Amalawi don't repeat the same mistake, osavoteraso chakwera ay.

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 4 гру 2024

КОМЕНТАРІ • 23

  • @JameGues
    @JameGues Рік тому

    Mtundu uwu unawuziwa kale ndikumuvotelanso eshiii Malawi

  • @EliahLetulo
    @EliahLetulo Рік тому

    Ndipo olo December yomweyi hiyaaa😂😂😂chakwera achoke

  • @JustineWillard-s5o
    @JustineWillard-s5o Рік тому

    Aaaaaaa.zazii inuyo ndindani kuposa court

  • @JustineWillard-s5o
    @JustineWillard-s5o Рік тому

    Mwayiwala.akuru chisankho chidzachitika 2025/pa.16 sepetember.

  • @joicemartin-ji5zu
    @joicemartin-ji5zu Рік тому +2

    Zoonadi zisakho zikhale 2024 ladzaro acoke walephera sakufunika waononga dziko comwe akudziwa kuba kupha ndi kuononga

  • @amabhohlela.3492
    @amabhohlela.3492 Рік тому

    Aaaaah akulu inu,,,mpaka mupite ku Britain Embassy?????kodi tizasiya liti kudalira ma Westerners???kodi Mzunguyo aliwamdzeru kuponsa ma AFRICA ife??bwanji nkhayo muwuze ma AFRICA amnzanu .mpaka kwa Mzungu eish mMalawi ukapolo sunathe

  • @CharlesclusNyirenda-x4k
    @CharlesclusNyirenda-x4k Рік тому

    Kunena zoona madala 2024 tifuna zisankho agalu choke awa

  • @KasimuKk
    @KasimuKk Рік тому

    Chakwela achokhe batsi

  • @gladysbonongwe1038
    @gladysbonongwe1038 Рік тому

    Mau

  • @DoricaGoweka
    @DoricaGoweka Рік тому

    Ndipo zoona zake!😢

    • @mcfordmumbo2083
      @mcfordmumbo2083 Рік тому

      Tikufuna chipani chini osati UDF,DPP,MCP UTM.

    • @mcfordmumbo2083
      @mcfordmumbo2083 Рік тому

      Sukulu ndiyabwino wamoyo ndi omwalila ndi anthu awiri isiyana. Vote 2025.

  • @PaulKwenda
    @PaulKwenda Рік тому

    Zosatheka kumwera komweko

  • @tasmania527
    @tasmania527 Рік тому

    Otsaphatikiza a Malawi ena ayi, ndinu anthu akumwera mukulira ndi zimenezo.

    • @osmanmailosi6654
      @osmanmailosi6654 Рік тому

      Zopusa ukati anthu akumwela ukutanthauza chiyani galu iwe? Or amayi Ako ukulephera kuwagulira fertilizer chitsiru

    • @jeffulejames3550
      @jeffulejames3550 Рік тому

      Pamnya pa amako amaja makoswe mmalo moja nyama ya ng'ombe garu iwe olima maganyu wee chakwera amakuziwa iwe mtumbo wa amako

  • @ROBERTMUKHAYA
    @ROBERTMUKHAYA Рік тому

    Never again kkkkkkkk nkhanga zaona ulamuliro wankhadza

  • @destinymyson2611
    @destinymyson2611 Рік тому

    Zivute zitani, I would never vote for UDF, DPP, MCP UTM or any other party I would rather go to the farm.

  • @georgednthala-wh3pf
    @georgednthala-wh3pf Рік тому

    Sizingatheke kupanga zisankho 2024, pamene bwalo ka milandu linapereka chigamulo kuti masankho tipangeso masonkho, dziwani kuti ma date amasankhi anasintha. Chakwela nda chilima akuyenela ku server 5 years term not 4 year. Ife sitipanga nawo ma demo amenewo, iwe uli ndi zilinga zako and ngati akupatsa ndlama ingodya ndlamazo usatisokose apa

  • @NKHANTV
    @NKHANTV  Рік тому

    Chonde osayiwala kupanga subscribe

  • @JustineWillard-s5o
    @JustineWillard-s5o Рік тому

    Mwayiwala.akuru chisankho chidzachitika 2025/pa.16 sepetember.