CHIFUKWA CHIMENE CHAKWERA WAPITIRA KU SAUD ARABIA KOMANSO ZOONA ZENIZENI ZAKUTSIKA KWA KWACHA

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 4 гру 2024

КОМЕНТАРІ • 38

  • @NKHANTV
    @NKHANTV  Рік тому +2

    Hello
    Takulandirani pano pa NKHANI TV
    Chonde osayiwala kupanga subscribe
    Ngati mwapanga kale , mulungu akudalitseni

  • @EffieSibande
    @EffieSibande Рік тому

    OK ok

  • @joicemartin-ji5zu
    @joicemartin-ji5zu Рік тому

    More fire Mr nan longwe

  • @musician.426
    @musician.426 Рік тому

    Bakili muludzi news is the Best.

  • @HusseinKachala-ml7ut
    @HusseinKachala-ml7ut Рік тому

    Ben Longwe, phawawa phanyenye mkolongo!, Umatiimilila brother along side Munlo, u r indeed our heroes, not bon kalindo, bon kalindo ndimthira kuwiri and ndiwa mcp

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm Рік тому

    Kumayankhula mwachindunji kuti mutu wa nkhani udzidziwika . A Ben Longwe ingobwerani mudzidzatokotera konkuno ngati mumaimira pa chilungamo .

  • @mariochris7199
    @mariochris7199 Рік тому +1

    welcome back bro 🇲🇼🔥✊

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn Рік тому

    True ,ndalamazo tilandira koma kuvotera mcp ndie kuphwambanatu

  • @yohaneluciano1949
    @yohaneluciano1949 Рік тому +1

    Muli ndi mfundo zabwino,vuto mukukuwira kutali ndipo pawindo nde ife sitikukutengani kukhala aphindu kwenikweni

  • @generouszimpita5959
    @generouszimpita5959 Рік тому

    Zaziii.. Ndye mukwezeso malipilo anthu..

  • @PabroOwen
    @PabroOwen Рік тому +1

    Chitsiru chakwera wamva?chiyambi ndimathero chakwera now chitselepwete

  • @DaudBonomali
    @DaudBonomali Рік тому +2

    Koma abe chakwela sangaone chitsanzo cha Ibrahim trioe waku bokina fanso ndi mwana kuyelekeza ndiza ndi chakwela mwana ameneyu akupanga zakupsya mdziko lake koma awa ango nyeranyeramo m'bomamu moti ena kamalowa peza manyi okhaokha

  • @HusseinKachala-ml7ut
    @HusseinKachala-ml7ut Рік тому

    Panopa our heroes kumalawi kuno ndi Munlo and his friend Ben

  • @malawijohn5297
    @malawijohn5297 Рік тому +1

    Muzifulumila kufika pa point yomwe mwabweletsa kuti zisamabowe kumvela please

    • @DoYouKnow3838
      @DoYouKnow3838 Рік тому

      Eti, kungozungulira uko koma mfundo imodzi. Bolaso Born Kalindo 🙌

  • @HusseinKachala-ml7ut
    @HusseinKachala-ml7ut Рік тому +1

    Kumangogona tulo kuparliamentko chikhalilenicho mukudya misonkho yathu agalu inuu

  • @hudsonkawinga685
    @hudsonkawinga685 Рік тому +1

    Tugambeje kutama mwakwe nda

  • @MatiasPiloti
    @MatiasPiloti Рік тому

    Bwana tukupangani sapoti, mumakhula zowona,zomwe anakakambilana kusalima zachitiladi

  • @ShupiMakwinja
    @ShupiMakwinja Рік тому

    Mbuli chakwera iweee galu kwabas wamamuna mutu iweee kumen ulko umve

  • @daviekamanga1417
    @daviekamanga1417 Рік тому

    nkhani ndikugwilana manja kuti tithane ndi umphawi zokamba sitingapange phindu

  • @umalimaganga
    @umalimaganga Рік тому

    Kodi mesa unkati wasiya kuyankhula iwe? Nanga you are talking about Bon Kalindo iwenso ndiwozungulira mutu pita uko

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda9830 Рік тому

    Ndipo usavege weniweni

  • @nditumenichagunda4192
    @nditumenichagunda4192 Рік тому

    Telela nyani umakwana kalindo ndi mbava

  • @NELSONFERGUSON-j5w
    @NELSONFERGUSON-j5w Рік тому

    Tiyen tisalimbane tokha tokha mukaona kut muthu wamugululanu akupangachinyenge osatukwanana

  • @happinesskamwendo2106
    @happinesskamwendo2106 Рік тому

    But y chakwera ingotulani udindo aaaaaa

    • @andrewkiwombwe8895
      @andrewkiwombwe8895 Рік тому

      Alibe oro manyadz amwene even this guy he is coming with no sense speech telling us that what chakwera he is doing is wrong while even him is in that fuckin gvmt ,am talking about chilima , chilima plz don't even think that Malawia are going to hear that nonsense Yu r talking about, just know that Malawia the don't need Yu and chakwera anymore fuck Yu guys it's enough shupiti,, ,

  • @BathromewsChimbwandira
    @BathromewsChimbwandira Рік тому

    Aise vuto umatokota uli kunja osabwela kuno bwanji tizakhale limozi tizaonese kwiyo

  • @LqdexiDexi
    @LqdexiDexi Рік тому

    Iweyo tilibe nawe ntchito koma bon kalindo the dc

  • @HusseinKachala-ml7ut
    @HusseinKachala-ml7ut Рік тому

    Inunso osusa bomanu ndizitsiru kwambiri, mukungoyang'nira zinthu zikulakwika mmalawi muno, mukungovomeleza ma bill opusa mkumadusa kuparliamentko, opanda osutsa kuopa kumangidwa eish!.
    Osamachangamuka ngati Julius Selo Malema wapa South Africa' pa bwanji?.

  • @YollamMphande-yj7oe
    @YollamMphande-yj7oe Рік тому

    Malawi will not Malawi in two years coming,

  • @VictoriaKumwenda-k6o
    @VictoriaKumwenda-k6o Рік тому

    Mnati mwalapa machimo mkadali kupyaa muyambiila pompano ndi maboza anuwo

  • @roddiemanase8956
    @roddiemanase8956 Рік тому

    Nkhani ndi inkonome

  • @princemcdonald007
    @princemcdonald007 Рік тому

    Kodi iweyo ndiwe wa chipani chanji? Becz zipani zonse zimene zikukutumazo ndilolephera,a malawi siopusa ai kuti akhoza kumangotsatira kulikonse,mcp,udf,utm,dpp wonse sangasithe zithu pa malawi pano,ndiye iweyo ukufuna kugwetsa mcp ndifuna kubweretsa mbava zina zija ukutaya nthawi,amalawi siungawapangire zochita,more mavuto amene ali kuno umangowavera pa fon,ukutaya nthawi aise

    • @ChikondiNelson-ur2tq
      @ChikondiNelson-ur2tq Рік тому +1

      Point yanu ndiyoti chani bwana?🙄🙄🙄

    • @RobiamShabah
      @RobiamShabah Рік тому

      🎉ai zawonjez

    • @daviekamanga1417
      @daviekamanga1417 Рік тому

    • @princemcdonald007
      @princemcdonald007 Рік тому +1

      @@ChikondiNelson-ur2tq my point is,Anthu ambiri maka kwa iyo amene akhala akuona maboma wonse a democracy,akudziwa mavuto anthu a ndale kuti they are good in speaking koma kupanga zithu 0/10,ndiye my main point is,uyu asamataye nthawi kuwapangira amalawi zochita,amalawi akudziwa kt anthu awa amene amati ndi omenyera ufulu wa anthu ndi wofuna kukhutitsa mimba zawo,we know kt akulandira ndalama zambiri kwa anthu andale ena,ndiye amalawi siopusa ai

  • @HusseinKachala-ml7ut
    @HusseinKachala-ml7ut Рік тому

    Iwe bon kalindo, stop confusing malawians ok!, Kangojowina ndale zako zamatuvizo