadamabwera ndi ma reaction anu osamangoloza ena

  • @KumbukaiMtawaliWaMoffat
    @KumbukaiMtawaliWaMoffat Рік тому

    Paja mupita dark liti?

  • @KumbukaiMtawaliWaMoffat
    @KumbukaiMtawaliWaMoffat Рік тому

    Kodi nkhani ya online banking timaidziwa?

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 Рік тому

    It's happening right now ,sindinanene kuti ndikuti Chauta akuona mbamba

    • @AgnesMatola
      @AgnesMatola Рік тому

      Zimanveka Sir, osawukafe tilibe nkuwo Sir B
      Longwe. Musadzatisiye tokha bwana

  • @giftmasenti5732
    @giftmasenti5732 Рік тому

    Had it been this people are going to Russia mukanaona reaction ya USA 😂😂😂😂

  • @KumbukaiMtawaliWaMoffat
    @KumbukaiMtawaliWaMoffat Рік тому

    Ngati mumakhala ndi information, mumaphonyetsa bwanji? Eh dzulo ndinalakwitsa, eh ulendo wachiwiri or wachitatu.

  • @WilliamCharles-m9w
    @WilliamCharles-m9w Рік тому

    Fakiyu onamaiwe

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 Рік тому

    Opposition ili dyoo kudikilira kuti they are gvt in waiting azikuyankhulirani ambuyanu mxeuii

  • @WilliamCharles-m9w
    @WilliamCharles-m9w Рік тому

    DPP oyee bonirongwe ndichisiru

  • @VictorHSmith-v8w
    @VictorHSmith-v8w Рік тому

    Uyudi ndioputsa bwanji akulimbana ndi munthu wankulu bon kalindo

  • @charleskambalame7927
    @charleskambalame7927 Рік тому

    Ku Malawi tamva za manyazi anthu akuphika chitedze mmalo mwa kalongonda, baks mmalo mwa shuga, mango porriedge shame

  • @Abdul-xk8dq
    @Abdul-xk8dq Рік тому

    Sizikuveka inu mukufuna dpp osati kusintha zithu

  • @KumbukaiMtawaliWaMoffat
    @KumbukaiMtawaliWaMoffat Рік тому

    Munthu akamuchita tocha magazi amasanduka drag !! Ehh!!

  • @EliasKawuwa-um6wj
    @EliasKawuwa-um6wj Рік тому

    I think bwana Longwe , you have lost the direction, what you are doing is just a confirmation of what MCP has done to you activists, devide and rule,that's what MCP has done you, you are still busy tearing each other amongst yourselves,why ? I think you need to put your house in order,and start all over again

  • @umalimaganga
    @umalimaganga Рік тому

    Ben longwe umangolimbana ndi Bon Kalindo that's being stupid. You are doing stupid things

  • @SelinaLuhanga
    @SelinaLuhanga Рік тому

    M cp siyikufuna anthu osusa don't bleam D PP we must bleam our self cozy ubuli sitiziwa chabwino kwanthu kususa basi to saute we. Fall