Це відео не доступне.
Перепрошуємо.

Kusumira IMF? Uyuyu ndi Future President

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 14 сер 2024

КОМЕНТАРІ • 116

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg Місяць тому +13

    Azungu amakonda dzisilu monga chakwera

    • @AustinChiyembekezo-cx4mz
      @AustinChiyembekezo-cx4mz Місяць тому +1

      Ndipo nzungu Amazonia zisilu kwambili powagwilitsa ntchito mwauchisilu like chakwela

  • @user-cq7zi3xu5l
    @user-cq7zi3xu5l Місяць тому +1

    Palibe chosatheka,ndizotheka ndithu kusintha malamulo amenewo before 2025.ndizotheka ndithu let's give support him.

  • @victorykaminjolo4635
    @victorykaminjolo4635 Місяць тому +1

    DENIS MAHATA ndi Thomas Sankara wa malawi 🇲🇼

  • @GiftKananji
    @GiftKananji Місяць тому +2

    Ine ndiye ndamukonda

  • @raytavares2256
    @raytavares2256 Місяць тому +2

    Malawi has a lot of intellectual people and mostly very talented and like late sk they knew that he was wise but was polluted with his mind with corrupt money at the time he was very desperate for saving enough money to use for his upcoming UTM campaign and unfortunately he was assassinated bcoz the other party knew he was getting equipped to severed his relationship with Tonse but the problem was that he also knew that the very ruling party at this moment also stole the same am of money and even more than him. He knew what was under the scrotum of his opponent and he was done and finished, ndale za usiku. Greetings from UK.

  • @HallimaMakwinja
    @HallimaMakwinja Місяць тому +7

    Zoonadi brother munthu ameneyo alibwino alibwino ndipo chakwera samaziwa nthandauzo la ( IMF )

  • @PeterChalechale-pz2bp
    @PeterChalechale-pz2bp Місяць тому

    Captain Ibrahim Traore 36yrs wasinthiratu dziko lake panopa dziko lonse likusapota Traore koma zisiru za ku Malawi kuno zosakonda dziko lathu lino limangogwadira imf pomwe ndiyokuba

  • @vivianmkwate8536
    @vivianmkwate8536 Місяць тому +1

    we need young smart men like him look at Ibrahim very young but smart he took over the country couple months the country has been changed. why not us let him be a president and bring changes to our country

  • @HallimaMakwinja
    @HallimaMakwinja Місяць тому +3

    IMF kuthandauza kuti freemasons members intentional .koma Satanic mauwa amawabisa ndizolinga zao ndechoti muziwe ndalama ija akakupasa simumapindula zosatilake ndimavuto monga njala kugwa kwandalama yanthu kukwera mtengo kwazinthu ifa pafupipafupi Ngozi zonsayembekezera

  • @vivianmkwate8536
    @vivianmkwate8536 Місяць тому

    He’s young, however super smart, genius, talented young men,he knows how to improve our country being land locked country.

  • @Realbaaadman
    @Realbaaadman Місяць тому +5

    Tiyeni tipange ma demo atsitse zaka akulu akuluwa atitopesa

    • @innocentmusuli7380
      @innocentmusuli7380 Місяць тому +1

      Any time any day any week any month from now tiwone zomwe sitinaziwone a chinyamata azuka

  • @PeterChalechale-pz2bp
    @PeterChalechale-pz2bp Місяць тому

    Uyuyu ndiwoganiza, zitsiru zimangovomera zina zili zonse IMF ndiyokuba koma ife a Malawi timagwadira azungu kupotsa

  • @omanm2919
    @omanm2919 Місяць тому +1

    Wachinyamata ndi amene akufunika ngati president wa Bukina fanso

  • @AudettaYohanie-fl3oc
    @AudettaYohanie-fl3oc Місяць тому

    Ndili pambuyo pake , and zikangotheka zoti aimile u president watenga vote yanga sure

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b Місяць тому +3

    Ndizoonadi azungu samafuna kuti africa ipite pa tsogolo ndinkona amabweretsa ngongole zawozp

  • @gwatandingo9502
    @gwatandingo9502 Місяць тому +1

    Kwambili azungu amakonda zitsilu kwambili koma amwene kwathu kuno mmmmmmmm

  • @user-mf8fi8wt5d
    @user-mf8fi8wt5d Місяць тому

    Chakwera ndi puppet wa azungu and thats why you see kuti ndalama za IMF zija amati Extended Credit Facility zakhala zikubwera since Chakwera became President and amatiuza kuti their govt has trust of the donors komano on the ground chomwe tikuwona ndi umphawi okhaokha

  • @blessingmanda
    @blessingmanda Місяць тому +3

    lets welcome him

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of Місяць тому +2

    Zopanda tchito zimenezo munthu aliyese akakhala kunja kwa boma amaoneka ngati azelu

  • @PatrickMwamcheka
    @PatrickMwamcheka Місяць тому

    Inu mayiko onse muwaunawa otukukawa ali ndi ngongole zambiri mbiri ku chokera ku IMF for example south Africa zambia Nigeria just to mention a few

  • @LessonMnelemba
    @LessonMnelemba Місяць тому

    I know this Dennis. He was our university president. He is strong.❤

  • @SyilesChebomba
    @SyilesChebomba Місяць тому +1

    ❤❤❤❤❤ .koma uzamasionese ngope ata kukupanga chiwembu chimwene

  • @InnocentThamangani
    @InnocentThamangani Місяць тому +1

  • @kestenlemucha8316
    @kestenlemucha8316 Місяць тому

    he is a supper hero

  • @afonsolucias9339
    @afonsolucias9339 Місяць тому

    But he should be careful coz azungu safuna anthu okuda kom Ali anzeru...

  • @user-nd9cm3yl7e
    @user-nd9cm3yl7e Місяць тому +1

    Sumaona bakili muluzi tv amakationetsaso mapick omwe achimene akuyakhulacho katundu bakili muluzi tv

  • @khwimashawa9040
    @khwimashawa9040 Місяць тому

    ❤ tilipa mbuyopake

  • @HaliJana
    @HaliJana Місяць тому

    TIMUVOTELA KUSIYANA NDI MANYI ACHAKWERAWO MBOLA YOPINDIKA YA CHAKWERA, MFANAYO TILINAYO PA MBUYO BOLA ASAMUPHESO

  • @user-ie5pc4ox8i
    @user-ie5pc4ox8i Місяць тому

    Nokha mukumuyamikila nokhaso mukut ndindan alibe dzina aaàaaa😂😂😂😂😂mwatani kod

  • @kestenlemucha8316
    @kestenlemucha8316 Місяць тому

    NRC Natural Resources College-Tikuchidziwa bwino chipani chmenecho...😅😅

  • @salafinamhone-rd1ku
    @salafinamhone-rd1ku Місяць тому

    Yes Thomas njala was 29 from Burkina Faso, Abraham Tiro from South Africa was 28 but he asked un comfortable questions to these lolonial masters

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 Місяць тому +1

    Ndimaganizo abwino potengelanso kuti alikunja kwaboma ,
    Nkhope yeniyeni yamunthu imaoneka akakhala president wadziko , palibe amadziwa kuti uyuyu alipoyu ndi mwini umbava ndi umbanda ,

  • @cynthiataulo5211
    @cynthiataulo5211 Місяць тому

    Akhale careful with prayers and wisdom. Azungu ngakhalenso mbava zandale kumalawi zimusowesa.

  • @user-du8jv9oi5e
    @user-du8jv9oi5e Місяць тому +1

    Munthu ameneyo abwele bas 😊

  • @nafejonga972
    @nafejonga972 Місяць тому +1

    Tell him, he is welcome tinve zomwe akufuna kupanga

  • @Realbaaadman
    @Realbaaadman Місяць тому

    Munthu wa nzeru ameneyi, ati Denis Thanthwe Nkhang’a Mahata Eeh 🔥🔥

  • @runkenkasale4057
    @runkenkasale4057 Місяць тому

    Kwa ine uyuyu ndi munthu wofunika kwambiri muno mmalawi same like kabambe

  • @JaneMoyo-ws2di
    @JaneMoyo-ws2di Місяць тому +1

    Koma nde mwatilongosolera bwino. Great improvement bro. Kp it up

  • @williamhami1243
    @williamhami1243 Місяць тому +1

    Are countries forced to borrow money from IMF??

  • @gwatandingo9502
    @gwatandingo9502 Місяць тому

    Ngati kuli Anthu akuba kwambili pa dziko ndi IMF fiti za Anthu

  • @georgezikabuma9396
    @georgezikabuma9396 Місяць тому

    Bwanji sanasumire a president anthu? Mwawona tsopano kuti president mmangompaka zinthu zoti sizimukhudza. Mesa Inu mmati president ndi amene amatsitsa kwacha? President alibe chifukwa anthu mmangomunena popanda chifukwa.

  • @charlesdaisi616
    @charlesdaisi616 Місяць тому

    Bola azipanga zakezo mwanzelu, sikuonpa koma moziwa chomwe anguchite akaziwa ndekuti udolo wake ukhaladi odalilika zikomo

    • @charlesdaisi616
      @charlesdaisi616 Місяць тому

      Umakhala ndi nzeru zabwino koma ukazitulusa ndikumakhalabe mokhulupila aliyense umaphedwa nde azikhala oziwa. Tikufuna anthu oganiza zanzeru chocho koma azichenjela , osangoganiza then kufa aaa.

  • @andrewBwanaisa
    @andrewBwanaisa Місяць тому

    Mwana uyu ndi katakwe

  • @TraverMbewe
    @TraverMbewe Місяць тому

    Mmmmmmmm brz sadasumile km amangowaunikila anthu

  • @talentfreshfoods4607
    @talentfreshfoods4607 Місяць тому +1

    IMF sikakamiza ngongole. Timapita tokha kukagwada. Wamwa Ambuye mtengeni ameneyo.

  • @stephenkasusubanda3550
    @stephenkasusubanda3550 Місяць тому

    Izitu ndi zoona ndipo ine ndi zomwe ndakhala ndikumaganiza koma poti tiribe kuthekera kothandizira kusinthako. Anthu oganiza chonchiwa (let's support them)

  • @user-cy9zp4fb2m
    @user-cy9zp4fb2m Місяць тому +1

    Za zakazo zikumphinja kwambr look at Burkina Faso president zaka zake 35 akukwanisa kumene km izi zoti president akhala wazaka 35 above szoona zmnezo

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera  Місяць тому

      That's true bro za zakazi azioneso bwino

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b Місяць тому +1

    That's true

  • @ophlexmkondowe8107
    @ophlexmkondowe8107 Місяць тому

    Vuto si IMF koma amene amapita kukatenga ngongole kumeneko

  • @MorrisMapiri-d6z
    @MorrisMapiri-d6z Місяць тому

    I have loved him most

  • @tiyaselemani4203
    @tiyaselemani4203 Місяць тому

    Dziko la pansi limadani ndi anthu ozindikila take note

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg Місяць тому +1

    Munthu ameneyu Kodi chakwera samupha chifukwa chakwera mmmmmm palibe kalikose. I

  • @user-dc7qq9yz3v
    @user-dc7qq9yz3v Місяць тому

    Ndi chigayo Mr Mahata

  • @gwatandingo9502
    @gwatandingo9502 Місяць тому +1

    Koma muthu amwene ndi dolo kwambili

  • @user-um6ob9sf3g
    @user-um6ob9sf3g Місяць тому

    Vuto ndi asogoleli amafuna za IMF cholinga agawane

  • @MemorieMwasinga
    @MemorieMwasinga Місяць тому

    The great achievement

  • @alexanderlipenga1330
    @alexanderlipenga1330 Місяць тому

    Malawian cameras mwabwera inuyo, ask him akupasenso video ya press briefing yomwe anachititsa some two years ago around July 18/8. Ada awawa has what it take to be a leader except the so called age. Ngat presidential age ili open kwa gogo ikhalenso open kwa mwana.

  • @JustinLipipa
    @JustinLipipa Місяць тому

    Mmmmmmm atha kukhala president kwakanthawi kochepa, azungu atha kumupha

  • @staprickskilled8589
    @staprickskilled8589 Місяць тому

    Tili pambuyo pake 🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @AminAbbass-xc4qk
    @AminAbbass-xc4qk Місяць тому +2

    🎉🎉🎉🎉🎉🎉

  • @AaronzoAaron
    @AaronzoAaron Місяць тому

    Owo

  • @salafinamhone-rd1ku
    @salafinamhone-rd1ku Місяць тому

    And we need other kind of education,

  • @isaaczuze
    @isaaczuze Місяць тому

    Chakwera ndi mbuzi kodi ameneyi timakamutenga kuti mbuzi yosaziwa chilichonse

  • @user-xm3zl5cg6x
    @user-xm3zl5cg6x Місяць тому +1

    Ali bo kwambili tamulandila

  • @joelmakwinjakambalame9652
    @joelmakwinjakambalame9652 Місяць тому

    Kodi chilima nayeso mumati ndi wanzelu. Nzelu nsi ku school chifukwa zomwe timamphunzula ku school ndizoti ena analemba or they experienced it

  • @JohnPusi-c9f
    @JohnPusi-c9f Місяць тому

    Bola asasowesedwe

  • @BlessingsNyirenda-ru7ss
    @BlessingsNyirenda-ru7ss Місяць тому +1

    Tamulandila ife

  • @user-xd2iz1yx4z
    @user-xd2iz1yx4z Місяць тому

    Amwene mumvereni Denisyo mofatsa ndiye mubwerenso ndi presentation ina.

  • @EmmanuelMoyo-hy5ni
    @EmmanuelMoyo-hy5ni Місяць тому

    Malawi akufunika anthu ngati awa gwenembe amangovomelera chili chonse..

  • @MuhammadBAKILI-kl2mj
    @MuhammadBAKILI-kl2mj Місяць тому

    Mwasowatu boss

  • @user-xc2zm9bu1i
    @user-xc2zm9bu1i Місяць тому

    Amwene chakwera ndi wamkulu kwambirii, computer saikudziwa zangovuta Chilima uja
    Taonani 4 yrs yatha kuno ku Ntcheu wapanga chiyaniii
    Nsewu opita ku Dzunje panopa zoopsa kwambirii
    MCP sikuona kuti paground palibwanjii
    Ine siwandale,zithu zakwela kwambirii
    Dzikoli likufunika anyamata oganiza mwakuya not malilime
    Fertilizer mmmm zafikapa boma likadangonena kuti mafumu ayambeso kulamula anthu awo basi
    Boma lalephera
    Katangale mmm
    Kuvetsa chisoni mafana oganiza bwino akupitaso mmm

  • @JhdaLifi-vu9sd
    @JhdaLifi-vu9sd Місяць тому

    Tell them

  • @HamidavioletYassin
    @HamidavioletYassin Місяць тому

    Biseni chakwela asamuone asowatu kkkkk

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera  Місяць тому +1

      @@HamidavioletYassin 🤣🤣🤣🤣🤣 muli ndi Lawyer?

    • @alexanderlipenga1330
      @alexanderlipenga1330 Місяць тому +1

      ​@@MalawianCamera hahaha musiyeni nzanu alire mwamtendere kkk

  • @user-ln5hw7dn9g
    @user-ln5hw7dn9g Місяць тому

    Ndamukonda uyuyu

  • @user-nd9cm3yl7e
    @user-nd9cm3yl7e Місяць тому

    Dolo ndiyemweuja bakili muluzi tv bas km iweyo mani palibeso umalankula zogwila ntima kaya umaona ngati timazikonda umakambazi umazinamiza zd bola ungosiya umataya thawiyo zd

  • @user-jl6sq3ph1b
    @user-jl6sq3ph1b Місяць тому

    Eeeee ndi mwanadi ameneo kma ndi wa mzeru ka bwanji Ibrahim traole ndi mwanaso osakwana zaka 35 km bwanji akumukonda kwaoko ndie anawo amzeruwo kusiyana ndi akulu akuluwa ka

  • @user-wk9zh1qc5b
    @user-wk9zh1qc5b Місяць тому

    Okay

  • @user-ox4fh8pw9z
    @user-ox4fh8pw9z Місяць тому

    Kd Mesa ndalama za ku IMF timakapempha tokhaa?

  • @FlorahBanda-fl4vf
    @FlorahBanda-fl4vf Місяць тому +1

    Ali ndizaka 32 not 29

  • @MustapherDavie-su3nk
    @MustapherDavie-su3nk Місяць тому

    Tili Pambuyo pake

  • @MadalitsoChinkhonyo
    @MadalitsoChinkhonyo Місяць тому

    Palibe zosatheka man bwanji kodi

  • @alickmodi6449
    @alickmodi6449 Місяць тому

    Ndidolo mfanayo😂

  • @PatienceMhone-n5w
    @PatienceMhone-n5w Місяць тому

    Your talking zoveka zokha zokha

  • @hissimajohn965
    @hissimajohn965 Місяць тому

    Komano iyeyo Ali nazo ndalama?????

  • @PatrickThomson-p9u
    @PatrickThomson-p9u Місяць тому

    Ali bho ameneyo

  • @user-jl6sq3ph1b
    @user-jl6sq3ph1b Місяць тому

    Anawo ndie ali bwno km kunoko ndie eeeee sizingatheke

  • @AyamMkango
    @AyamMkango Місяць тому

    Abwinowa akumaphedwa chonde asamale mwanao

  • @Thembokatuli
    @Thembokatuli Місяць тому

    Amupha ngat chilima uyu

  • @user-nd9cm3yl7e
    @user-nd9cm3yl7e Місяць тому

    Komaso iweyo aseyee ndiwe kape zd umakambs zaukape ulibe zelu zd

  • @BakaliAdam-d3j
    @BakaliAdam-d3j Місяць тому

    Kamer❤❤❤

  • @user-nd9cm3yl7e
    @user-nd9cm3yl7e Місяць тому

    Ndesudziwaso kulondolalozakhani

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm Місяць тому

    Akhalise Malawi tankonda

  • @husseinmponda
    @husseinmponda Місяць тому

    Kkkkkkkk zachabe

  • @user-kj4kd1jo1z
    @user-kj4kd1jo1z Місяць тому +1

    Ayambe kaye u MP then next tym azaimile u President

  • @user-tb6yh1kx3o
    @user-tb6yh1kx3o Місяць тому

    Big lie alipo ena atha kusintha Malawi

  • @ritchardchakuma5725
    @ritchardchakuma5725 Місяць тому

    Tayipangani muve

  • @JohnAsendi
    @JohnAsendi Місяць тому

    Kodi sheikh mufuti madengo Ali kuti nkhani imeneyo amailongosola bwino ndithu ine ndimamusatila maulaliki ake Osati masheikh anawa satanizm

  • @sallymahata4376
    @sallymahata4376 Місяць тому

    🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @user-oc1uc6gz3w
    @user-oc1uc6gz3w Місяць тому

    Ndindanikwenikweni

  • @AudettaYohanie-fl3oc
    @AudettaYohanie-fl3oc Місяць тому +2

    Ndili pambuyo pake , and zikangotheka zoti aimile u president watenga vote yanga sure