Inuyotu mukamaopa kutukwanidwa simukwanitsa zofuna zanu. Achina Timothy ntambo aja ankatukwanidwanso mwa nyooo ndi ma cadets mmene amapanga ma demo. Stay focused on ur agenda n goal, focus on the few people supporting u and keep going. Osatanganidwa ndi ma negative voices. You will succeed.
Daily daily kukamba zaanzanu inu bwanji? Bweranitu inuyo mudzayende sienawa alephera,, ndeiweyo ndiwangwiro? I will neva follow munthu olimbana ndianzake, alikutali nkumati akulira nafe. Pompa pa joz osabwera bwaa, God will be with us with or without mademo ❤
Iwe Longwe pansana pako. How can you say you're fighting corruption koma apa mukuikira kumbuyo chisale yemwe anapanga business ya cement of 5 billion using tipn ya APM? That's corruption whether u like it or not. This is why we never take you people seriously
Umatiyimelira mr Beni Longwe
Tili nawe brother 💪💪💪💪💪
Kodi. Mesa mukati mwasiya muzipanga zanu ine ndili pambuyo pa booooòooooon kalindo. Inuyo muma ndibowa .muli miseche maboza kwambili musinthe mupange umozi ndi booooòooooooon kalindo
Aaaaa iziso, aliyese kwa Mulungu wake basi
Ben Longwe kwake nkuyankhula Demo ndi imodzi yomwe sinamuoneko iyeyu.😂😂
😊
😊
😊😊😊
Inuyotu mukamaopa kutukwanidwa simukwanitsa zofuna zanu. Achina Timothy ntambo aja ankatukwanidwanso mwa nyooo ndi ma cadets mmene amapanga ma demo. Stay focused on ur agenda n goal, focus on the few people supporting u and keep going. Osatanganidwa ndi ma negative voices. You will succeed.
Ntambo trampesi komwe muliko mupange zoti kuzunzika komwe kulipo kumalawi muthese munabweresa mavuto ndiinu
Achisiru amiseche inu palibe angakusateni
Inu ndi ogulidwa ndi andale, ndimu makape, mumawona ngat amalawi ndife opusa et? Mafuso opusa sitimawafuna ay. Umphawi ndiwathu bas.
Iweso mesa umati wasiya kod kumenyela ufulu nde ukuti bwanji apapa ine sindikukuvesatu aaah usamatipepelesa wava
Kod andale ationelelatu ndiposamvana kwanu ma actives nonse
The DC osati iweyo ase
Siinu activist inu tamangokhalani iwe ndiye wadyera theratu , tinakudalirani koma mwatigwesa mphwayi . DC pachiongolero
Bwelani abwana tilowe paseu
🔥🔥
Pamavuto akuchitika Pamalawi solutions ndi 2025 basi
Mulungu bas anthufe sitizikwanisa
Tadzuka bwino kayainuyo
Mukunena zowona sa
Bwelani kuno
😂
The cause its you, you better solve ur problems with boni kalindo please otherwise goverment will still play with your mind.
Daily daily kukamba zaanzanu inu bwanji? Bweranitu inuyo mudzayende sienawa alephera,, ndeiweyo ndiwangwiro? I will neva follow munthu olimbana ndianzake, alikutali nkumati akulira nafe. Pompa pa joz osabwera bwaa, God will be with us with or without mademo ❤
Mukuchita kufusa bwana, Inu simukuziwa kut Malawi yose ikut chakwela BOMA, mcp moto kut buuuuuuuuh! 2025
Iwe Longwe pansana pako. How can you say you're fighting corruption koma apa mukuikira kumbuyo chisale yemwe anapanga business ya cement of 5 billion using tipn ya APM? That's corruption whether u like it or not.
This is why we never take you people seriously
Sakupezeka tafabas
Mangochi mulanje tabwran what bout you ku Dbn ubwelak
Iwenso vaya uko omenyera ufulu ali kuno
😂👍
Nawe galu iwe ubwere