Це відео не доступне.
Перепрошуємо.

ZOMWE AYANKHULA KU NDILANDE ATUPERE MULUZI NDI FREDOKISS

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 12 лип 2024

КОМЕНТАРІ • 90

  • @user-wi9pe2hz7e
    @user-wi9pe2hz7e Місяць тому +7

    Atupele akuyenela utsogoler kma ugwilizane nd Dpp coz 2025 Peter akuwina no doubt ❤

  • @GladysBombeya
    @GladysBombeya Місяць тому +2

    Wabwela lweyoo fredoo 🎉🎉tilipa mbuyoo pako SKC forever in our hearts ❤🎉

  • @ErnestChansa
    @ErnestChansa Місяць тому +5

    Mcp asaza bweleleso boma paka kale kale chipani Cha mcp chikanango kutha Malawi anthu awa ndakupha fiti za anthu

  • @user-qp8kh2hj9o
    @user-qp8kh2hj9o Місяць тому +6

    UTM my vote ❤❤❤SKC forever in our hearts 🎉🎉🎉🎉🎉

  • @MAPAGASTUDIOS
    @MAPAGASTUDIOS Місяць тому +3

    Good bless Hon ryt atupele the only last hope in Malawi with utm and dpp afford more fire

  • @RoyBanda-d7h
    @RoyBanda-d7h Місяць тому +1

    Atupele is good coz had to manage all the position given as a minister. Mainly Health ministry the guy did well. He never failed

  • @rashidlamos3403
    @rashidlamos3403 Місяць тому +7

    God bless you Atupele muluzi

  • @Freedomchennl47
    @Freedomchennl47 Місяць тому +9

    Ife tikuyang'ana Atupele kaya atitengela kut 2025 tilinao mpaka tikhalowe Boma ❤❤❤❤❤❤❤

  • @chikondichabwera6974
    @chikondichabwera6974 Місяць тому +1

    Fredo alindichikoka but one thing aphunzire bhobho ndale from his father komanso mfundo akunge tili pambuyo pa utm..❤ skc forever in our hearts ❤❤

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 Місяць тому +16

    Atupele is the only hope Malawians have. Let me give you the reason why I think so. ATUPELE IS THE ONLY PRESIDENT WHO STOPS DOING POLITICAL CAMPAIGNS AFTER ELECTIONS. Let's try Atupele.

    • @evancejimu2872
      @evancejimu2872 Місяць тому +2

      I second sir

    • @SamKaposa-i5c
      @SamKaposa-i5c Місяць тому +1

      We are together bro

    • @preciousnombo6875
      @preciousnombo6875 Місяць тому

      Mmmmmm boza

    • @actuarialscience2283
      @actuarialscience2283 Місяць тому

      @@preciousnombo6875 Mwaonapo Atupele akuuza anthu kuti akafotere UDF zisankho zili kutali? Ine ayi. Koma ndaona kongeresi(=ufiti), DPPigs, UTMiths, and other guys akupanga ndale daily. Koma uyuyu anali bize ndi ma biziness ake. Kwa ineyo ndingavotere Atupele panopa. Think wisely.

    • @MirriamChakanza
      @MirriamChakanza Місяць тому +1

      Atupele our only hope. #changebegins#

  • @user-iq5xk6ju7y
    @user-iq5xk6ju7y Місяць тому +5

    Atupele very humble always. Fredokiss achinyamata tikupatsa support. Taona mmene Burkina Faso yikusinthira ndi ulamuliro wa mwana Ibrahim Truore. 2063 ndi ya achinyamata not makolo akukakamilawa

  • @AlickChima
    @AlickChima Місяць тому +6

    Atupele Muluzi, a seasoned and mature politician. Mwaiyeyu tsogolo tiliona

  • @emmanueljelemani4203
    @emmanueljelemani4203 Місяць тому

    Osaopa, osatopa, osafooka SKC will fight with us..... Let God guide us

  • @PrinceKachimanga
    @PrinceKachimanga Місяць тому +2

    fredokiss needs ukali unali ndi SKC...TO sound relevant.avule chigoba cha munthu oyimba

  • @user-dn3gp6yi4y
    @user-dn3gp6yi4y Місяць тому +1

    Tatopa ndi abilimangwe omati lelo ali uku mawa ali uku tikufuna achinyata omwe ali kuthekela kosinda zindu m dziko muno osati ma gogos party Atupele more fire

  • @user-vm7iz6oz6r
    @user-vm7iz6oz6r Місяць тому +2

    2025 mcp tiyezeka

  • @user-ju7vc1uv7m
    @user-ju7vc1uv7m Місяць тому +3

    Atupele it's my vote

  • @LuwisKaigwaze-gr6cg
    @LuwisKaigwaze-gr6cg Місяць тому +2

    Ku UTM kukusowekelabe mwini wake sindikuonakoso ntsogoleri wazeru

  • @YamikanGomonda
    @YamikanGomonda Місяць тому

    utm udf and dpp tikuybekezela kuti mutithandiza mutati mwagwilizana chifukwa 50 +1 siyophweka kuipeza chipani chimozi

  • @mphatsosadiki4983
    @mphatsosadiki4983 Місяць тому +4

    2025 kukhale alliance ya DPP, UTM,UDF,Aford.....
    Wokha Alliance achoka m'boma basi😂😂😂😂

  • @LeviChakwira
    @LeviChakwira Місяць тому +3

    Put much effort kuti anthu akalembetse mwaunyinji

  • @manasemaposa
    @manasemaposa Місяць тому

    UTM my vote with no contradiction SKC in my heart forever.

  • @Atheeeefire
    @Atheeeefire Місяць тому +4

    Together we can fight guys unity basi

  • @giftsalijeni6962
    @giftsalijeni6962 Місяць тому +1

    Dpp + Udf + aford+ utm we are deleting Mcp in 2025

  • @andrewngowe8836
    @andrewngowe8836 Місяць тому

    Wina apenga misala apo ayi wina ayendera wheel chair kunamizira kudwala 2025 kuli ntchito

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg Місяць тому +3

    ❤❤❤ utm together us one OSAOPA guys

  • @khadijailiyasa5315
    @khadijailiyasa5315 Місяць тому +1

    UTM ❤ ipatse moto 🔥 🔥 🔥 tiyenawo makape ang'onawa

  • @amoschataika7440
    @amoschataika7440 Місяць тому

    Big up Brothers, Njawala, Fredo, Atupere ndi ena nonse let's kick out these idiots of MCP

  • @SaeedHurzrut
    @SaeedHurzrut Місяць тому

    ndizisilu za nkhanza zimenezi UDF moto moto

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 Місяць тому

    More 🔥 ma gyz❤

  • @shotsfired588
    @shotsfired588 Місяць тому +1

    Don’t be fooled by Atupele, he feels entitled to be president that he didn’t want to work with chilima in 2020 but to work with mutharika. He’s not humble enough.

  • @user-hb2hr5oc9l
    @user-hb2hr5oc9l Місяць тому +3

    Koma maboma onsewa chipani chimene asangalala amalawi ndi chiti amalawi mugani MCP ndiye mwayiona kuyipa kwake muganize bwino

  • @MATHEWSMAYIRA
    @MATHEWSMAYIRA Місяць тому +1

    UTM 2025 my vote

  • @TemwaMazuma-gs5de
    @TemwaMazuma-gs5de Місяць тому +1

    Sure, we can very much fight

  • @Yusufu-Daudi
    @Yusufu-Daudi Місяць тому +2

    Tayedzeka 😂😂😂

  • @tracybennie7783
    @tracybennie7783 Місяць тому +1

    Mulungu atsogolele

  • @janemanyamba7201
    @janemanyamba7201 Місяць тому

    Camera simaonesa bwino bwino mmene tinakunganilana ndilande ❤❤❤❤

  • @FelixBoss-yn9pe
    @FelixBoss-yn9pe Місяць тому +3

    Wagulu lathu fredo ometa mwamakono ipatse 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w Місяць тому

    UTM, UDF, AFORD ndi DPP pangani alliance mutebge bomali, koma pasakhale ophangila ai, President aliyense wa chipani mu alliance apatsidwe udindo mu bomalo.

  • @user-dn3gp6yi4y
    @user-dn3gp6yi4y Місяць тому

    Atupele more fire

  • @AdiniKhama
    @AdiniKhama Місяць тому

    Don't give up I'm with you people

  • @LazaroSinerioSineiro
    @LazaroSinerioSineiro Місяць тому +1

    Limbikirani anyamata muchose nyasizi mbava

  • @user-qs2kr4gl6t
    @user-qs2kr4gl6t Місяць тому

    Big up UTM

  • @InnocentMtafya
    @InnocentMtafya Місяць тому

    Kkkkkkkk😂😂😂😂😂😂😂 kkkk ine ndidzuke ndikagwire ntchito zanga ndikuona ngati it's what will make me better later, anatilodzayo eeeh! Ndi captain,anakuuzani ndani kuti kusintha sintha nkazi kumathandizila kupeza banja labwino, 😢😢😢mwiniwache Ndi mwiniwache Basi skc😢😢😢😢😢😢😢

  • @AnthonyMhango-e9q
    @AnthonyMhango-e9q Місяць тому +1

    Umakwana bro

  • @giftsalijeni6962
    @giftsalijeni6962 Місяць тому

    Candle light mpaka 2025

  • @user-kf3qm3or8l
    @user-kf3qm3or8l Місяць тому +2

    Tikufuna sapato zomwe qnatiwuza adadi ako

    • @neemahkapatamoyo9563
      @neemahkapatamoyo9563 Місяць тому +2

      Zaziii kusowa zolankhula zikugwilizana bwanji? Osangosiya bwanji Kupanga comment

    • @JumaKachala
      @JumaKachala Місяць тому

      Kkkkkkkkkkk

    • @actuarialscience2283
      @actuarialscience2283 Місяць тому

      @@neemahkapatamoyo9563 Uyuyu ngwa ufit=MCP.

    • @SamKaposa-i5c
      @SamKaposa-i5c Місяць тому

      ​Ukufuna chilima osati zopusazo

    • @user-ri2vi2fd5v
      @user-ri2vi2fd5v Місяць тому

      Kupusa kwako iwe uzilimbukila kusaka mwana wa ng'ona iwe

  • @asiyatujuma5507
    @asiyatujuma5507 Місяць тому

    Atupele

  • @jeremiambendera2749
    @jeremiambendera2749 Місяць тому

    Morefire
    MCP out

  • @LeviChakwira
    @LeviChakwira Місяць тому

    This must be preached extensively. Anyamata akalembetse mwawunyinji please

  • @jaydee1236
    @jaydee1236 Місяць тому

    Atupele❤❤❤

  • @bismarkmhone
    @bismarkmhone Місяць тому

    LETS JUST TRY THEM ALL PAJA TIMAKONDA KUYESA🔥

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy Місяць тому

    😂😂😂😂😂 chakwera unya manyi chakachino nd makape anzakowo

  • @JasonMailos
    @JasonMailos Місяць тому +2

    UDF my vote ❤

  • @macmanyusa8242
    @macmanyusa8242 Місяць тому

    😂😂 mcp mmimba bwaaa

  • @EmmanuelDanitsa
    @EmmanuelDanitsa Місяць тому

    Fredokkis akadzitorere mfundo anakalibe

  • @UseniMailosi
    @UseniMailosi Місяць тому

    Musamaike maodio. mutikomola skc

  • @mnnyirongo2934
    @mnnyirongo2934 Місяць тому

    Kuswa kuswa UTM madolo kwambili

  • @GLABELMW
    @GLABELMW Місяць тому

    Osawopadi osafooka simulungu iyeyo

  • @Stewartchikoja
    @Stewartchikoja Місяць тому

  • @SheriffDyson
    @SheriffDyson Місяць тому

    Yomweyo mchana wamugeto umakwana

  • @EmmanuelDanitsa
    @EmmanuelDanitsa Місяць тому

    Koma za Atupere yekhau ine ay.. alibe mfundo but am strong follower of UTM

  • @MzikaPhiri
    @MzikaPhiri Місяць тому

    MCP paulendo basi

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 Місяць тому

    🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @atanasioestevao9707
    @atanasioestevao9707 Місяць тому

    ❤❤❤

  • @mswatizumalizwe4
    @mswatizumalizwe4 Місяць тому

    Zalowa zibwana

  • @LindaNkwazi
    @LindaNkwazi Місяць тому

    UTM woyeee

  • @TroubleMuthala
    @TroubleMuthala Місяць тому

    Ng'ona zisazatulukenso m'mabango

  • @SarahMusama-eu7wt
    @SarahMusama-eu7wt Місяць тому

    Njawala moto

  • @user-gd2kl1fx1q
    @user-gd2kl1fx1q Місяць тому

    Utm forever not udf

  • @thomaschipinda6952
    @thomaschipinda6952 Місяць тому +1

    Uyu mukuti fredokiss pa fair mfundo alibe infact the whole utm

  • @MAPAGASTUDIOS
    @MAPAGASTUDIOS Місяць тому +4

    Good bless Hon ryt atupele the only last hope in Malawi with utm and dpp afford more fire