KWAVUTA KU NYUMBA YAMALAMULO UKU // PRESIDENT CHAKWERA

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 6 гру 2024

КОМЕНТАРІ • 77

  • @EvansPhiri-ug4oz
    @EvansPhiri-ug4oz Рік тому +4

    That sounds great so chakwela can be know Kuti ndichisilu chamunthu

  • @DaudBonomali
    @DaudBonomali Рік тому +7

    Chonde aphungu kambilanani zoti chisankho 2024 basi tikavotenso basi nyasi zatikwana

  • @LuciusMorson
    @LuciusMorson Рік тому +1

    Keep it up our beloved mps

  • @Yusufu-Daudi
    @Yusufu-Daudi Рік тому +7

    Kwayakad 🔥🔥🔥🔥

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc Рік тому +6

    Sitinayembekezele,kuti Mr president,angamachite,izi anthu kubvutika,ngati si democracy 'aaaaa,apeleke mpata kwa ena.

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm Рік тому +1

    Achoke Achoke basi

  • @johnkumbanga3369
    @johnkumbanga3369 Рік тому

    More fire🔥🔥🔥🔥 mps respect for you guys

  • @IdrissahChuma
    @IdrissahChuma Рік тому +4

    Dzausilu bas asamatenge ngati ife ndimbuzi zake

  • @FunnyKatchenga
    @FunnyKatchenga Рік тому +6

    Ambuye apitilidze kukuyenderani inu aphungu ku nyumba ya malamuloko, kut mutiimilire ndithu ife anthu ovutika😢😢😢

  • @MosesKatunga-r5n
    @MosesKatunga-r5n Рік тому +1

    ine chakwela wanditopesa zomwe amalakhula ngati akulakhula anake ndizizukulu zake ayi God tichitileni chifundo uyu achoke

  • @IbrahimOmar-f8g
    @IbrahimOmar-f8g Рік тому +2

    A choke bas

  • @AbdulNyambi-n4s
    @AbdulNyambi-n4s Рік тому +1

    Plz arrest him chakwera that one is failed there no way and no way just move forward for nosense what are doing chakwera about to be a president

  • @SHARFBASHIR-t7s
    @SHARFBASHIR-t7s Рік тому +3

    Choke chakwera

  • @JuliyaschitsekoJuliyasichitsek

    Chakwela achoke bas nkhan ndiyomweyo bas

  • @MilliamBanda-u7b
    @MilliamBanda-u7b Рік тому +5

    Chakwela watikwana achoke

  • @RaheemAli-v9h
    @RaheemAli-v9h Рік тому +3

    Kkk😂😂 he can't wht yoo
    Akugwa chifufu ndithu😂😂

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu Рік тому +4

    Thanks MP of Malawi, chakwera achoke musankhe ndi cabinet yake, musankhe m'modzi wa aphungu kuti atsoholele dziko . Uyu achoke

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 Рік тому +2

    Achoke sitikumufuna

  • @NorahKajombo
    @NorahKajombo Рік тому

    Gule kwawo gule kwao

  • @Ruth-y5q9n
    @Ruth-y5q9n Рік тому +4

    Dziko ndianthu osati ndziko ndiachakwela ndi ndondocha zao ayi

  • @petertaulo8014
    @petertaulo8014 Рік тому +1

    Komadi Chakwera must step down.

  • @robertrichman9376
    @robertrichman9376 Рік тому +2

    Chakwera watikwana

  • @gracechiumia7103
    @gracechiumia7103 Рік тому +4

    Chakwera ndi chipani chake chichoke boma

  • @usumanidaudi
    @usumanidaudi Рік тому +1

    Ndiposo musabwerere mbuyo chipurumuso chathu ndinuyo busa ameneyo achoke chakwera akutipha ifeyo amarawi

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 Рік тому

    Ok ok ndaitolera

  • @MikishoniMajuri
    @MikishoniMajuri Рік тому +2

    Kunena zoona Chakwela watikana ndi akuchita atule pasi udido basi

  • @princedetbozsmallboy1749
    @princedetbozsmallboy1749 Рік тому +2

    Achokedi galuyu

  • @AllieKaisi-je6rm
    @AllieKaisi-je6rm Рік тому +2

    Aphulesidenti alephera kuyendesa dziko muzit chocho

  • @giftmasenti5732
    @giftmasenti5732 Рік тому +1

    Ine cheteeee Kuma stand 🤣🤣🤣🤣

  • @PreciosNdlovu
    @PreciosNdlovu Рік тому +2

    chakwera out out out.anthu akufa ndinjala

  • @AhmedAli-l3l6t
    @AhmedAli-l3l6t Рік тому +1

    Malawi ikuvutika chifukwa cha munthu mmodzi, achoke basi ife tatopa naye

  • @gladysbonongwe1038
    @gladysbonongwe1038 Рік тому

    Following

  • @HanishaissahKagansa
    @HanishaissahKagansa Рік тому +2

    We don't need chekwela whatever hi are his must know that the malawian people we don't need him

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj Рік тому

    Anthu onse ali kumeneko pa nyapawo ndi amene akuzuza Anthu osauka

  • @FelesiNkhuza
    @FelesiNkhuza Рік тому +1

    Koma kumeneko !!!!!!

  • @ThoccoBondo-mx7vt
    @ThoccoBondo-mx7vt Рік тому

    😂😂😂😂😂 Chakwera

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 Рік тому

    Za liti izi kodi

  • @AllieKaisi-je6rm
    @AllieKaisi-je6rm Рік тому

    Kodi aphungu nonse ndinu amisala kapena akuyankhula kuti minster wasowesa ndalama? Nanga ngat ili nduna yasowesa ndalama achoka bwaji president.ife tizimva kuti president atule pansi udindo chifukwa pamalawi zithu sizili bwino

  • @idris6597
    @idris6597 Рік тому

    Achoke nyani ameneyu watikwana

  • @ElijahChikwakwa
    @ElijahChikwakwa Рік тому

    Koma chakwera ndiokakamila paliponse akukanidwa koma asangozisiya zinthuzi

  • @babranzima8120
    @babranzima8120 Рік тому +1

    Accokeek ndithu

  • @haliluanusah5090
    @haliluanusah5090 Рік тому

    Aaaaaa kwavutadi

  • @TomatoKabichi
    @TomatoKabichi Рік тому +1

    Mulungu yakhan gulu la anthu asat Munthu chakwela achoked

  • @ElizabethKazambwe
    @ElizabethKazambwe Рік тому

    Tapangani zothekera abale anthu athatu kumudziko ndi president ameneyu

  • @shayrafernandeslatif9556
    @shayrafernandeslatif9556 Рік тому +3

    Boma ndi anthu

  • @CJAY-kx7eu
    @CJAY-kx7eu Рік тому +1

    Achok bas galu ameneo

  • @andsenJeke
    @andsenJeke Рік тому

    Atulu atikwana bwanawa ndinachoka ku Malawi pano nduvutika ku rsa kuthawa kwathu komwe

  • @andrewmwale1912
    @andrewmwale1912 Рік тому +1

    Akhalepo ndani agalu inu

  • @StainGondwe
    @StainGondwe Рік тому

    Ose ndi mbuzi kuparimetiko agalu

  • @fredrickkabuwe9908
    @fredrickkabuwe9908 Рік тому

    Zaliti izi?

  • @ChancyNguluwe-fi5eq
    @ChancyNguluwe-fi5eq Рік тому

    Wafumepo uyo

  • @moffatsoko8547
    @moffatsoko8547 Рік тому

    Achoke amenyi angalole athu azivutika

  • @JohnChibalo-wf8gr
    @JohnChibalo-wf8gr Рік тому

    Palibe kuchitira mwina tisakhalire usiru chakwera wautali

  • @IdrissahChuma
    @IdrissahChuma Рік тому

    Kkkkkk aziona

  • @MickeyJustine
    @MickeyJustine Рік тому

    Ndinchanizo

  • @SafariBvumbwe
    @SafariBvumbwe Рік тому

    Uyu aziwona

  • @LesterTchaka-rl1tg
    @LesterTchaka-rl1tg Рік тому

    Komano mutu wankhani ndizimene zikukambidwa zikusiyanatu mmmm amalawi tiyeni tidzinena chilungamo

  • @MussahImulan-yp4fs
    @MussahImulan-yp4fs Рік тому +3

    Haha 🤣 achoke

  • @dawoodissah1611
    @dawoodissah1611 Рік тому

    Chitsiru ichi chakwera chimangoyendayenda kuwononga ndalama ya amalawi kulibe chomwe amakaphulako kupatula kukajambulitsa ma pictures basi.

  • @rhodahjere8747
    @rhodahjere8747 Рік тому

    Chakwera ndi galu mbuzi

  • @innocentissah2636
    @innocentissah2636 Рік тому

    We can intrupt that blood fucken manyakanyaka a president, mbava yachabe chabe

  • @kondwamlungu8384
    @kondwamlungu8384 Рік тому

    Koma Malawi tifapotu apa

  • @bernardchithumba6040
    @bernardchithumba6040 Рік тому

    Ma MP nonse ndiinu zitsilu kwambiri kodi mwa nonse palibe emwe angathe kutenga u president wo kuti tione zina? Chakwela watikwana ndipo sitikumufuna nso and had it been that am one the MDF Chakwela mkadashuta ndi mfuti,,,,,,,,,,sadalowe ndi mphamvu ya mzimu oyela koma satanic way

  • @YUSUFUALI-u8j
    @YUSUFUALI-u8j Рік тому

    MP onse mbudzi za anthu mwatikwana sopano

  • @joicemartin-ji5zu
    @joicemartin-ji5zu Рік тому

    Ine ndiri ndi. Funso ??Kodi ladzaro chomwe amalowera uprezdent ndi chani ? Kodi padzaka zitatu zomwe iye mwini amati ndi prezdent anayamba wayankhula speech yomveka Anthu mkudziwa kuti prezdent sayakhula ? Kodi ladzaro unalidi mbusa wa anthu abwino bwino kapena unalidi mbusa wapansi pa nyanja ? Chifukwa chani sukumva chisoni Ndi mmene amalawi akuvutikira Ambuye mukantheni ladzaro ndi lupanga

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 Рік тому

    Zakalekalw

  • @DoricaGoweka
    @DoricaGoweka Рік тому

    Chakwera must go! Corrupt president.

  • @Haricemaseko
    @Haricemaseko Рік тому

    😂😂😂

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 Рік тому

    Chakwela osavinidwayi mpaka amulola kukalowaku Saud Arábia, ndiyekwakhwekatu

  • @dallasmwanza
    @dallasmwanza Рік тому

    😂😂😂😂😂😂

  • @danielsulani8689
    @danielsulani8689 Рік тому +1

    😂😂😂