Uthengawu special ukupita kwa abwana a Bakili Muluzi tv

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 4 гру 2024

КОМЕНТАРІ • 29

  • @Adini-d2f
    @Adini-d2f 6 місяців тому

    U speaking true brother my Allah protecte ameni

  • @richjames8707
    @richjames8707 Рік тому +3

    Uthenga waveka bwino uwu ine ndi christian km zomwe amachita azunguwa sizindisangalasa tiyeni tigwilane manja poteteza ufulu wanthu ndife anthu ovutika chifukwa Cha azungu amenewa tiyeni kulikoseko tigwilane manja posayang'ana chipembezo 🇲🇼🤝🤲

  • @IshmaelNesta-rb8dx
    @IshmaelNesta-rb8dx Рік тому

    Uthengawu nde uli bwino sheikh...ndayamika chifukwa Cha mau anu achilimbikiso ndiponso aumodzi...👏👏

  • @ishmaelbilali574
    @ishmaelbilali574 Рік тому

    That's true bro,good advice

  • @GILBERTMGJMTUMBULAH
    @GILBERTMGJMTUMBULAH Рік тому +1

    Masukani mukufuna azinena kuti bwanji inuyo
    Ku DRC kuli maguru ochuluka amatchedwa zigawenga Mozambique nakoso amati kuli maguru ochuluka amatchedwa zigawenga chifukwa si asitikari aboma
    Ndeinuo ndandaulo lanu ndilozizira ngakhare Ari ngati omenyera ufulu komabe ndizigawenga chifukwa sigulu la boma.....
    Kupembedzana eti 😂😂😂

  • @chauncychauncy1683
    @chauncychauncy1683 Рік тому +1

    palibe chanzeru chayankhulidwa apa,zaziii zen zen🙄

  • @InnocentEdasi-n5z
    @InnocentEdasi-n5z Рік тому +1

    Taninane zonveka bwinobwino inu kd chavuta ndiyani apa, . asimuh musamasankhe kukhala uvuta inu

  • @KenesiDaitoni-ob5st
    @KenesiDaitoni-ob5st Рік тому

    Chiganizo Ichi sheQ sindikugwirizana nawo zigawenga zambiri zikuchuidwazo zachoka kuti malume muri ndiudani omwe mukuxiwa inuyo kwa bakili muluz

  • @thokoJames-gp8mk
    @thokoJames-gp8mk Рік тому +1

    zaziiiii

    • @Mrdkmw
      @Mrdkmw Рік тому

      Zopandazo Mazi ayiniyakhe channel yii ndigalu kwambili iyeyo sakufeseza pathi mbuziyamundu😂😂😂😂😂😂

  • @AndrewDeeBastola-q6j
    @AndrewDeeBastola-q6j Рік тому

    Ambri

  • @OwenNyangu-nv1yt
    @OwenNyangu-nv1yt Рік тому

    Akubwela khasu kwamwini Mundaanaziyamba athanenazo. Adalila nyanga yamsatsi iwafotera mmanja

  • @adamusaidih8570
    @adamusaidih8570 7 місяців тому

    Km uyu akukamba chulungamo

  • @jamesmfune8448
    @jamesmfune8448 Рік тому

    Zaveka ndithu

  • @KenesiDaitoni-ob5st
    @KenesiDaitoni-ob5st Рік тому

    Ndiye zomwe musakuvesa ndiziti

  • @EkraihgiffiMoffat-e3j
    @EkraihgiffiMoffat-e3j Рік тому

    Inuyo tangokozani ubale wanu ndi mulungu basi

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete Рік тому +1

    ❤ zoonadi zimenezo isha Allah

  • @adamusaidih8570
    @adamusaidih8570 7 місяців тому

    Gyz taganizani azungu amamenyana ndiathu achilunga km simungaone akubwela kno ku African kuzamenya khodo amaziwa kt ndife zisilu

  • @Gabriel-ff7pn
    @Gabriel-ff7pn Рік тому

    Kodi zigawenga ndi aliyense Kumbali ya zipembezo

  • @AliNtolera
    @AliNtolera 5 місяців тому

    Fotseki iwe iwe ndi mwarabu wokuda ngati iwe. Iwe ndi mu Africa zikukukhuza Pati a anena bwino zigawenga zachisilamu chifukwa chisilamu ndi chobwera fitseki

  • @NoahKalima
    @NoahKalima Рік тому

    CHISILAMU ndnkhondo,, asilam anakaiyamba okha nkhondo ,akuyenela amenyedwe aphedwe

  • @lastonekaponya7675
    @lastonekaponya7675 Рік тому

    Ife sitingakonetsere a slamu munachita kuwayamba akumalizeni kumene

  • @FrederickFbandah
    @FrederickFbandah 6 місяців тому

    Ndimene amanenela okha polankula kut athu adziwe athuonse

  • @lastonekaponya7675
    @lastonekaponya7675 Рік тому

    Nkhani ya ku Israel ndi gaza munachita kwayamba nokha kutengera mutsiku larero akumalizeni kumene

  • @Moses51
    @Moses51 Рік тому +1

    Zoonad

  • @Malani41
    @Malani41 Рік тому

    So what did Bakili Muluzi channel say that you disagree with? You seem to be collaborating with everything that he said but you think that you are saying something different. Why not find your own topics and go with that? Translation of Rebel is Chigawenga. Rebel is not necessarily a bad word.

  • @RodrickKansadwa-ji8wp
    @RodrickKansadwa-ji8wp Рік тому

    Man mkulu ndi odzerezeka osamunyengerera palibe chanzeru amakamba uyu ameneyu akanakhala wanzeru bwezi akumabwera poyera ,mtayeni opoira uyu

  • @NKHANTV
    @NKHANTV  Рік тому

    Chonde osayiwala kupanga subscribe ❤