Akuti Awamangatu chifukwa amafuna kupha munthu mungakhulupilira zimenezo? 😳

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 23 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 111

  • @JeremiahFalakeza-c1m
    @JeremiahFalakeza-c1m 2 години тому +7

    A malawi tidzuke tipepherere dziko lanthu makamaka 11:pm and 02:pm popephera timupephe Mulungu Atipulumutse.

  • @IshmaelLosani-cs4cl
    @IshmaelLosani-cs4cl 32 хвилини тому +1

    Osamatengera malamulo mmanja dikirani chilungamo chioneke 👏

  • @AshimayeGama
    @AshimayeGama 55 хвилин тому +2

    Chilima analakwitsa yekha kuwinitsa mcp lelo akuvutitsa otsala

  • @HalimaShafie-q9k
    @HalimaShafie-q9k Годину тому +1

    Vuto apolice aku Malawi alowa mcp agalu okhaokha a mcp komaso chakwera mboloyao

  • @HarrisonTembenu
    @HarrisonTembenu 2 години тому +4

    Chiwembu cha abambo ake asikono Ichi. Maganyatu ndi owukira nd mfitiso

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 3 години тому +5

    Apapa Malawi yense timayenera kupanga mademo a emergency

  • @Willardmakande-p2q
    @Willardmakande-p2q Годину тому +1

    Amafuna kupha munthu koma opha SKC alikuti?

  • @JasonMailos
    @JasonMailos 46 хвилин тому

    Ndiusi ameneyo manganya Ngati anapeleka chilima akalephele kumupeleka kaliyati

  • @NicholasMackinnah
    @NicholasMackinnah 2 години тому +1

    Kodi mwayamba za one party system

  • @edwinnyasulu2088
    @edwinnyasulu2088 Годину тому

    Thanks for the update

  • @HevenChiwaya
    @HevenChiwaya 2 години тому +1

    MCP chifukwa chiyani ikumawatengela a Malawi kuntoso a kweni alakwanji koma

  • @BrandinaMphuka
    @BrandinaMphuka 2 години тому +1

    Mmmmmh mayi kaliyati sanamvekepo ndi mbiri imeneyo zalowa ndale iziiii

  • @angelmwethewa8010
    @angelmwethewa8010 2 години тому +1

    Kodi zafika poti apolice kulesa anthu kuti asatenge ma placards?mpaka ma placards kusungidwa kuseli kwampando?ok

  • @DavieKumbanga
    @DavieKumbanga Годину тому +1

    Mwaona inu ana amma 2000 zomwe munapanga? 1 million jobs ija ndiimenei

    • @HabrilMalaya
      @HabrilMalaya 28 хвилин тому +1

      Vuto ndife 😂😂😂😂

  • @BrianMamiwa-k8m
    @BrianMamiwa-k8m 2 години тому +1

    Eeee koma mcp a zoona ng'ona ndi ngona mcp sizasintha

  • @justinmalala-e4o
    @justinmalala-e4o 43 секунди тому

    Vuto la opposition yogona, kumangana sikungathe

  • @JudithKatungwe
    @JudithKatungwe 21 хвилина тому

    Bola muzimanga umboni ulipo,,osati misonkho yathu ipitenso apa

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc 58 хвилин тому

    Amalawi mizimu zukani,monga nzika ya chimalawi,yambaponi kutibula,mpolice aliyese ndi odelela kwambili.

  • @DysonChiumia
    @DysonChiumia 2 години тому +1

    Aah police yaku Malawi penapake💔

  • @mrcool531
    @mrcool531 36 хвилин тому

    Munthu wake ndani?

  • @RhodaPhiri-d6q
    @RhodaPhiri-d6q 4 хвилини тому

    Aliyense wandale ndioipa bas ndipo ife ndiomwe timapanga zopusa kumataya nthawi yathu

  • @PaulPhiri-c5u
    @PaulPhiri-c5u Годину тому

    Koma zoona zimenezi achakwera mbiri yanu isaonongeke chifukwa cha anthu anu oipa mtima chifukwa chipani cha mcp anthu akchita kunenakuti. Ndi chakhaza kwambiri pamene chafika aliyese akuopa kufikira pafupi

  • @InnocentEdasi
    @InnocentEdasi 42 хвилини тому

    Police yathu ikugwlisidwa ntchito ndiandale basi zitsiru zapolice

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 2 години тому

    Broh panopa ndpamene ndikumamva zoona.zake pitilizan kutiunikira koma after kulephera kumugwira wa Bakili Muluzi TV komas Ntanyiwa muone adzimanga aliyense apa angoyamba kumene

  • @AlexKamfosi
    @AlexKamfosi 51 хвилина тому

    Zosezo. Ndizaboza. Akufunakupasa. Poizoni. Mapulaniawo. Alichocho. Pakufunika. Kuchitapokathu. Akweni tialuzaso. Ngati chilima bomaili. Liphaathu

  • @BennettNjedza
    @BennettNjedza 2 години тому +1

    Apapa akuonjezera mkwiyo wa anthu

  • @PATRICKTHlMZY
    @PATRICKTHlMZY 26 хвилин тому

    Kmaso sizikufunika kupephela kma kupita kukagona kupolice

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu Годину тому

    Amafuna kuphaa muthu kutiko kapena zalowa kundale. Muthu wake ndani , palowa ndale apapa sizonamizana. Ayiwala kuti ndamene analowetsa boma

  • @EvasonThupilifana
    @EvasonThupilifana 11 хвилин тому

    Ine ndine wakumudzi ndimafuna boma limeneli litandimanga a police angazaone polekela sure

  • @Peter-w7h
    @Peter-w7h 43 хвилини тому

    Zopusa basi kwacha mumango ngwesa basi pangani zoyendesa ziko mmmm

  • @MarthaBalakasi
    @MarthaBalakasi 12 хвилин тому

    Boma ndilomweli tingositha president ndi apolice

  • @AndersonBishop-i2t
    @AndersonBishop-i2t Годину тому

    Chikalayayo ndi wawusilu walandila ndalama km kungoluza onsewo azakhala ma lova azawonas tizalemba ntchito ena nosenu a mcp mpakana ndi ma judge omweso ntchito yawo izawathla kmaso azamangidwa ndi awusilu mesa ndi Andale amene apolicewo

  • @JoaquimNasiyaya
    @JoaquimNasiyaya Годину тому

    Vuto apolice aku Malawi amakhala Ngati Siaku Malawi

  • @MikeMpapasaJeremia
    @MikeMpapasaJeremia 2 години тому

    Akufuna tibweleleso ku one party system. Akukanika bwanj kunena mulandu wenewen omwe amangila mmmmm

  • @SifatiMoses
    @SifatiMoses Годину тому +1

    Muli busy kumanga anthu malo moti mukhale busy kusaka njira yomwe mungapezere mafuta dziko. Mcp ndiyochitisa manyazi poganiza koma chalakwe amaganiza ngati mwanadi ndithu, zina umangoona waziyambadi.

    • @PidoMaganga
      @PidoMaganga Годину тому

      Ndye mwati chalakwe kkkkk

  • @ShukuraniTonex
    @ShukuraniTonex 3 години тому +1

    Akupanga zopusa kwambiri anthuwa

  • @PATRICKTHlMZY
    @PATRICKTHlMZY 28 хвилин тому

    Kmatu aboma akuyesa zida

  • @MussaAndreQuenessi
    @MussaAndreQuenessi 2 години тому

    Zachamba chikangawa chakwera garu 😮

  • @PaulPhiri-c5u
    @PaulPhiri-c5u Годину тому

    Koma mulungu akuchitileni chifundo pa nkhaza mkuchitila anthu zikutikhuza kwambiri zimene zikuchitika mziko mwathu muno ngat mtsogoleri kulibe zoona chitanipo kanthu achakwera

  • @EdsonGeorgeViagem
    @EdsonGeorgeViagem Годину тому

    Mbava zosowa pogwila

  • @BridgetKondowe-j4f
    @BridgetKondowe-j4f Годину тому

    Maro Moti azirimbana ndi dzikori kuti Kodi dzikori rikuyenda bwanji koma akurimbana nd chirima amene amumangayo ndi skc Muzimu wakhe uwuse mumutendere

  • @michaelkallyz2425
    @michaelkallyz2425 15 хвилин тому

    Malo mosaka Mafuta mwayamba kusaka Anthu😄

  • @SHAIBUSALIMU-l1o
    @SHAIBUSALIMU-l1o Годину тому

    Izitu zomwe zikuchitikazi ndi khaza kwa amayi chifukwa chani koma ziko mukuliwona ngati ndilanu

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 2 години тому

    A polisi musayiwale kuti mnzanu waphedwa ndi MCP yomweyo

  • @JeanBanda-zy6wu
    @JeanBanda-zy6wu 2 години тому +1

    Apha chilima ndi witika muwamanga liti?

  • @chemandotamwale
    @chemandotamwale 40 хвилин тому

    Sizachilendo m c p kupanga nkhanza

  • @ChimwemwePhiso
    @ChimwemwePhiso 2 години тому

    Manganya Manganya Manganya manganya

  • @johnlameck8366
    @johnlameck8366 Годину тому

    Munthu wake uti yemwe akuti amafuna kumumpha mmmm

  • @HafizahHarack-bn3bf
    @HafizahHarack-bn3bf 2 години тому

    Police yakumalawi is very useless amumanga bwanji muthu mulibe umboni wina uliwonnse, this is proper gander srious.

  • @FlynessWinga
    @FlynessWinga Годину тому

    Iiiii koma ndale

  • @BrianMamiwa-k8m
    @BrianMamiwa-k8m 2 години тому

    Apapa akanamangidwa wa mcp akanawalola kuti amuone m,balewao koma pot ndiosusa alibe ufulu

  • @GeorgeFrank-k1q
    @GeorgeFrank-k1q Годину тому

    mbuye menyeleni nkhondo,malawi okoma uja waonongeka,ivani kulira kwathu

  • @EthelKubalasa
    @EthelKubalasa Годину тому

    Kungowonjezela mkwiyo kwa aMalawi. Ma plan anu sayenda MCP

  • @wisdomchilanga723
    @wisdomchilanga723 Годину тому

    A police opusa awa

  • @McDonardMapala
    @McDonardMapala Годину тому

    Mukuwopa chan titulusilen munthuwanthu

  • @AshimayeGama
    @AshimayeGama 53 хвилини тому

    Yakuphandiyakupha mcp anapha chilima kasambala Mia

  • @FlorenceBanda-w5s
    @FlorenceBanda-w5s 57 хвилин тому

    Zarowa ndare izi

  • @Agness-ic9tl
    @Agness-ic9tl 46 хвилин тому

    Tumizani mafuta anthu akufa sanafike kuchipatala muwasaka anthu kuti atani

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 3 години тому +1

    Amalawi ufulu wathu tinaugulitsa povota nthawi ijayi mmmmm

    • @HabrilMalaya
      @HabrilMalaya 27 хвилин тому

      Tichilape😂😂😂😂😢

  • @paulpaseli6310
    @paulpaseli6310 2 години тому

    Amafuna kupha Muthu koma chakwela anapha mumugwila lit

  • @AbdulMalik-o7n1q
    @AbdulMalik-o7n1q Годину тому

    Manganya usi ndiwe mfiti ndi chingawayo

  • @JaphetSakala-u5j
    @JaphetSakala-u5j 2 години тому

    Magalimoto asilikali ose aja amapita uku

  • @SamukLungu
    @SamukLungu 2 години тому

    Apangisa zosezi ndi manganya ndi chikangawa

  • @DavidFyson
    @DavidFyson 2 години тому

    Zoopsa

  • @GamaChifundo
    @GamaChifundo 2 години тому

    Wathilila mchenga mpunga

  • @SelinaGamaliyere-q8v
    @SelinaGamaliyere-q8v 2 години тому

    Ma plan amanganya awa

  • @michaelkallyz2425
    @michaelkallyz2425 14 хвилин тому

    Boma ndilomwelii😁

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 2 години тому

    nkulu wina wake akuti quarter chani kaya sangapiteko muona

  • @FrancisChikazunga
    @FrancisChikazunga 2 години тому

    Umboni mulinawo

  • @JohnmarkNazombe-hi9xd
    @JohnmarkNazombe-hi9xd 2 години тому

    UTSI ALIKUTI?????

  • @patriciajangaza675
    @patriciajangaza675 2 години тому

    Zonsezi ndi manganya tikamati ngoyipa bamboyu mwaonatu

  • @SelinaGamaliyere-q8v
    @SelinaGamaliyere-q8v 2 години тому

    Chipani cha nkhanza osamakasaka mafuta bwanji

  • @DanielJuwawo-s5n
    @DanielJuwawo-s5n 2 години тому

    Apolice akumalaw ndiofoira kwambiri

  • @JuliusMtalika
    @JuliusMtalika 2 години тому

    Iiiiii koma boma ili ayi ndithu

  • @LeonardJere-r5y
    @LeonardJere-r5y Годину тому

    Kod moyo umeneu nduyekut ufulu wathetsad chikangawayu

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx 3 години тому

    Manyazi akuwagwira apolice akuwaletselanji ma poster a, ikasaka mafuta kumene

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera  3 години тому

      Eti amwene mafuta Akusowa akusaka anthu

  • @HarrySteven-d6e
    @HarrySteven-d6e 59 хвилин тому

    Yesaya 54v17

  • @CorneliusSande
    @CorneliusSande 30 хвилин тому

    Mumtima ndi muthumba salowana

  • @PeterJere-ot5mg
    @PeterJere-ot5mg 2 години тому

    amafuna kupha ndani?

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 2 години тому

    Malo mokasisa mafuta aja amati alingambwi ngambwi aja koma satana alipantchti

  • @KentWilliam-r2v
    @KentWilliam-r2v 2 години тому

    Mcp ndye chipani choyipa ichi

  • @NelsonKasanga-b6q
    @NelsonKasanga-b6q 2 години тому

    Tiyeni mahdemo

  • @MaxwellKapalamula
    @MaxwellKapalamula 2 години тому

    Mcp chidure avomere kulephera

  • @MaxwellKapalamula
    @MaxwellKapalamula 2 години тому

    Malo mokasa mafuta, mukumanga anthu

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx 3 години тому

    Munthu amafuna kupha yo Ali kutiko poyamba anena kuti chakwera tsopano tiva zoti tsopano

  • @WhyteSmart
    @WhyteSmart 2 години тому

    A police omvetsa chisoni kwambili

  • @Sofi-p1v
    @Sofi-p1v 2 години тому

    Komatu bambo a sikono longosokani

  • @ChirwaSanama
    @ChirwaSanama 2 години тому

    Zovesachison mcp mbuzzi

  • @GiftKananji
    @GiftKananji 3 години тому

    Aaaa koma police yaku malawi

  • @ChimwemweNthenda
    @ChimwemweNthenda 2 години тому

    Koma mcp amuziwe yesu

  • @EmilyKanyika
    @EmilyKanyika 3 години тому

    Iiiiiiiiiiii koma machimo

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 2 години тому

    amafuna kupha munthu kuti

  • @YamieManda
    @YamieManda 2 години тому

    Kodi peter sanamange jese ndi sungama mwazionalero agwepe inu

    • @MzadziWanga
      @MzadziWanga 30 хвилин тому

      Takasambeni uko uli mbuu apa ngt unagona paphulusa mwana wa njoka iwe