KODI IFE NGATI AMALAWI TITANI KUT TITETEZE DZIKO LANTHU LA MALAWI ? // BEN LONGWE

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 4 гру 2024

КОМЕНТАРІ • 69

  • @NKHANTV
    @NKHANTV  Рік тому +1

    Hello
    Takulandirani pano pa NKHANI TV
    Chonde osayiwala kupanga subscribe
    Ngati mwapanga kale , mulungu akudalitseni

    • @YohaneChinthomba
      @YohaneChinthomba Рік тому

      Kulakwa kwanu linabwera kamba kophatikizana ndi winiko

  • @ThomasTrein
    @ThomasTrein Рік тому +1

    Zona zake mr longwe

  • @MdEliya-yx8qj
    @MdEliya-yx8qj Рік тому

    Mwanveka uncle Ben,, pano pa Joburg ine mwana wa kwinu waku mzimba boma, vuto ndiloti ife ovutika tlibe mphamvu osadziwa ndi umbuli wa ife aMalawi timadana ndi chilungamo zikundi Wawa Kodi zimene amanena abambo athu ankati uza ngati history pa nthawi ya kamuzu lelo tikuzi wona ndi moso sorry aMalawi anzanga ine Ndi indipendence freedom fighters mundimva musogolo mu ndine mwana koma mawu anga muzamva nthawi yolankhula ine ndi Eliya chirambo, mwana wa ku nzimba I over now thanks Uncle Ben, ndili pambuyo panu

  • @JohnConar-kq4hi
    @JohnConar-kq4hi Рік тому

    ✊✊✊✊✊✊🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @anthonysawa2039
    @anthonysawa2039 Рік тому

    Ben nkanakonda ukanabwera kuno what you are talking is wise Bon kalindo ali ziiiiiii

  • @gwee967
    @gwee967 Рік тому

    Mr Longwe, mukuyankhula monyozanso anthu omwe muktfunsa maganizo. Mwatitchula kt tizaganiza mopepera, mopusa etc. MWatulutsa zichewa zonyoza ife omwe mutifuna kukhala kumbuyo kwanu. Amatero. Amwene, tangobwerani tizathandizane nkhondo yi. Siziphula kanthu mukamatokota muli ku Joniko. Palibe chomwe tipindulepo mukamatokota muli kunjako

  • @GiftMatimati-x4l
    @GiftMatimati-x4l Рік тому

    Ben longwe timqkudalira pls kambilanani muyambe kugwiraso ntchito limozi mudali maso amalawi pls pls

  • @MedsonLossan
    @MedsonLossan Рік тому

    Bro, this is the time of liberty Mr Longwe. Everybody have seen him/herself. We need to go on the street as soon as possible.

  • @JohnConar-kq4hi
    @JohnConar-kq4hi Рік тому

    Later fight again amalawi okaoka guys this is home landi😢😢😢

  • @HusseinKachala-ml7ut
    @HusseinKachala-ml7ut Рік тому

    I agree with you Ben kuti amalawife nditiwanthu topusa kwambiri and sitimadziwa chomwe timafuna pamoyo wathu.
    Sitili ngat tiwanthu tammaiko enawa toti tikangoti tsiku lakuti mademo!, Tiwanthu tonse timatuluka mmanyumba mwawo, S.. AFRICA', ZIMBABWE, imatuluka yonse!, Koma mmalawi amangopanira mchira wake ngati galu

  • @BouWnder-js5to
    @BouWnder-js5to Рік тому

    Zoona 😊😊😊😊😊

  • @AbuOsman-ts6ef
    @AbuOsman-ts6ef Рік тому

    Angogwizanani basi pitani mu Lilongwe mo😊

  • @denndavie6041
    @denndavie6041 Рік тому

    Tiyambe kupha atsogoleli andale opusa. Maka maka tiyambilile a opposition amene anagulidwa.

  • @MunillLasheed
    @MunillLasheed Рік тому

    wapagrawundi bas

  • @HusseinKachala-ml7ut
    @HusseinKachala-ml7ut Рік тому

    Ben and Munlo please pangani zoti malawiyu asakagwele kuphompho, pomwe zafikapa osamuphatikizanso kalindo ayi chifukwa kalindo ndimthira kuwiri and ndamene akuonongesa mademo mmalawi muno.
    Please, tell Munlo kuti mademo ayambilenso mmalawi muno and we don't need kalindo kumademo omwe ati ayakewa

  • @RAJABUALLIE
    @RAJABUALLIE Рік тому

    Asilikali aku Malawi Ali kt? Kugona bas

  • @HusseinKachala-ml7ut
    @HusseinKachala-ml7ut Рік тому +1

    Ife nde tikupwetekela zaweni coz zitsiruzi tidazikana koma amalawi nomwenu ndomwe munazisiya pampando, lero siizii!?, Mukutipweteketsa ife

  • @montymilanzi5664
    @montymilanzi5664 Рік тому

    Kodi mmesa mumkati simuzakambanso khani zokhuza malawi?????

  • @NELSONFERGUSON-j5w
    @NELSONFERGUSON-j5w Рік тому

    So kumbali ya ma demo Ben longwe panopa mademo akufunika kwambili

  • @VictoriaKumwenda-k6o
    @VictoriaKumwenda-k6o Рік тому

    Iwe ben ukuyankhula ngati chani kod kutukwana ndi kwabwino mau amulungu akuti chani

  • @WhitefordZenizeni-io8ev
    @WhitefordZenizeni-io8ev Рік тому

    Ayi kulakhura khani ndikumvana ndikupanga chimodzi

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc Рік тому

    Kuyankha topic imeneyo,musiye kulankhulila zipani kufuna ndalama.munayambitsa,chipani koma simugwilidzanako, chifukwa chofuna ndalama musiye dyela tikuvoteleni

  • @georgednthala-wh3pf
    @georgednthala-wh3pf Рік тому

    Zoona Ben koma kutukwa doesn't show anything apart from uchitsilu, kupanda nzeru, kusiwa zonena koma umunthu Kwa munthu amene akuyankhulayo. Utereku munthu utukwana or ataoereka ntundo yabwino bwanji people ignore him.

  • @MalawiMalawi-x8c
    @MalawiMalawi-x8c Рік тому

    Komad mwanena Dzoona Eeeeeee watimpha ife mmmm 19:35

  • @AbuOsman-ts6ef
    @AbuOsman-ts6ef Рік тому

    Dziko lagulisidwa kare

  • @ROBERTMUKHAYA
    @ROBERTMUKHAYA Рік тому

    Big up brother that's true I support the motions

  • @KhadijaLifa-ny6yo
    @KhadijaLifa-ny6yo Рік тому

    Pangani umozi bon kalindo

  • @GeraldMustafa
    @GeraldMustafa Рік тому

    Kulibe kumalawi osusa boma ndi chifukwa chakwera akupanga zomwe angafune

  • @jonathanchiweza3543
    @jonathanchiweza3543 Рік тому

    Malawi first zina zonse pambuyo .tiyeni tigwirane manja mu umodzi muli nzeru

  • @NehemiyaSoko-es6ru
    @NehemiyaSoko-es6ru Рік тому

    Yang'anani kumwamba kwa Mulungu mupeza mtendele

  • @HusseinKachala-ml7ut
    @HusseinKachala-ml7ut Рік тому

    Mkhuyu zodya ana zidapotadi akulu, ife agulewa tidawana kwamtuu wagalu

  • @alexandermwale4669
    @alexandermwale4669 Рік тому

    Zinthu zinali bwino pa nthawi ya malawi first koma kutha kwa malawi first chakwera watengapo ma chance mmm my malawi 😢

  • @gwee967
    @gwee967 Рік тому

    Anakusankha ndani kt uzitiyankhulira? WAbisala ku joni nkumatukwana ife omwe ufunanso tikhale pambuyo pako? Ziipanga zaku Ukraine and Israel. Za kuno zisiye tithana nazo tokha. Munthu wamantha, wonyoza and or otukwana sitikumufuna. TAKUSIKA

  • @MariamBanda-p9t
    @MariamBanda-p9t Рік тому

    Kumalawi mademo sangayende bwino. Chifukwa anthu omenyera ma ufulu angofuna kukhutisa mimba zawo

  • @Ruth-y5q9n
    @Ruth-y5q9n Рік тому

    Nonse amene mumati muli ndimagulu omenyela ufulu tikukupasani masiku atatu kuyambila lelo loweluka pa 10 nov ngati sipapezeka gulu ngakhale limodzi lopanda kuulusa tsiku lopanga mademo ndziwani kuti maufulu mumawanenawo muzizamenyela amanu kuteloko apa mukudikila kuti papite mphepo ndiye muziti tiyeni kunseu muzapitako ndiamanu nthawi ndiyomweyi ngakhale mutati mawa tituluka mwaunjinji nawenso ben ife tatopa ndi ma oudio wa tapangani zoti olo mawa tipite panseu zolankhulazo pano zikutitupisa makutu tatiyeni kumseu

  • @CJAY-kx7eu
    @CJAY-kx7eu Рік тому

    Ben longwe bwela kumalaw osamagoyakhul mle out off Malawi ngathi muli crc bwra kuno osamaglalata muli Deben

  • @LaynaAdam
    @LaynaAdam Рік тому

    Chakwela anagulitsa kale nyasaland yu

  • @bernardchithumba6040
    @bernardchithumba6040 Рік тому

    Ifetu zativuta basi koma ngati mkotheka Asilikali alande boma basi

  • @VictoriaKumwenda-k6o
    @VictoriaKumwenda-k6o Рік тому

    Uchisiwo wonyoza anthu mmalo moyankhula fundo ndalama zikupwetekani aben mnanena kuti mwalapa kodi manalapad kom izi mazisiya koma mkapye chifukwa chotukwana ndi kunyoza mulungu sangakondwele ndi zimene zikuchitika nosenu mwasandu asatana palibe wabwino

  • @oliviamphande1900
    @oliviamphande1900 Рік тому

    Tipange mademo bwana

  • @KenedyBizwick
    @KenedyBizwick Рік тому +2

    Beni longwe mwayambilatso kulankhula zanzelu, osalimbana ndi bon kalindo, ngat the DC mukumuganizila kt wapanga corruption mutayen koma muzipanga zothaniza amalawi.

  • @Ruth-y5q9n
    @Ruth-y5q9n Рік тому

    Olo utatukwana olo osatukwana
    Koma tikuti tapangani zoti mawa ndiye siwafunsa kuti titani diye tikuti pangani mademo ngakhale atakhala mawa abomawo ayala mphasayo chifukwa chauchisilu wainu amene mumati ndinu omenyela maufulu anakuwelengani kale kuti inu kwanu ndikukuwa basi palibe chimene mungachite apanso timaona ngati kuti mwina kucha kwalelo timva wina akutiuza zasiku lopita kunseu koma kudabwa aliyense akungobwebweta apa

  • @JoãoChirwa
    @JoãoChirwa Рік тому

    Takambilanani ndi azako bon Kalindo Kt Ife tizikudalilani usamalimbana ndi zithu za ziiii

  • @jamusnamwino-br2iz
    @jamusnamwino-br2iz Рік тому

    ndizoona mukuyangulazo

  • @JusticeKawilira
    @JusticeKawilira Рік тому

    Bwana apatu ndizongofunika kupanga ma demo Koma otsogolera ake akhale anthu awiri osati chigulu, mukambirane ndi a Munlo musakhale ndi wina aliyense mwa anthu omwe anapita ku Salima aja inuyo ndi okwanira musadziderere

  • @HendrickLanga
    @HendrickLanga Рік тому

    Tiyeni kumalawi tichoke kuno matha akukulilini mukapange mademo

  • @NELSONFERGUSON-j5w
    @NELSONFERGUSON-j5w Рік тому

    Bon kalindo musiyen azipanga zamwachita bwino kumutuluka iyeyo apange group lake inuso mupange lanu ngat kuli kuwathandiza mukhonza kumawathaniza koma osauzana zisitsi ximenezo zingathe kutithandza

  • @MustafaLikaomba
    @MustafaLikaomba Рік тому

    Dziko lathu laola palipose pali chinyengo chosaonanao manyazi

  • @patiencetebulo
    @patiencetebulo Рік тому

    Mademo sangathandizeso koma asilikali nthawi yawo agwile ntchito bas

  • @tingamasi106
    @tingamasi106 Рік тому

    Kwacha sinagwe chifukwa cha iwe kape osatinamizapo pano. Unayamba kuyankhula kalekale koma chimasintha ncha? Ndiwe galu kwabasi osatinamizapo apa as if ur audios has any impact at all

  • @histingsshaha6471
    @histingsshaha6471 Рік тому

    Gwilizana ndi anzako

  • @histingsshaha6471
    @histingsshaha6471 Рік тому

    Bilimankhwe

  • @amonfrancisautotune2073
    @amonfrancisautotune2073 Рік тому

    Palibe tingachite zavuta kose

  • @muhamadshaibu9261
    @muhamadshaibu9261 Рік тому

    Iwe umangoyankhula ulibe chanzeru chilichonse chimene umapanga

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule Рік тому

    Tipange ma medemo

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 Рік тому

    Iweyo panga zaku south Africa ko ifeyo tisiye Mesa umati uzipanga za Ukraine aaaa fisi

  • @phillipstamaley7901
    @phillipstamaley7901 Рік тому

    Choka iweee fokofo fwetseke

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn Рік тому

    Chomwe chikufunika mchakuti,ngakhale atangawa zindalama kwa anthu zochuluka koma asapangeso mistake yovotera manyaka,komaso inu nomwe ndi a mene munapangisa kt izi zilowe m'boma ,ndie lero muzame mwakuya kuti anthu awawa asazabere mavote,komaso zinatheka bwanji kut tizavote 2025? Inu ngat omenyera ufulu munali kuti ?

  • @feehasaidid.r.d
    @feehasaidid.r.d Рік тому

    Malawi ndiopusa koopya

  • @tingamasi106
    @tingamasi106 Рік тому

    K9ma kalindo akukumvetsan8 kuwawa, kambani za malawi osati bon kalindo thats why we hate u

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole Рік тому

    Tayambani mwataya uko ma shit mwatsirana aja iwalani ndikugwirana manja ngakhale mukhale magulu osiyana km come on and shake

  • @tingamasi106
    @tingamasi106 Рік тому

    Aaaaaaaah pilizi chonde iwe Ben? Kwacha yagwa chifukwa iweyo wasiya kutukwana? Asaaah komatu inu amalawi mumawatola, kutukwana kwawo kwasintha chani malawi muno chiyambire? Aaaaaash kwacha yageq chifukwa wasiya kutukwana? Man dont think malawians ndi mbuli

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 Рік тому

    A Malawi siowafela amane anthu opanga ma demo amvekere anthu osowa zochita asiyeni ali dyooo ndiyeMMalawi akuti warm heart zaziii titayeni basi

  • @tingamasi106
    @tingamasi106 Рік тому

    Mukumayankhula zotukwanizana nokhanokha Malo Moti muzipanga za boma.........u r busy accusing ur fellow fighter Malo molimbana ndi boma, mukupindulapo chani? Ma demo akubwera ndi bon kalindo inu zidyani zoloso kumeneko, inu mumadyera pakamwa. Stop attacking ur fellow fighter then u will get back the respect

  • @thommgombe7804
    @thommgombe7804 Рік тому

    Ambwiye bwerani paground bas, osakhala munthu opanda mantha munthima koma physically u ar a cowards