Це відео не доступне.
Перепрошуємо.
Enock Chihana kuulura poyela zinsisi zomwe chilima anamuuza asanamwalire zokhunza Tonse Alliance
- Додати в
- Мій плейлист
- Переглянути пізніше
- Поділитися
Поділитися
Вставка
Розмір відео:
- Опубліковано 12 лип 2024
КОМЕНТАРІ • 409
Наступне
Автоматичне відтворення
KOMATU BON KALINDO SAMAMVA NANGA ZOMWE WAYANKHULA LERO PA 14 AUGUST A BOMA AKAMVA ZITHA BWA?Makosana
Переглядів 40 тис.
ZOMWE PRESIDENT LAZARUS CHAKWERA ANAYANKHURANA NDI VICE PRESIDENT MICHAEL USI PAMENE AMASANZIKANAMakosana
Переглядів 25 тис.
ZA NGONGOLE YA NEEF TINAYAMBA NDIFE ASANATIBELE BOMA - MAI MARY NAVITCHA A DPP AINGALURA LEROMakosana
Переглядів 10 тис.
😭ЛЮДИ ВОВКАМИ СТАЮТЬ....5 канал
Переглядів 2,8 млн
На Курщині НАСТУПАЮТЬ ПОЛЯКИ 🙈 Росіяни МАСОВО ТІКАЮТЬ З ПРИКОРДОННЯВікна-новини
Переглядів 150 тис.
РЕЙНДЖЕРС - ДИНАМО. Ліга чемпіонів. ПРЯМА ТРАНСЛЯЦІЯFootball Hub
Переглядів 454 тис.
СТАСЯ МАКЄЄВА: СЕРДЮЧКА на гендер паті. Тато ЗРАДЖУВАВ, коли мама хворіла на РАК. Коли українською?Okay Eva
Переглядів 454 тис.
KONDWANI NANKHUMWA WAULURA PA INTERVIEW ZOMWE SAULOS CHILIMA ANAMUUZA ASANAMWALIRE ZOKHUNZA DPPMakosana
Переглядів 44 тис.
Tamale Mirundi JR ali mu maziga 🥹🥹Kasuku Live
Переглядів 20 тис.
BON KALINDO LERO 12 AUGUST WANG’ALURA MCP AKUTI AKUPANGA MA PLAN OFUNA KULIMBANA NAYE KOMA SAMUTHAMakosana
Переглядів 71 тис.
Breaking News. Tamale Mirundi afudde. Bibino ebimu ku bigambo byeyayogeraCavton Music UG
Переглядів 66 тис.
Bambi Tamale Mirundi Afudde Asonyiiwe Mutabani we Mirundi jr. Simon Muyanja Lutaaya Abotodde EbyamaKookie Promotions
Переглядів 47 тис.
MAFUNSO AMTOPORA OMWE ATOLANKHANI ANAFUNSA KU PRESS BRIEFING YA DPP LERO ZOKHUNZA CONVENTIONMakosana
Переглядів 18 тис.
Tamale Mirundi; Mukulu we ayogedde obudde bwe obwasembye ku nsi.Bukedde TV
Переглядів 60 тис.
JOYCE BANDA WAING’ALURA POYELA LERO KU ZOMBA PA NSOKHANO KUTI IWO NGATI PP ARE NO LONGER IN ALLIANCEMakosana
Переглядів 38 тис.
Zomwe Zinachitika Kut Ndege IsoweSam Malvitha
Переглядів 220 тис.
«Його, каже, не зламали. Ви гляньте на його очі - вони злі»: Розповідь матері полоненого бійцяСуспільне Донбас
Переглядів 664 тис.
Втрачене дитинство | GOVOR TikTok #govor #shotsGOVOR
Переглядів 338 тис.
РЕЙНДЖЕРС - ДИНАМО | Ліга Чемпіонів. Кваліфікація Q3 | 13.08.2024ФК «Динамо» Київ
Переглядів 332 тис.
Что под плащом? 😱 #тнт #shorts #юмор #шоу #однаждывроссии #моргунова #картункова #кошкина #летоОВР Шоу
Переглядів 4,5 млн
СТАСЯ МАКЄЄВА: СЕРДЮЧКА на гендер паті. Тато ЗРАДЖУВАВ, коли мама хворіла на РАК. Коли українською?Okay Eva
Переглядів 454 тис.
Алексей Щербаков разнес ВДВшниковBody Mania
Переглядів 10 млн
Битва умов. ❤️ПІДПИШИСЬ! Андрій Попик. чат рулетка.Андрій Попик чат рулетка
Переглядів 435 тис.
Eleftherios Petrounias helped by Arthur Zanetti = epic gala moment ❤️Olympics
Переглядів 46 млн
Akatundu awa!!!!! He is so courageous!!! speaking with no Fear,, he sounds like Chilima in his Bond of courageous.
Munthu koma uyu speaking without fear....Big up Mr chihana
eeee kma this man is so courageous
Eeeeee
Koma SKC 😭😭😭😭
Ine imfa iyiyi..
Imandiwawa.. eeeeee
Mr. Chihana is man of his word, ndipo zikupanga prove that he is the son of his father. Amenewa ndi amene anathema ndi kamuzu, apa chakwera akuchoka, ndavomereza anthufe sitimafa koma maonekedwe athu ndi amene amasintha
Afford my vote
Koma ndiye.big up chihana❤
So powerful bwana We need this Energy in our country honestly achinyamata ambiri akufuna ngati iziiii
Ramaphosa wanthu waku Malawi 💪💪
😂😂😂😂even me I thought like that ndtaona pic yake poyamba
true ..they are resembling very 😅
SKC has gone leaving a message that malawi is the land with possibilities but the problem are the leaders. What a humble guy. Rest well sir
I didn't know dis guy can talk lyk dis🙌🙌🙌🙌🙌🔥🔥🔥🔥🔥
Anthu akwiya mkoz
@@hopesato ndaonaso🙌
Straight wise proud of you chihana🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
This guy is very strong 💪 🎉🎉🎉
God protect Mr Chihana....we love u
Km ndi zoona chakwera popanda chilima sukanawina galu iwe chakwera unapanga ndiwolotse ndikakutafune galu iwe chakwera dzimaso dzako unatiphera ngoni wathu
Pankongo pake ameneyu ndipo mabala awawa sazapola taaaa
Ndipo dziko lino analitembenuza dziko lino
Ndiye chilima popanda chakwera adakhala vp tisamalakhule mbali imodzi chilima tu adali vp from 2014 up to 2024 ineyo ndimafuna nditadziwa zomwe adapanga kapena ankadikila adzakhale President kuti inuyo mudzayamve kusangalala to me i don't know thanks God ineyo ndimadziyimila from nyumba ya maudzu to mansion bra inuyo dikuilani chiloma wina kuti moyo wanu udzasithe
@@user-rf4br1fv2z chilima anakhala vice president chakwera kulibe kapena wadya chamba eti?
Kuno kwa msundwe keep it up chihana we need truith,
We need fearless leaders like you! Ndipo ma leaders ena atengelepo phunzilo, learn to be fearless like Chihana osamangokhala phwiiii osalankhula
Wise leader...... Tell them
Powerful, proud of you Honourable Chihana
Didn't know this guy amayankhula mwamphamvu chonchi ❤🔥
Tell them the truth don't be afraid 😨 GOD will guide and protect you, we relay behind your your back.
Voice iyiyi itha kundipangisa kuyamba kusapota afford 💪💪💪💪
Koma ajoinane ndi utm ndili mumbuyo mwao
Akut Chisilu chilichonse Chitha kukhala nduna
Even the bible itself says do not touch my anointed ones.
Good Messnge Mr Enock Chihana❤
Enock Chihana (Akatundu aboma) 🎉🎉🎉🎉 Thawi yakwana 🎉🎉🎉🎉
You are the great man thanks for the truth
Good leader
Chihana we dont want hate speech be like you father who never preach hate speech
Am not a politician and am from kumwera but ilove ana achihana personally.Courage ya nyoo
Mwana wa Simbi ya Moto 🔥🔥🔥💪
Watching from Soweto Johannesburg.
Powerful.
Sadzagona tulo wopha chilima
Great leader 🎉mr chihana keep up
Lero ndiye kuli kung'aluladitu sizinaoneke
Kuli zinthutu👐
Haaaa mwatipha basi tonse Amalawi mukanamuuza zoona mwanao kuti fisi ndi fisi sangasithe mawaanga 😭😭😭😭
The guy fearless and speak energetic
All the best Aford
Congratulations honorable chiana
I lv it.
A chilima asanduka kamupeni pano 😢😢😢 ambuye nkhondo ndiyanu chilichose mukudziwa ndinu
Zomvetsatu chisoni kwambiri.
Ndikanakonda a ku Banja akanaketsa Zopusa zimenezo.
Chidziwika ndi chakuti SKC ndi CHIHANA were not Friends.
Ngati zomwe akunenazo ndi zoona tione umboni wake.
Atiuze nthawi, tsiku komanso Audio or ma message olemba.
Musaiwale kuti ndi yomweyinso anabweretsa nkhani yonama ku Nyumba ya Malamulo atafunsidwa za umboni anakanika kupereka.
SKC awuza bwanji iyeyo kusiya kuuza utm members?.
CHIHANA ndi ONAMA kwambiri
@@user-tk6qh9zs7h ndipo inu koma ambuye akuwona zomwe akupangazi ziwabwelela wokha kapeni ngati yavuta kungosiya mbanji elsh
Palibe wasanduka campaign apa ,akungokamba chilungamo period
Ndipo live akunenazo ndizoona ikakhala campaignyopangila munthu nawonso apanga ya kamuzu iyaaaa
@@mishecksipolo7153 musalowetse ndale pa imfa yamunthu muziganiza mofatsa musanayankhule nyasi zanuzo inu simulungu
achihana uko muli uko Pala pangawa mwayi mwizeko ku nkhatabay mkondezi area I beg
We soldier on!... very brave mr chihana junior 💪🏼🇲🇼... speak it like it is....
No rest for the wicked
Chilungamo sanong'onotu 😢😢with heart broken
True voice of a leader, thus why he was the first to demand enquiries into the death of Chilima
Kuyankhula koma ukuuu aaaaseeeee👊😂
You are not alone mr
Ndipo simunati akanantchulidwabetu chilima mpaka mpaka muphulikeee amfiti inu
Aford the mother of all political parties in Malawi, it's your time Big Man, mcp is afraid of you in Jesus name
Mcp inalakwitsa kwambiri kuphwanya lonjez ndipo izizi zimenez amalawi zatikwiitsa kwambiri from molongolo Tanzania
Km Inu simudzalowapo mboma truth
Our own leader
Go ahead mr Cihana
Kumeneko nde kulankhula dad🥰🥰🥰🥰🥰
Chakwerayutu si m'busa anthunu mangosokoneza munthu uja ndi nthakati. Mfwiti ya tyala iliye na mzeru ingaphepese yai after those words pray hard angakusowetse
❤❤❤ love you dad. We all cry our vice president chilima.😢😢😢
Viphalileni bwana viwanthu voina mitu ivi you are my vote
Powerful voice
Akamuna awa❤ osati akapamba enawa😢
Kumeneku ndiye kuyankhula Kwa Mtsogoleli wadziko kuyankhula mosaipa wina aliyense
God is watching from a distance
So courageous
RIP CHILIMA....😢😢. Auzeni live live..akapukuu ..nduna zokuda mbuuuuuuu
Appreciate you chihana🎉🔥🔥🔥🐐
Ilov AFORD leader fearless
Your the best speach 💪💪
We have lost a great leader SkS because useless party mcp😢😢
Ndiye cadet wachabechabe uzithupsya amalawi kuya nkhula chilungamo.apa ngakhale wina azinama koma imfa ya chilima ipase phunziro
Speak out Mr Chihana
Chakufwa Chihana weniweni
Mudzamwalira osalamulirako dziko inu! Chifukwa chachimtima chasanje
Whoever has a hand on SKC will never have peace and enjoy his days of life.
Ana achibwanaa
For sure
In Jesus name Amen
True
Enock chihana akunena zoona ...amasuleni agaluwa
..chimwendo ndiye akuzimva kwambili ndipo ndi munthu amane amakonza ziwembu zonse za chakwera
Ndayamba afford basi😂😂😂
😂😂😂
😂😂😂
No SKC, indeed no MCP
Kuulula nzinsinsi za chulungamo timauula miniwake ali ndimoyo osatizi izi menenezo ayi ulekeni Mzimu wa chilma uuse mu mtendere osati zonena mbweeeee pezani zina zonena osati kutukwana anzanu .😅😅😅
Maliro aja trapeze zolankhula pa campaign popanda maliro aja fundo tinalibe fundo zake zimenezi zingatukule Malawi?
Umbuli wazika mizu pa Malawi! Kwawo safa agalu awa komanso ngozi saidziwa. School ija ndiyabwino umbuli chihana chonsecho akudziwa kuti munthu anafa pa ngozi🚮
My vote
Chilungamo osamaopa chakwera aziziwa
Nanga zoona tizingomva zoti a Chilima adandiuza 😅😅😅 usiyeni Mzimu wa Vice President wathu uwuse mumtendere
Ndifera ndembera no2
Thanks for the information
Big up 💥💥💥
Chakwela mfiti kobasi waiwala kuti anakupangila campaign Chilima analakwa chani
Well spoken
Powerful talk
Go deeper Enock chihana
I respect this guy
Kkkkkk chitsiru chinachake ndi nduna,,,,moto buuuuuuu
Chilungamo chonsechi bwana mumasuga mukudziwa etii 😢
Kumakhala munthu wolimba mtima ngati chihana💪
Nice ndzaknda
Koma yaaaa❤
Ngati mulibe chokamba ndibwino kudekha coz zimenezi si fundo zoti zingatukule dziko ayi, mpake Malawi ali otsalira kwambiri kamba kosowa fundo .
Mbuzi iwe
Machende ako iweo osabweletsa fundo yako
Ndizomwe akunenazo kapena akuchita kuwuzidwa
Dolo 🎉
Chakwela wanyema mu 18 an box mu thawi yoonjezela then refer lee mkuzaimba penate... Mu thawi yonjezela
ZIKAMBANI ZOMWE MUZACHITIRE ANTHU , MAKUTU ANU
Kkkkkkkkk 😂😂😂 ati kambuku koma amalawi munasiya mantha
Koma chakwera azibibira muthrauza ndithu .
Ulemu wanu bg