Ngati amalawi sitikwanitsa kumuchotsa chakwera chifukwa cha deflation iyiyi, sadzatheka kumuchosa ndi mavote coz ndi MCP yokha imene ipange kampeni next year and mmalawi akangopatsidwa kanthu amaiwala zakale check out the lomues
Zoona zeni zeni,amenewa achoke,akadakhala APM tonse tikanakhala tili ma demo,awa akungokhala let's stand together malawi it's our duty to save our country
GENERAL ELECTION IN MALAWI IS ALWAYS CONDUCTED AFTER 5 YEARS. IT TOOK PLACE IN 1994, THEN 1999, THE 3RD ONE WAS DONE IN 2004, THE FOLLOWING WAS IN 2009, THEN 2014, AND THE RECENT ONE WE WENT TO THE POLLS IN 2019. WE THEREFORE EXPECT THE SUBSEQUENT ONE IN 2024. MALAWIANS GET READY FOR GENERAL ELECTIONS IN 2024. MEC COME IN THE OPEN AND DO THE NEEDFUL.
Vote MCP BOMA ILOO❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉😂KWACHA KUTI MBEE KWA HIS EXECELLENCY DR LAZURUS MCCARTHY CHAKWERA WAMUYAYA TILI PAMBUYO PANU PULEZIDENTI WAMUYAYA MKANGO WA MALAWI WABWINO.
Koma kumwopa mulungu ulamuliro wuu Amalawi mwaniyika pa moto.Si mkutifunila za mwino hata .Chimanga chafika pa K15000 this is november uli ikafika december tigula zingati Amalawi.Zoona all Malawian is suffer for every things .Mkulu ameneyo watipa Amalawi .
Let's try to vote for someone raised from a rich family oti sanakule movutika waphunzilapo kunja akafuna holiday amapita kuja using ndalama za makolo or zake or ngati azizaba azizangoba coz ndalama sizikwana koma awa okula movutika okulila kugwila utaka fumbi awa azingotizuza chonchi maulendo ongofuna kukaona kuja kuba ndalama poganiza kuti mmene ankavutika anthu ena anali kuti nde basi osaganizila ena I need full biography ya chakwera guys
ViVa-UFF
This is Great Voice Comrade Mr Game Changer ViVa don't lose hope
Father in Heaven will help us to protect our Fellow Malawian.
Ngati amalawi sitikwanitsa kumuchotsa chakwera chifukwa cha deflation iyiyi, sadzatheka kumuchosa ndi mavote coz ndi MCP yokha imene ipange kampeni next year and mmalawi akangopatsidwa kanthu amaiwala zakale check out the lomues
Zoona zeni zeni,amenewa achoke,akadakhala APM tonse tikanakhala tili ma demo,awa akungokhala let's stand together malawi it's our duty to save our country
Amene akusapota cha kwela nd anthu akumidima okhaokha
Ameneyu nde game changer more fire tiyese inu aborn atitopesa maboza
we follow you MR Game changer. tikudikira kuvota 2024 no mater what
Very true azipita bas tatopa nawo mavumbe amenewa achoke
Powerful points from you Mr Gem Changer Mtholo chikuni cha Usi, apapa zafika posapilira tsopano.
That's great speech mulungu akhalenanu dziko laipa koopsa zomvesa chison
Kumapeto kwa mwezi uno kwatalika akamabwera Akafika Ku air port asafikire kustate house ayangane kopita sakufunika watopetsa
Ndipo omenyela ufulu akewa sali serious amwene, akuti kumapeto Kwa mwezi uno kapena kumayambiliro kwa mwezi wammawa tikupanga mademo, what's that!?.
Zikufunika kuti asabwelenso komwe aliko and ngati angayelekeze kubwera kwathu kumalawi kuno, azapeze titatseka ma airport onse, komanso nyumba zathu zaboma tikatseketseke, and izizi kuti zitheke zitengela apolisi ndi army yathu yopoilayo kukhala nafe oazochitazi.
NAMALENGA ATITHANDIZE NDIKUTISOGOLELA KUTI NKHONDO IYI TIYIWINE BASI, AMEN AND AMEN!,
Umodzi ndi umene ukusowekela,kulakhula sikungatipase chiyembekezo
Chakwera and chilima mukudzuza amalawi 😢😢😢 panya panu
Game changer taika chikhulupiro mwainu
Nyimbo pansewo pali nyimbo iyi, timalidzeni watimpha kare chakwela timalidzeni watimpha kare chakwela
Mademo akayambile Ku Lilongwe osat Mangochi please gyz let's go together
Allah bless you and your family mwavek kwambil big man
Osapagiratuu bwanji mene katundu wakwerera muz mwez athu akhara azorowera mitengo..zimafunika week ino😢😢malawi wanga😮
Iyeyo chakwerayo akuyenera ature udindo pas watikwana
We're going to support you Mr game changer.
A malawi ndi anthu onvesa chisoni matha too much koma tikhuphinjika, if we can stand up as one we can declare this nonses zopusa basi.
Count me in ndikufuna kulowa UFF
It is end time events Yes but these thieves has done a greater part of our destruction...
Good Message big man achoke
Mudzina la yesu chakwera anchoke atule pansi udindo
Big love brother ❤❤❤
Tiyeni tilimbe mtima tipite kusewu, tiwonetse kukwiya kwathu
Watutu kale panopa si presedent nso ayi Lest in peace chakwela 😭😭😭
GENERAL ELECTION IN MALAWI IS ALWAYS CONDUCTED AFTER 5 YEARS. IT TOOK PLACE IN 1994, THEN 1999, THE 3RD ONE WAS DONE IN 2004, THE FOLLOWING WAS IN 2009, THEN 2014, AND THE RECENT ONE WE WENT TO THE POLLS IN 2019. WE THEREFORE EXPECT THE SUBSEQUENT ONE IN 2024. MALAWIANS GET READY FOR GENERAL ELECTIONS IN 2024. MEC COME IN THE OPEN AND DO THE NEEDFUL.
Vote to 202_
Vote to 2024
Vote MCP BOMA ILOO❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉😂KWACHA KUTI MBEE KWA HIS EXECELLENCY DR LAZURUS MCCARTHY CHAKWERA WAMUYAYA TILI PAMBUYO PANU PULEZIDENTI WAMUYAYA MKANGO WA MALAWI WABWINO.
Nga ngaa pambuyo pa mkango wa Malawi WAMUYAYA chakwera tili pambuyo panu nga nga nga
Komanso mulungu athenge mbali chakwera waononga dziko lamalwi
Pangani action Mr game changer osat enawa akungolubwalubwa
Tiyambe kumenya majaji komanso kodwani nankhumwa chifukwa aguru amenewa ndiamene akuchititsa osadandaula tiyamba kuocha manyumba amajaji komanso leader of opposition
Tigwilane manja pochosa agulu amenewa😢
enough is enough achoke ana anjoka zinkhanira zoyipa kwambiri ndipo amene akupanga support chakwera ndi fiti zotamba masana
Amalawi anthu aku south africa samadikila kuchotsa president ndima vote ngati zinthu sizikuyenda, kodi amalawi uchitsilu udzatithela liti please kumangokhalila kumangoyang'anila matudzi ngati amenewa a chakwera akununkha chonchi, Eish
Koma kumwopa mulungu ulamuliro wuu Amalawi mwaniyika pa moto.Si mkutifunila za mwino hata .Chimanga chafika pa K15000 this is november uli ikafika december tigula zingati Amalawi.Zoona all Malawian is suffer for every things .Mkulu ameneyo watipa Amalawi .
Munthu mmodzi avutitse dziko lonse zoona palibe ali ndi mfuti kodi akuluakulu uyutu akufunika chipolopolo kuyankhulaku sangamve ndi Satana uyu
Ilipo big man mukufuna bwelani mutenge big
Malema number 2 in malaw
Even thoughtl the situation sili bwino pazapezekanso zisilu zina akamabwera Komwe wapitako azikavina kumunyadira zisilu zimenezo
Azimayi ndi anthu opusa kwambiri akamabwera azikufusa IWe ndalama ya ndio
zinthu zafika povuta. Chakwera alibilethu nzeru. Koma vuto lathuso ndikuchepa nzeru kwathu a Malawi 🇲🇼 tikufuna tiyikeposo Peter Muthalika oyipa. zikuonetsa kuti timakonda mavuto a Malawi. tiyeni tiyensekoso ena omwe sitidawayesopo kale.
Big up UFF use the law of impeachment
I am with you... Let me know your meetings zachikape izi
2024 ,ndi General Election afune asafune awonjeza
Wathawira ku Igupoto akokedwe abweleko azachite feel the stuation this called president
Achakwela pam'kholopanu
Mbudzi iyiii ndithu ichoke
Yaaaa galu iyi chakwera achoke pamene uyu palibe chomwe akuchita
Utokotatu utopa iweyo but nothing tangible uziona
Nkhani yaikulu ndi mantha kwambili malawi, maiko akunja sapanga zibwana ziiii. Komanso asilikali athu kodi akuti poo chiyani mwina zao zili pabwino? Cause maiko ena olo asilikali amakhoza kulanda dziko ngati president asakulamula bwino.
Yehova atichitile chifundo plz
Asilikali athu ndimanyi enieni angoyanyanila zonyansa zikuchitika
Mwalankhula bwino ndithu. Kambiranani nd a president athu aKalindo mupange mademo non stop. Kma mukanakayambira ku Lilongwe konko
Atupele Muluzi ananena kuti achakwela awa sangayendetse boma sadziwa kuti boma limayenda bwanji.
Chakwela ndi mbuli ndipo anakula moyo usaikitsika kwmbili nde apa anangobwera kudzaba
Matembelelo amulunga akhale pa chakwela 😢
Bad luck for Malawians we don't have MDF even police because there is no any action from them (this is big nonsense)
life is too hard nowadays. malawians must do something
Changa chikwanje pakhosi pa sakwela
Koma asilikali akutani koma guys
❤❤❤❤❤
Maka a police awa at akugwilabe ntchito za boma. Ndachoka ku malosa lero kubwera Blantyre tadutsana ndi a traffic ma station 7 zachani
Nanuso zikayamba kuchitika panopa akamabwera akapeze kuli moto Kuno ka 😢😢😢 kumapeto amwezi kwatalika mademo amafunika osachedwa muganize bwino pamenepo
Mau amenewa, asilikali, ndi apolice, amenewa ndi odikila kutumidwa bas, Koma mavuto alipo
koma phuma eeeeeeehhhh!!!! no man is an island, u cant do mademo wekha without ur fellow activist.
Time is getting for huder
Mbuzi zamanu
Awudzidwa Kuti walephera akuyenera kupita kustate house
Takango funani futi tatopa ndi usilu
Mbuzi za asilikali
@@lewisbonongwe8518 zi asilikari dzopusa mu Africa ndi dza malawi
That's game chager I know
Let The DC joined UFF
Koma chakwera uyu a kuononga dziko tonse tikuona,,,, maiko azathu ngati Kuno ku south Africa sangapange manyi akewo mpaka atapilikitsa,,
Komanso ndimaganiza ngati m'mene constitution imanena kuti chisankho chapatatu zidakhala bwanji kupanga cha president chokha
Tiyeni tiyende pansewu chakwera awononga Malawi ife tikukanika kukhala mziko lokhala lathu chifukwa Cha mavuto
Tilipambuyo panu osafooka.
Koma akulu akulu kunena mwachirungamo Usogoleri wa chakwera ndiosathandidza pachilowereni m'boma mavuto okha okha nankha taonani chaka chino za macoupon zomwedxi ndi anthu ochepesesa omwe apedza pomwe maboma ambiri kulibe kusowa forex fuel chimanga kukwera kwazinthu kuphedwa anthu chitetedzo kulibe ndiye upresidernt wachakwera uli pati ?chakwera akuyenereka kuchoka 😂😂😂😂😂😂
Nanuso amtolo kulslata nkuna mulungu anakupasani mau wogotha mfundo mulibe nenani fundo yeyeni not kubwe bwetuka waka
IFE TIRI PAMBUYO PANO MR. GAME CHANGER KOMA MUGWIRIZANE NDI THE DC BON KALINDO PRESIDENT WA MALAWI FIRST, THE PEOPLE FIRST.
Tili pambuyo panu mr
I agree with you vote to 2024 woyeeee
Kalindo takhumidwa naye. Zowona kutiyika pa drama kufuna chuma. Ndataya nthawi kumusapota
Amalawi akuvutika kowophya
Mawu amphamvu kwambiri, inafe tilowa mtengo tigwetsa anthu onse oipa
Moyo wafika povuta kwambili ndikufuna ndifunse kodi tingadziwe bwanji mtsogoleli wabwino wolamulila dziko woyang'ana mavuto anthu?
Yehova ndi Yesu basi. Yeremiya 10:23 read
Let's try to vote for someone raised from a rich family oti sanakule movutika waphunzilapo kunja akafuna holiday amapita kuja using ndalama za makolo or zake or ngati azizaba azizangoba coz ndalama sizikwana koma awa okula movutika okulila kugwila utaka fumbi awa azingotizuza chonchi maulendo ongofuna kukaona kuja kuba ndalama poganiza kuti mmene ankavutika anthu ena anali kuti nde basi osaganizila ena
I need full biography ya chakwera guys
Achoked garu ameneu
Tatopadi vote ndi ,2024
Anthuwa ndizithumwa zochokelakwasatana atikwana azibwelela kwao kusataniki
Ashoke abusa opanda manyasi ngati simany
Enanuso mutola chikwama ndi mademo omwewa .Wina kukatayako moyo.
Apolisi ulendo uno musamale ilipolipo
Manyi ako iwe usatisokoseko apa
Mulungu azakhala mpomp siku limeneli
Dziko lamalawi likufunika kuganiza kwambili zakutsogolo
👍 show
Pantumbo pako sulimalawi muno ukana khala kuti uli muno sungalembe zapantumbozi ikudziwa kuti kino nima wafika pa 500
Tatopa ndi a dlees yawoyo,ngati boma la Malawi atopa,achoke,basi.tinawasankha, ngati achita zazelu,achoke a chilima a chakwela achoke basi.
Every politian is a liar. Malawi needs togetherness
Chakwera ndi onse ma am'boma boli zamanu agalu Anu ndi chilimayoso
Useless president and his government 😂😂😂
Awuzeni
Big ukali
Mademo achiteke bass chakwela achoke
Mfiti tilipo ambiri
Anthu awawa onse panyo pawo ndithu
Ulemu wanu madala
Zoonad mchimwene
Tiyeni timatche basi