OTSATIRA CHIPANI CHA UTM AFIKA KALE KU POLICE KOMWE AKUSUNGAKO KALIATI

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 23 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 64

  • @ChomboNgosi
    @ChomboNgosi 3 години тому +4

    We love you Mamie always on ur side

  • @YasmeenYalabi-b2c
    @YasmeenYalabi-b2c 39 хвилин тому

    Allah akangolowela nyengo zonse zisinthilatu mama

  • @TominicMlowoka-v5k
    @TominicMlowoka-v5k 3 години тому +4

    Anyamata a UTM ponyani miyala kuli bwino civil war yiyambike

  • @MarryNyilongo-s5x
    @MarryNyilongo-s5x Годину тому

    God bless you akwen

  • @JosepJemu
    @JosepJemu 3 години тому +3

    Afuna kumupha achakwera ndi ndale ayika poison mu selo anthu oyipa inu koma chomwe mungadziwe palibe wamuyaya mulungu akuchitireni chifundo simukudziwa chomwe mukupanga

  • @IsmaelBilal-lh1pi
    @IsmaelBilal-lh1pi 2 години тому +1

    Bravo Malawian 🇲🇼 ✊️✊️✊️

  • @LameckNgwangwa
    @LameckNgwangwa 2 години тому +1

    More fire people bravoo

  • @HopkinsChataika
    @HopkinsChataika 2 години тому

    Viva UTM, I love you Mamie, osaopa ndipo osafyooka

  • @JacintaAntóniocharecachareca
    @JacintaAntóniocharecachareca 2 години тому +1

    Viva UTM ❤🎉🎉🎉🎉🎉

  • @GeraldMukhuna
    @GeraldMukhuna 2 години тому

    Tiyambepo mademo lelo tigone konkuno sitigaive imeneyo tiyeni konko🏃🏃🏃🏃🏃

  • @MelodiYohane
    @MelodiYohane Годину тому

    UTM komko ndikumene kwatuluka zimenezo chifukwa kuli chimkulirano cholimbirana mpando wa president.
    Tisamangoti Chakwera onani kae mmene zikuendera za ndale kuyambira ku Chipani chaocho.
    Chakwera tamunamizira zinthu zambiri koma akutitsutsa ndi Mulungu. Mapeto ake tikanthidwa Ndi Mulungu ngati tingamaweruze kuti ndi Chakwera tisadafufuze bwinobwino.
    ZIKOMO KUMPANDO

  • @samdiverson9733
    @samdiverson9733 2 години тому

    Viva akweni ngamo abusawa tribalism kwambiri kwake ❤❤❤❤❤

  • @PollyLysonLutepo
    @PollyLysonLutepo 2 години тому +1

    Ngati a Usi ndi a UTM, achitapo Chiani pa kumangidwa kwa Kaliati?
    Ngati sachitapo kanthu ndiye kuti ndi Iwowo amapangitsa kuti pa Convention yomwe akhale nayo azayende poyera.
    Kariati ndi m'modzi amene amawanjenjemeletsa.
    Koma ngati ndi amodzi a UTM a joiner azawo ku Police.
    Koma ngati ndi nyenga sangapite. Chifukwa Chakuti pamenepo amasangalala. Koma akunama.

  • @NeezeahKumbanga
    @NeezeahKumbanga Годину тому

    Tayatsanipo aaaaaaa akutiwoonjedza Panja akawoona Kt munth akumuremphera amamubaya Jackson amutulutseko wanthuyo

  • @amonechirwa
    @amonechirwa 2 години тому +1

    Viva UTM osaopa

  • @SoundmasterElectronics
    @SoundmasterElectronics 3 години тому +3

    Tiuzeni tilipo ife akaziotche tiphwanya police imeneyo

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc Годину тому

    UTM moto kuti buuuuuu.go,koko.ahlomwe,onse ku mwela tiyeni koko police ya pa 18 isatizolowele.

  • @EsnartSimenti
    @EsnartSimenti Годину тому

    Mumatiimilirq mom❤❤

  • @PatrickMacheso-r6z
    @PatrickMacheso-r6z Годину тому

    The biggining of Mai Kaliati successful political journey

  • @WilfredGunya1
    @WilfredGunya1 2 години тому +2

    Iyambike bas

  • @HajjiFreza
    @HajjiFreza 2 години тому +1

    Osa wopa osa fooka malawi 2025 tichose satana chakwela 💪💪💪

  • @MillieMalakam
    @MillieMalakam 3 години тому +2

    Umakwana mammy

  • @ussimasi2458
    @ussimasi2458 2 години тому

    Bravo mama💪💪💪

  • @BerthaKasambala-y5k
    @BerthaKasambala-y5k 2 години тому

    Kkkkk zokambirana ayi awoneseni kt amarawi munatopa aporice opusa jombo zawo zinatha kare kare timanyumba tawo tonvesa chisoni

    • @ElizabethZiyadi
      @ElizabethZiyadi 2 години тому

      Iwe osakayambitsa bwanji ukufuna akayambitse anzako?bweraniko ku joniko muzidzayambitsa inuyo

    • @BerthaKasambala-y5k
      @BerthaKasambala-y5k 2 години тому

      @@ElizabethZiyadi kwacha ikugwa deiry tibwera boma rikasintha anthu akasiya kudya chiteze

  • @FatimaMwanyali-k2l
    @FatimaMwanyali-k2l 3 години тому +2

    Sakuyankhulilanji chifukwa chomwe amangila bwanji kumangot ndi mulandu wa srs zopusa bas

  • @Dauson-j5i
    @Dauson-j5i 4 хвилини тому

    Ndiye nanga ngati nkhani zake zili zomwezi amanama

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 Годину тому

    Koma apolice Aku Malawi ndi chani mukuwoneka ngati mwayamba kupenga misala

  • @RestarUmi
    @RestarUmi 2 години тому

    Viva UTM

  • @JusticeMikondo-i9e
    @JusticeMikondo-i9e 2 години тому

    Zangovuta I need ndikanakhala pafupi kwangotalika ku l city

  • @STEVENMPONDA-o6r
    @STEVENMPONDA-o6r 2 години тому

    MANGANYA ndiyemwe akudziwapo kathuu tamufusan ndiyemwee akukwedzera MOTO kt akwen amagwidwee

  • @dalitson3558
    @dalitson3558 Годину тому

    I can see very chaotic situations Happen next, probably civil war

  • @JaphetSakala-u5j
    @JaphetSakala-u5j Годину тому

    NDI jocka uyo ndintengo omweuli ndizipaso zakupya ayamba kuugenda.

  • @SoundmasterElectronics
    @SoundmasterElectronics 3 години тому +4

    Awuzeni za chamba ayi

  • @PreciousKARINGANIZA
    @PreciousKARINGANIZA 2 години тому

    Tiyatsa police imeneyiiiii

  • @engieberlmaguaire5473
    @engieberlmaguaire5473 Годину тому

    Vuto loweta ng,ona ngat mphaka wannyumba ndiizi , awa munawakweza muntengo nokha.

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 3 години тому +2

    Guys let's just demonstrate

  • @DennisChikoti
    @DennisChikoti 2 години тому

    Ndathokoza a UTM pa zimene mukuchita pamenepo

  • @SuzgoMkandawire-ss4kh
    @SuzgoMkandawire-ss4kh Годину тому

    Gendani miyala polisiyo

  • @kevinchipembere1137
    @kevinchipembere1137 Годину тому

    Nde ukakhala mmalawi uzipanga zirizonse wafuna? No! We need to be civilized at all cost

  • @JACKSONHULUWA-j2n
    @JACKSONHULUWA-j2n 2 години тому

    PK awina, mtsogoleri akamangidwa amawina

  • @AshimayeGama
    @AshimayeGama Годину тому

    Anapha chilima lelo akufuna kupha amayiwa dzonakoma amalawi tingo yang .Ana atitolatu uyu

  • @MadalitsoChilinjala-f9v
    @MadalitsoChilinjala-f9v 2 години тому

    Tili nanu mayi tikukuikizani mapephero mulungu yekha ndi amene akudziwa

  • @owenkazembe5636
    @owenkazembe5636 24 хвилини тому

    Akuyankhula zopanda nzeru

  • @Joe-h9v
    @Joe-h9v 49 хвилин тому

    Dziko ndila amalawi silamunthu Osama ophezana apolice mupandidwa zikutiwawa ifeyo sitikuwopani nanu

  • @RosetNkhoma
    @RosetNkhoma Хвилина тому

    Auzeni Kuti simukuopa ,chilima anafa kale musope

  • @SimonMochede
    @SimonMochede 12 хвилин тому

    Kodi azipani Zina zosutsa ali Kuti?

  • @SoundmasterElectronics
    @SoundmasterElectronics 3 години тому +2

    Tengani ma pic a apolice wo tiwasaka mmakomo ndipo tiwanyenyanyenya

  • @DixonChimanya
    @DixonChimanya 2 години тому

    Osaopa

  • @Joe-h9v
    @Joe-h9v 53 хвилини тому

    Amenyedwe apolice

  • @AlfonsoTheo
    @AlfonsoTheo 6 хвилин тому

    Km mai wanga sadalakwe atulutseni

  • @justinmalala-e4o
    @justinmalala-e4o 50 хвилин тому

    Vuto la zipani zosusa zikakhala zogona everything can happen

  • @EmmanuelNgambi-y6h
    @EmmanuelNgambi-y6h 56 хвилин тому

    Zifukwa zopangira mademo zikuchulukirabe osaopa osafooka osatopa

  • @MosesDicostar
    @MosesDicostar 3 години тому +2

    Viva Malawi viVaaaa

  • @patricksamson4852
    @patricksamson4852 Годину тому

    Manganya ukunama wadya magazi a mcp sizitheka

  • @GraceMasiye
    @GraceMasiye 2 години тому

    Khwiya iwe,Koma kumeneko,tiye nawoni osalola

  • @EmilyKanyika
    @EmilyKanyika 2 години тому

    ❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @MoosaSidrick
    @MoosaSidrick 2 години тому

    Otchani chipolice chawocho abele amenyen apolicewo

  • @ChisomoLester-h7x
    @ChisomoLester-h7x 2 години тому

    A Malawi kumbukilani kt Vice president wa dziko ndi wa UTM ali ndikuthekela komanga munthu amene akulimbana naye ,osamangoti boma ayi. Unkutheka kt upo ukunenedwawo akulimbana ndi manganya tadekhani kaye ndizandale izi mukuvutika ndi inu anthu ovutika

  • @Joe-h9v
    @Joe-h9v 45 хвилин тому

    Usi ngwa mcp mungovela zakamanjekete munthu asayakhule mcp mwatitopetsa situkufunani kamuzu amavuta pano alikuti mpando womwe muliwo amcp ngosiyilana

  • @louisgolden
    @louisgolden 2 години тому

    Osawaselelera