Oganiza mopepela alikumbuyo Kwa usi.koma munthu okonda dziko lake sangapange support Michael usi chifukwa kamunthuka ndikoipa kosakonda dzikolake. zonse zomwe akupangazi nzotumidwa ndi MCP chonsecho MCP ndiyomwe inapha SKC Ka usi Kali busy kufuna kupasula chipani cha UTM
He has no timing Malawian are suffering but manganya is busy with politics we don't want such people in Malawi. It's like a house is burning then instead of helping to quench the fire you are busy questionin
Uyu sanali wa UTM anali running mate chabe, u VP ku UTM wake sunaoneke poyela mene malemu SKC analimoyo, anali spy wa MCP, sanakhalepo pa msokhamo wa UTM ndi ma executive members or candle right uyu ndiowukila mvundula madzi, Usi sanasakhingwe ndi ma delegates a UTM. Ameneyo apite kwa chikangawa basi, asamabisalile ku UTM.
Michael usi ndichifukwa anampereka chilima pofuna u president ndichifukwa akukakamira u president akanakhala dolo si akanakapikisana nawo pa convention
Ayende bwino azazindikira bwino patsogolo za Ku MCP akulowerako
very good ❤❤❤❤
Ayende bwino ife timafuna munthu wa mtendele osati manganyayo ai kabambe yemweyo tsogolo lathu lili ku UTM
Atuluke ameneyo
Oganiza mopepela alikumbuyo Kwa usi.koma munthu okonda dziko lake sangapange support Michael usi chifukwa kamunthuka ndikoipa kosakonda dzikolake.
zonse zomwe akupangazi nzotumidwa ndi MCP chonsecho MCP ndiyomwe inapha SKC Ka usi Kali busy kufuna kupasula chipani cha UTM
Adzaiona MCP kutsogoloku.
A usi ndachisilu koma ATI adapita ku school ATI ndiochenjera ATI nda president ATI nda vs president ATI amayesa dram ATI amayesa adafelanje😂😂😂😂
😂😂😂😂😂😂😂😂koma na nkhani ya manganya ikubweretsa phwete
Sitimamufuna ndiwa chikangawa party
Usi ndi dolo zimenezo muziwe chifukwa ali ndi anthu ambili amene akumusata moreover ali ndikuthekera chifukwa anthu akukonda ndalama ndiposo Utm ilibe power ngati Kaliyati adaluza
A mcp amene aja omwe amamulondora manganya
Ayambitse chake ndiomutsatirawo
@SabinaNkhoma-o1h ayambise kangati poti ichi ali ndi gulu lake moreover adayambisa nawo
Usi Ndi wandale becareful of usi
He has no timing Malawian are suffering but manganya is busy with politics we don't want such people in Malawi. It's like a house is burning then instead of helping to quench the fire you are busy questionin
Be careful of what
We need to forget about this guy . It's a bad guy
Uyu sanali wa UTM anali running mate chabe, u VP ku UTM wake sunaoneke poyela mene malemu SKC analimoyo, anali spy wa MCP, sanakhalepo pa msokhamo wa UTM ndi ma executive members or candle right uyu ndiowukila mvundula madzi, Usi sanasakhingwe ndi ma delegates a UTM. Ameneyo apite kwa chikangawa basi, asamabisalile ku UTM.
Sanathawe convention ameneyo
Amuchita bwino, ayende bwino ameneyo abwerere azikachita masewelo ake aka.
Ndipo zoonadi kukula mtima ko azikakulira kwina osati ku UTM
Ayende bwino
Ukalozedwa sumanunkha usi chakudya Cha ng.ona za mcp
Manganya akuona ngati akuchenjela koma one day azathamanga
Akudzimva a Ausi, Ali pauchi pano adziwanso patsogolo.
Achoke. Ameneyondikape. Ndioipa
Manganya alibe DEMOCRACY....Munthu anathawa convention and thinks anafikapo owning UTM....Ma leaders oterewa sakufunika m'Malawi...
Michael usi ndichifukwa anampereka chilima pofuna u president ndichifukwa akukakamira u president akanakhala dolo si akanakapikisana nawo pa convention
Usi anapanga bwino otsapita and UTM apanga bwino ayambise chipani chake chifukwa Usi support ali naye. Ambiri amulondola Usi and amamukonda
Usi ndi sikwisija ndigwenembe muthu oyipa kwambili
Musachedwe ndi kunyoza gwirani baibulo.... masiku omaliza baibulo linanena zamasoku omaliza. Sipadzapezeka wangwiro ochoka mwa mkazi
Manganya siokula mtima koma ndichisilu cha munthu
Manganya ndi kape, koma azaziona mcp sipanganika amufuse chilima ndi mia
Kape ndi amako
manganya achoke ndithu ayende bwino
manganya. ndifiti. ameneyo. mphaka wachabechabe. akuona ngati. madilama. akanakhala kuti ndiwa UTM. sibwrzi. atapeleka mwiniwake. wa UTM.
ndipo. manganya. chomwe. angaziwd. mcp. yake azavotela. iyeyo ndi. male. sikono. uzivele. chocho. manganya. mau unayankhula. aja. oti. boma. ndilomweli. zimenezo. uzakauza. achambuyako. machi. ameneo. a mcp .sitikupanga nao
Usi sazikonda is politics kunyozana sikwabwino
Adzipita basi😂😂😂
Vuto lake ankadzimva kuti UTM singakhalepo popanda iye...kamdothi
😂😂😂😂Ndipo chikangawa akuwonesa nyekwe Ndipo ukhaula apite futsek
Amuchita bwino kumuchosa apite komwe amasatira malamulowo apite basi asasokoneze
Amuchita bwino watitukula ameneyo akakhalise akupitako
Tamangogwirani magobo ku ukapolo wanuwo nanuso munthawa kwanu kale kale
Usi ndi dolo mwachepa ndi akabambe anuwo.munaoneka uchitsilu ogulitsa chipani kwa kabambe.olo zitatani kabambe sangalamulile malawi.munamizana
Inunso mukuonesa uchisiru moti simukuona.
Kodi anthu amene akumusatilayo azavotera bwanji manganya popeza sazakhala nawo pa baloti kumaganiza zinazi please anthu Ngati amenewa ndamene akusokoneza ziko
Manganya ndi osokoneza,
Nkhazereza ako kachitsiru keni keni kamaziwona ngat kanamukonda Chilima koma ata ndamene wamuphesa nzake
Chatikwana chitsilu chimenechi
Chitsiru ndiweyo
Zopepela basi usi ndindani kundale
Awadi afupiwa ndikape kwabs munthu oipa
Awusi ayende bwinp
😂😂😂😂 manganya chisiru kwabas
Usi akufuna kugawanisa chipani
Kod ndmakapetu mu2 opanda maso mphenya osazifunsa kuti iyeyu pano ndmu2 wamba
Kabambe,m'maonekedwe ndi wa UTM,koma mumtima ndi wa DPP,omwe muli a UTM eni-eni,khalani maso
Chipani chinatha kale
Manga ndifukwa chani ukukakamila tuluka yamba zako wava!!!
MCP imuchosanso