Ati akaonekele Ku committee ya UTM, ATI alemba kalata, don't go bwana Usi, anaba chipani cha Chilima awa, UTM B under the leadership of DPP. Manganya yekhayu mutsagula naye mmimba kkkkkkkk
Mr. Usi musaoneke dolo koma muli kape you're dolo pa tikuferanji koma pa politics nde ndi 0 pa ten so be careful Mr Man udindo muliwo you know why you are there.
Ovota ndi anthu azavotera Michael Usi wa chipani cha UTM. Achina Kabambe musamale muzadzidzimuka pa ballot ya paper ya UTM pa nkhope ya Usi ndipo it will be too late. Waponda mwala uyu. Muonetseni kuti Institution is bigger than anyone
Ku Mulanje atsogoleri ake pa ndale ndi agalu. Amayamba bwino koma chifukwa cha dyera ndi ugogodi amatha mwa uchitsiru. Ena amagulitsa chipani ena anachotsedwa komanso ena amathera munsewu.
Akulu awa Alandidwa mpando ndi Kabambe. Ndeno mmalo mot apite akakhale Vice president. Next year MCP sizawaganizira chifukwa kuli anthu oti azakhala VP. Okay?
I love you Michael Usi... umakwana ndipo we are behind you Usi..wodana ndi inuyo akuzida yeka.
Bravo Mr usi inuyo muli bwino basi🎉🎉🎉
Muchredwa ndikulemba za tikuferanji, Chilima pomutenga tikuferanji Mesa inalipo and amaziwa kuti uyu ndi wa tikuferanji? Guys mukamati tikuferanji, Chilima pomutenga tikuferanji kunalibr?
Manganya Moto kuti buuuuuu ❤❤❤❤
Mooo fire 🔥🔥🔥🔥🔥 motooooo
Ichi ndi chida chomwe MCP ikugwilisa ntchito pofuna kuononga UTM ndi kubwelesa mupungwepungwe pa ndale kuno ku malawi.
Those commenting against Usi they are killers of Albinos, never again DPP, Kabambe ndi otumidwa Ku DPP that's why Usi akukumasulani
Ichi chinabwera I love him😂😂
I love this guy for no reason 😂😂
Mwabaya bro
Kabambe ndi kape that's why enanu mukutukwana😂😂
usi fundozake zimanisangalatsa kwambil ndipo usi nidolo osat akabambe aja nimanyaka anthu otsatila akabambe saganiza
UYu ndee yudasi amene anampereka yesu
My vote my Usi ❤❤❤❤
Nkhani ya ada awa izakoma musogoro atawataya ngati ma vp Azawo aja
Ati akaonekele Ku committee ya UTM, ATI alemba kalata, don't go bwana Usi, anaba chipani cha Chilima awa, UTM B under the leadership of DPP. Manganya yekhayu mutsagula naye mmimba kkkkkkkk
Niveverere niveverere 🎉 ihave mulo🎉 tahava kale mulo
UTM inabedwa ndi DPP functionaries
Anthu akhungu akungotsatira osapenya chomwe chikuchitika
Awa apenga awaa
Mbuzz iyi, achotswdwe mu utm,adatumidwa ndi mcp
Wakwiya ndi mfiti Usi ndi akatundu
Mr. Usi musaoneke dolo koma muli kape you're dolo pa tikuferanji koma pa politics nde ndi 0 pa ten so be careful Mr Man udindo muliwo you know why you are there.
Uyutu ndi wa maboza cholinga chake asokoneze chipani basi mesa uyu ndi wa boma ndilomweli akusintha bwanji kuti ndi wa UTM akuzitenga wochenjera
Basi Tingopanga Za Tikuferanji Yimweyu😅 aah Nanga Nkutani...💔💔😔
Usi is slowly invading UTM begninly, Tactian he is. I salute you.
Kaya ku utm mabvuto anu amenewo ife tayima njii ngati chisa chotsala mulupya pano tingoti DPP OYEE! APM OYEE! 2025 BOMA!
Udisi sikaloti muthu oipa mugwela limodzi mr chikangawa ndipo mudziyakha ndithu pakhoti ife tikadziwa kuti ndinu mcp kale ndiye umafuna utingulitse kwa zingawenga za mcp udisi sikaloti udisi sikaloti udisi sikaloti udisi sikaloti udisi sikaloti
Njara yakupwetekani
uyu mungomusiya otherwise akuyalutsani!!!!!! koma penapake akunena chilungamo!!!!
In black missionaries word "angochimwirabe, chimwirabe"
Zipita ku tikuferanji make sikono akudikila uko.
Ovota ndi anthu azavotera Michael Usi wa chipani cha UTM.
Achina Kabambe musamale muzadzidzimuka pa ballot ya paper ya UTM pa nkhope ya Usi ndipo it will be too late.
Waponda mwala uyu.
Muonetseni kuti Institution is bigger than anyone
100% i can agree with you n people on that day will be shocked
Anaononga malamulo komwe angakaaumeko kuti mwina chilungamo chiziwike,,nanga muzichedwa ndikuyankhulana zamalamulo mpaka riti?
Uyuyu nde amene adatumidwa kusokoneza chipani osati zomwe akukambazo ngosokoneza awa
Koma man wa ndiofoila. Tsiku lina amati boma ndi lomweli kunena MCP
❤ 7:00 7:06 7:06 7:06 7:07 7:07
Ngati kuli munthu oipa ndiye mwandionera patiyu anampeleka chilima kamba kofuna u vp,musatinamize akuluwa nga mcp kuchokera nthawi yomwe tinataya anthu pangozi ya ndege munamuonapo atachitisa msonkhano?mudabwe naye kapilikoniyu ndi wachakwera
ausi,akukunyozanio,asiyeni,apatseni,anthu,chakudya,
Mkuli bwanji osangonena Kuti ndinu A MCP bwanji😊😊😊😊
Uyu adzipita, ku UTM sitikumufuna
Drama yeni yeni iyi!!
Ku Mulanje atsogoleri ake pa ndale ndi agalu. Amayamba bwino koma chifukwa cha dyera ndi ugogodi amatha mwa uchitsiru. Ena amagulitsa chipani ena anachotsedwa komanso ena amathera munsewu.
Akagwere uyu
Ndalama zapa maliro zikukukhunzan chan bwana??
Za imfa zizaululike kaye
Kuulula ndiye kofunika ndithu
Za ndale sungazimvetsetse😮
Utsi kape 😂😂😂😂
I❤him
Km iwe manganya ndwe munthu omvesa chisoni, ndpo ukumvesa mzimu wachilima chisoni ndpo mulungu kumwambako akuone manganya iweyo ndpo ndiwe yudasi
What will my grandkids say about this incident ?😂😂😂💔
Drama at its best 👌
Ukungotaya nthawi munthu opanda chipani kapolo wa chakwera
Ati ndikamat ndilibwino,, ine ndilibwino 😂😂😂 baller
More fire usi
Alomwe busy kulimbana nokhanokha tikuonerani. APM, Usi, Kabambe. Zikatero MCP ikumva kukoma pomwe dpp ikupasidwa mpata ozawina😅
I don't understand Michael Usi Kodi Ali chipani chanji?
Iwe ukuona chipani chanji apa?
Michael usi ndidolo
Adawa akuzibalalisa okha
Ngati siatsogoleri nde ku utm atsogoleri ndani?
ma journalist tamafusani mwanzeru. mukufusa ngat mukumuopa michael usi bwanji. akuzemba mafuso inu mungoyangana
Manganya mapwal ako wav
Kape iwe unathawa convention
Alibe Chipan
He is not happy with what is Happening 😔💔
Yawawatu eeeee 😢😢😢
Uyu AKUTENGA ake Ku UTM ndipo igawikana siinati kukhoza kukhala kutha Kwa UTM
Ndinapita andi ndimapuma ayi dzikomo 😅😅😅😅😅
Anathawa ku convention galu uyu
Mpomwe aziwe usi anrju amakonda Utm oho apitilize anthuwo kuwapasa za utm oho
Koma ndiye akwiyatu bwanawo kkkk
Pa dziko lapansi palibe munthu yomwe amakondedwa ndi munthu aliyense.... Kaya ujoina mcp ndilikoko... Kaya uyambisa chipani china go konko
Ndale zochedwetsa izi
Muli bwino vice president
Usi akuti ndi wa UTM nde povota amene akutsatira Usi azavotera ndani poti akuti ndi a UTM
Usi ndi akatundu
voti,yanga,kwausi
Mabi eni eni😂
Manganya iiiiiiii uyu anakonza 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Mutiwuzekolowela bwana njawala atisokeletsa
atsutse,ngati,ukunama,patilisha,kaliyati,anadya,km,kutukwana,anzawo,
Ubwino wake SKC adaona kale tikuferanjiyo nde olo tizinyoza ndekuti tonsetu tidakonda drama
Koma uyu ndiwachipani chiti?
Usi ali ndi nsanje yopanda nayo manyazi akungolankhura zopanda pake
Ndipo iyeyo ndiamene akulimbana ndi UTM mmalo mopanga ake
Kkkk wapenga 😅😅😅😅😅
Koditu mungoyakhula zanzanu. Ka u president kaja mumakafuna Kwambiri eeee
anjawala,musamutenge,ngati,mbuli,usi,,muchedwa,naye,musiyeni,,mupusanaye,pangani,zanu,manganya,sigalu,ayi
😂😂😂😂😂 ine ndir bwino
iwe,manganya,alomwe,anzakowo,,amafuna,nlomwe,aliyese,azipanga,zaiwowo,basi,ndalezawo,ndizimenezo,ndiye,wakumananaye,manganya,,,,safuna,zasankho,
Sinaimverer ndi kape man awawa
Akatundu omanga Ndi mawaya kkkkkkk
Akulu awa Alandidwa mpando ndi Kabambe. Ndeno mmalo mot apite akakhale Vice president. Next year MCP sizawaganizira chifukwa kuli anthu oti azakhala VP. Okay?
This is drama at the lowest level this total madness
ukunena,zoona,ukapanga,nsonkhano,umapeleka,chakudya,nanga,enawa,akukunyozawa,amapeleka,chiyani,,
watenga,utm,yose,manganya,
Tiyen tidye ndalamazo ndimisokho yathu sizake
Umatha bwanawe
Tsono ngati munadya ndalama za pa maliro ndiye nanga mutalowa Boma tizaona zotani? Tikalodzedwa ndikuvotera DPP or UTM basi Malawi wathera pamenepa.
manganya,tikufuna,mutenge,masapota,ose,
Openga ndiopenga sangasinthe
usi,enawa,ndi,ana,akhululukile,ndiwe,dolo,
Ine ndingotsatiraso usi emwei zinaz ndizigawenga km uyu yekhe ndlibe nayo mulandu
Nanga MCP inapeleka ndandandz wa ndalama zomwe anayendetsela maliro
Nakhuma ankalimpha lumpha chonchi koma pano kuli ziiiii onse ankaoneka ngati ali limoz aja anamutuluka
Born kalindo ndi dolo kwambiri adanena kale izi zogawana UTM
Kkkkk iwe ndiye uli kutikuferanji kkkk