😂😂😂😂😂 Mwandiseketsa modzi wawo ndine a chilima sindikuwadziwa km tikuchoka tonse kuntcheu km ndadziwa bwino pangoziyi😂😂😂😂😂 ing'aluleni kampeni ikhala yandenge🤣🤣🤣🤣 ndimva kuwawa ndimfa yachilima ndi anthu 8 aja km Mwandiseketsa sakufuna koma ndye zawadera amcp km zinazi mukamapanga kumaunikila zithu ziwiri tikupangazi ubwino uchuluka kapena kuyipa kuchuluka km satana wakudodani achakwera ndi anthu anu muyisova 2025 is near😂😂😂😂😂😂
ZOONA MCP CHIPAN CHAMAGAZ SITIKUCHIFUNASO 2025
Kkkkkk big man kuswakuswa basi
Powerful 🔥🔥🔥🔥
Chakwera wamupha chilima 😭😭 2025 pack & goooo......!!!!
Zoona zoona man , auzeni zoti poyambila campaign tapapeza
Brother auzeni achakwela mbuzi yosamva wakupha galu
Kkkkkk Ndenge kuchikangawa campaign yinukhaaa😂😂😂😂
Iweyo umatha ase kkkkkkk
We have to subscribe this channel guys this guy is fun
Good massage
Angopachira azipita
Malawi adzakhalabe movutika chifukwa cha mantha ndi dyela kaya ndiumphawiwu tizizunzidwa chonchi ndi mcp
Ndege kuchikangawa kkkkk
😂😂😂😂 ipase moto braz anyenayo chakwerayo
😂😂😂😂😅😅 koma chakwera tamva ndenge kuchikangawa
Good message
Brother inu ndege kuchikangawa kkkkk inu osekesa bwanji 😅😅😅😅
Kikikiki mwandi Nizoona my brother that's true bro let them just come out in Truth tell us how the killed our people
Momwemo Bale wanga❤❤❤❤❤❤
Uku ndiye kulankhula mozama
😂😂😂😂😂😂 Afa katatu
That's true kumanga anthu cholinga atiopseze palibe kuopa chakwera park and go mmalawi pano anachangamuka siwa ma 90 u have to this
Koma ndiyedi all this time, where are the investigations results?
Kkkkkk awuze adziwe kuti anaocha okha pomupha chilima
Akauza kuti feteleza ndi 20 pin kkkkkkkk
Kkkk chikangawaa
Zooonah!!¡!
Wang'alura iwe kkkk 2025 kudzangong'alura kuchikangawa bac nkhani yatha
Manu bgy
Bwinotu akupangani brai chakwera ndiwa nkhwirutu kkkkkk
Pano aphaso lucy Banda oyimba 😂 Lucius banda
Inde inde Pano Malawi tinasukusula iyaaaa wiring for the report
😅😅😅😅😂😂😂Ndege kuchikangawa basi game down 😂😂😂😂😂😂
Kkkkkkkkkk sure Ada
Anthu aing'aluradi
Nkhawa yanga ndiyoti akakumangani phone yanuyo ngakhale mutagulitsa singakwane ya bail
Kkkkkkkkkkk umakwana
The facts is that! Chakwera anapha Chilima
Kkkkkkkkk auzemwina sakuziwa
Tinva kuti mwakalowatu inu 😂😂😂panotu asiya kumanga mbanva akumanga Anthu ngati inu😂😂😂😂
Kkkk kkkkkk ayelekeze
@@Nthambi-zg4nu 🤣🤣🤣🤣zitsilu za Anthu,,,,moti A malawi azizavotelasotu nyasi zimenezi poti timayiwalatu ngati kuyamwa
Amalawi ndikudikila kuzamva paka mpeni yawo kuti azizati bwanji ,, bola ife tazionela tokha fertilizer akuchoka pa 20 pin to 100 pin, and Kwacha itagwesedwa ngati ndenge ya afiti Komanso anthu 9!! Atafa kuchikangawa😭😭😭
@@user-mz8nw6nx6p ayi plz ponkhapa sawina olo atabera anthu saimva ndye poti boma analowera popita mankhothi anthu zikatheraso kukhothi komweko
Ngat akufuna alitenge zikoli aziyenda nalo muthumba asa
Kodi ngakale akufuna asimanga wina aliyese kod ziku lovota asizamuopsesa munthu kapena asosayamba amanga Kaye mundu Kuti ukandivotere ine Ali ndichibwana nyamako yawoyo
Kikikiki yaba let chakwela go
Ndege kuchikangawa achinagwenembe
Hahaha hahahaaaa!
❤
Ízooo ndipo tikuwona kuchedwa kuvota kuti aChakwera ndinduna zawo akalowe kundende
PhaaAAaaaaaaaaaaa
Auzeni zoonad
Chakwera wazungulira mutu, amampha mzake amaona ngati sitizindikira, wanya nayo, wazungulira mutu stupiet
Koma ndipoo ngati mukunama nthumazi ikwakwapula
😅😅😅😅
😁😁😁😁😁😁😁😁👍👍👍👍👍👍👍👍👍👍
Anyapalawa ankhawula a MCP
Kkkkkkkkk
Chamba
Chitsiru iwe
Auze kkkkk
Kkkk awudze a MCP kuti aying'alula apa nsapulumuka 2025 wawutali kubela tsikuthekaso mwadzi wamunthu omvuta
Auze anthu oipa
Akumanganitu boma lake lopengali
Ndizoona chinachake chaola
Munthu oipa kwambili
Zoonandi
Zoonadi idzi atifuna
😂😂😂😂😂 Mwandiseketsa modzi wawo ndine a chilima sindikuwadziwa km tikuchoka tonse kuntcheu km ndadziwa bwino pangoziyi😂😂😂😂😂 ing'aluleni kampeni ikhala yandenge🤣🤣🤣🤣 ndimva kuwawa ndimfa yachilima ndi anthu 8 aja km Mwandiseketsa sakufuna koma ndye zawadera amcp km zinazi mukamapanga kumaunikila zithu ziwiri tikupangazi ubwino uchuluka kapena kuyipa kuchuluka km satana wakudodani achakwera ndi anthu anu muyisova 2025 is near😂😂😂😂😂😂
Mwana waine amachita kulila ,, kumufusa ukulila chani ? Ati achilima aphedwa😂😂😂
@@Nthambi-zg4nu😂😂😂😂😂
@@user-ru5xg9qw4x 😂😂kd achilima Mzimu wawo ndiwinawinatu azidandaula ndazungu omwe kumangalande mcp muziwona
Chakwela wamupha chilima zasala zosatila Zach
Iwe ndiye walasatu
Waukape iwe dzko chakwela awinaso wav uziona
Iwina kumtumbo kwa mayi ako ase
Panyapako iwe