MPAKA VICE PRESIDENT WADZIKO MICHAEL USI KUYANKHULA IZI PAMBALANGANDA?? UTM AKUIPITITSA KUTI KAYA

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 10 лют 2025
  • MPAKA VICE PRESIDENT WADZIKO MICHAEL USI KUYANKHULA IZI PAMBALANGANDA?? UTM AKUIPITITSA KUTI KAYA

КОМЕНТАРІ • 76

  • @FransBanda-z9g
    @FransBanda-z9g Місяць тому

    Well articulated, tell them the truth.

  • @MichaelpenielPhiri
    @MichaelpenielPhiri Місяць тому +5

    This guy is so wonderful

    • @WelingsLongwe
      @WelingsLongwe Місяць тому

      This guy is saying the truth and he what is talking

  • @fatsanibanda5733
    @fatsanibanda5733 Місяць тому +4

    UTM ndye Usiyo....uyu apweteka gulu
    😂🤣

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick Місяць тому

    usi,woyeeeeeeeee

  • @YohaneChinkombelo
    @YohaneChinkombelo Місяць тому

    Please change Malawi people they worried .. no food, no jobs, no money. Please your are front because of pple

  • @Maishandagundi
    @Maishandagundi Місяць тому

    Mudyeleni ameneyo,
    Nebukandinezara,alezera udindo,kmaso akunjoya imfa ya chilima,
    Ndipo akusakira chikangawa anthu coz adzapanga alliance

  • @VictoriaKumwenda-k6o
    @VictoriaKumwenda-k6o Місяць тому +2

    Ausi moto kuti buuuu❤❤❤

  • @geraldmtika7961
    @geraldmtika7961 Місяць тому

    Koma anthu ambiri avala utm ,mwina samaziwa?

  • @asamzymw571
    @asamzymw571 Місяць тому +3

    Ine usi amandiwaza

  • @danielstorey5655
    @danielstorey5655 Місяць тому +2

    Next year manganya azasowa kopita izo tudziwa

  • @tamalangoma2765
    @tamalangoma2765 Місяць тому

    🤣🤣This is so entertaining, Mr Usi my VP.kkkkkk

  • @Maishandagundi
    @Maishandagundi Місяць тому

    Amalawi ena? Alibe manyazi

  • @AlexisKantondo
    @AlexisKantondo Місяць тому

    History is the best teacher be careful

  • @IsaacChitaro
    @IsaacChitaro Місяць тому

    Ndikape usi

  • @HenryLaidon-pl9ly
    @HenryLaidon-pl9ly Місяць тому +1

    Things for NATIONAL INTEREST basi kumajambulanso SEWERO

  • @MeruMitha
    @MeruMitha Місяць тому

    excellent vp ulemu wanu mwanjoyetsa anthu 😅😅

  • @AdamJuma-q7m
    @AdamJuma-q7m Місяць тому

    Musamasokoneze ,anthu wo ndi a odya zake alibe mlandu , not UTM 😂😂😂😂

  • @giftmeck
    @giftmeck Місяць тому +2

    A usi ndinu mbambade

    • @giftmeck
      @giftmeck Місяць тому

      🔥🔥🔥🔥

  • @emmamolande8193
    @emmamolande8193 Місяць тому

    Sewelo la kapalepale 😅😅😅

  • @AgrihortSuppliers-s7m
    @AgrihortSuppliers-s7m Місяць тому +1

    Utsi ngati uli ndi misala . iwe Ku mnsonkhano waukulu sunapiteko ndipo sunasankhidwe, ndipo omwe akukusatilawo ndi odwala anzako.

  • @ManjeUphl
    @ManjeUphl Місяць тому

    Usi kama ulemu ndiwabwino osasokoneza Anthu zochita mpaseni kabambe chance inu munanena simukhala nawo

  • @stanphordsongeahwell
    @stanphordsongeahwell Місяць тому

    Kod uimila upule🤣🤣🤣

  • @JohnKanyenda-c9e
    @JohnKanyenda-c9e Місяць тому

    Usi my vote

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu Місяць тому +2

    Usi iweyo osokoneza isiye utm ukulimbana chani ndi utm

  • @MartinKapanga
    @MartinKapanga Місяць тому +1

    manganya ndikufuse Kuti ngati church mulibe ndale chakwela zinantheka bwanji kukhala president iyeyo sinali ndale popedza akuti ndi busa

  • @ChristopherTchale
    @ChristopherTchale Місяць тому +1

    Angotenga azimayi aganyu

    • @FlorryVugy-g4f
      @FlorryVugy-g4f Місяць тому

      Chipani cha akazi okhaokha kut mudziwe akuchita zaziiiiii😊😅😅😅

  • @MadalitsoIbrahim
    @MadalitsoIbrahim Місяць тому

    Kodi manganya ndi pule wachipani chanji?

  • @wisdom20mkango49
    @wisdom20mkango49 Місяць тому

    Uyu ndikatundu ana achepa

  • @felixjoseph8161
    @felixjoseph8161 Місяць тому

    Wadzibwana uyu akuona ngati angawakankhire anthu Ku MCP zoti angomudyera sakudziwa

  • @thomphalavi5027
    @thomphalavi5027 Місяць тому

    Movie iyi ikatuluka zaipeze mophweka

  • @MaxwellSakwata-wb8ep
    @MaxwellSakwata-wb8ep Місяць тому

    Tikufelanji live in politics

  • @mcrayansimwaka8890
    @mcrayansimwaka8890 Місяць тому

    Kodi a VP ndi msogoleri wa zimayi?

  • @NekhasonLarkim
    @NekhasonLarkim Місяць тому

    Tionana 2025 azasowa kopita ameneyo

  • @OmegaChingamuka
    @OmegaChingamuka Місяць тому

    Nfiti iyi tsiku likubwela

  • @MosesMbale
    @MosesMbale Місяць тому +1

    Koma mwati ku UTM ko simukhapanako koma😂😂😂😂 DPP my Vote
    Koma malemu saulos chilima sindiza wayiwala makamaka manganya azalongosola bwino 2025 akachoka mu boma

  • @chrischigoma5854
    @chrischigoma5854 Місяць тому

    Mukanangonena chipani chanu a UTM asiyeni then mudzipanga zanu, koma DK sanayime pachulu kukunyodzani plz asiyeni mwamtendele ngati akuswa malamulo

  • @YowelichipapaYowelichipapa
    @YowelichipapaYowelichipapa Місяць тому +1

    Iwe unali kuti mene azako amatenga ndalama zapamalilozo

  • @MzikaPhiri
    @MzikaPhiri Місяць тому

    Koma Zakeyu nde zimenezo nzomayankhula mwamatama choncho?

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu Місяць тому

    Usi garu iweyo usapusitse a 🇲🇼

  • @FlorryVugy-g4f
    @FlorryVugy-g4f Місяць тому

    😂😂😂 ndi wodya zake alibe mulandu 2025 azachita alliance ndi mcp koma smuzawina inu Ausi

  • @FrancisKalavina
    @FrancisKalavina Місяць тому

    Zopanda zeru kugawa ndlam moti apange Zzithu zitsike nde agawa ndlam kwa athu angat

  • @blessingsmimu5236
    @blessingsmimu5236 Місяць тому

    😂😂😂wodwala uyu

  • @StoneckJali-s3n
    @StoneckJali-s3n Місяць тому

    Komatu munthuyu kumupitikiisa Wina athyola naye bond

  • @harrytuliyani8957
    @harrytuliyani8957 Місяць тому

    Koma bwana usi mukungofanana ndi nzeru za mbuzi ukuganiza kuti anthu akamakavota akakuvotera iwe ulibe chipani?

  • @HestingsEdward
    @HestingsEdward Місяць тому

    Kodi apapa vp adayamba kumpatsa mpata olankhura akuvekatu Ausi koma ngapa chilima samamupatsa mpata oyankhula kapena malamulo adasintha atango mwalira

  • @IBRAHIMWILLIAM-o9d
    @IBRAHIMWILLIAM-o9d Місяць тому

    Nthawi nkachitsiru

  • @AimanTwalid-o6o
    @AimanTwalid-o6o Місяць тому

    Inu akuvinatu kunooo reagy ,koma inu mukuti sapweteka gulu uyuuuu

  • @EnockMvula
    @EnockMvula Місяць тому +1

    soka apa ukunama ndarama zapamariro unadya ndiweyo osati kabambe ineyo umboni ndiri nawo ukunama kabambe warowa sopano pa up nthawi ija unari iweyo munthu woyipa kwambiri murungu simunthu azakurangani siku ndirimozi tafa ndifeyo wathu wapita kharani wamuyaya

    • @MichaelpenielPhiri
      @MichaelpenielPhiri Місяць тому

      @@EnockMvula sananene kuti ndalama wadya ndikabambe muzimvesesa koma iyeyo amafunsa

  • @EliasBwanali
    @EliasBwanali Місяць тому

    Ulibe ntchito olo usapiteko angakudaule ndani

  • @GreyMwanyimbo
    @GreyMwanyimbo Місяць тому

    Dolo katatu

  • @yamikanijoseph9381
    @yamikanijoseph9381 Місяць тому +1

    Boma ndilomweli

  • @StellaMicheal-q1j
    @StellaMicheal-q1j Місяць тому

    Yomweyo usi boma

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick Місяць тому

    ausi,vp,zimene,mukupangazi,anzako,sangakwanitse,kuthandiza,anthu,ambili,,chomchi,,komaso,ena,akudananazo,

  • @EliasBwanali
    @EliasBwanali Місяць тому

    Mbuzi iyi palibe chomwe inganene chanzeru

  • @tamalangoma2765
    @tamalangoma2765 Місяць тому

    🤣🤣🤣🤣🤣

  • @HamiltonSinosi
    @HamiltonSinosi Місяць тому

    Wafupika ndi mzeru zomwe uyu

  • @dzingasubonajambo4390
    @dzingasubonajambo4390 Місяць тому

    Yudas

  • @PeterMagombo
    @PeterMagombo Місяць тому

    Mwapenga misala inu

  • @DymonMphito
    @DymonMphito Місяць тому

    Masewero anamusokoneza mutu uyu ukuongati ndalama nd

  • @MatthewKaliyati
    @MatthewKaliyati Місяць тому

    Manganya ulibe umunthu komaso manyazi, lapa nthawi idakalipo

  • @StellaMicheal-q1j
    @StellaMicheal-q1j Місяць тому

    Ulemu wanu bwana ivahemulo

  • @VincentMaluwa-o4i
    @VincentMaluwa-o4i Місяць тому +1

    Kkkkkkkkk speechless

  • @StevieChilinde
    @StevieChilinde Місяць тому

    Kodi AUSi Inu mulindivuto kwabasi Kodi ndalamazo anadya ndindani?Komanso iweyo Ukumakhala.ngati ndi wa UTM bwanji?Kodi iweyo ndi wa UTM? Tikumana nawe kukhoti.kodi iweyo wasanduka wa Dotima?

  • @AimanTwalid-o6o
    @AimanTwalid-o6o Місяць тому

    Utu apweteka gulu uyu kkkkkkkk ivahemuloo

  • @RodgersNthengwe
    @RodgersNthengwe Місяць тому

    Usi matongo ngat mphundu

  • @ELLENKANJERE
    @ELLENKANJERE Місяць тому

    Kampeni Kodi yayamba kale?m'm office akhalamo liti?

  • @StellaMicheal-q1j
    @StellaMicheal-q1j Місяць тому

    Muona malaulo