THE D.C ... MALAWI WATHA CHOFUNIKA APA MDIKUGWIRANA MANJA BASI // BON KALINDO

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 6 гру 2024

КОМЕНТАРІ • 138

  • @NKHANTV
    @NKHANTV  Рік тому +3

    Hello
    Takulandirani pano pa NKHANI TV
    Chonde osayiwala kupanga subscribe
    Ngati mwapanga kale , mulungu akudalitseni

  • @AlickMDayi
    @AlickMDayi Рік тому +1

    Brother Kalindo apatu ndiye mwalasadi njoka kumutu💪🏽💪🏽 The DCCCCCC
    Apaki mwawachulawa zisilu zokha~zokha zikugofanana ndi Chakwera ndinso Chilima alibe chifundo ndi anthu osawuka pamodzi ndi dziko la Malawi
    Asogoleli opanda manyazi polibera dziko Shame

  • @cassimmeleka40
    @cassimmeleka40 Рік тому

    100% well said from nkhotakota boma to chia k5000 poyamba tima lipira k2000 mavuto ndi2 awa, kalindo amatiyimilira

  • @MadalitsoChisale-j2o
    @MadalitsoChisale-j2o Рік тому +1

    Kalindo more fire and tikudira mademo anyooooo ziko lonse and we're leady

  • @HusseinKachala-ml7ut
    @HusseinKachala-ml7ut Рік тому +4

    Ku meeting kumenekotu, Ben Longwe and his friend Redson Munlo kunalibeko, kunali iweyo Basii, and ukuziwa zimene zikuchitikazi, usawatenge amamalawi uchitsiru ayi

    • @NedsonKanjira-qj2ig
      @NedsonKanjira-qj2ig Рік тому

      Man inuyo munena zoonadi uyu anaziwa kale ndipo ndinasiya kumumvera chisiru

    • @innocentmusuli7380
      @innocentmusuli7380 Рік тому

      Onsewa ben, Redson, kalindo onse omenyera ufulu + andale zawo nzimodzi osewa ndi mabwantasa

  • @robertrichman9376
    @robertrichman9376 Рік тому +4

    We need mademo, tangolengezani

  • @joicemartin-ji5zu
    @joicemartin-ji5zu Рік тому +4

    Kodi ndifunse amalawi army ali kuti kusonyedza kuti dziko lathu kulibe Army's sangadzuke mkulanda mboma kuti cakwera walephera amalawi army ndi omwe akukhala anthu

  • @HanishaissahKagansa
    @HanishaissahKagansa Рік тому

    Powerful mr boooon the dc

  • @MatiasPiloti
    @MatiasPiloti Рік тому +1

    Munadziwa abon chifukwa munalinawo limodzi kusalima,kuwuzana zoti mutinamize. Inu ambuye akukhululukileni

  • @NkhomaPrecious
    @NkhomaPrecious Рік тому +1

    Zafika posauzana apa mmmmmmmmmmmmmmmmm love you born kalindo

  • @GiftFrancesco
    @GiftFrancesco Рік тому +2

    Timakunyadlan bwana The DC

  • @HamidahshaibuHamidah
    @HamidahshaibuHamidah Рік тому +3

    THE D .C.......TIYENI TIGWILANE MANJA TITHANE NDI CHAKWERA 💪💪💪💪💪

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu Рік тому +1

    Koma Bon mumalankhula zoona , boma ili litipha, zinthu sizili bwino , tafinyika. Chakwera wadya zomwezi.

  • @PuliscaShyton-ot6my
    @PuliscaShyton-ot6my Рік тому +2

    The DC 🙌🙌🙌🙌🙌🙌🔥🔥🔥🔥

  • @PriscaPahuwa-j2n
    @PriscaPahuwa-j2n Рік тому +1

    Long live Mr kalindo❤❤❤❤❤

  • @SheenahMwalabu-iz3pr
    @SheenahMwalabu-iz3pr Рік тому +2

    Only activists john kapito ndeokamba zanzeru,, eish koma taphinjika nalo bomali from the day 1 analowa mboma haa😢

  • @HusseinKachala-ml7ut
    @HusseinKachala-ml7ut Рік тому +2

    Iwe kalindo usatitenge kupusa amalawife wamvaa?, Kodi mmesa ndiwe amene unatiuza kuti unaitanidwa ndiaboma kusalima komwe mumakakambilanako zakayendetsedwe kachuma?. Nde mmene mumakambilanamo mumagwirizana zogwetsa kwacha ndaboma akowo sichomcho?.
    Lero nde usatimyansepo apaa coz zonsezi ndiiweyo kalindo ukutipwetekesa kwambiri ngat siukudziwa, ndepano uzit amalawi tiyeni tigwilane manja, ugwilana manja ndindani popeza unagwilana kale manja ndi aboma akowo, ukuona ngati amalawife sitikudziwa zoti ulimbali yaboma heti!?

    • @SheenahMwalabu-iz3pr
      @SheenahMwalabu-iz3pr Рік тому

      Imagine aa, tsiku amati ee nnapitako ku salima lija bwenzi ataulura kuti akuti kwacha akuigwetsa ndipo kwakambidwa izi ayi ndelero adziti chani BIG NO inutu a DC takutulukani

  • @kassimumar6421
    @kassimumar6421 Рік тому +1

    Ma soldiers tiribe basi shame on us Malawians
    Ndiye ndalama zomwe akubazo adzatipusitse nazo ndikuzamvotera nyani yemweyi kaya

  • @JoãoChirwa
    @JoãoChirwa Рік тому

    Zoona zak Pano Malawi wafika pa mwana wakana phala

  • @FrancisDay-br7xb
    @FrancisDay-br7xb Рік тому

    I secure my vote for chakwera and chilima, tonse alliance woye, chakwera 2025 BOMA

  • @JusticeKawilira
    @JusticeKawilira Рік тому +1

    Mukayankhula yankhula choncho kenaka mudzikasonkhana nao kusalima ndikumakamwera limodzi Fanta koma 😂😂😂😂

  • @mariezorgen7735
    @mariezorgen7735 Рік тому +2

    Some wonder why is he allowed to enter again muziko??

  • @AndisonSaidiKhunjuh
    @AndisonSaidiKhunjuh Рік тому +1

    Eeee apa nde zafikapotu

  • @blandinabonaventure
    @blandinabonaventure Рік тому

    Opposition ndiopusa kondwani uyu ndi galu chifukwa iwowo ndamene akayamba MA complain kma kuli xii amaenera ku wapanga support achina bon
    .. Kalindo mademo akanakhala amphamvu

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule Рік тому +1

    The DC bon kalindo ❤

  • @georgesmart3791
    @georgesmart3791 Рік тому +1

    The DC more fire🔥 🔥

  • @bayview4554
    @bayview4554 Рік тому +2

    Kod ndiye Kut chakwera ndiwasatanictu bwanji amalawi tangokhalapwi no tolk

  • @rabsonbenson-wx1jv
    @rabsonbenson-wx1jv Рік тому +1

    Ine apa ranga ndi Pephero KWA mbuye atimenyere khondo chakwera angosiya YEKHA udindo taonani zikori likupita kt amalawi

  • @AlexKinunda-j9l
    @AlexKinunda-j9l Рік тому

    Amalawi panopo akukumbukila mau a Former P M ,kuti amalawi muwona nyekwe ndi ziona ,Malawi yafika pa moto.

  • @MarryMummy
    @MarryMummy Рік тому +1

    If a leader love his county, the actions will follow. If a leader hates his county actions will follow.

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete Рік тому +1

    The DC ❤❤❤❤❤❤

  • @asiyatujuma5507
    @asiyatujuma5507 Рік тому +1

    Zoyonadi ❤❤❤❤❤

  • @robertrichman9376
    @robertrichman9376 Рік тому +1

    Waiting for mademo

  • @VanaciohMbewe
    @VanaciohMbewe Рік тому +1

    Chakwera ndi mbuzi yamunthu😢

  • @omanm2919
    @omanm2919 Рік тому +1

    Eya akufunika impeachment apite

  • @MosesPhiri-pk8ct
    @MosesPhiri-pk8ct Рік тому +1

    Ndizomvekadi bwana zomwe mukunenazi Komano panopa ndinyengoyi mmene yafikapa mademo azathandizanso Kodi si nthawi yakampenino iyi bwana okay mutiuza

  • @PaulMvuma
    @PaulMvuma Рік тому

    I have never taken this man serous, awa zawo ndizamasuzo

  • @LaurentAmbassador
    @LaurentAmbassador Рік тому +1

    The dc❤❤❤

  • @ChikondiNelson-ur2tq
    @ChikondiNelson-ur2tq Рік тому +1

    Masiku akungopitatu palibe chomwe chikusintha🙄🙄 tiyeni tingozisiya basi😂😂😂

  • @AndrewInnocent-he8gs
    @AndrewInnocent-he8gs Рік тому +1

    Moto ku booooo

  • @bernardchithumba6040
    @bernardchithumba6040 Рік тому

    Chakwela watuluka kale kupita kunja ndie bwanji mtsogoleri wa MDF ndi onse akumbuyo kwake apanga attack mma airports, government radios stations and other governments offices including the state house and announcing that Malawi government now is under control by military forces ndipo Chakwela asaloledweso kulowa mdziko lino .............please help us out of these evils

    • @ShupiMakwinja
      @ShupiMakwinja Рік тому

      We haven't strong military hear in Malawi zose nd mbuli zophunzira very rubish chakwe ur fired with all ur followers

  • @MoosaSame
    @MoosaSame Рік тому +3

    Malawi army there are too scared n there are 2 sleeping nonsense

    • @SolomonNjolomole
      @SolomonNjolomole Рік тому

      Malawi army sangatenge action pano zonse zili mmanja mwathu coz mission yolanda boma siyophweka amaopa Trizon

  • @GeraldMustafa
    @GeraldMustafa Рік тому

    Ndiye inu osapanga mademo bwanji asanabwele komwe aliko

  • @wysonmpatama4393
    @wysonmpatama4393 Рік тому

    The DC kodi zaliti izi

  • @EmmanuelJoseph-cj3pc
    @EmmanuelJoseph-cj3pc Рік тому +1

    Zoonadi Mr DC

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 Рік тому +1

    Iwe kalindoo, lemme tell u something ok, leave it for Ben Longwe and his friend Redson Munlo when it comes to fight for malawians, iweyo ulimbali yaboma, izi Ndanena coz ndiweyo amene unapita kukambirana zakayendesedwe kachuma chaboma ku salima week yathayi, kodi izi ndizomwe munakambilana zofuna kugwetsa kwachayi?.
    Uyankha kumtundu wamalawi panoo, zomatiyenda pansizo ife takana wamvaa?

  • @georgednthala-wh3pf
    @georgednthala-wh3pf Рік тому +1

    The DC, why is ur information of the procurement of the jet by malawi gorverment different from the one we 've from Ben longwe?

  • @omarajibu860
    @omarajibu860 Рік тому +1

    Munthu ameneyu watipweteka kwambiri.

  • @ishakatimbe7341
    @ishakatimbe7341 Рік тому +1

    Mademo ndiomwe tikudikira

  • @MikeJalison
    @MikeJalison Рік тому +2

    A born kalindo mukamanena nkhani ya boma yanuyi muzikumbukila kuti ndinuso amene munamenyela nkhondo chakwela ndi chilima

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn Рік тому +1

    Munayesa nonse aMalawi first koma apa ndie bas Mulungu yekha yemwe angatipulumuse tonse Malawi muno😢

  • @bernardchithumba6040
    @bernardchithumba6040 Рік тому +1

    Simkutha kumvetsa kuti kodi ku Malawi kuli MDF? Ngati MDF ilipo bwanji sakulanda boma mkuliyendetsa kwa few months then declare election day to the civilian so that we can make a better change not this manyaka MCP ,,,,,,,,,,,,,,blood shaded party

  • @AltafBarejia
    @AltafBarejia Рік тому

    Tili pa mabvuto osaneneka bwanji asilikali athu osangolitenga dziko la malawi likhale mmanja mwawo kumuwudzilatu komwe wapitako kuti utsogoleri wanu watengadwa

  • @tonemuyaya6284
    @tonemuyaya6284 Рік тому +2

    ❤✊✊✊✊

  • @LacksonKalawa-co2ms
    @LacksonKalawa-co2ms Рік тому

    Ndukanika kupita kumalawi kuti ndikapume kamba ka kwacha mmene ilili kumalawi.

  • @WinstonNyadaufe-d1o
    @WinstonNyadaufe-d1o Рік тому

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 Рік тому +1

    Eeeeeee dc heartbreak dziko lonse

  • @ErickMulenga-oe1mz
    @ErickMulenga-oe1mz Рік тому +1

    Tili mavuto real crisis

  • @gladysbonongwe1038
    @gladysbonongwe1038 Рік тому

    Mr boni pls t shirt yo muchose pls chilima ife ayi

  • @MikeMiggeri
    @MikeMiggeri Рік тому

    Yona uyu😮😮😮

  • @MikeMiggeri
    @MikeMiggeri Рік тому

    Yes ma 😢😮

  • @Ruth-y5q9n
    @Ruth-y5q9n Рік тому

    Koma born ife zomango tulusa mau tatopanazo tatiyeni tipite kunseu koma mukudikila kuti zizizileko kaye kenako muziti tiyeni kunseu nchifukwatu anthu amagwa mpwayo apa zimafunika olo mawa tiyeni kunseu pasanapite mphepo apa

  • @IbrahimMatias-te1kc
    @IbrahimMatias-te1kc Рік тому +1

    Takulandilani born kalindo

    • @KennethKadawati-jc1el
      @KennethKadawati-jc1el Рік тому

      Apapa kunakakhala maiko Ena ndiye kuti maofesi onse aboma akanatsekedwa kupanga mademo anyooo koma ife manyasa aaaaaaa kadi ya kamuzu inatipweteka.
      Umodzi
      Kusunga mwambo
      Kumvela
      Zinatifoola mitima

  • @DaudBonomali
    @DaudBonomali Рік тому

    Koma DC kungwirana manja kumeneku tisangwiranenso ndi chilima chonde chonde a DC chifukwa manyakanyaka alipowa ndichifukwa cha chilima zongwirana manja zikumveka koma osatinso ndichilima

  • @samuelliphava
    @samuelliphava Рік тому

    Sitiyiwar ndnu nomwe amene munathandzir kt boma ili lilowe,mmesa tonse ija munali mmomo,ndangonena

  • @JannatuHassan
    @JannatuHassan Рік тому +1

    Ai zikom

  • @kondwaninqumayo4397
    @kondwaninqumayo4397 Рік тому

    Zinthu zili bwino kwambiri. Keep it up chakwera and chilima. 2025 bomaaaaaa

  • @chikagwaharrison389
    @chikagwaharrison389 Рік тому

    Usiye kuyankhula Kapolo iwe. Mmesa umadya nawo limodzi?

  • @andsenJeke
    @andsenJeke Рік тому

    Kani ndiwe wa chiima kalindo?

  • @BrightClementziongabanda
    @BrightClementziongabanda Рік тому

    T-shirt yo bwanji mwalowa utm?

  • @HappyGoldfish-bl7zn
    @HappyGoldfish-bl7zn Рік тому +1

    Bon kalindoooooooooooooooo

  • @chikagwaharrison389
    @chikagwaharrison389 Рік тому

    Umawauza ndani pamene iwenso uli kapolo wa ndale? Chitsiru ngati iwe.....

  • @melodybashiriahmad914
    @melodybashiriahmad914 Рік тому

    inuso mukudyera mumademo momo pogwilitsa ntchito anthu wamba

  • @amabhohlela.3492
    @amabhohlela.3492 Рік тому +1

    Aaaah uyu osamumvera,,akabwetuka bwetuka chonchi m'mawa akutizemba mumalandila Ndalama uyu..zomwe akulankhulazi sikuti CHAKWELA alinazo Ntchito,amangomugwilitsa ntchito....kuti azitimata phula basi

  • @chikagwaharrison389
    @chikagwaharrison389 Рік тому +1

    Manyi President wa osauka wake uti? Mmesa unali nawo limodzi and muli limodzinso? Ukuziwa chomwe chikuchitika mmesa muli limodzi? Chitsiru iwe......

  • @paulmakaula4937
    @paulmakaula4937 Рік тому

    Vuto andale aboma ndi opposition MPs izizi siziwakhudza or dontho...a Malawi ganizani mozama aliyese ali ku parliament walephera ndipo chipande chidzadziwe poomola

  • @HusseinKachala-ml7ut
    @HusseinKachala-ml7ut Рік тому +1

    Kalindo usamatiyende pansi amalawife wamvaa, don't undermine us please,
    U r de very same guy amene unapita ki salima to attend the meeting ndi aboma and I told ife kut mumakakambilana zakayendetsedwe kachuma chadziko, look at now kalindo!.
    Nde tikamakuuza kuti ndiwe mthirakuwiri ukana!?.
    Tikamakuuza kuti ndiwe mthirakuwiri waboma ukana?

    • @MusaFrackson-n8l
      @MusaFrackson-n8l Рік тому

      Koma anthu timangopanga against zazii. Analongosola bwino bwino za kusalima. Simunamve?

    • @HusseinKachala-ml7ut
      @HusseinKachala-ml7ut Рік тому

      @@MusaFrackson-n8l palibe chanzeru chomwe analongosolapo pankhani yakusalima ija, Kodi zoti hrdc imagwira ntchito ndi mcp mndani sadziwaa?.
      Nde iye amkati anapita kusalima coz a hrdc anali komweko, zoti hrdc ndiya mcp asamadziwa ndindani mdziko muno?
      Bon kalindo ndimpeni wakuthwa uku ndi uku and asamatipusisepo apaa.

  • @SheenahMwalabu-iz3pr
    @SheenahMwalabu-iz3pr Рік тому

    A DC mukanakhala dolo simukanapita ku btz crossroads, Salima padzana. Now zomwe munakakambilana kumeneko simunatiuze, lero yagwa ndalama mukubwera apa ngati wabwino after kupatsidwa chibanzi. Munandikwiyitsa kwambiri l was so inlove ndizomwe mmachita koma pano l lost hope in you. Only God will make us through this 🙏

  • @dawoodissah1611
    @dawoodissah1611 Рік тому

    Inu ma top activists especially you! Amalawi atopa tsopano ndi phokoso without action where are we going with this voices without action please,
    Kodi inu achikulire mudakadali mu (utm) kuteroku mukuchita campaign ya utm?
    Mupulumutsa bwanji Malawi muli mu (utm)?

  • @Chiso2019
    @Chiso2019 Рік тому

    Vuto ndilakuti akalindo mumayankhula zinthu zamphavu kwambili zabwino koma platform yomwe mumagwilisa tchito chifukwa uthenga wanu sumapita patali ndiokhawo omwe Ali ndi data komaso ali ndi smart fon......that's why mukamapanga mademo ena amadabwa kut kodi kuli mademo chifukwa samakhala ndi information yokwanira

  • @samdiverson9733
    @samdiverson9733 Рік тому

    kuti chakwera ndi chilima alowe m'boma ndi ndani?

    • @MusaFrackson-n8l
      @MusaFrackson-n8l Рік тому

      Zimenezo zinapita ndichifukwa chake leronso akudzudzula poona kut anayikidwa m'boma kma sakutha. Ndipo ndi ambiri onse achina Sandra achina Ben Longwe anali gulu lomwelo loyika m'boma anthu amenewa. Lero bwanji? Onse sanatembenuna akudzudzulanso chimodzi moz

  • @MussaChitimbe-xq2dm
    @MussaChitimbe-xq2dm Рік тому

    Za Chamba bas unayambila kulankhula muja palibe chikusintha

    • @dysonkhofi-gv4uy
      @dysonkhofi-gv4uy Рік тому

      Wachamba ndiweyo , munthu wopanda nzeru, uyuyu atimenyera nkhondo.

  • @FiannaFiannakaponda
    @FiannaFiannakaponda Рік тому

    Eeeee boma limeneli amalawi mawu alibeso 😊

  • @ZONKEMASEKO-rm5fn
    @ZONKEMASEKO-rm5fn Рік тому +1

    The DDDDD CCCCC

  • @LuckyKaponda
    @LuckyKaponda Рік тому

    Mudapita ku Salima akulu
    Musatinyase.

  • @CatherineMatiki
    @CatherineMatiki Рік тому

    Ayi fwenkisi

  • @alexandermwale4669
    @alexandermwale4669 Рік тому

    Nzovuta kumvesa

  • @MuhammadBAKILI-kl2mj
    @MuhammadBAKILI-kl2mj Рік тому

    Vutonso bon kalindo ndi nanzikambe sachedwa kusintha mawanga, akatero ndekuti akufuna kukapochera ndalama zina

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 Рік тому +1

    Wachita kuvala manyaka ako a utm for wat?, that guy isn't helping us maan!.

  • @MartinMajola
    @MartinMajola Рік тому

    Chilima moto

  • @Lizzie-h1k
    @Lizzie-h1k Рік тому

    Boma lopanda manyazi😢😢😢

  • @geraldtuwaga-iz6ll
    @geraldtuwaga-iz6ll Рік тому

    Izi ndizomwe mudakambirana Ku Salima Kuna ETI?

  • @Goliath461
    @Goliath461 Рік тому

    I don't have something to say at this time

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda9830 Рік тому

    Tsopano kuvala za UTM ndi chani poti onse akugwilira ntchito limodzi ndi Mcp

    • @FrancisDay-br7xb
      @FrancisDay-br7xb Рік тому

      A photo before activism

    • @MusaFrackson-n8l
      @MusaFrackson-n8l Рік тому

      Anthu inu amabweletsa nkhani za anthu amenewa simwini wakeyo ai. Ndipo ameneyoyo akamayika nkhani yo ndamene amayika chithunzi chomwe wafuna uyika nkhani yo. Sikuti photo ilipamenepoyo imakhala nthawi imene akulankhulayo ai.

  • @FrankStoro
    @FrankStoro Рік тому

    Mesa mumkayenda ndi panti yskha pa central mvula nitso

  • @YomeChima
    @YomeChima Рік тому

    Agalu amboma

  • @PatriciaJames-g3n
    @PatriciaJames-g3n Рік тому

    Iwe chitsiru mutu ngati dzuwa nawe ukungotipusitsa wavala chani galu iwe ndichifukwa chake unaluza kwanu

  • @chikagwaharrison389
    @chikagwaharrison389 Рік тому

    Unkanena kuti chani Bon Kapolo iwe...... mbava

  • @patassonelucaszovuta3431
    @patassonelucaszovuta3431 Рік тому

    Kodi iwe kalindo mesa pompano iweyo ndi aboma munaputa ku salima kukambilana mumati nkhani za chuma ndie chuma chake ndi chiti apa ukusokosa chiyani

  • @PaulMvuma
    @PaulMvuma Рік тому

    Choka iwe, ife a malawi tili bwino 😂😂