Next time we must vote in people with solid plans. Candidate must give details in there manifesto , policies, strategies. Failure to do so their names must be removed the ballets. The current president is a complete idiot it's so shameful.
That's the Dddddd Ccccccc!!!!! whom I know, the only trusted and true freedom fighter, our own president, president for the poor, fight on and always proud of you our president, ulemu wanu munthu wankulu, musamasowe
Is better to live without president zan chimbuzi ngat icho no he but I can say it becoz it poor in mind he is accustomed with corruption anawaberapo acathoric roman
This is well said Mr DC. We love you Bon Kalindo
Well done Mr kalindo❤
Thank you Mr DC for speaking to power
Mmene mwayankhuliramu zoti mumagulidwa ndi boma ndakayika
Ndipo ine sindimatsimiza
Kuyankhula ngati unalowa mumtima mwanga kalindo.big up
You're number 1 mr kalindo
Ayi koma apa pokha, tiyeni tiyendenaye the DC, Bon Kalindoooo.
Yes we can agree but not ma demo
I proudly you Mr 🎉
My only one!! The D c trusted person ❤️❤️
We love you, true opposition leader and the president of the poor Malawians. WE THANK YOU
you bon kalindo aaaaa ur no 1 mmmmmm im telling bon keep t u
God bless you boni kalindo🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏
God bless and protect the Dc
We done Mr Bon kalindo ❤ the Dc
We love you DC
THE DC tsogoleli wathu wa ifeyo anthu osaukafe 💪💪💪✊✊✊✊
Bravo speech
Watitola Chakwera ndithu
More fire Mr kalindo
Kalindo mumakwana big up 2025 ikuchedwa tisamutse anthu
Ndipo kwambiri esh
Eeh koma adha.kuyankhuratu mosang'ana m'mbali... mwana mulomwe ❤
Big up the DC Kalindo
Thanks mr D.C. tikufuna zisankho zikhale 2024 osati 2025
Ndipo kwambiri
The Dc❤❤❤❤
Ndimakunyadirani Mr Bon kalindo
Congrants
Well done Mr. Kalindo
The D.C l will stand with you for all the time like our poor president ❤❤❤❤
Boni kalindo your number one
Umakwana iweyo bon
Kuyankhula kokoma DC kalindo❤ akumbuseni aiwala zomwe analonjeza pali mwambi apa👉 wakuti kovutula satenga chiwaya
😢😢😢😢 Malawi uja aliso pamoto again
Kuyankhula mwanzelu❤❤❤❤
Chonde mademo akufunika😢😢chonde mwina ndikupezako mpumuro😢
We are waiting madem
The DC mau amenewo
Bravo the DC go konko kumademoko
Mulungu akudariseni a Mr Bone Kalindoo
Next time we must vote in people with solid plans. Candidate must give details in there manifesto , policies, strategies. Failure to do so their names must be removed the ballets. The current president is a complete idiot it's so shameful.
❤❤❤❤
Usamasooooooooooowe my bulasa
Chakwela ndi mbuzi kwambiri😢
Kuswakuswa fundo boni kalindo.❤❤
The DC ❤❤❤❤
That's the Dddddd Ccccccc!!!!! whom I know, the only trusted and true freedom fighter, our own president, president for the poor, fight on and always proud of you our president, ulemu wanu munthu wankulu, musamasowe
Exactly
The DC Bon Kalindo. ❤
I a gree with u mr kalindo
Kalindo suzatheka sure wamusambwazatu nkhutu kumveyu
The DC ❤
Bon kalindo woyeeee
SAD Situation. Abusa mwalephela basi tulani udvinding.
Asilikali akumalawi ndihopusa soja bobhokilat 🐊🐊🐊🐊🐊🐊🐊🐊🏁
Aaaaa
Powerful Mr kalindo
Shakwela
❤
Well said Kalindo
Bon kalindo timakudaliran kwambili ambuye azikutetezera
Fact
I'm very happy with u we r together
I salute u Mr Kalindo awawa anakangopanga resign there's no leadership in him he should think of poor people akutipha uyu
Chakwela ndi mwana wachepa naro dziko
Kkkk
Some people don’t know they know NOT. Ignorance and hate are no defence
Ndakunyadiran bon kalindo pukumfa mawu anu bwana
❤❤❤❤
Pambuyo pan mr kalindo,chifukwa chotimilira amalawi,we need people who are carigious to stand up to all malawians
Iweso umatipusitsa tiyamba Kaye iweyo kuku matcha akupasa chithum Acho umadya wekha apa ukuti amalawi tulukani iweyo ndi chakwela tikumatchilani limozi uzingotipusisa
Aaah choka iwe ndi osauka ? Galu kwabasi, but to say the fact apulewa ndi panja basi
Ndimadikiratu inu kumva mau anu bwana musamasowe ayi.
Mumakwanila Akalindo
Machin anga booooon kalindooooo ndimanva kukoma mukamayankhula the DC dangerous chld
Mwalatsa abwana
Mr empty promise (chakwera) palipepo chomwe alankhula chaphindu.mbaza yaikulu asisira dala ndalama cholinga Abe ndarama zomwe apempha
Bon kalindo
Chakwera atiphatu uyu Anthu akumudzi omwe anamuvotera Aja wawataya mmmm
The DC
The d c mwana woopsa
Mumayankhula zanzeru koma vuto ndiloti mumaziyika pa business akulo. inu mumadyera pa nsana pa a Malawi.
Born kalindo akuyakhula za zelu chakwela nd mbuz athu kuvotela busa iye sanakhale mp zaboma saziwa galu chakwela
Uzathe mpweya wakowo pachabe zotii unadya chibanzi chamcp timaziziwa ifee
Mr kalindo muuzen chakwera kut ifeso ngankhale tili kunja kuno ku joni sitikumufunaso chakwera
THE DC PANGOLINI💪💪💪💪💪💪💪💪🇲🇼🇲🇼
Usatimnyasepo apaa iweee ndizamademo zakozo wamvaa?, takangosainila ndlama zomwe akulonjezazo ukoo, asatipusise ife kuti ukumenya nkhondoyi mudzina la amphawi okudya mkumakhala iweyo osawuka akufa ndinjala mmidzimu.
Kkkkkkkkkkk akalindo ndi mbuzi koma athu samadziwa
Soja of malawi NDI P30
Kuli mkokemkoke mgomomo. Do not budget lest ye be judged.
Chakwera ndimbuzi yeneyeni
Is better to live without president zan chimbuzi ngat icho no he but I can say it becoz it poor in mind he is accustomed with corruption anawaberapo acathoric roman
Ndiye ngati iweyo uli president wa anthu osawuka bwanji osapangilo anthu wakowutu ndiye chitsilu
The DC mungolakhula koma pa nseu bwanj tiyeni pa nseu zomangolakhula ayi apa
Mawuu
Usatimnyasepo apaa iweee ndiwamcp
Asakuwopsen inu simawopa the DC mwana oopsa kwambiri. Speech yozikonda apite Chakwela
Wambaya
Mmmmmh
Mr BN kulankhula moona ntima sure amenepajadi munthu osauka Palibe chomwe atapeze
Zoonad point
Tinakusowani The DCc
Tikumalandira ma message mmalowa mwa ndalama
Mofaya mademo ndipo tiliokozeka
Kalindo ndi 1 more fire basi chakwera ndi panja basi
Kuswa kuswa ishiii
❤❤❤❤❤😢😢😢
Mau mau amwene akalindo ndipo mademo achitike ife akuno Kumangochi Tili okhonzeka
Nanuso Kalindo nkumamupopa chonchi za zzzzu