COMRADE SALLO KUSWA MITU OPPOSITION - OPPOSITION YAKU MALAWI *NDIYA CHIFUFU*

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 23 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 71

  • @FrankHenry-pu4dc
    @FrankHenry-pu4dc 5 годин тому +3

    kkkkk npakana Ndwiiiiii, Wotsutsa boma azazivotela wokha asandipwetekese Mutu Ngati akawina amandilipilila mwana wanga Sukulu fees ngati iyaaaa

  • @SABITIKAISI
    @SABITIKAISI 2 години тому +1

    Ophusa nda malawi si asiphani anafuna khuwona Sina ❤❤❤

  • @IbrahimMatola-h4i
    @IbrahimMatola-h4i 2 години тому +1

    Inuso bwelan tithandizane

  • @TottiesJackie
    @TottiesJackie 5 годин тому +3

    Broh sallo osatha zakamwa nkhondo si yosutsa boma nkhondo ndiyatonse ife amalawi

  • @KimDexonAdamson
    @KimDexonAdamson Годину тому

    Chilungamo chinayandikana ndi chipongwe ,TIYENI MAN🤸🤸

  • @amidujohn6566
    @amidujohn6566 5 годин тому +4

    Bwerani braz sallo mutitsogolere mademo

  • @VictoriaBakuli
    @VictoriaBakuli 6 годин тому +4

    Zikundipweteka ngati amanga mai anga

  • @jixonromeo4111
    @jixonromeo4111 3 години тому

    That’s true my brother

  • @lacksonsiyadi943
    @lacksonsiyadi943 5 годин тому +1

    Zonadi bro. Sallo tulodi tanyanya ku opposition

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 5 годин тому +1

    Zofunikatu tonse tipangre limodzi zinthuzi mwaona inunso mukufunika mukhalepo

  • @KondwaniBanda-ul8sj
    @KondwaniBanda-ul8sj 5 годин тому +2

    A UTM afikatu ajawala akambala ndi amtumbuka ali papolice Ku 18

  • @VictoriaWilliam-ms2ft
    @VictoriaWilliam-ms2ft Годину тому

    Musableme opposition siyomwe yapangitsa kuti kaliyati amangidwe, nenani za manganya ndiyemwe akudziwa zonsezi

  • @FrankMsiska-i9j
    @FrankMsiska-i9j 6 годин тому +3

    Iweyo osapita bwaaa zitsilu ndinuyo mumangoyankhula

  • @RonnMtafya
    @RonnMtafya 6 годин тому +1

    GOD IS OUR JUDGE

  • @ReginaMulipa
    @ReginaMulipa 3 години тому

    Ndipo zoona izi Malawi akupanga dara awa kuti khani za kalembera akwanuse zifuna iwo athu akhare busy ndizimenezo uku akupanga zawo anyapapi awa matha osavotaso bas tiyituluke oppostion yamanyi bas tingosiya mcp yomweyi bas malemba akwanilisidwe amulungu

  • @marthablessings1314
    @marthablessings1314 4 години тому

    Tiyeni mutitsogolele inuyo man😂😂😂😂😂

  • @EsetaGerate
    @EsetaGerate 3 години тому

    😂😂😂😂ma toilet azimayi nde otani ❤❤

  • @elizachisi
    @elizachisi 6 годин тому +1

    Opposition tsegukani mutu please

  • @justinmalala-e4o
    @justinmalala-e4o 2 години тому

    Apapa mpamene zipani zosusa zingazindikileno kuti tulo silabwino. Umatha kupangidwa chilichonse

  • @DennisTobias-b4r
    @DennisTobias-b4r 5 годин тому

    Choipa chisata mwini, mulungu ali pheeee, ndi omwe anaika mcp boma lero a kupha Kasambara, chilima and 8 aja, osusa alibe nazo tchito a phunzire kuti mcp ndi yoipa

  • @DennisChikoti
    @DennisChikoti 5 годин тому

    Timawelengela kuti tili ndi opposition gulu la anamalomba koma aaaaa ayi ndithu kulephela kuteteza anzao

  • @PatienceMphuche
    @PatienceMphuche 5 годин тому

    Koma ndiye mwayankhula mai amphamvu opposition ikugona ndwiii koma akufuna vote yathu aaaa

  • @AlumakioChingalu
    @AlumakioChingalu Годину тому

    Malangizo auchitsiru awa

  • @CathrineRamseyJafaal
    @CathrineRamseyJafaal 3 години тому

    Tiyeni tikawotche ma police station onse

  • @BlessingsTembenu
    @BlessingsTembenu 6 годин тому

    Uthengawu undiperekere kwa opposition kuti dzimitu dzawo,zitsilu,afinye,and sakutithandiza agalu amenewa and tatopaso ndi opposition yopusa ngati imeneyi aaaaa.chilima yemwe uja ndiye anali olimba mtima pochita zinthu

  • @VincentKalata
    @VincentKalata 4 години тому

    Zislu za opposition umoz wake akuupanga pakamwa sakupanga action

  • @EvansNaphazi
    @EvansNaphazi 3 години тому

    Iweyo uli nziko lit kodi no brem game here

  • @EllinaBitto
    @EllinaBitto 2 години тому

    Zoona bro❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @chrisschikozera7271
    @chrisschikozera7271 5 годин тому

    Amalawi kupusa komaso opposition ikugona kwambiri I hate this opposition eeich now mcp is doing whatever the do the like

  • @SoundmasterElectronics
    @SoundmasterElectronics 5 годин тому

    Iwe ndiye munthu wanena zowona koma vuto opposition yathu tulo basi tipezeni mmizimu tipange zimenezo ife tinafakale kukhala moyo or kufa palibe kusiyana

  • @blessingsmwenela1308
    @blessingsmwenela1308 4 години тому

    Unena zoona Sallo ndipo ndiogona zenzeni hmmmmm

  • @OssmanAbubaker-v7t
    @OssmanAbubaker-v7t 5 годин тому

    Zoonadi brother Salo opposition yathu ndiyofoila

  • @GiftNorton-s3g
    @GiftNorton-s3g 4 години тому

    Nkhaniyo ndiyoona ine ndanyamuka kale mukandipeza komweko

  • @JuniorHala-vf9ov
    @JuniorHala-vf9ov 3 години тому

    Komaso amene tili kunjafe tisamangoyankhula chifukwa chot tilikunja ai ine ndimapasa ulemu kalindo akung'alula koma ali komweko kumalawiko enafe timazitenga ngat zopweka just because tilikunja ummmm John chilembwe adapanga chani nanga ife tilikunjafe tikupanga chani

  • @GrecianWyson
    @GrecianWyson 4 години тому

    Vuto ndinuyo otsutsa boma muli chete policeyo ilikumwamba osagamula bwanji chipolisicho esh zathu andarewa inu kuzizila mkhongono moyo wanga ukuchita kuwawa bwanji eshi

  • @JustinWBanda
    @JustinWBanda 5 годин тому

    Sikulakhula kwabwino uku. Km watinyoza kwambili samalakhula Chocho koma

  • @HassanSaid-q8q
    @HassanSaid-q8q 5 годин тому

    Mulungu angothesa dziko la malawi chifukwa sitionanso sogolo

  • @ChimwemweMathyola
    @ChimwemweMathyola 2 години тому

    Sukunama bro

  • @mabvutomichaelpanagona1949
    @mabvutomichaelpanagona1949 5 годин тому

    Wapanga zimenezo ndi Michael usi

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 15 хвилин тому

    Vuto inu mumalankhulila kutali mukuwopa kumangidwa mukunamiza anzanu inu

  • @FonnexBalakasi
    @FonnexBalakasi 6 годин тому

    Kkkkk koma ndasekatu ngati zosekesa koma zili zoona

  • @EvansNaphazi
    @EvansNaphazi 3 години тому

    Iweyo ukutani

  • @UncleShopRite
    @UncleShopRite 5 годин тому

    Amanga kaliati tiyeni tikawontche ma police station

  • @InnocentManganiNkhoma
    @InnocentManganiNkhoma 5 годин тому

    Sure

  • @ThoccoChimbali-h6g
    @ThoccoChimbali-h6g 6 годин тому

    Opposition zitsilu zokha zokha

  • @riccodeeforces8097
    @riccodeeforces8097 5 годин тому

    Ukanayankhula zanzeru... Pang'ono ng'ono

  • @StevenKupheka-k6b
    @StevenKupheka-k6b 5 годин тому

    Zoona amalawi ife ndife opusa kaya matha ndichani kaya

  • @MarcyKamaga
    @MarcyKamaga 6 годин тому

    koma ndare ndinchocho kodi anthu awa akufuna chani kufika size iyiyi

  • @Rose-wu5ef
    @Rose-wu5ef 5 годин тому

    Tiyen tiksomtche ma police onse

  • @OscarKathumba
    @OscarKathumba 5 годин тому

    Iweyo osabwera bwanji , mbuzi iwe

  • @boikieyuze4672
    @boikieyuze4672 5 годин тому

    Iwe osapita ku police bwanji galu iwe

  • @LuciusPatrick-f2c
    @LuciusPatrick-f2c 5 годин тому

    Brother salo ukunena zoona

  • @KettieNathaya
    @KettieNathaya 6 годин тому

    Tili kale konkuno ku police tikufunq Kaliati atuluke basi

  • @TicknessKondowe
    @TicknessKondowe 6 годин тому

    Kod iweyo usapita bwanji ukungoyakhula

  • @Mbeta-q8v
    @Mbeta-q8v 5 годин тому

    Mademo yambani pano
    Pompano sindilora pa 30 ayi

  • @RonnMtafya
    @RonnMtafya 6 годин тому

    MCP NJAKUPHA

  • @MagieJames
    @MagieJames 6 годин тому

    Zoona otsutsa tengani gawo

  • @Lushaka
    @Lushaka 6 годин тому +1

    Inuyo muli khuti phitani mukamuthenge kaliyatiyo pilibe ndiinu amene mulibe respect to your government since 1994 u never put really readers always u like talking nonsense without yourself starting something don't just come with your phone then start talking no respect to our country an people please don't talk to shirt to our people of Malawi bec of politics if your khaliyati never started politics today no since 1994 up to now busy different politic part so now u busy tell people to go against government bec of khaliyati no bra please respect your mouth who told u Malawi we need people like khaliyati still to run Malawi if Peter is no needed if atupele is no need now if chakwela is no need now bec people is tried with him an his group of readers who follow all government bt no one comes with new Malawi always talking shirt each other without respect because all of them comes one group just different names so u busy today telling to do something for khaliyati if yourself are u sure u need people like him to be president sorry guys shame on our country 😢is to much drama funny 😁

    • @LastonMmanga-r2u
      @LastonMmanga-r2u 6 годин тому

      But this Chakwera is the worst president since 1994 after multiparty,

  • @JaneMoyo-b7i
    @JaneMoyo-b7i 6 годин тому

    😂😂😂😂😂😂 opposition😢

  • @DysonTummiesSajiwa
    @DysonTummiesSajiwa 6 годин тому

    Iweyo pita ku police ko ukagone ndi mkazi wako

    • @OscarKathumba
      @OscarKathumba 5 годин тому

      Kkkkkkk mbuli sallo uyu,, abwere adzagone ndi ana ake

  • @AchiwaNikisya
    @AchiwaNikisya 5 годин тому

    😂😂

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 6 годин тому

    Eeeee zovuta

  • @LeoMisokwe
    @LeoMisokwe 5 годин тому

    Mphamvu

  • @AlinafeChimoto-pp7wp
    @AlinafeChimoto-pp7wp 6 годин тому

    😂😂😂😂

  • @LeoMisokwe
    @LeoMisokwe 5 годин тому

    Mphamvu