nkhani yakuphedwa kwa anthu M'malawi yavuta uku , tanvan izi

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 4 гру 2024
  • #malawi #satanic

КОМЕНТАРІ • 15

  • @andsenJeke
    @andsenJeke Рік тому

    2024 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @joicemartin-ji5zu
    @joicemartin-ji5zu Рік тому

    Eeee chakwera chakwera chakwera chakwera ameneyutu Mulungu amuone

  • @joicemartin-ji5zu
    @joicemartin-ji5zu Рік тому

    Zoonadi

  • @GiftRichard-b1o
    @GiftRichard-b1o Рік тому

    Zoona d pano adya mabazi amenewa 😂😂😂😂😂

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 Рік тому

    Akuti PAC yonse ndi ya kongolesi

  • @NKHANTV
    @NKHANTV  Рік тому +1

    Chonde osayiwala kupanga subscribe ❤

  • @andsenJeke
    @andsenJeke Рік тому

    Munthuyu akulankha zoona Tina voter a chakwera ndi chilima potsatila malonjezano awo lero palibe tu or chimodzi

  • @folamitowing238
    @folamitowing238 Рік тому

    PAC si anthu achipembedzo.Anthu oyipa amenewa kwabasi led by the catholics.

  • @patricksinyala1345
    @patricksinyala1345 Рік тому

    Owe ndithu opusa kwabasi, Ngati ulamuliro was pm inali wokoma ndiye achotsedwelanji mmboma? One sindikanayankha MCP ikuchita bwino ayi, olonso p and ng'ono. Koma iweyo usalankhule Ngati boma la pm linalibe nafe mavuto.

    • @MussaCabbage
      @MussaCabbage Рік тому

      You don't know what ur saying shirt ur mouth

    • @vincentjaja5893
      @vincentjaja5893 Рік тому

      Anachita kulanda boma

    • @folamitowing238
      @folamitowing238 Рік тому

      Kusiyana kulipo kwambiri amwene.
      Olo nokha simungaone kuti pano life ili much tougher kusiyana ndi nthawi ya DPP.inuyo zoti DPP inachotsedwa kamba koti ma European analowelera underground kuti achotse Peter .Peter sankalola kugwetsa kwacha,sankalola nkhani ya yamathanyula kuti izikambidwa mu parliament.zimenezi ndizimene a Europe ankadana nazo ndiye anafuna kuyika chitsilu!!??

  • @ChifundoBeston
    @ChifundoBeston Рік тому

    Galu iwe ndiwabodza kwambiri. Utsogoleri wa amaliseche akumwera umapitsa pagolo moyo wa amalawi, amalawi ake ati? Ukati umakomera amalawi tonse Mulungu akukhululukire galu iwe. Ife tinamva kuwawa kwambiri ndi boma la DPP. Ndipo ndikutsikimizile DPP sitikuifuna wamva? Umuuzeso maliseche akumwera wakoyo