KHALANI OKONZEKA PA 23 NOVEMBER PANSEWU BASI, CHAKWERA ACHOKE

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 5 гру 2024
  • #nkhanitv #chakwera #chilima

КОМЕНТАРІ • 159

  • @NKHANTV
    @NKHANTV  Рік тому +7

    Hello
    Takulandirani pano pa NKHANI TV
    Chonde osayiwala kupanga subscribe
    Ngati mwapanga kale , mulungu akudalitseni

    • @MaxwellBanda-xd6oh
      @MaxwellBanda-xd6oh Рік тому

      Chakwela achoke pampando akuluakulu chonde mulungu akudaliseni dziko lamalawi koma zonsezi chifukwa cha Chakwela tiyeni tonse panseu timenyele nkhondo anthu osauka

    • @alexfredrickmkandawire5222
      @alexfredrickmkandawire5222 Рік тому

      À/.0)00000) for

    • @Falesibandason
      @Falesibandason Рік тому +1

      Ok plz I said that I want number of mother joice Banda i want Mai joice Banda 2025 ayimilile osati achina Peter ndi achilima ine ayi ayi ayi ndikuti ayi

  • @HamidahshaibuHamidah
    @HamidahshaibuHamidah Рік тому +2

    Mulungu akhale nanu pamene mukupita pansewu,,ndipo chilichonse chikhale chotheka kuti malawi 🇲🇼 wathu atuluke muchipululu chimenechi in the name of God 🙏🙏🙏

  • @TrynessPhiri-bz9yu
    @TrynessPhiri-bz9yu Рік тому +7

    Mpaka pa 23 konseko osati mawa bwanji😢😢

  • @simonpaul6567
    @simonpaul6567 Рік тому

    This is good speech brother

  • @TobiasFanuel-ch6mb
    @TobiasFanuel-ch6mb Рік тому

    Powerful massage

  • @frankkaipa8925
    @frankkaipa8925 Рік тому

    Opo ndiye wanena zina la chakwela likupasa manyazi kulitchula kumayiko anzathu

  • @FunnyKatchenga
    @FunnyKatchenga Рік тому +2

    That's true my brother, you're welcome.

  • @ThokiseWiriyam-ws1ec
    @ThokiseWiriyam-ws1ec Рік тому +1

    Ameneyi watikwana mbava yachabechabe

  • @SostenKalumo
    @SostenKalumo Рік тому

    Chakwera achoke mu2 oyipa hvy

  • @joicemartin-ji5zu
    @joicemartin-ji5zu Рік тому +2

    Bwanji osangomuudza cakwera kuti asafikire ku state house ayangane kofikira

  • @simonpaul6567
    @simonpaul6567 Рік тому

    Wa traffic yo achoke sitikumu funa he must go

  • @alexjeremanuel2541
    @alexjeremanuel2541 Рік тому +1

    Mademo akuyenera kuchitika Blantyre, Lilongwe, Mangochi ndi mzuzu

  • @JamesPhiri-y7k
    @JamesPhiri-y7k Рік тому

    Mmmmmmmmm guyz ili ndivuto ladziko lonse lapansi even here south Africa anthu akubangula mokweza, so poti stima imapweka akamayendesa wina!

  • @AndrewInnocent-he8gs
    @AndrewInnocent-he8gs Рік тому

    Kuimbila kanyimbi mmanja from kasya Lilongwe

  • @omanm2919
    @omanm2919 Рік тому

    Good speech brother, in 23 we need come out to demonstrate Malawi is crying 😢😢😢😢

  • @JannatuHassan
    @JannatuHassan Рік тому +2

    Mpakana 23 kalindo akut. Week yammawa. Kuyambira loremba. Alipo Moto kutbooooo🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @AmoniCVwalika
    @AmoniCVwalika 11 місяців тому

    😅 good

  • @RodrickKansadwa-ji8wp
    @RodrickKansadwa-ji8wp Рік тому

    Umbuli uwu kodi ndalama mkoyamba kugwa?ngati mukufuna peter osantenga kupanga dziko lanu bwanji ?

  • @collennyadile8179
    @collennyadile8179 Рік тому

    ndipo mukunena zoona tonse amene tinkapanga support chekwera ndi chilima mulungu atikhululukire chifukwa anthuwa ndi nthumi za satana zutumidwa kuzawononga dziko lathu mcp ndichipani chamatembelelo

  • @RAJABUALLIE
    @RAJABUALLIE Рік тому +3

    Pa 23 kwatalika konseko eshhh Malawi salibwino uyu😢

  • @joicemartin-ji5zu
    @joicemartin-ji5zu Рік тому +1

    Acoke acoke acoke ladzaro woipa wasatanic

  • @KasimuKk
    @KasimuKk Рік тому

    Tiyeni khumademo khoko

  • @Falesibandason
    @Falesibandason Рік тому

    Ine mungonditumizila nambala ya Mayi joice Banda or nambala ya Amuna awo Ananda ine ndiwapemphe azayimile I president 2025 plz osati pamene zafikapawa ayi dzina langa ndine Lenard msukwa

  • @GiftFrancesco
    @GiftFrancesco Рік тому +1

    Please gyz tiyen tigwilane manja ndkuvakuwawa Malingana Nd mziko lamakolo Anga tiyen pansewu please

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule Рік тому

    God u my brother

  • @sgemshane3645
    @sgemshane3645 Рік тому

    Koma chimanyera chinyau chimenechi

  • @DavidPeter-z4s
    @DavidPeter-z4s Рік тому

    Kkkk koma bwana Inu kkk oky

  • @phillimonzgambo1663
    @phillimonzgambo1663 Рік тому +1

    The problem is the demos leaders some need money from the government , you start powerful
    The moment you start slow which bad

  • @alexjeremanuel2541
    @alexjeremanuel2541 Рік тому +1

    😂😂 😂 my brother you're number one and it's obviously that those ones supported Chakwera are the wicked

  • @ajasikalonga3210
    @ajasikalonga3210 Рік тому +1

    Komanso chakwera afa posachedapa

  • @marydaka512
    @marydaka512 Рік тому

    Asilikali kodi mulikuti? Anthu avutika mungowona , coup bwa?

  • @isaackinod1256
    @isaackinod1256 Рік тому +1

    Tiyen tilapedi tinachita mistake yaikulu

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu Рік тому

    Brother, tisanakhalepo ndi President ngati chakwera, President wopanda nzeru, chitselekwete, chidantanta chamunthu, mmmmmm Malawi wathadi. Chakwera wadya zomwezi.

  • @alexjeremanuel2541
    @alexjeremanuel2541 Рік тому

    Nkhani ikhale yoti iyeyu atule pansi udindo komanso onsewa amangidye kapena aphedwe tiwadyere nsima

  • @moseskavalo3304
    @moseskavalo3304 Рік тому

    Amwene ku Malawi kuno vuto ndi corruption basii,, kupita kumsewu opindula amakhala ochepa,, kunoko churches don't help us bringing godliness to our country

  • @AndrewDeeBastola-q6j
    @AndrewDeeBastola-q6j Рік тому

    ✊✊✊

  • @HamidahshaibuHamidah
    @HamidahshaibuHamidah Рік тому +2

    Asilikali athu ndiwopusa kwambili,,anzawo akulanda boma mayiko anzathuwa koma ife amalawi kuli ziiiii agalu achabe chabe

  • @KenChitete-pg3ws
    @KenChitete-pg3ws Рік тому +1

    In Malawi we don't have a leaders,,,atupele muludzi he can't be a leader even saulos chilima all of them are the same,,, because now is chakwela and same one he thinks like him can be a good leader,,, please Malawian people don't sale your life because of small things those people berging you to go to demonstrations is making money on top of your heard please my fellow Malawian don't allow them to using you like a machine.

  • @RobertMhango-y2t
    @RobertMhango-y2t Рік тому +1

    Aaaà mpaka pa23 mukungofuna ndalama basi kuti ena akupaseni basi osanena kuti week ya mawa bwanji

  • @innocentissah2636
    @innocentissah2636 Рік тому +2

    Ofunika nduna zina kuziombera zizisowa ngati maiko anzathuwa.

  • @KhimzyMike13
    @KhimzyMike13 Рік тому +1

    Mawu sakuvekatu boss

    • @NKHANTV
      @NKHANTV  Рік тому +1

      Tayeseraniso
      Ndapanga Chek ikuveka

    • @VenançioZocueza
      @VenançioZocueza Рік тому

      Iwe malawi watch watha dziko lonse lapansi likudziwa.mvetsa mwene

  • @KenChitete-pg3ws
    @KenChitete-pg3ws Рік тому +2

    A Malawi musakhale mbuli,,,athuwo asakugwiliseni tchito ya ulele ndalama akudya wokha,,,kumademo kuli zochitika zambili mutha kukaludza moyo wanu zithu zopanda pake,,,ine sindidzayiwala abale anga amene anamwalila ku nzuzu chifukwa cha mademo ndipo sikuti ndidzawaonanso ayi plz otsapita ku mademo,,,ngati tikufuna titchose president tili ndi Asilikali athu amene akagwilidzana ndi amatchalichi atha kutchosa president otsati athu adzipita kunsewo ayi.

  • @ajasikalonga3210
    @ajasikalonga3210 Рік тому

    Me i don't know who is the president of Malawi .

  • @GiftPhiri-nn9kb
    @GiftPhiri-nn9kb Рік тому

    Yes madala apo mwanena chilungamo chakwera simnthu ndigalu or garu angamupose zeru it’s very stupid also chilima

  • @samchibenene4458
    @samchibenene4458 Рік тому

    Achakwera anthu akakunyozani chonchi iii mlibe manyazi turani pansi udido basi

  • @gracechiumia7103
    @gracechiumia7103 Рік тому

    Chakwera must go

  • @JackMillicent
    @JackMillicent Рік тому

    Chakwera anabera mavuti chifukwa mavoti savotakawili

  • @MariaSingini-pp9ov
    @MariaSingini-pp9ov Рік тому

    Chakwera apa aaaaaaaa

  • @omarajibu860
    @omarajibu860 Рік тому +1

    Yense anavotera izizi ndiopanda nzeru

  • @MoosaSame
    @MoosaSame Рік тому

    Galu ameneyu ndimanyazi omwe alibe chakwera ndi gututu inu chokodzeramo

  • @patrickkhomba3446
    @patrickkhomba3446 Рік тому

    Kuyankhula kopanda mzeru kumeneko mukuganizakuti panopamutasankha munthu wina ndiyendalamaikwera? Haaa mukunamatu inu asiyeni achakera akudziwa chimeneakuchita kunyozako mudzinyoza mukudziwakuti mutha kukwanitsa

  • @priscaleofranknakari3117
    @priscaleofranknakari3117 Рік тому

    vuto la amalawi mantha kwambiri amapezeka kuyamba ma demo then akalindo apolice akangowatenga mademo akuthera pomwepo why not anthu osalawo akupitiliza kodi amakhala mantha kapena chani?

  • @HumeyaAnussasahid
    @HumeyaAnussasahid Рік тому

    Chakwela ndinfiti

  • @JohnChibalo-wf8gr
    @JohnChibalo-wf8gr Рік тому

    God bless you

  • @martinnyirongo2892
    @martinnyirongo2892 Рік тому

    Azibusa a mumalawi ndi anthu awoopsa kwambiri, mwawona nokha, don't try again kutenga mubusa kumuika pa usogoleri wau president.

  • @FunnyKatchenga
    @FunnyKatchenga Рік тому

    You're talking ❤

  • @bernardchithumba6040
    @bernardchithumba6040 Рік тому

    Chakwela akachotsedwa pa udindou obwelawo please adzalande ma account onse a Chakwela, ana ake onse ndi chilima, vitumbuko Mumba ndi nduna zonse ndalama za onsewa zidzabwerere ku boma la nthawi yo because awa aba movuta than all

  • @husseinmoffatt
    @husseinmoffatt Рік тому

    Sim busauyu nkhwoyake mbamva

  • @YasiminAdamuzey
    @YasiminAdamuzey Рік тому

    Malawi siilibwino tilikoko wausilu chakwela mbolo yache

  • @DaytonIsumaira
    @DaytonIsumaira Рік тому +1

    Chakwera machende ake

  • @jalisuman6073
    @jalisuman6073 Рік тому

    Mbu ya President ngati iyi sinayi wone akulamulidwa ndi azungu aku America i think amawanyenga kokhalila azungu mosakayika. Tikumawona mma media Azungu askumachita kunena kuti Malawi is for sale😢😢😢😢😢😢😢

  • @CharlesBanda-ek9ru
    @CharlesBanda-ek9ru Рік тому

    Alikuti mtambo timoswe, who is you?

  • @ChifundoBeston
    @ChifundoBeston Рік тому

    Zinazi tizinena zoona, kugwa kwandalama sizitanthauza kuti boma lalepherayi galu iwe Siya kuuza mabodza anthu. Mavuto tikukumana nawowa sichokwa cha Chakwera ai. Ndichifukwa cha amaliseche akumwera anaononga dziko lino. Pomaliza ife amalawi sidya pa kuyenda panseu. Naweso imfa yako izakhala iwawa kwambiri

  • @JaneMoyo-ws2di
    @JaneMoyo-ws2di Рік тому

    Musatikumbuse Bingu wa Mtalika MHSRIP. Abwino sakhalitsa eee mh

  • @thesocietynews3181
    @thesocietynews3181 Рік тому

    MAVUTO ALIPO PA MALAWI. CHISANZO, NGATI MUNTHU ANALI NDI 1 MILLION KWACHA KU BANK LAST WEEK PANOPA ALI NDI 556,000 KWACHA MPHAMVU YAKE KOMA FIGURE NDI 1 MILLION. NGATI ANALI NDI 100,000 KWACHA KU BANK NDE KUTI PANOPA ALI NDI 56,000 KWACHA YOKHA BASI. SHAME ON CHAKWERA AND CHILIMA.

  • @AndrewMandala-yz8ri
    @AndrewMandala-yz8ri Рік тому +1

    Aaaaaa inu 23 kwatalika osanena kuti Monday li bwanji

  • @KenChitete-pg3ws
    @KenChitete-pg3ws Рік тому

    Inuso mukufunapo ndalama pamenepo sikuti mukuthandidza ziko ayi,,,amalawi musalole kulemetsa athu ena chosecho anzanu akupanga ndalama.

  • @benkamanga-mn9dh
    @benkamanga-mn9dh Рік тому

    Ndikanapita Ku mademo koma iweyo nawe wunene komwe watenge ndalama zopangela mademo chifukwa nanu oipa anthu opanga mademo

  • @MajidKasim
    @MajidKasim Рік тому +1

    Chisilu chamunthu chakwela

  • @RhodaTembo-s6k
    @RhodaTembo-s6k Рік тому

    Achoked ameneyo

  • @HusseinKachala-ml7ut
    @HusseinKachala-ml7ut Рік тому

    Akulu ndathokoza chifukwa chamfundo zanu zabwino, timafuna anthu ngat Inu kumalawi kuno, anthu olimba mtima komanso oyima pachilungamo.
    Komano ine ndili ndifunso, munthu amene akusogolela mademoyo yemwe dzina lake ndi kalindo, last week anakapanga nawo meeting ndi aboma ati yakayendesedwe kachuma chadziko kusalima, now after two days kwacha yathu yagwa, funso mkumati,
    kodi kusama kunapitideako amakakambilana zogwetsa kwacha?
    Nanga mademo amene akusogolela kalindo ndi azimzakewa, akhala aphindu bwanji popeza kalindoyo alimbali yaboma?

  • @mcdonaldchipesu6437
    @mcdonaldchipesu6437 Рік тому

    Let Jesus Christ come and all Will be over

  • @RasshidMadi
    @RasshidMadi Рік тому

    Koma zoona anangoona atakhsla President wa dziko la Malawi

  • @AndisonSaidiKhunjuh
    @AndisonSaidiKhunjuh Рік тому

    Ukungoveka ngati kt ndiwe wa ku Mozambique

    • @VenançioZocueza
      @VenançioZocueza Рік тому

      Let us visualize it well,if he is a foreigner, or not.

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm Рік тому

    Bambo Chakwera tabwerani poyera mutiyankhule ntundu wa a Malawi .

  • @LaynaAdam
    @LaynaAdam Рік тому

    Chakwela ndi galu akukhala ngati sanabadwe kwa munthu galu wakenso wachiwewe akufuna alume a malawi tonse galu ameneyu

  • @Yahiya-wm8nd
    @Yahiya-wm8nd Рік тому

    Guys mademo amafunatu ndalama tiyeni athuwa tidziwavesa pena

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule Рік тому

    Amen

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule Рік тому

    Zoona big man

  • @Georgephiri-l7x
    @Georgephiri-l7x Рік тому

    Sichakwera ayi kumawrlengako buku lopatulika pang'ono udzasiya zimene ukunenazo

  • @andrewmwale1912
    @andrewmwale1912 Рік тому

    Tibwera tikakupangiren salary agalu inu popanda ife sangakupatsen ndalama mabungwe.akapolo inu

  • @husseinmoffatt
    @husseinmoffatt Рік тому

    Zoonadi galuameneyu achoke pwalalake achoke zamanyi bas

  • @Goliath461
    @Goliath461 Рік тому +1

    Ulendo uno si wakukenani koma wa ku Ukraine 🇺🇦 😭

  • @triza.kamwanjatalandira446
    @triza.kamwanjatalandira446 Рік тому

    Kkkkkkk mademo ndaamenewo muzikapita kwachakwera yemweyo osati muzikathyola mashop anzanu omwe nawonso akulira

    • @KenMasta-w6c
      @KenMasta-w6c Рік тому

      We are against the dog chakwera not our fail brother and you will see him down now

  • @AnoldKapolo
    @AnoldKapolo Рік тому

    Kutereku akutumani, shaaa mukalamkhula choncho basi akulipirani mkumadya kunjako Muli tilukani tipite pamsewu, aahmwauponda chakwerayo 2030 woo. Ife takana sitipanga nawo upange ndi ana Ako Kuti akakakulipirani okutumaniwo kwacha O'Keefe mphamvu manga siinu madolo

  • @starlonJames-qr4xl
    @starlonJames-qr4xl Рік тому

    chidule chakwelayo kwapitaiyeko asabweleso kuno kd ameyanthu ilikuti ee zoona ife amalawi tikuvutika pomwe chitetezochanthu ngati tilibe km sizona uyu achoke

  • @StevieTaiza-h2z
    @StevieTaiza-h2z Рік тому

    Kwatalika Kwatalika pa 23

  • @JusticeKawilira
    @JusticeKawilira Рік тому

    Guys ingolimbani mitima za mademo mukungonena mukangogendedwako kumeneko panopa apolice ndi anyamata a MCP ali ready kulepheretsa mademo

  • @ajasikalonga3210
    @ajasikalonga3210 Рік тому

    Zopsetsa mtima galu ameneyu Chakwera

  • @lamecknyadani1905
    @lamecknyadani1905 Рік тому

    Simuli serious... Ma demo mpaka 23 November, kutali konseko??? Mukanakhala serious ma demo amayenela kuchitika next week Wednesday.... Munthu watimenya bagela lero inu nde mukufuna muzabwenze after 1 month

  • @MaxwellBanda-xd6oh
    @MaxwellBanda-xd6oh Рік тому

    Chakwela achoke pampando akuluakulu chonde mulungu akudaliseni dziko lamalawi koma zonsezi chifukwa cha Chakwela tiyeni tonse panseu

  • @Pangolinimw
    @Pangolinimw Рік тому

    ❤❤❤❤💪💪💪💪💪💪

  • @sylvesteralfred8355
    @sylvesteralfred8355 Рік тому

    Zoona mpaka pa 23 konseko kwatalika aaah guys bwanji osangoika week yomwei bwanji

  • @LionZion-u9k
    @LionZion-u9k Рік тому

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 Рік тому

    Paja ananena kuti ndi wa traffic 😂😂😂

  • @alicehananiya
    @alicehananiya Рік тому

    Ndipo chakwela asowe mwa changu asafukilenso Ku steti house sinyumba yokhala Bulutu ngat ameneyo achoke

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 Рік тому

    Kutsegula Admarc kenako kuyitseka pasanachite operation iliyone ,koma abale chipongwe

  • @harrymicah6140
    @harrymicah6140 Рік тому

    😂😂😂😂 eeeee kusabwaza

  • @Georgephiri-l7x
    @Georgephiri-l7x Рік тому

    Iwe ndi wabodza khalaphe iwe sungathe kuyendetsa dziko

  • @KenChitete-pg3ws
    @KenChitete-pg3ws Рік тому

    Kugula box la malilo sikuti ndikugula moyo wamuthu ayi,,, abale athu anamwalila ku nzuzu chifukwa cha mademo omwewo ndipo forever sadzaonekaso kale lonse pano mukufuna kuti tiludzeso ena,,, ayi zimenedzo sidzitheka pitani ndi ma family anu ku mademo

    • @LastonMmanga-r2u
      @LastonMmanga-r2u Рік тому

      Pantumbo pako mwana wa hule Bola ukanangokhala without comment PAm' nyero!!!! 😢