Phawawa phanyenye mkolongo kkkkkkk, mtelela nyani abwana kkkkkkk, apabwalo sakuchoka kkkkkkk, anthu adyoo, adyooo, adyooo, ambele mfuti kwabiti nyono kkkkkkk, chili kwipiii. Keep the fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥 Ben and Munlo, chakwela don't deserve ulemu ayi coz he's been taking malawians for granted. He must step down coz he has failed us!
Keep the fire burning Ben and Munlo!, all the malawians are right behind you 2 guys, u the only courageous pple here in malawi and if we had a lot of brave people like you in malawi, malawi anakakhala otukuka kwambiri unfortunately its only u n Munlo the whole country la malawi eish!
Ngakhale Ben Longwe amayankhula zina zosakhala bwino but amakhala ndi point sometimes, Nkhani ya Chakwera yafika poti kulitchula dzina lake pamanso pa ana, Anawo akumangolira chidzina chobweretsa Minyama mdziko.
Iwe tangopanga forcus mbari yako osakhara busy kumakamba za azako... and palibe siku lomwe The DC anapita ku state house kukakumana ndi chakwera kugulitsa mademo... ndipo chomwe ndikudziwa ine chakuti .Chiyambireni gulu la Malawi 🇲🇼 first siinachitisepo mademo dziko lathu ..ndipo nthawi zonse mademo a malawi 🇲🇼 first amangorephereka ..ndipo ngati taonapo mademo mu uramulire umenewu ndi a bon kalindo kudzera ku gulu lake ls cctv.
Aaben longwe iwe chhapwetejka ndi chiyani iwe ndiwe galu yeni yeni palibe chimene ukuchita uli kummalawi iwe ntchito kupephesa osalowelela zaaeni aachisilu inuu
Iwe ben ndi amene ukuononga chifukwa umalimbana ndi azako ndiwe galu kwambili chitsiku cha munthu amwene tatsisani mfundo wosati zolimba ndi ndi born kalindo iweyo olo utatani born sungamukwanise iweyo ukunama kwambili
Mmmm iwe Longwe you're talking nonsense. Pitani ku ICC kwanuko you won't win. IMF, EU & World Bank siipereka thandizo ku dziko lophwanya maufulu anzika zake. Inuyo palibe chilichonse chabwino chomwe Chakwera angapange....
zina zonse mwanenazo eya zoona zanzeru, komano zochita ma word play zo nde zopusa, heart ear hear art zopusa zimenezo, just be doing the real serious business here.
Inetu siwamademo ngatimukuwona kuti mademo ndi yankho, i do a lot of things apart from mademo, panopa mukumverawa simademo, just an audio mwavutika nayo mpaka kuponya audio yanga pa you tube nkuyitanizana, ndiyitumiza kuti onse ayiwone akunyetseni. Ma audio anga amapinyedwa pa you tube ndi mtawaya not akambwe mulenga
Aise Ben ma audio ako nthawi zonse akumamveka moonetsa kut ukulimbana ndi Bon Kalindo pamene mzakoyo samalankhula zolimbana nawe and samakonda kumakuyankha vuto nchani ase? Zikumaoneka ngat umanchitira nsanje nzakoyo ngati zili ndalama za MCP bwanji nawenso osabwera udzalandire nawo ngati zili zoona? We are sick and tired of listening to such audios of criticism. Please behave yourself and continue fighting for the Malawians in good manner hence majority of people will like you. Please don't waste your time in criticizing and stigmatizing your fellow activists on the issues that you don't have a cast-iron alibi with.
Tamayeserani kumakamba zanu big man osati zamunthu mzaunu ayi please
Iwe ndiwe uli oduka Mutu asiulikuno mbalame azako alikumalawi akuwona zinthu ndimaso
Komano man mukanabwera mwina komano mumangoyankhula mulikutali aaaa
Koma inuyo ndinu agalu bcz mukusiya kuyankhula point zanu mumakhala bzy kuyankhula za kalindo bwanji osamapanga zanu mmmmm mwanyanya guys,paja kalindo sanayambe akambapo zainu zikuoneselatu kt inu mukunjenjema ndi the DC pangan zot zingathandize amalawi zitsiru inu panyo panu
Ndipo inuso kukonda kuyambana ndi kalindo bwanji ndinudi abusa inu?
Phawawa phanyenye mkolongo kkkkkkk, mtelela nyani abwana kkkkkkk, apabwalo sakuchoka kkkkkkk, anthu adyoo, adyooo, adyooo, ambele mfuti kwabiti nyono kkkkkkk, chili kwipiii.
Keep the fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥 Ben and Munlo, chakwela don't deserve ulemu ayi coz he's been taking malawians for granted.
He must step down coz he has failed us!
Umakwana Ben keep the fire 🔥 burning
Mumakwena Ben🤜🤛💪💪💪💪💪💪
Tabwelani mr Ben kumalawi kuno Mupange mademo tikuwoneni
Musalimbane ndi Bon Kalindo pangani zanu ndiponso Bon Kalindo ma Audio ake samakamba zainu
Chitayipi chamamuna wamabodza kuposa mzimayi haaa everytime kulamba zanzako iwe 😤
Uzingolankhula zako. Usamatchulemo za Bon kalindo sizikukukhuza. Kuteroko ulindicholinga choyipitsa mademo aanzako wo. Ngati kuti alipo anakuletsa kupanga mademo. Unasiya wekha
panyapako Ben Longwe mtchona iwe mbolo yako wava
Keep up mkuyitha inu bwana
Keep the fire burning Ben and Munlo!, all the malawians are right behind you 2 guys, u the only courageous pple here in malawi and if we had a lot of brave people like you in malawi, malawi anakakhala otukuka kwambiri unfortunately its only u n Munlo the whole country la malawi eish!
A Longwe😂😂😂pa ground muli inuyo ndiye pati, ku SA? come here and fight these people
Inu alowengwe takamban zopulimutsa dzulo osati kulimbana mkunena zanu musamuipitsire mbili nzanu cholinga anthu amude kalindo ngokondedwa kumtundu wamalawi
Chakwera mulungu anamu Landa zeru wangofana ndi lusifa anaukila mulungu palibe chazeru chimene atapangepo
Ngakhale Ben Longwe amayankhula zina zosakhala bwino but amakhala ndi point sometimes, Nkhani ya Chakwera yafika poti kulitchula dzina lake pamanso pa ana, Anawo akumangolira chidzina chobweretsa Minyama mdziko.
Telela nyani sakuchoka mmatimilila💪💪💪♥️
Imwe aben longwe mmalankhula zopanda pake ndiwe achakwela anakhalepo aphawi ngati iweyo ben ukulephela kuwalipilila kudyesa ana ako ndiwe chindele
Zokamba zidakutherani abwana
instead of u and munlo others must continue to fight chakwera
Iweyo osakamuuza wekha bwanji chakwerayo daily kung'amba kukamwa.
Umangolankhula uli kutali bwanji osapita ku malawikomweko ndiwe woman wamantha ndiye osamamuyipisa nzako kalindo anakutengela chiyan
Apabwalo sakuchoka, ntelera nyani abwana 🔥🔥🔥🔥
Muuze ameneyoo aisee kkkkkkk
Telela nyani
Ben Longwe a kunena zoonadi ndipo amanena zoonadi, angochepetsa kunena za nyumba mwake.
Opita kosiyana samapikisana,kalindo akupita kumademo,iwe ndi munlo munati muzipanga ma talkshow ,why mukulimbana ndi B kalindo? Sibwino choncho
Inu inu mmmmmm
Mbwelera aben inu😂😂😂😂😅
Iwe tangopanga forcus mbari yako osakhara busy kumakamba za azako... and palibe siku lomwe The DC anapita ku state house kukakumana ndi chakwera kugulitsa mademo... ndipo chomwe ndikudziwa ine chakuti .Chiyambireni gulu la Malawi 🇲🇼 first siinachitisepo mademo dziko lathu ..ndipo nthawi zonse mademo a malawi 🇲🇼 first amangorephereka ..ndipo ngati taonapo mademo mu uramulire umenewu ndi a bon kalindo kudzera ku gulu lake ls cctv.
Komaso unati wasiya kkubwe bweta ukkulephela kusiya chifukkwa ndi we mphawi wachabe chabe ndiwe nmunthu wankkulu uzipase ulemu kayo ndiwo ben longwe
Iwe panyini pa mako ndiwe galu bwanji ukulephera ku pita ku Malawi uzikalakhulira kumeneko iweso ukudana ndi bon kalindo
Kukhesa mwazi kuyankhuya kwa Chakwela nthawi yimeneyo akufunisitsa u president kkkkkkkkk pano awonesa utsilu wawo.
Kodi iwe osamapanga zako bwanji dc sapanga za iweeee
The king 👑💖 l love u big brother
Apabwalo sakucoka😂😂😂😂 mesi jakakaka dyakumwelera😂😂 big up
Gututu Ben longwee
Ndiwe opanda dzelu ndwe ben longwe achakkwela sakunama ayi
Ndiwe wazelu
Chi Born Kalindo,,,changoti ziiiiiii!!!!! achipwichika chim'banzi kuchikamwa.
Mm bodzatu limenelo, simunamuone Crip yomwe anathulutsa ija ku Blantyre?
Tikuku pephan malume Ben bwanj mungopta inuyo Ku Malawi ko muzkapenga Mademo coz mumazwa kuweluza Koma ndkuzwakut mulindmatha ndpo Mademo simungaapange ndnu mwana
Sir Charles ben longwe tikufuna tikhale manso patsogolo ndi zisankho 2024 osati 2025 mukamapanga odiyo komanso mudzilankhula kwambiri
Big boss
Ben. longwe ndiwe galu yamunthu. Chisilu
Ma jacket ndi zimphonongolo kkkkkkk
but one guestion to u is that why are you fighting amongst yourself
mr ben longwe ilike u so much
Chakwela moyenda zoonadi ndi mbuzi ya munthu galu weniweni pastor kamwendo njila nyau yoputsa komanso watikwana boma la mbuzi
Apa ndiye zowona zenzen
Mnilo kalindo satukwana kommma iwe beni longwe
Ben Longwe kkkķkk chakwela Achoke
Yankhulani tikumvera, apa tilipo anthu 18
Aaben longwe iwe chhapwetejka ndi chiyani iwe ndiwe galu yeni yeni palibe chimene ukuchita uli kummalawi iwe ntchito kupephesa osalowelela zaaeni aachisilu inuu
Ben longwe ndiwe chitsilu pa thako pako ukulimbana ndi born kalindo ndiwe galu
More fire Ben don't sleep
Mwaiwona imeneyoo?
Ndewati heart mchichewa ndichani?, Kkkkkkk
Ati munali ndi zimphonongolo Ben longwe adha😂😂😂😂😂😂😂
Boss we support ur audios
Big love brother ❤❤❤❤
Mugwirizane ndi Bon Kalindo.
Ai asagwirizane nd Bon kalindo ameneo,simunthu wabwino. Tiyeni timusiye bin kalindo agwire ntchito nd omwe alinawowo.osati Ben Longwe mmk mmk

Iwe ndiwe kambweee ben
Kape ndi beni longwe nddipo ndiwe chisilu
Cholinga ulepheretse ma demo mapwala ako longwe
Akolo 😂 patumbo pano
Chakwerayo pa zakuti activists akumafuna asipasidwa ndalama yogulitsira mademo, zimenezo ndidzaboza achakwera wafika pa misalano chitsiru chodwa manyi aakamano mutu wa iyeyu wabaizika ndi ndalama ya Malawi osauka watembereredwa ndi Chauta ameneyu.
beni longwe iweyo osamagitsa mnsewo wa makanjirawo bwanji kod iweyo ukuchitapo chiyani kuti dziko lino litukuke?
Muuze amvetse
Mhuuu ayi chabwino
Ndiwe chiphwisi chonunkha
Ndmakunyadilan abraz
Love u ben longwe
Iwe ben ndi amene ukuononga chifukwa umalimbana ndi azako ndiwe galu kwambili chitsiku cha munthu amwene tatsisani mfundo wosati zolimba ndi ndi born kalindo iweyo olo utatani born sungamukwanise iweyo ukunama kwambili
God bless sir
Iweyo uberetu kuno
Guys munayamba kale kusokosa chili pano ndichakuti mumakuopa ku state house your not a fighters
Zikomo Sir mumatiyimilira Sir
Zowona sa timakukondani
Palibe chomwe chilichomveka chomwewayankula chingachitikeku malawi kuno
Ada ben uziwachiyani bweraiweyo kunoko ngatiuli dolo kkkkk nkhothiko iweyo ukakhalako?
Mr ben longwe ur a lier please speak English
Sindipempha zitsiru za MCP kumamvera ma audios anga komabe amalephera kuti asamvere, amamverabe chifukwa mfundo zanga zimaposa za Chakwera yemwe amalephera kuyendesa dziko
Ndakupanani atomato awiri awiri
Mmmm iwe Longwe you're talking nonsense. Pitani ku ICC kwanuko you won't win. IMF, EU & World Bank siipereka thandizo ku dziko lophwanya maufulu anzika zake. Inuyo palibe chilichonse chabwino chomwe Chakwera angapange....
zina zonse mwanenazo eya zoona zanzeru, komano zochita ma word play zo nde zopusa, heart ear hear art zopusa zimenezo, just be doing the real serious business here.
Inetu siwamademo ngatimukuwona kuti mademo ndi yankho, i do a lot of things apart from mademo, panopa mukumverawa simademo, just an audio mwavutika nayo mpaka kuponya audio yanga pa you tube nkuyitanizana, ndiyitumiza kuti onse ayiwone akunyetseni. Ma audio anga amapinyedwa pa you tube ndi mtawaya not akambwe mulenga
Aise Ben ma audio ako nthawi zonse akumamveka moonetsa kut ukulimbana ndi Bon Kalindo pamene mzakoyo samalankhula zolimbana nawe and samakonda kumakuyankha vuto nchani ase? Zikumaoneka ngat umanchitira nsanje nzakoyo ngati zili ndalama za MCP bwanji nawenso osabwera udzalandire nawo ngati zili zoona? We are sick and tired of listening to such audios of criticism. Please behave yourself and continue fighting for the Malawians in good manner hence majority of people will like you. Please don't waste your time in criticizing and stigmatizing your fellow activists on the issues that you don't have a cast-iron alibi with.
Aaaaaa za ziiiiii
Umalimbana ndi kalindo chifukwa chani utapanga zako ungafe aaaaaa umatibowatu ukamadana ndi DC mwana oopsa kwambiri
Komatu ben longwe keep burning
@@aggogokina8992 thank you brother 😊
Kkkkkkk
Omwe mukudana ndi Ben longwe ndi mitu yani siimagwira mukufunikila mawaya okwanira
Kagwere uko iwe
Mwaiona imeneyo? Chakwera stupid