Michael Usi - Akanaziwa sakananena izi

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 4 січ 2025

КОМЕНТАРІ • 116

  • @MathewsChitambe-m6o
    @MathewsChitambe-m6o 2 дні тому +9

    Kupepela ,kuzimva kuchenjera osadziwa ndi kupepela.,kutha kwake kwa manganya pandale kwafka..

  • @jeremiahmalikebu2393
    @jeremiahmalikebu2393 День тому +4

    Ichichi mchitsiru kwambiri. chimvekere don't fight on social media, pomwe icho chiri busy kuyankha zinthu pa msonkhano, zinthu zosayenera kuyankha pa nsonkhano. Ngati ali dolo akanangovomereza chiganizo apanga a UTM cho mwamtendere basi, atenge anthu ake akumutsatirawo.

  • @Nelson-yu2tm
    @Nelson-yu2tm 2 дні тому +15

    Kuchenjera mopusa manganya

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 19 годин тому +1

    Manganya anabalalika u vice wamuwonongela sogolo pa ndale litha pa September apa

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 День тому +4

    Nancy wa Chenkope akuti akuti ndale zawo zochititsa nselu kkk

  • @JoefreyGongoni
    @JoefreyGongoni 10 годин тому

    Aka kagalu, kupha Chirima kufuna kukhala vice president zachosoni 😅

  • @ManzeEmmanuels
    @ManzeEmmanuels 2 дні тому +7

    The biggest mistake SKC did pomusankha Manganya kukhala VP wake mistake yayikulu lero Manganya anatengapo gawo pa chiwembu cha SKC Manganya akuzitenga ngati dolo chifukwa SCK kulibeko if Manganya was a true of SKC lero bwenzi Ali munthu mmodzi amene akanafuna kudziwa chimene chinapha Best friend wake SKC may his rest in power kuti mulungu alange onse amane anatengapo gawo Esp Manganya

  • @charlesdzinkambani5478
    @charlesdzinkambani5478 6 годин тому

    Kodi bwana ngati convention siyovomelezeka inuyo muyitanitsa yovomelezekayo liti?

  • @muhammadstaubi4604
    @muhammadstaubi4604 17 годин тому

    Kaliati sadziwa ndale,akanakhala ochenjela akanakhala pansi ndi usi ndiye kuti akanayiwina utm.

  • @DOLADAUSI
    @DOLADAUSI 12 годин тому

    Bwana asakutopetseni tangotulukani ku UTM 😅

  • @shinyrobert2003
    @shinyrobert2003 2 дні тому +6

    Angomuchotsa koma mvula lero ndiye yavumba eeee😊

  • @RoseMkandawire-e2g
    @RoseMkandawire-e2g День тому

    😂😂😂😂ineso nakomoka muribe fundo.umo mumuone kakono ako

  • @ChristinaMdeza
    @ChristinaMdeza 2 дні тому +4

    Abambo woyipa inu munapha chilima inu kodi Mesa inu ndi a.mcp leo kumagoti chilima ngati mumamukonda inu

    • @WysonChilonga
      @WysonChilonga 2 дні тому

      Ndikudabwa nawotu,osamaganiza ngati mzibambo iyayi😢😢😢😢,anafupika ndi nzeru zomwe

  • @ValerianMwafongo
    @ValerianMwafongo 19 годин тому

    Kakuthawa funso ali chipani chiti atiuze 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 19 годин тому

    Akuyankhula ngati akuyqnkhulila bungwe la tikufelanji osati nkhani za dziko

  • @DOLADAUSI
    @DOLADAUSI 12 годин тому

    🤸🤸🤸🤸

  • @AlubiRafiq
    @AlubiRafiq День тому +1

    Manganya is a reader of wadya zake alibe mulandu

  • @MarthaMagwede
    @MarthaMagwede День тому +1

    Ndiye anthuwo akuwauza kuti akavotele ndani? Uyu ngwa mcp uyu,, may the soul of SKC continue resting in peace

  • @RolrandNyirongo
    @RolrandNyirongo 2 дні тому +12

    Ine I don't see any mistake mwa usi people will always throw stones on a productive fruit tree, chilima new that this man is not just amare man

    • @StarfordKAMOTO
      @StarfordKAMOTO 2 дні тому +1

      Kkkkk muzaziwa pasongolo

    • @LinlyMathewe
      @LinlyMathewe День тому

      Aaaa ana anjoka inu yemwe angayankhule izi ndi wa Mcp yekha kuti sakuona vuto la usi

    • @HarryYottam-ft1bo
      @HarryYottam-ft1bo День тому +5

      Iwe usapuse naye uyu, iyeyu ngat mtsogoleli anachitapo chan pa imfa ya chilima, tikunenapano mwambo wa ma candle Even single day, kuchikangawa mpaka pano sanakaonepo panafera chilima, ngat kuli munthu anasangalala ndi imfa ya chilima ndi ameneyu, yudase wachabechabe

    • @SolomonNjolomole
      @SolomonNjolomole День тому

      @@RolrandNyirongo ndiye kuti muli ndi vuto inuyo ngati simukuona chakwika .

    • @noelcheonga8247
      @noelcheonga8247 День тому

      Inuyo sumungaonepo vuto sinanga nonse ndinu ayudasi okhokha

  • @DumiMhango
    @DumiMhango День тому +2

    Kachindele aka

  • @sthoramexjrsa902
    @sthoramexjrsa902 2 дні тому

    Komatu awa zot history is best teacher saziziwad mmmhhhh😮

  • @GraceChenda-q2g
    @GraceChenda-q2g День тому +1

    UTM iyi nde ya Chilima::osati iwe wopusa

  • @MaryBushiri-s1f
    @MaryBushiri-s1f День тому

    Kkkkkkkkkkkkk mpaka kuyakhula chi bwibwi uyu nde wantha pasi

  • @corretabanda7685
    @corretabanda7685 15 годин тому

    Inunso muli ndivuto

  • @TryceMagombo-sh7kb
    @TryceMagombo-sh7kb 19 годин тому

    Mufuna utm igwane pakati zomwe nzosatheka mulungu watumoza munthu weni weni amene angapite pasogolo ndi chipan Cha utm mwakhala matako kuwiri bwana

  • @Mervic-vm8eo
    @Mervic-vm8eo 9 годин тому

    Manganya bwererani ku tikuferanji ,,you taking no Sense 😂😂😂

  • @MercyNkhoma-b6h
    @MercyNkhoma-b6h 2 дні тому +2

    Koma mpakana Henry Gopani 😂😂

  • @christopherbanda1084
    @christopherbanda1084 День тому

    "...Wherever I go, they come.." Anthu ake ndiomweomwewa eti?

  • @muyabasamson
    @muyabasamson День тому +1

    Galuiwe

  • @MavutoFodya-p1u
    @MavutoFodya-p1u День тому

    Kkkkkk kma mpaka thukuta kkkk ndakomoka🤸🤸

  • @jameskachulu8141
    @jameskachulu8141 2 дні тому +5

    Amanyadilatu uyu imfa ya chilima

  • @AlexMaganga-u7p
    @AlexMaganga-u7p День тому

    mmmmh koma ndalamaaaa abaleeee.....ayi ndthu

  • @FayinesiKondwani
    @FayinesiKondwani День тому

    Uyoooo yudasiyoo muntu ngat phonda😅

  • @SydneyNyasuli
    @SydneyNyasuli 2 дні тому

    My vote ❤

  • @StellaMicheal-q1j
    @StellaMicheal-q1j 2 дні тому +1

    Usi ndi Boma bs tilinganganga ndi usi jelasi bwanji musiyeni usi muona malaulo

  • @LM-gz5pk
    @LM-gz5pk 13 годин тому

    Pangan chipan chanu akulu

  • @JulietLizziePhiri
    @JulietLizziePhiri День тому

    Kudzitenga u Mr know it all Manganya

  • @IsaqueFernandoAntônioAntônio
    @IsaqueFernandoAntônioAntônio 2 дні тому +2

    Manganya amalankhula ngati gopani henele

  • @jameswajumpha6790
    @jameswajumpha6790 День тому

    A usi akamanena Za ndilama Za maliro ndekuti iyeso anali mu gulu ndekuti iyeyo ndi olakwisa coz anali osogolera that time

  • @SherifaG.Mlelemba
    @SherifaG.Mlelemba День тому

    Atenthedwa munthu wamkulu😂😀😀😀😀
    Koma olo ine ngakhale UTM, simbari yanga koma zomwe akuchita awazi Aaaa! Zimachita kundilowa mumtima, kuli kundikwana..... Akondwa nawo udindo akuluwa....
    Ati achipani changa ndi awo, muwaona apowoo😀😀😀😀

  • @ChristianThipa
    @ChristianThipa 21 годину тому

    Awa offcourse chomwe akufuna ndi ndrama kma sakazidya mosangalara akazakhara pa chete ndikuganiza mofatsa about SKC

  • @MoosaBinamu
    @MoosaBinamu День тому

    China chimene manyanya akanachita ndikupitilidza kumenya khondo imene Dr skc anasiya pofuna kuwamenyera amalawi khondo yofuna kuthesa uphawi ndi jala ku malawi 🇲🇼

  • @mophatblessednyirongo7647
    @mophatblessednyirongo7647 2 дні тому

    No matter what one says here, Usi remains the right vs candidate for UTM.
    Kodi pomwe chilima ankasankha manganya ena onsewo adali kuti. This shows that all other members were Manyaka and Chilima wasn't stupid for opting for manganya, there is a doctorate mindset in him

    • @MathewsChitambe-m6o
      @MathewsChitambe-m6o 2 дні тому

      Manganya anasankhidwa kut zomwe malemba anañena zikwanilitsidwe zot nkhondo ndi anasi.komanso kut anthu MCP aidziwe bwino bwino zot ndiyakupha

    • @YohaneStevenMhone
      @YohaneStevenMhone День тому

      Manganya anasankhidwa ndcholinga

  • @TendaiKachingwe-f5s
    @TendaiKachingwe-f5s День тому

    Ngati inali convenient yolakwika iweyo osapangitsa convenient ya UTM yo bwanji

  • @muyabasamson
    @muyabasamson День тому

    Akuvotera niamako

  • @JuniorSamalia
    @JuniorSamalia День тому

    Munthu osokoneza, asatha nthaw imodzi mkulu uyu

  • @Edward-t2z
    @Edward-t2z День тому

    Adye nawo basi. Atipeza vinyo akatha

  • @MacxwellStuarts-h9r
    @MacxwellStuarts-h9r День тому

    Chilima pamene amkatenga usi ngati wachiwili wake ku utm samkaziwa kuti akhonza kuzamupereka mphoto yake ndi u vice president ku mcp

  • @nickmumba2131
    @nickmumba2131 День тому

    Mbola iwe usi

  • @SYDNEYMUHAMBUWAGIBSON
    @SYDNEYMUHAMBUWAGIBSON День тому

    Za ziiii

  • @Davis-qo4qp
    @Davis-qo4qp 2 дні тому +3

    Chilima he was not utm but leader of utm

  • @mabvutomichaelpanagona1949
    @mabvutomichaelpanagona1949 2 дні тому +1

    Iweyo usi ukuumirirabe chifukwa chiyani ?ukungoti anaphwanya malamulo malamulo ake atiwo kodi munapangana chiyani ndi malemu chilima RIP usiye iweyo kumangochula dzina la achilima chifukwa iweyo ndiwe wa MCP ukukamba zazii asiye anthu a UTM ayendetse chipani ndiwe chitsiru manganya ukufuna kuonetsa ngati chilima umamukonda mpamene ayi sumamukonda ayi, kazitape iwe manganya.

  • @StanleyChamasowa
    @StanleyChamasowa 2 дні тому +2

    Ndikhoswe uyu swiswili

  • @WillianBanda-p7d
    @WillianBanda-p7d День тому

    Iwe usi ndiwe munthu wopusa kwambiri

  • @DavidPhiri-o6w
    @DavidPhiri-o6w 2 дні тому +1

    Usi is best leader, njawala kaliati kambala mutima yoyipa

    • @LinlyMathewe
      @LinlyMathewe День тому

      Chikangawa child Sasowa zo yankhula zake like you

  • @CatherineNantchengwa-d4w
    @CatherineNantchengwa-d4w 2 дні тому +2

    Gopani kkkkkkkkkkkkkķkkkk

  • @wonganimwase9881
    @wonganimwase9881 9 годин тому

    Heard his first wife left him due to kulalata and umbombo....

  • @kondwanimunthali7401
    @kondwanimunthali7401 День тому

    Akufuna kudya awa

  • @BruceBanda-q3p
    @BruceBanda-q3p 2 дні тому

    Kodi suuja mmati boma ndi lomweli mmatanthauzanji? Boma lake liti?

  • @DumiMhango
    @DumiMhango День тому

    Yudasi ndiweyoka

  • @beatsbymcstevens
    @beatsbymcstevens 2 дні тому

    Ngat chakwera wataya Hara VP wake Usi ndi ndani? Dziko lidzamuseka

  • @kennedybanda
    @kennedybanda День тому

    A utm chomwe akufuna kuchita ukuchidziwa kutanthauza kuti iwe ndi wa mcp nde ukukakamira bwanji utm yo.

  • @eulamandra
    @eulamandra День тому

    The afrika i know, instead of developing their countries bizy forming parties inorder to steal from poor pipo

  • @ashingsmvula3357
    @ashingsmvula3357 День тому

    Usi is innocent, kungoti UTM is full of hate...it's sheet, no need to be called a youth party...muli mangawa oipa kwambiri

  • @AndrewChaipa-ub5zu
    @AndrewChaipa-ub5zu 2 дні тому

    Iwetu manganya ukhale pasayizi yabwino koma zotengela madramaz mmmm Malawi wake siwalero, mmmm, ubwini wake uti mh

  • @PartsonMdeza
    @PartsonMdeza 2 дні тому

    akut anthu akalembetse
    funso ndlot akavotere MCP UTM or alliance yawo

  • @GodfreChayamba
    @GodfreChayamba 2 дні тому

    Usi ndi ndiwe kasongo koma uzasiya usaiwale kuti mcp. Sipanganika

  • @victormbwanda-b3e
    @victormbwanda-b3e День тому

    I think bwanawa akuyenela kutiuza kt malamulowo opitila ku convesation amati chani

  • @MoosaBinamu
    @MoosaBinamu День тому

    Koma manganya amayenela to stand has a vaise president of skc not has a vaise president of chikangawa ayi.

  • @DalitsoPhiri-sq5nl
    @DalitsoPhiri-sq5nl 2 дні тому

    Anafupika sinkhu including zeru zomwe usi

  • @andreabanda7838
    @andreabanda7838 День тому

    But he missed the chance at the convention. Now he has no mandate whatsoever.

  • @ExcitedBreakingWaves-oh3zb
    @ExcitedBreakingWaves-oh3zb 2 дні тому

    Ausi zanu zayipa apa.

  • @MadaloMachedwetsa
    @MadaloMachedwetsa День тому

    Anafupika ndi mzeru zomwe uyu

  • @NdaonaMsowoya
    @NdaonaMsowoya 2 дні тому

    Uyu ndi yudas wen wen

  • @petertengani
    @petertengani День тому

    What's new here?. You won't go far in life, with click baits.
    Za ana, safuladi eti?.
    Ma 2000's.
    🤦🏽‍♂️🤦🏽‍♂️🤦🏽‍♂️.

  • @FalesiKasiya
    @FalesiKasiya День тому

    Komatu ukuku sikopangira misonkhano, dziwani kuti anthu amapezerapo mwai olowa kumalo ngati awa, this is exposing Malo awa, and it's a threat Kwa Anthu Omwe angadzakhaleko inu mukachoka masiku akubwerawa. Kusatsata malamulo akunena ko, osatsata malamulo ndani? Msonkhano ku nyumba za boma

  • @JacobMsukwa-q6v
    @JacobMsukwa-q6v 2 дні тому +3

    Am happy anakachotsa muchipani aka 😢

  • @blessingsmasina9254
    @blessingsmasina9254 День тому

    Why hasnt he spearheaded the truth about Chilima's death.

  • @DanielJuwawo-s5n
    @DanielJuwawo-s5n 2 дні тому

    Adachenjera udyo

  • @patricksinyala1345
    @patricksinyala1345 2 дні тому

    Chitsilu Usi mfiti opemphela

  • @GraceChenda-q2g
    @GraceChenda-q2g День тому

    To see you for what?Satana oyenda ndi myendo::apatse ndrama zama tembererozo

  • @TerryNac
    @TerryNac День тому

    Manganya iwe ngati anthu sakukufuna sakukufuna basi osalimbila udindo iwe mzeru zautsogoleri ulibe koma ma drama

  • @OdettaLowrence
    @OdettaLowrence 2 дні тому

    Two between iwe manganya

  • @TerryNac
    @TerryNac День тому

    Manganya 1:59

  • @SandfourKatambo-r4v
    @SandfourKatambo-r4v 2 дні тому +1

    Abwerele ku tikufenji bas fundo alibe

  • @maxwellngulandebanda
    @maxwellngulandebanda День тому +1

    This man is controversial and he's not even relevant politically

  • @IsaacEMadeya
    @IsaacEMadeya 2 дні тому

    Uyu ndiye Gopani weniweni(papa)kkkkkkkkk

  • @EUGINEMWADALA
    @EUGINEMWADALA День тому

    Awa anakakhala a nzeru akanatuluka okha before kuchotsedwa not kumangoyankhula zaziiii
    This guy is 'attention seeker'