Malawian Cameras
Malawian Cameras
  • 353
  • 4 630 728

Відео

Pepanitu Lero tili kunkhondo that's why pamudzi pano pali ziii
Переглядів 1,1 тис.17 годин тому
Pepanitu Lero tili kunkhondo that's why pamudzi pano pali ziii
A Moses Kunkuyu BFU sibungwe lodalilika kufufuza zandege funani kampani ina ifufuze za Ngozi ija.
Переглядів 2,2 тис.2 години тому
LYTON MANGOCHI AKUTI KAMPANI YOMWE IMAFUFUZA ZA NDEGE IJA SUNGAIKHULUPILIRE moti iwo anaiyang'ana pa Google ili ndi milandu yosokoneza report la ndege mpaka anailipilitsako chindapusa nde iwo ati A Moses Kunkuyu afune kampani ina yolongosola zimenezi osati BFU
ma Investors akwiya ndi Katangale wa anthu a M'boma moti anapakira kumapita Mwai ndi Manganya
Переглядів 3,2 тис.2 години тому
Corruption is a Cancer Slowly Killing Malawi - Vice President The tendency to demand bribes from investors is a cancer that is slowly killing Malawi, Vice President Dr Michael Bizwick Usi has said. Dr. Usi was speaking at Mudi House in Blantyre after hosting two German investors operating under Landt Foundation. The two investors complained to the veep that some government officials have been d...
Amalawi Maganizo anu akutinji pa nkhani ya Secondary school Yaulele Mdziko muno???
Переглядів 1,2 тис.2 години тому
Member of Parliament for Rumphi East, Kamlepo Kalua has asked Government through the Ministry of Education to implement free education in secondary schools. He says a lot of people are failing to pay school fees due to economic hardships and the only way to help them is by implementing free education to secondary schools. According to Kalua, Malawi should implement free education to secondary s...
Nonse Amene Muli Jonz tili nanu M'ma pemphero Inuyo mwathandizira mu economy ya Malawi.
Переглядів 3,5 тис.4 години тому
Chairperson of the Portfolio Committee on Home Affairs, Advocate Bongani Bongo, has welcomed the arrest of illegal immigrants during a multi-organisation raid in inner Johannesburg’s central business district (CBD). “It must remain clear that while legal and developmental immigration is encouraged and can be beneficial to the growth prospects of the country, we remain steadfast that illegal imm...
Nkhani ya Ndege yavuta Atolankhani akwafusa a CDEDI mafusono lero
Переглядів 8 тис.7 годин тому
The Center for Democracy and Economic Development Initiatives (CDEDI) has called on President Lazarus Chakwera to institute a commission of inquiry into the plane crash that killed former Vice President Saulos Klaus Chilima and eight others. This follows an interim report released by German experts last week. Addressing the media in Lilongwe on Wednesday, CDEDI Executive Director Sylvester Nami...
kodi Dr Lazarus Chakwera anatinamiza ndi Iwowo kapena iwo ananamizidwa mkutinamizaso?
Переглядів 2,8 тис.7 годин тому
Bungwe la Centre for Democracy and Economic Development Initiatives (CDEDI) lati mtsogoleri wa dziko lino Dr. Lazarus Chakwera akuyenera kubwera poyera ndi kuyankhulapo pa zomwe ananena itachitika kumene ngozi ya ndege yomwe inapha wachiwiri wakale kwa mtsogoleri wa dziko lino Dr. Saulos Chilima. Mkulu wa bungweli Sylvester Namiwa wayankhula izi pa msonkhano wa atolankhani ku Lilongwe. Namiwa w...
Ineyo ngati Ndinalowa MCP Inuyo mkulekeranji? Uladi Musa
Переглядів 1 тис.7 годин тому
Ineyo ngati Ndinalowa MCP Inuyo mkulekeranji? Uladi Musa
Kubera Zisankho kuvutatu Dpp Ikusewera Game Yapansi😂😂😂
Переглядів 11 тис.9 годин тому
Apart from Dr Mathanga and Chipungu, Professor Arthur Peter Mutharika has also included Dr George Chaponda, Dr Clement Mwale, Charles Mhango and Everton Chimulirenji as his aides among others Senior former Commissioner at MEC Hon Jean Mathanga has been appointed as Presidential Adviser on Elections
Tiyankhuleni a Chakwera Fetereza wakwera
Переглядів 3 тис.9 годин тому
Tiyankhuleni a Chakwera Fetereza wakwera
Gotan Hara wauza anthu ku Church kuti Tisasinthe Mtsogoleri msonkhano wu sunathe ena anayamba kulira
Переглядів 7 тис.9 годин тому
Gotan Hara the deputy President has urged people at CCAP Livingstonia Synod Church in Mzuzu not to remove the President from his position rather help him to rule and govern this Country
Moses Kunkuyu kuwerenga Report la Ndege Mchichewa
Переглядів 1,1 тис.12 годин тому
Minister assures access to interim plane crash report Lilongwe, August 31, Mana: Minister of Information and Digitilization, Moses Kunkuyu, has assured that every Malawian will have access to the interim report released by the German Federal Bureau of Aircraft Investigation (BFI). Kunkuyu made the remarks during a Press Conference on Saturday, held at Central Office of Information (COI) in Lilo...
Fredokiss Walusa Uku Akuti Apolice Shame On You?!!!!! 😳😳😳😳😳😳
Переглядів 6 тис.12 годин тому
To every police officer who arrested and mistreated Hon Kamlepo Kalua over fake allegations SHAME ON YOU! To the police officers who smashed my mothers car SHAME ON YOU! To every police officer who arrested The Rev from Mzuzu who was saying correct things in his Vn SHAME ON YOU! Go give Hon KK his phone back plz! To all of you who celebrated the arrest of anthu osalakwa just because you hated C...
Uyuyu adzathera m'manja mwa aanthu mbambadi apa
Переглядів 3,5 тис.14 годин тому
Uyuyu amayankhula motumbwa
Report La Ndege ati ili ndiloyamba latsala lomaliza koma tidikre chaka Chamawa
Переглядів 3,7 тис.14 годин тому
Report La Ndege ati ili ndiloyamba latsala lomaliza koma tidikre chaka Chamawa
Report La Ndege longoyembekezera latuluka
Переглядів 4,4 тис.16 годин тому
Report La Ndege longoyembekezera latuluka
Kwacha Yagwa koma mwasiya kutiuza Chonde Muzitiuza tikuoneka ozelezeka, Wina wadandaula.
Переглядів 4,1 тис.16 годин тому
Kwacha Yagwa koma mwasiya kutiuza Chonde Muzitiuza tikuoneka ozelezeka, Wina wadandaula.
Deputy Speaker wakalipa! Muziyankhula chizungu tioneseni kuti Mumatha chizungu
Переглядів 6 тис.16 годин тому
Deputy Speaker wakalipa! Muziyankhula chizungu tioneseni kuti Mumatha chizungu
kodi Report la Ndege lo mufuna kuchita edit?atero a Gorge Chaponda
Переглядів 1,1 тис.16 годин тому
kodi Report la Ndege lo mufuna kuchita edit?atero a Gorge Chaponda
DRC yatipatsa mafuta posinthitsana ndi asilikali anthu koma mafutato boma lagulitsa 😳😳😳
Переглядів 8 тис.16 годин тому
DRC yatipatsa mafuta posinthitsana ndi asilikali anthu koma mafutato boma lagulitsa 😳😳😳
Kandinvelere kulimbana ndi Hot Current ai Zikomo kuli zinthutu
Переглядів 4,8 тис.19 годин тому
Kandinvelere kulimbana ndi Hot Current ai Zikomo kuli zinthutu
Sameer Suleiman Wauza A president Kuti Akhansule ulendo waku China kuononga ndalama
Переглядів 10 тис.19 годин тому
Sameer Suleiman Wauza A president Kuti Akhansule ulendo waku China kuononga ndalama
Zakufika kwa Report la Ndege kuboma zimenezo tafufuza koma sitinganene source yake (DW)
Переглядів 11 тис.21 годину тому
Zakufika kwa Report la Ndege kuboma zimenezo tafufuza koma sitinganene source yake (DW)
A Mcp Chilima munkamunyoza lero bwanji mwaveka anthu zovala za UTM kuti zinveke bwanji? Born Kalindo
Переглядів 2,5 тис.21 годину тому
A Mcp Chilima munkamunyoza lero bwanji mwaveka anthu zovala za UTM kuti zinveke bwanji? Born Kalindo
Ichichi Amwene Eeeeee chinabadwa kuzakonza dziko
Переглядів 6 тис.21 годину тому
Ichichi Amwene Eeeeee chinabadwa kuzakonza dziko
Report La Ndege Atsutsana A president akut latuluka nduna zikuti silinatuluke kwavuta
Переглядів 6 тис.21 годину тому
Report La Ndege Atsutsana A president akut latuluka nduna zikuti silinatuluke kwavuta
Kungomung'alula President wa Dziko La malawi Sameer Suleiman Mp
Переглядів 7 тис.День тому
Kungomung'alula President wa Dziko La malawi Sameer Suleiman Mp
Pakufunika 20 Billion tikawahonge azungu kuti atiyendere ku Malawi kuno
Переглядів 4,4 тис.День тому
Pakufunika 20 Billion tikawahonge azungu kuti atiyendere ku Malawi kuno
Lyton Mangochi Wafananiza ulamuliro wa Dr Chakwera ndi Ibrahim Traore???
Переглядів 5 тис.День тому
Lyton Mangochi Wafananiza ulamuliro wa Dr Chakwera ndi Ibrahim Traore???

КОМЕНТАРІ

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 12 хвилин тому

    Kkkk aaa bodza ngati anamangdi koma nkhani tsiyonyodza boma la malawi ayi ku south Africa nawo ali ndimamvuto awo kuti atsiye adzilimbana ndi nkhani zaku malawi aaa bodza uyu mutayeni akuchedwetsani

  • @clementchatepa
    @clementchatepa 24 хвилини тому

    Njovu zikumane

  • @ChristopherKabanga
    @ChristopherKabanga 40 хвилин тому

    zilibe ntchito zimenezo coz kwawo adachita ajeni ansa amachita kuonekeratu kut ndi wa dpp galu uyo

  • @user-fb7ki3hc7y
    @user-fb7ki3hc7y Годину тому

    Kodi mulikuti brother 😂😂😂

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera 59 хвилин тому

      @@user-fb7ki3hc7y Malire a Lebanon ndi Israel 🇮🇱😂🤣🤣🤣

  • @ShanaChitunga
    @ShanaChitunga 2 години тому

    My vote is special for him, let's support

  • @JOHNOlesmasCosmas
    @JOHNOlesmasCosmas 2 години тому

    Aise ndikutuluka zomwe wayambazi usamatinamize kut tingoononga bundle apa

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 2 години тому

    MANYI YAMAKO GUTANI HALLA ULIDZIWA DZIKO USAYEREKEZE KUWONETSERA KUTI NDIWE WA MCP ZIKUVUTA KWAMBILI SIKUTI PALI CHIMENE TIKUWOPA KWA CHAKWERA AI AWONA AYAMBE KUYENDA DZIKO MUNO CHAKWERA KUPANGA KAMPENI NDIPAMENE UDZIWE KUTI KODI NDI MALAWI YEMWE UJA

  • @madalitsomisomalih5411
    @madalitsomisomalih5411 2 години тому

    Munali ndimatha mumaopaso 😂mesa mumati agogo anu anakusiilani zinthu zoopsa ,bwanji simunalote?

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 2 години тому

    KWANOSE AMENE MUKUNKHUDZIDWA KAPENA KUTI MULI PANDANDA WAKUPHA CHILIMA OLO MUTASITHA CHIPANI KULOWA CHINA IFE AMALAWIAN TIDZATSANA NANU KUCHIPANIKO KUTHANA NAWE UDZIVERE MTOLO CHIPANI CHINA CHILICHOSE UNGALOWECHO TIDZAFUNAKO IWEYO BANSE MUTHA APO NDIYE TISABAMIZANE MUNATILAKWIRA KWAMBILI MUNTHU KUKUPATSANI MPATA KOMASO KUMUPHA MUNAPALAMULA KWAMBILI INU AKUNKUYU NDI ANTHU ANUWO ENANU MUFA KUYIPA

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 2 години тому

    Amangidwe amene analoreza ndenge kuti inyamuke ndipo amen adachosa black box amangidwe, ndipo adasunga battery ndindani? Amkasunga kapena kuchotsa ndicholinga chanji? Angati amafuna kukangura adachosa liti? Chakwera as a state president amkakwera ili choncho ndipo black box ibwere ifotokoza tsiku idasiya kugwira ntchito,

  • @louismagongwa
    @louismagongwa 2 години тому

    nde mu cell amalowa ndi phone ndiwe zoba ase😂😂😂😂😂

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera 2 години тому

      @@louismagongwa adhawa amachulutsa bodza😂😂😂

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 3 години тому

    NDIWE NDANI GUTANI HALLA UNGAMAWYZE ANTHU ZAWUTSILU ZAKOZO NDI CHAKWERA WAKOYO MATAKO YAKO

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 3 години тому

    PAKUFUNIKILA KWAMBILI ONSE AMENE ANATENGA GAWO MONGA GUTANI HALA NDIGULU LAKE KUWACHITA CHIPONGWE CHIFUKWA MAI SAKUDZIWA CHOMWE AKUYANKHULA AI IFE SIFE ANA AGUTANI HALLA KAPENA ANA CHAKWERA AI MUWONA ONE BY ONE TIBWEZA ZIPONGWE ZOMWE NACHITA CHILIMA MIMBA ZANU

  • @YaqoobStandwell
    @YaqoobStandwell 3 години тому

    Akuziwa kut palibe zawo nkona akuyeselabe kumuchrmelela chakwela palibe

  • @user-vw2jc2qw2e
    @user-vw2jc2qw2e 3 години тому

    Zaziiii

  • @S-rr1eu
    @S-rr1eu 3 години тому

    Mayi iwe!,,, zakoma ndarama zakuba?

  • @user-zl1xz9kt5s
    @user-zl1xz9kt5s 3 години тому

    Aaaaaa kutiona kupusa chani, muselo mpaka akulola foni kumajambula aàaà

  • @francismphande7181
    @francismphande7181 4 години тому

    Malawi Parliament house is not for azungu. Here shows speaker ndi mbuli,sadziwa tanthauzo la Nyumba ya Malamulo. You are there to bring development to the people who elected you,not show off ya English. Maiko ena amayankhula their local languages and chituko dziko likunka chitsogolo. English si kanthu amwene!!!!

  • @GeoffreyMaulana-rh5rx
    @GeoffreyMaulana-rh5rx 4 години тому

    Kutuluka big imakhalanthawi basi

  • @KestherMkandawire
    @KestherMkandawire 5 годин тому

    Wakhaula waziona

  • @user-hp4rl8cv3h
    @user-hp4rl8cv3h 5 годин тому

    Keep it up

  • @user-jk8sh7fh2d
    @user-jk8sh7fh2d 5 годин тому

    Thrend tv ukunamatu iwe sindimapangaso like ukumachuluka boza

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg 5 годин тому

    😂😂😂😂😂❤❤❤❤❤❤ umatha ase kulibe kunjonja mcp mafada bas

  • @MaikNkhoma
    @MaikNkhoma 6 годин тому

    Machende ako galu iwe

  • @robsontyg3928
    @robsontyg3928 8 годин тому

    Magobo pa John's

  • @ClaudinaAugustoAugusto
    @ClaudinaAugustoAugusto 8 годин тому

    Kkkkkkkk mu Celo amalolasi telfon 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣

  • @yotamumahomed1313
    @yotamumahomed1313 9 годин тому

    Chilima anafa chifukwa chamakani ake coz amadziwona ngat amaganiza kwambiri

  • @JuniorHala-vf9ov
    @JuniorHala-vf9ov 10 годин тому

    Tizimbuzi taku bala osati ku selo mwaona bwanji mapetedwe akewo ku selo amakhala ndi 4ni kkkk

  • @brainsmkumbwa6267
    @brainsmkumbwa6267 11 годин тому

    Uyu ndakayika kuti akunenazo ndizowona,ngati amangidwa ku South Africa wangomangidwa pa zifukwa zina,kumbukilani amalawi kuti Prophet Bushiri anali ndi milandu yambiri ku South Africa,milandu yili mukati mozengedwa iye anapezeka kuti wathawa ali kumalawi,boma lakuno ku South Africa linayetsesa kupanga chilichose kuti atumizidwenso ku South Africa koma sizinaphule kanthu,choncho boma la South Africa ndilokwiya kwambiri moti munthu utapalamula mulandu woopsa bwanji ndikuthawira ku South Africa boma la malawi silingakupeze ndipo boma la South Africa silingalore kupeleka munthu wosakidwa kuno ku South Africa ndi boma la Malawi chifukwa choti iwowo anakaniza Bushiri

  • @EVANCEKAGONEGONE
    @EVANCEKAGONEGONE 12 годин тому

    Muselo samalolq kukhala ndo 4n

  • @josephchisale4143
    @josephchisale4143 12 годин тому

    Ndiwe msilikali

  • @usumanidaudi
    @usumanidaudi 12 годин тому

    Uyu ndi muyawo akangomupha ife ayawo takozeka ifa ya chiwaya imatipweteka ka

  • @hissimajohn965
    @hissimajohn965 13 годин тому

    Za ziii

  • @Cubotenterprise
    @Cubotenterprise 13 годин тому

    Mtulutsen

  • @DeviBanba
    @DeviBanba 13 годин тому

    🤝👍

  • @user-wj6oc8yt4v
    @user-wj6oc8yt4v 13 годин тому

    Koma agotani akuthatha uza kuti achilima anali onyowa koma ,😥😥😥 nde Tika para kusinda musogoreli koma aku ononga zikoratu

  • @MirriamKambale
    @MirriamKambale 13 годин тому

    Kumalawi tilibe mtsogoleri panopa mtsogoleri anali uja anapheradalayi alipowa ndiokupha kuba ndikuononga kuteleko awa ndiokwanilitsa malemba malomokhala achakwera pachuma chadziko ndiachagwa,sangathe kuyendetsa dziko awa mmanja mwawo mulimagazi

  • @Gwedeza-oz3jv
    @Gwedeza-oz3jv 13 годин тому

    Ndizowona ndithu mr jox