Big up to you Mbenjere, phunzitsani uwuzeni mtundu wa aMalawi adziwe kuti chiphaso chawo sichofunika kumupatsa munthu wina iyayi. May God bless you Mbenjere.
@@LindyRich whats ur benefit on this nosense? Basi ka Bando akugulilani andale kuti musokose pa social media? Ife ndi magraduate a xool osati aphuzo ngati inu 🤣🤣 ulenje umasimba wako🤣🤣
Well spoken DC a malawi tonse tikudziwa kuti dzifwambazo ndi dza mcp sangakanenso ai nkhani yake ya bishop msusa nde aganiza kuti alimbane ndi a katolika. Aaah uku nde kutha kwa mcp mufune musafune nonse a mcp muli pa mabvuto nkhondo idzidzi mwayambazi ndimmene muthele. A zathu a katolika musadalire chitetezo cha boma ili chifukwa a police a boma ili ndi a mcp pakufunika private security.
Akuti ndikavote pa 20 pano. Meaning Nyimbo iyi Mbenjere anaimba dzaka zambuyozo. Chorus ndiya Mbenjere koma wina walowa ma verse`wo ndi kuika zomwe zachitika chaka chino cha 2024.
Big up to you Mbenjere, phunzitsani uwuzeni mtundu wa aMalawi adziwe kuti chiphaso chawo sichofunika kumupatsa munthu wina iyayi. May God bless you Mbenjere.
Wazindikila chilungamo ndiyemweyo 😂
Yes his voice is there ya mbenjere even the beats are his
Nyimba ya kale kale 😊
This song has been there for over 5 years
Sounds like retouch
Yakale munalibe yandege
Ameneyu ndiye timati Legend Mbenjere💪 Not anyapapi omwe akumakayimba ku MCP music Show!
good composition Mbenjere amatha
Mbenjele kubaya pa liwombo 😂
Nice song mbenjele tufuna izizi iyi ndiye sound yanzelu
Nyimbo ya2017
Yaaaah bro ndimbenjere ameneyo I know this guy he has also another style of singing
Inu Nd nyimbo yake imenei Nd nyimbo ya 2013- 14 time ya Joyce Banda
@@PhillimonMwale ndiye 2013 kunali lipoti la ndege?
Yes mbenjere has three styles of singing
@@BazaarShaibukomadi nthawi yimene ija kudalibe za report ya ndege 😂😂😂
@@MichaelJohnMbewe-sk7jd akutinamiza awa
anthutu chilungamo akuchidziwa mutha kuona & mbenjele ndi ozindikila😂😂
Kkkkk wazindikila cuz Ali kuchikangawa party? Ndipo Kodi akat kuzindikira nchani ngat sikuchikuta zinthu mwanzeru munthawi yoyenera? So ngat nkuzindikira KO kwagona pati pot posatengera ndale or chipan chosatira koma kuima pachilungamo zinthu sizili bwino pankhan ya umoyo kamba Ka usogoleri ulipo omwe anthu Ake akukhala ngati agontha komaso khungu moti sakuoan ndikunva mmene anthu Ake akuvutukira then kod Munthu ozindikira panthawi iyiyi yomwe anthu akuvutika ndipo akusowa anthu omwe angathe kuwayankhulira zammene uli Moyo angasapote zomwe zikuzunzitsa anthuzo?
Ndi inu mbuluchabe. Nyimbo ya nthawi yabongi... Ma vote a20 Mya adalichakachanj
@@paulgchabvunyaInu ndiinu achitsiru zedi, so apanga upload wa ndiosadziwa odziwa ndiinuyo. Mbuzi Garu tombololombo iwe ndithu mwana wahule obadwira mistake condom ataphulika
@@LindyRich whats ur benefit on this nosense? Basi ka Bando akugulilani andale kuti musokose pa social media? Ife ndi magraduate a xool osati aphuzo ngati inu 🤣🤣 ulenje umasimba wako🤣🤣
@@paulgchabvunya tiphuzitseni bwana mwinadi ndife mbule pa zosezi
Nyimbo waswa iyi eeeeh, mpaka Mr Chi........ atayimva Mmmmh
Yaphedukadi for real, big up!!!love it
Mbenjere,uziyenda mosamala akuyika musaka anthu akwiya nawe awa🤣😂🤣
Zoona Chakwera you must go, watikwana
Mbenjere ho yeeereeee😂 . Ndipo tonse tavomereza kuti ndiyemweyo Mbenjere basi
Anthu alowetsapo zawo apa mbenjere maimbidwe ake timawadziwa kkkkkkk izizi ndingati zomwe zinawachitikira mablacks kungowanamizira😂😂😂😂
Kaya ndi mberedi kaya siiyo koma wanena chilungamo.❤❤.wayitulukira
Kkkkk mbenjele umakwhana
Munthu wa Nkulu kwambiri Mbenjere
Pure mbenjere .
Nice song .
😂😂😂😂 ameneyo nde mbenjele timamuziwayo
Chorus ndi beat ndi mbenjere koma zinaz ndi wina 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
❤❤❤ Komatu wakwapula beat iyi
😂😂😂😂😂😂😂😂
Nyimbo ya kale kale ngati iyi
Ndiyake mbenjere koma ndiyakarekare
😂😂😂😂😂 kulitu ntchito yayikulu kunoku guys😂😂😂😂
Ndiyemweyo mbenjele waing'alula
this is Mbejere ........Big up
Adaimba nthawi ija joice banda sdagulitsa ndege ija
Mwaitha gayz
AMENE ALINAYO AYIPONYEMAGULUPUMU ITIPEZA
Ndiyemweyu mbenjere no matter how now you the truth more fire ❤❤❤❤❤
Mbenjele katundu wa amalawi uyu 😂😂😂
Mbenjere motoo kuti booo koma guys mbenjere wagogoda sindikukhulupirira 😂😂😂😂😂❤❤❤❤
😂Wathila mchenga mumpunga😂😂😂😂
Wathilamo bwino😂
Well spoken DC a malawi tonse tikudziwa kuti dzifwambazo ndi dza mcp sangakanenso ai nkhani yake ya bishop msusa nde aganiza kuti alimbane ndi a katolika. Aaah uku nde kutha kwa mcp mufune musafune nonse a mcp muli pa mabvuto nkhondo idzidzi mwayambazi ndimmene muthele. A zathu a katolika musadalire chitetezo cha boma ili chifukwa a police a boma ili ndi a mcp pakufunika private security.
Kaya ayimba zandale Kaya Chani ine I just like any song imene yayimbidwa mwambenjere beat
Undihale Ku inbox ndikuponyere kangachepe, nice song.
More 🔥 🔥🔥🔥🔥
Ya full bwanji 😂😂😂😂 ndiyemweyu uyuu
😂😂😂 Nyimbo nd iz zot ukamamvera uku ukunyekhula
Kkkkk
Nyimbo yiyi adayimba kale kwambiri thawi yomwe Joyce atagulitsa ndenge ya Malawi zango ndisangalatsa kuti zafanano ndi zofuna yena 😂😂😂😂
Ku galula basi
😂😂😂😂 ndiyemweyo....
He's the one 😂😂😂, galu wake yomwe wayamba kukuluma
Zikatelo imakhala minyama kwabasi
Koma ndiye mumangaza bro.big up good job
Zoona chilingamo mukuchidziwa. Dzopatdidwa dzisiyana ndi zako
Mmmmmmmm amwe uyu ndiwina amubela mental
😂😂😂😂Kaya ndi iyeyo kaya si iyeyo nyimbo yi ilibwino😂😂😂
😂😂😅kkkkk
Ndi mbenjere ameneyo 😂😂😂😂😂😂
Eeeee koma anthu amakhala ndi mfundo 🙌🙌 na iyi waikazinga timvere basi
😂😂Ndamumva ndiyemweyo
Mbenjere ulemu wanu big brother be strong 💪 🙏 that is true 👍 🙏 👏 🙌 😄 😆
This is real mbenjere and real sound
Tikumva kuti wamangidwaso anyway Mchinji simagawa kamba😂😂😂
Yomweyo mbenjele 😂😂😂
Mbenjere yemweyo😂😂😂😂😂😂
Azibambo Mr mchinji mbenjere
Ndiya chinkangawa yoo😂😂😂😂
Km boma ndilomweri stikusintha m'paka 2030 wooooo
Yemwe akufuna kusintha
boma angosintha mkanzi oro mwamuna pamenepo ndiyekuti zimunthekera
😂😂😂😂😂😂
Imbwaiwe
Mbuzi 😂ndi mbuzi olokuyingenda pompo imaona ngati dzuro
ine ndikusitha ndi vote yanga
Wakhuta chan
Ekha ekhatu angompasa ka data 😂😂 ati anene kuti boma ndilomweli😂😂😂😂
Zoonad ndi mbenjele 😂😂😂😂
Aaaa nyimbo ya 2019 iyi kkkkkk inu mwayivela kumene aaaaa zazi
2019 kunagwa ndege?
2019 kunagwa ndege?
Waing'alula mbenjele😂😂😂
Mbenjele uyu wabandulatu ✔️
Beautiful Mbenjere
Wawonatu mbenjele😅😅😅😅😅😅😅😅😅
😂ndiyakale 2019
2019 kunagwaso Ndege kod? kapena sinave bwino ndine nyimboyi
Kayatu😂😂@@djnyau7468
Nyimboiyi amaimba kalekale thawi pp
Akuti ndikavote pa 20 pano. Meaning Nyimbo iyi Mbenjere anaimba dzaka zambuyozo. Chorus ndiya Mbenjere koma wina walowa ma verse`wo ndi kuika zomwe zachitika chaka chino cha 2024.
Iwe wabodza nyimbo yaimbidwa Pompano usaname
Uzinva nyimboyo message yake, Kodi mesa zotenga ziphatso Kuti abere mavoti zikuchita pompanopa kumawanamiza anthu Kuti awapatsa chimanga apititse ma ID. Open your eyes big Amalawi ndiochenjera MCP Siingatipusitse
😂😂😂😂lpatse moto ❤❤
Koma nyimbo imeneyo anaimba 2019 ndiyakare kwambili ine ndilinayo kare .anayimba ndimbenjere ndithu koma siyapano ayi
Iwe wabodza kwambiri kalero kunaliso nkhani yokhudza ndege??
😂😂😂😂😂😂😂😂😂 akutukwanitsadi mbenjere
Kkkkk ndiyemweyo😊
Mbenjere ndavera kwambiri ine this is 100% mbenjere. Koma wabwela ndi moto hevy
Ndiyemweyo mbenjere kkkk koma ndiye wabayatu
😂😂😂😂😂❤❤❤ mbenjere
💪💪💪
I like mbenjere they song sound malawi ❤
Nyimbo iyi anaimba ndi mbenjere mu 2020 nthawi yamavoti,ndiyakalekale amknena dpp
Nyimbo iyi ndi yakale kwambiri I have a strong connection with him ndipo nothing can pass my eyesight concerning him musically
Inu ndi mbenjere uyu weni weni
@@ShamilahSaizi 🤣🤣🤣😂😂
Ndiyemweyo
@@GoldenNamanguya-q9u 🤣🤣 afananaditu komaso Bit yo ndiya Mbenjere
We need some more teachings!!
😂😂😂😂 zikolapasi 😢
Kkkkkk nice song
Kkkkkkkkk koma ayi mcp mwanyanayo basi sinchewa ameneyi ayi zikomo
Ombenjele ndinu ozindikila muli boh🎉
Big up mbenjere
Ndikalekale nyimbo iyi kkkkkkk , inu mwaivera kumene.
Big man Mbenjele nyamata wama suit otchena
ndyemweyo , cyakareso cmukuva akukamba zandege
Nyimboyo angoipanga Remix ndiyakale kale
MCP my vote
Ine mbenjele ndimakhala naye kuno uyuyu simbenjela koma amene wayimba nyimboyi wangotengako ma part ena ambenjele anyimbo zakale
Ai simbenjere
Ndiyomweyo mbenjere
We are creating the Kamangilas more and more ❤
Is it real mbenjele the voice😊
Mbenjele more fire
Nyimbo yakale kale iyi iwe cadet😢😢
Kathu kumangocji timati nijujojo kkkkkkkk