ANTHU AKUYANKHULA MOKHAZULA KU CHIKANGAWA 🤔🤔🤔

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 5 лип 2024

КОМЕНТАРІ • 67

  • @LeonardMhone-cg1tk
    @LeonardMhone-cg1tk 7 днів тому +8

    Kufa kwa SKC ndale ku Malawi sizizakomanso😭😭

  • @bayanimponda8746
    @bayanimponda8746 7 днів тому +7

    SKC rest in peace. We will fight for you and complete the mission. Youthful nation will speak in 2025

  • @user-vw7tj2ss3l
    @user-vw7tj2ss3l 7 днів тому +8

    Chilima anali magufuli waku mw daily sindingona

  • @JohminMatick
    @JohminMatick 7 днів тому +3

    Zimandililitsa ndikamaona SKC 😭😭😭 koma zose amadziwa ndi mulungu

  • @semunchombo9737
    @semunchombo9737 7 днів тому +6

    Koma saulosi mmmmmh ayi zikomo

  • @HappyMshali
    @HappyMshali 7 днів тому +3

    We still love you our hero God is great continue rest in peace

  • @user-pg7co4bx9j
    @user-pg7co4bx9j 7 днів тому +1

    Ku Malawi kuno tili ndi ndale zawumbuli. So Painful to us SKC 😭😭😭😭😭 RIP

  • @DennmichSimb
    @DennmichSimb 6 днів тому

    SKC is in our blood the youth of Malawi. RIP SCK my great and visionary leader.

  • @BlessingsTembenu
    @BlessingsTembenu 7 днів тому +2

    Koma chilima anaferanji abale,sangafeko asatanawa koma

  • @user-xe1so5xj2w
    @user-xe1so5xj2w 7 днів тому +1

    Amalawi phudziro ndilimenelo mutsangovota chifukwa mukuvutika ndiutsogoleri ulipou

  • @user-lb6ek3ee6d
    @user-lb6ek3ee6d 6 днів тому

    Rest in enternal peice Dr Chilima your soul is still talking in Malawi and we will solve this coming 2025

  • @ElizabethMaononga
    @ElizabethMaononga 7 днів тому +3

    Zopanda phindu izi.Kuitana ziwanda zonse. Palibepo Yesu apa.za ziiiiii

    • @user-kg5lf6bd1g
      @user-kg5lf6bd1g 7 днів тому

      Alipo

    • @user-qp8kh2hj9o
      @user-qp8kh2hj9o 7 днів тому

      Mmm azuwanda ndi inu mukuyankhula mudziweni yesu akuthandizireni pamene mukufuna kuyankhula

    • @Lee-lee-w1r
      @Lee-lee-w1r 7 днів тому +1

      Ndinu amboni za Yehova kodi??

    • @CHIWSABINYAMBOSE
      @CHIWSABINYAMBOSE 7 днів тому

      Akatero ndiodana ndichilungamo

    • @lindananthalo5327
      @lindananthalo5327 7 днів тому

      Why watching Ngati zikubhowani
      May SKC rest in peace

  • @PhillspicJere
    @PhillspicJere 7 днів тому +2

    Ndikanakhala ineyo wakubanja ndikanalesa miyambo iyi chifukwa zikuonesa kuti zalowa ndale

    • @mphatsojuliostandy4918
      @mphatsojuliostandy4918 7 днів тому +3

      Zikuyene kulowa ndale kumene Chilima anali wandale,komaso anafa mwa ndale.palibe cholesera izi

    • @VeronicaChirwa-ct4os
      @VeronicaChirwa-ct4os 7 днів тому

      Zoona ine sindikanaletsa ndikanakhala wa chibale wa malemuwa. Ndikanalimbikitsa anthu kuti apitilize mwambo oyatsa ma candle kuti amene akunamiza a Malawi kuti inali ngozi manyazi adziwagwira. Komanso yemwe akukhulupilira za bodza adziwe choonadi.​@@mphatsojuliostandy4918

    • @jogechawa6192
      @jogechawa6192 7 днів тому

      Waphedwa ndi andale ndiye mumati

    • @CeniaMayeni
      @CeniaMayeni 7 днів тому +1

      Mesa Naye anali wa ndale, Ndiwe wa congelesi ndakuona maso ngati bonya

    • @user-lz4kc5ob1t
      @user-lz4kc5ob1t 6 днів тому

      Or chilima anali wandale galu iwe

  • @user-co3wr3rn4h
    @user-co3wr3rn4h 7 днів тому +1

    Mupoto palibe angamake apa tikangoyankhula basi nonse munya muwona

  • @AminAbbass-xc4qk
    @AminAbbass-xc4qk 7 днів тому +4

    🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉✊✊✊✊✊✊✊

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y 5 днів тому

    Chilima its was good guy

  • @user-lz4kc5ob1t
    @user-lz4kc5ob1t 6 днів тому

    Mmmmmmm km president wangayu ndikumusowa ine winawake andibweresere chonde mopepha

  • @user-kg5lf6bd1g
    @user-kg5lf6bd1g 7 днів тому +1

    Mulungu apanse ntendele chilima

  • @user-le9su3mt7r
    @user-le9su3mt7r 7 днів тому +1

    Satana chakwela wati wawa

  • @MariamJohn-dg4em
    @MariamJohn-dg4em 6 днів тому

    We stil lov u dear, continue Rest in peace SKC

  • @user-rd2td7bg4c
    @user-rd2td7bg4c 7 днів тому

    😂😂😂😂😂😂❤❤❤ koma kuli mwambi

  • @user-gj4li2gc8o
    @user-gj4li2gc8o 7 днів тому

    Zonsezi tikupangazi zilibe sogolo, muzimu wa saulosi sungazukeso zinachitika zinachitika ndi chikonzero Cha chauta aliyense Ali ndi njira yake tiyenela kuvomereza

  • @planmalawi-sm2cw
    @planmalawi-sm2cw 7 днів тому

    Tikala tikulira thawing yaitali kwambili. RHS. SKC.

  • @CHIWSABINYAMBOSE
    @CHIWSABINYAMBOSE 7 днів тому

    Moyo waikhadzula 😢😢

  • @RaymondKamwendo-g5x
    @RaymondKamwendo-g5x 7 днів тому

    Kodi mukamati zalowa ndale matanthauza chiyani?

  • @Lee-lee-w1r
    @Lee-lee-w1r 7 днів тому

    Hmmm 🤔 🤔🤔

  • @user-sm8gx4vf1v
    @user-sm8gx4vf1v 7 днів тому

    Ndipo skc analidi mungufuli😂😂

  • @user-ie5pc4ox8i
    @user-ie5pc4ox8i 3 дні тому

    Uyuuu sanafe uyuuuuu

  • @Kasiya-gp7fm
    @Kasiya-gp7fm 7 днів тому

    Amen wutsani baba chilima,so sad

  • @ziwani3682
    @ziwani3682 7 днів тому +1

    R I P skc

  • @tandtrefrigeration
    @tandtrefrigeration 6 днів тому

    Bolo zanu onyoza za if achilima

  • @OnexAliMwale
    @OnexAliMwale 7 днів тому +1

    Zalowa chibwana...

  • @desmondMpuwala
    @desmondMpuwala 7 днів тому

    Aaaaaa anthuwa ndizisiru saulosi anali chimunthu chopanda nzeru chidebe chopanda nchenga

    • @ChisomoJinard
      @ChisomoJinard 7 днів тому

      Lankhula ngat nawe udzafa

    • @NatashaBema
      @NatashaBema 6 днів тому

      Iweyo usakhale ngati ndiwe wamuyaya uzilankhula mwanzerru imfa ndi chinthu chowawa osamachitira Chibwana ai khala ndi nzeru

  • @KennethMchenga-j9c
    @KennethMchenga-j9c 7 днів тому

    Skc mpaka kalekale

  • @PreciousPhiri-jr4sd
    @PreciousPhiri-jr4sd 7 днів тому

    Zowawa

  • @NaziruWapete
    @NaziruWapete 7 днів тому

    😢😢😢😢😢

  • @user-jn9tz3li3v
    @user-jn9tz3li3v 7 днів тому +1

    Useless gatherings

  • @Kenmoney-xp7tz
    @Kenmoney-xp7tz 7 днів тому

    Nde UTM yayankhula chani apapa

    • @petertaulo8014
      @petertaulo8014 6 днів тому

      Apatu Panali kuyatsa ma kendulo osati kampeni baba, akutumani a Mcp

  • @EdnahKachalie
    @EdnahKachalie 7 днів тому

    💔

  • @user-vm7iz6oz6r
    @user-vm7iz6oz6r 7 днів тому

    Okupha azafaso

  • @ItzMalawi
    @ItzMalawi 7 днів тому +3

    💔😢

  • @PaulChaleka-lb4vx
    @PaulChaleka-lb4vx 7 днів тому +1

    Continue mpaka 2025 mpaka eliko agwe

  • @davierbanda7026
    @davierbanda7026 7 днів тому +1

    rest in peace SKC

  • @giftkamwiyo9175
    @giftkamwiyo9175 7 днів тому

    RlP

  • @CharityChikomo-hl1gz
    @CharityChikomo-hl1gz 7 днів тому +3

    He was such alegend.

  • @PhillspicJere
    @PhillspicJere 7 днів тому

    Ndikanakhala ineyo kuti

  • @AminAbbass-xc4qk
    @AminAbbass-xc4qk 7 днів тому +1

    🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉✊✊✊✊✊✊✊