KWACHA KUTHERATU UKU ,, TANVAN KULIRA KWA AMALAWI UKU

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 3 гру 2024

КОМЕНТАРІ • 81

  • @NKHANTV
    @NKHANTV  Рік тому +2

    Hello
    Takulandirani pano pa NKHANI TV
    Chonde osayiwala kupanga subscribe
    Ngati mwapanga kale , mulungu akudalitseni

  • @isaackinod1256
    @isaackinod1256 Рік тому +2

    Osaiwala Born Kalindo tiyende naye limoz Monga president wathu💪

  • @TisaiwaleTewesah
    @TisaiwaleTewesah Рік тому

    Am sporting good working Sir ❤

  • @CJAY-kx7eu
    @CJAY-kx7eu Рік тому +2

    Don't 4get please osaikam a mnulo ad Ben longwe musaikem ngathi simukufun kuyaluk please

  • @FiannaFiannakaponda
    @FiannaFiannakaponda Рік тому +1

    Ayi Malawi 🇲🇼sali mwakale mulungu achite nawe chakwela chifukwa sudabwele kukalamulila dziko koma kukaononga Malawi wathu zaka zochepa zonkha😭😭😭😭😭🙌🙌🙌😊

  • @jonathanmbewe4246
    @jonathanmbewe4246 Рік тому

    United Freedom Fighter # UFF zabwino zonse abigy

  • @LaurentAmbassador
    @LaurentAmbassador Рік тому

    Game changer mwafika we as malawian we never get tired we are at your back

  • @HamidahshaibuHamidah
    @HamidahshaibuHamidah Рік тому

    Tili pambuyo panu💪💪💪💪💪💪💪

  • @thesocietynews3181
    @thesocietynews3181 Рік тому

    We work together to bail out our country Malawi. Keep up good work Mr Game Changer

  • @YusufNdege-o2u
    @YusufNdege-o2u Рік тому

    Akaone airpot yake yomwe ndege from soud arabia ikatere.

  • @PreciosNdlovu
    @PreciosNdlovu Рік тому

    Yilakwe yilakwe .Diso pa Diso i cant wait kumadermo

  • @MatildaTatos
    @MatildaTatos Рік тому

    More Fire UFF tailandila ndi manja awili Movement imeneyi and we will support you. Thanks

  • @AlexKaunda-x3p
    @AlexKaunda-x3p Рік тому +3

    Chekwera mbolo yake sure 😢😢😢

  • @alexandermwale4669
    @alexandermwale4669 Рік тому

    Welcome game changer

  • @AngieJulla
    @AngieJulla Рік тому

    Game changer for sure.

  • @ChifundoJohn-w3t
    @ChifundoJohn-w3t Рік тому

    Amen man of God

  • @sharifujoe7633
    @sharifujoe7633 Рік тому

    We're in broh

  • @GivenLongwe-j3r
    @GivenLongwe-j3r Рік тому

    Apo zithu sizili bwino president tilibe akadasisa fetereza kt athufe tilime koman akapanda kutelo atule pasi udindo😊

  • @Mannet-uf5
    @Mannet-uf5 Рік тому

    Tilikomko

  • @MaxwellBanda-xd6oh
    @MaxwellBanda-xd6oh Рік тому

    Go ahead please don't scared of president please fight for people

  • @HenlyMakawa
    @HenlyMakawa Рік тому

    Kodi ndiumfuti wamtundu wanji omwe wapanga chakwera,agame changer takulandirani kwabas komadi amalawi tizachangamuka liti? bwanji osapanga zoti munthu ameneu asafikeso mdziko lino tiyeni tidzuke

  • @AndrewAsanChipangaya
    @AndrewAsanChipangaya Рік тому

    zachabev bas chakwera atipha uyu

  • @nditumenichagunda4192
    @nditumenichagunda4192 Рік тому

    Inunso mukufuna kukhutisa mimba zanu ndizokhazokhazo Malawi si ife opusa muli ndi mau abwino muzingolalikila yehova mwamutchulayo

  • @VirgilioThinfu-br1jz
    @VirgilioThinfu-br1jz Рік тому

    Oooooo!!!!

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 Рік тому

    Ku malawi kuno tonsefe ndife zisiru, palibe angazitchure wanzeru this is y this government is mis treating malawians, chakwera mbuzi ya munthu kwabasi.

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete Рік тому

    Big love brother ❤❤❤❤❤

  • @WinesiMbalaka
    @WinesiMbalaka Рік тому

    Achoke chakwela
    😢😮

  • @LuckyKaponda
    @LuckyKaponda Рік тому

    Game changer

  • @LingstonWatison
    @LingstonWatison Рік тому +1

    Our MDF is useless

  • @PreciosNdlovu
    @PreciosNdlovu Рік тому

    Koma apa ndiye ndichikunidi chausi .welcome apa ndiye chiyembekezo chilipo .osati Akalindo kumakapezka ku hotel .kumisonkhano ya Mcp omvetsa chisoni.
    welcme Mr game change

  • @YusufNdege-o2u
    @YusufNdege-o2u Рік тому

    Panopa apolisi tikuphani zed muonanso maliro maliro

  • @chisomockuwa6869
    @chisomockuwa6869 Рік тому

    Tilinanu pambuyopo 💪💪💪💪💪💪💪🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @hastingsedward9873
    @hastingsedward9873 Рік тому

    Munthuyu mungo mutukwana koma vuto ndi lija adanena abingu wamuthalika kungolora ndalama yanthu divalie chilichose chidzakwera adayaluzira olo tomato ndiye adavomeleza divalie ndi chakwera mmm tisa lowetse ndale amalawi

  • @IbrahimDailes
    @IbrahimDailes Рік тому

    Eash zomvetsa chisoni srs dziko lanthu linali bwino akupita nalo kt abale. Let's fight now srs Chakwela resign plz we're tired with you.

  • @LacksonKalawa-co2ms
    @LacksonKalawa-co2ms Рік тому

    Chakwera ndi mbuzi ya muthu coz he don't think about poor people

  • @Donnex-f2d
    @Donnex-f2d Рік тому

    Nkhani koma imeneyo tilikomko

  • @hastingsedward9873
    @hastingsedward9873 Рік тому

    Azanthu akuzambia sadapite pa mseu adangochotsa ma zilo ku ndalama yawo pano chuma chawo chimayenda bwino mudapindulapo chani ndi mademo

  • @HildatoweraMhango-et4mz
    @HildatoweraMhango-et4mz Рік тому

    Tili mbuyo mwanu please pangani zinthu zoti zipulumutse malawi yathu

  • @alicephiri3706
    @alicephiri3706 Рік тому

    More fire tiri pambuyopo ulemu kupha

  • @johnman4619
    @johnman4619 Рік тому

    Ife tikufuna sandrass juma

  • @IshmaelNesta-rb8dx
    @IshmaelNesta-rb8dx Рік тому

    UFF...here we go....tiyankhuleni...

  • @ElizabethKazambwe
    @ElizabethKazambwe Рік тому

    Chichewa chabwanji ichi ma dzi,dzi pena palupose

  • @CJAY-kx7eu
    @CJAY-kx7eu Рік тому

    U well come big man malema

  • @HamidahshaibuHamidah
    @HamidahshaibuHamidah Рік тому

    Zoonad

  • @PreciosNdlovu
    @PreciosNdlovu Рік тому

    Akalindo anagulidwa ndi Mcp .chonde yesesani kuti tichoke pamoto.Takulandirani iyi yikuoneka kuti yafikadi ndimoto .Game chager welcome sizakalindo timawadalira aja pano anawapasa chibanzi chachikulu.Born kalindo 😢😢😢😢

  • @SheenahMwalabu-iz3pr
    @SheenahMwalabu-iz3pr Рік тому

    Mulitu slang mwainu 😂😂 welcome

  • @ibullahim
    @ibullahim Рік тому

    😂😂😂😂😂😂mwapya mtimattu eeeee😅

  • @DoricaGoweka
    @DoricaGoweka Рік тому

    Watiphaaaa chakwera munthu osamva chisoni ndi kulira kwa a Malawi

  • @stevechizaka9908
    @stevechizaka9908 Рік тому

    Pangani zotheka kuti mbuzi imeneyo ichoke 😮😮😮

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu Рік тому

    Mukulankhula bwino, koma zitheka? Mumayamba bwino koma mmmmm mumasokonekela mkatikati nga a kalindo.

  • @AfickPhonex
    @AfickPhonex Рік тому

    Koma ngati ndikotheka konzani mademo kwacha iyi ibwezeletsedwe pompaja sizoona zinthu kukwera double double mmmmm chonena ndilibe mmmm

  • @AYATU730
    @AYATU730 Рік тому

    Iwe chakwera machende ako ndi azigogo anu ose

  • @DCpangolin
    @DCpangolin Рік тому

    Mmmmm km kuvota 2025 mmmm atimpha ndioipa

  • @phillimonzgambo1663
    @phillimonzgambo1663 Рік тому

    Komo where is Malawi MDF to close this government please we are die Now ,if someone will hits you Mr to the demo time and also you must do

  • @neemahkapatamoyo9563
    @neemahkapatamoyo9563 Рік тому

    Izidi zikufunika Malawi yonse ikhale pamodzi kumubudula munthu ameneyo tivoteso hiya 2025 ndikutali 😢😢 atithatu munthu uyu alibiletu mzeru chakwela angokhala ngt chitini chobowoka

    • @NnoxyMtchessie-mp7yw
      @NnoxyMtchessie-mp7yw Рік тому

      Achoke watitopesa chakwera 2025 kwatalika kwambili tipange ma demo BC achoke bc

  • @JamesChimera
    @JamesChimera Рік тому

    Mukungolema musanza ndulu ndi kulankhula or inuyo mutayimapo lero pautsogoleri nothing canchange to the better zinayambikakale

  • @Danv-b7v
    @Danv-b7v Рік тому

    Tifa Chaka chinu

  • @GiftChadika-he7nd
    @GiftChadika-he7nd Рік тому

    Km chakwera iweyo mbolo Yamato amene anakubeleka,,,ukuzuzilanji anthu galu iwe kapolo iwe usadzafe wava wazuza ntundu wa amalawi kwakwana machende ako😢

  • @JamesChimera
    @JamesChimera Рік тому

    Anzanu zawakanika inu mukufunanso chanu chithumbacho koma sikuti mungasinthezinthu koma njirazofunira chuma

  • @marthansaliwa7732
    @marthansaliwa7732 Рік тому

    Apulewa analowa satanism ndimchoka samva langizo lililonse.

  • @DaudBonomali
    @DaudBonomali Рік тому

    Agaru amenewa anangobwela kuzanyeranyeramo m'bomamu akamachoka kuti ena adzawasiyile manyi okhaokha chakwela chilima pamodzi ndi tonse aallayasi mapadzianu agaru achabechabe sindikukulupilila kutinso a Saudi Arabia apatsa ndalama zimenezi komanso asawapatse chifukwa zikhala zakampeni amakanjiraonso mutu wambuyayo pamodzi ndi chambo komanso feegii maulana chematola

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda9830 Рік тому

    Kkkkkkk anthu akunena zoona kuti Chakwera sizinthu ena akuchita makani kulodzedwa

  • @FrancisDay-br7xb
    @FrancisDay-br7xb Рік тому

    Bon kuli zii

  • @folamitowing238
    @folamitowing238 Рік тому

    I chifukwa ndichifukwa chake Europe inathandizira kuti MCP kuti iloww m'boma chifukwa DPP inkakana kutsitsa mphamvu ya Kwacha.

  • @owenskabazanechiumia3543
    @owenskabazanechiumia3543 Рік тому

    Nchifukwa chache ndinangochoka pa Malawi A game changer, chikuni cha Usi, mulimba?? Anzanu Akalindo salinso mwakale pano, atabwera ku Sochi Boma li, ndi katakwe wogula ndi kuhonga ma Activist 😂😂😂😂

  • @GiftMaganga-o1i
    @GiftMaganga-o1i Рік тому

    Pitan kulilongwe mangochi ai

  • @HamzaChisale
    @HamzaChisale Рік тому

    Zinthu sizikuyenda management sikuyenda bwino mopanda kulankhula mobisa zatibvuta basi

  • @MustapherKassim-u8e
    @MustapherKassim-u8e Рік тому

    Vuto mumangoyankhula koma mupanga zitela mmadzira

  • @AugustineMwamadi
    @AugustineMwamadi Рік тому

    Kkkkkkkk koma mpakabolo yamache eeee wawonjeza mpaka lumuchula mbolo kkkkkkkk mpaka zowona mbolo ya amake eish ugwidwe basi chakwera mbolo ya make me kkkkkkkeish mbolo ya amake zowona mbolo ya amake eeeee ndawopa😅 ulemu ndi ofunka mbolo eeeee

  • @TrizaGeorge-q8w
    @TrizaGeorge-q8w Рік тому

    Ambuye atithandize 😢😢

  • @SamuelMchenga-b7z
    @SamuelMchenga-b7z Рік тому

    Achoke basi

  • @nellikkmwenda7087
    @nellikkmwenda7087 Рік тому

    Ulemuwanu atate mulungu akudaliseni

  • @ShaibuJames-s9l
    @ShaibuJames-s9l Рік тому

    Nanugagweleniwuuko anapakudyainu mwatikwana

  • @PrincellarJonathan-bd3xg
    @PrincellarJonathan-bd3xg Рік тому

    AM WITH U GUYS ❤UFF

  • @joicemartin-ji5zu
    @joicemartin-ji5zu Рік тому

    Ladzaro kukukamwa ngati wadya manyiii onyedwa kumene Kodi ukufuna Anthu afe iwe ndiwe ndani unawalenga Anthu ndiwe ndiwe Mulungu zomwe ukupanga mulungu akukuona satana iwe okumwa magazi wasatanic Iwe magazi sanakukwane kumpingo kwanuko ladzaro ladzaro ladzaro wapha anthu wasatanic samava chisoni eti

  • @patrickndojime1632
    @patrickndojime1632 Рік тому

    Chisilu cha munthu eeeechii kwabasi akubvutisa anthu anthu kumalawi ine sindikadabvomeleza zopusa izeeeee akumufuna Chakwera simunthu wa satanic uyu asamatisokoneze akufuna magazi basi makolo onse azintha ndikumwalira

  • @eliasMwamba-q5f
    @eliasMwamba-q5f Рік тому

    Tili pambuyo panu big,mfiti imeneyi ikutiyamwa kwambiri

  • @AgnesMatola
    @AgnesMatola Рік тому

    Zikomo kwambiri ,Ambuye akhale nanu....

  • @GiftFrancesco
    @GiftFrancesco Рік тому

    Tiyen tigwilane manja Koma please osatkhumudwisa