Apa Mpamene Amalawi timudziwe Denis Thanthwe Mahata, Masanje alekeke.

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 23 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 144

  • @amontchuwa6876
    @amontchuwa6876 15 годин тому +3

    Mr Mahata, Mr Fredo, Mr Kamangila, Mr Kalindo, ngat nkotheka kt anthuwa apange chinthu chimz ziko likhoza kusintha, mothandizana ndi ntanyiwa komaso wabakili tv Malawi 🇲🇼 akhoza kukhala strong 💪

  • @MikeTwaibu-i1h
    @MikeTwaibu-i1h 14 годин тому +3

    Forex inathera kukalimbikisa mkhondo ya Ayuda ku UNGA

  • @fredgabrielnyangulu
    @fredgabrielnyangulu 12 годин тому +2

    Kodi ndi mayiko angati omwe amagula mafuta through ndalama yakwao man sisanamizidwe ai nkhani ndi mbavazi basi😊

  • @mikebernabechimundi3472
    @mikebernabechimundi3472 День тому +5

    Amene aja ndi akamuna, samayankhula wamba

  • @JulianaMkonda-k2n
    @JulianaMkonda-k2n День тому +7

    Mayendedwe naonso anachuluka lero ndenge mawa ndege forex ingapezeke

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon3429 14 годин тому +1

    Mahatha mwana wonganiza boooo

  • @IshmaelAmos
    @IshmaelAmos 12 годин тому +1

    Danes is our future president period.

  • @enockkanyerere784
    @enockkanyerere784 День тому +6

    Inu ma dollars amaliza ndi maulendo ....

    • @JonesChingaya-yf4gg
      @JonesChingaya-yf4gg 17 годин тому

      @@enockkanyerere784 ndipo live amaziwa kut ma dollars ndiochepa koma kuyendayenda bas

  • @usherjamson174
    @usherjamson174 День тому +3

    He is wise, men

  • @NedsonKamwaza
    @NedsonKamwaza 12 годин тому +1

    What is this all about mr

  • @alexanderlipenga1330
    @alexanderlipenga1330 День тому +3

    Ma dollars mufupa pa ukwati...koma yaa
    Denis Mahata uja knows what he is doing n good for this country let's support him.
    Mind you kulibe zozipenta it's just working for the prosperity of our mother Malawi

  • @StaffordNgoleka
    @StaffordNgoleka 14 годин тому +1

    Boma yokuba mulibe experience yoyendetsa dziko chimene mukudziwa ndikuba bas agalu inu

  • @ThomuChiwanga
    @ThomuChiwanga 13 годин тому +1

    Choka iwe osati zaka 10 wachamba iwe nena kuti Kwa zaka 4 zokhadzi ndiye tawona malodza amenewa wamva iwe kulu nkhuyu

  • @samchibenene4458
    @samchibenene4458 14 годин тому +1

    Uyu ndikatundu mzito

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy День тому +1

    Amene uja si Muthu wamba

  • @ThembaniJikah
    @ThembaniJikah 9 годин тому

    mahata on fire 🔥 koma kuseliku ma judge akulandila ma Dollar 😅 mapwala anuo mr

  • @SUNGANANIGONANI-l5d
    @SUNGANANIGONANI-l5d День тому +2

    Dennis mahata ine ndinadziwa kuti ndidolo nditangowonela interview ija ndipo kudzangopezeka pa ballot paper voti yanga Watergate basi

  • @HajjiFreza
    @HajjiFreza День тому +2

    izi ndizowona br salut

  • @kubengovender6996
    @kubengovender6996 День тому +1

    Big up brother man!!

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera  День тому

      @@kubengovender6996 🔥🎉🙏
      Thanks brother

  • @Haka-tb8ih
    @Haka-tb8ih 12 годин тому +1

    Mukufotokoza nkhwangwa ili mmutu? For what? Sympathy? Hell no

  • @GitfIobodo
    @GitfIobodo 14 годин тому +1

    Kunkuyu ndi odwala magazi achilima akumudzunguza

  • @WorriedNdhlovu
    @WorriedNdhlovu День тому

    This guy is really genius

  • @Jacksonmuhackeya
    @Jacksonmuhackeya 14 годин тому +1

    Muvomeleze kuti mwalephela agalu inu

  • @Michaelaliemapira
    @Michaelaliemapira 14 годин тому +1

    Ok kunkuyuu takunva tapangaso apa masam a report la mafitalo which means totally amout fo petrol ls =Ltre's 29,800,000 twenty nine million eight handered Southend.
    Kudzaso Desilo Totally =4.500,000 Lter's. Four million five hundred thousand litres

  • @StewardKapoto-u7k
    @StewardKapoto-u7k День тому +2

    Inetu mahata amandiwaza kwambili

  • @LufaniAhamadi
    @LufaniAhamadi День тому +1

    My vote mahata

  • @JustinMatola
    @JustinMatola День тому +2

    Kunkuyu ndi waboza uyu zaka 10 zomwe akuzichulazi MCP inalipo nthawi Ya APM or ndalama ya Rand inali pose potse malawi muno koma pano or utayisaka mene ikusowelamo awatu akusowa chokamba ango siya asamayanguleko fundo dzake ngati mwana weni weni

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick День тому +1

    My Malawi mmmmmmmm atii kuli president mmmmm

  • @OssmanAbubaker-v7t
    @OssmanAbubaker-v7t День тому +2

    Brother Denis zoonadi iweyo ndi mtsongolere wamasomphenya

  • @LameckNgwangwa
    @LameckNgwangwa День тому +2

    Koma chakwera atati akutuluka kuja ma dolars apeza

  • @JamesChiphazi
    @JamesChiphazi 17 годин тому

    Maulamulilo apita mbuyomu madora samasowa mpamene yafika pano ganizilani maulendo aapresident opanda nao zelu apangisa kuononga madola oodela mafuta sogoleli opanda masophenya

  • @CharlesNyakuipa
    @CharlesNyakuipa День тому +1

    Chikangawa wooyeeeeeeee😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg День тому +3

    Komatu dziko muno muli anthu anzeru koma sali pamalo oyenera, this kind of kunkuyu sakuyenera kupezeka pamene alipa.

  • @NgeyasjuWadeya
    @NgeyasjuWadeya День тому +1

    Because of lack of leadership from the top ndi nduna zawo ndamene akuononga dziko chomwe akudziwa iwo ndikuba basi to proof this information, nkhani za serious samakhala nazo busy koma busy ndizopusa nde lero ndiizi follow denis mahata you will see the directon osti izi za Akunkuyuzi

  • @AliNtolera
    @AliNtolera 12 годин тому +1

    Mbolo yako fisi iwe kumkuyu ukulamkhuya chifukwa choti wakhuta ndalama eti amzako akudya chitedze

  • @JasonMailos
    @JasonMailos День тому

    Mahata number one

  • @PreciousSteven-e5s
    @PreciousSteven-e5s День тому +1

    Auzeni zandègetu kuti amalawiwo adzipanga. Chiganizo cha bwino monga munenera amozesimo

  • @LoydMcheleka-uq3ix
    @LoydMcheleka-uq3ix День тому +2

    That’s why the president and his administration are the to solve these problems not always giving unexplainetion no no no you hade failed us a lot if you don’t know what to do just leave our Malawi alone 😢😢😢 please

  • @JackElias-ty2tt
    @JackElias-ty2tt День тому

    Mahata❤❤❤

  • @IsmaelBilal-lh1pi
    @IsmaelBilal-lh1pi 5 годин тому

    Zangongole basi. Ngongole siyingathukule dziko iwe akunkuyu. Dairy bodza amalawi samadya mabodza

  • @ShayibuJames-xc8il
    @ShayibuJames-xc8il День тому

    ndigaileni ku wap chifukwa ndapombonezeka enable amati ndindale koma apapa inenso ndigwireko ntchito pang`ono please

  • @Khadija-q9r
    @Khadija-q9r 20 годин тому

    Nokha mafuta abwela kusowa.mafuta kwatha
    Apatu born kalindo.osazamuphweketsa

  • @Ishumail-t9o
    @Ishumail-t9o День тому

    BMtv is the best TV ever

  • @JimsonChisi
    @JimsonChisi День тому +5

    The future president Denis mahata

  • @AubreygEliasizia
    @AubreygEliasizia День тому +2

    D Mahata mbambande

  • @madalitsomisomalih5411
    @madalitsomisomalih5411 День тому

    Koma ndiye covid 19 simuzasiya kuunamizila oti kusogoloku muyamba kunamizila ziwawa za ku Mozambique kuti muzuzeso anthu pa Zina.

  • @Blessings-td4cr
    @Blessings-td4cr День тому +1

    Kunja kuno kuli ana anzeru koma mbava apsyatangu manjanjawide mfiti ndiso kutchuka mwauchitsiru mbuli!!!!! Ndizomwe zikugwetsa dziko lino,posafuna kupereka mpata kwa oganiza mwaukadaulo ngati achina bon kalindo,,mahata,,kamangira ,, bakili TV and others ndiomwe Ali ndi kuthekera .

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick День тому +1

    MCP kwawo kunatha firs day atangolowa kumene

  • @WorriedNdhlovu
    @WorriedNdhlovu День тому

    Kunkuyu matsinya pamaso akuopseza ndan

  • @giftmakoyo1441
    @giftmakoyo1441 День тому +1

    Koma zimenezi ndizouza ntundu wa amalawi mmmmm kusonyeza kuti mwalephera

  • @MonicaBvumbwe
    @MonicaBvumbwe 10 годин тому

    Mapwala ako akukuyu osangoti mwalephela

  • @OretarbadrBwanali
    @OretarbadrBwanali День тому +1

    Mnyamata wa nzeru kwambil

  • @giftkamwiyo9175
    @giftkamwiyo9175 23 години тому

    Chikangawa angoyenda timawulendo topusaa dollar ipezeka bwanji

  • @mabvutomichaelpanagona1949
    @mabvutomichaelpanagona1949 День тому

    Ulendo umene mukuyenda mumalipira ndi chiyani zopusa basi

  • @YasenYasen-q9g
    @YasenYasen-q9g День тому +1

    Ukuona kutuweka zinduzakukanika bwanji ozatula paziudido nanga kungokakamila zinduzizikuye ndakoma kufunapando iweyo nigalu

  • @MlaziJames
    @MlaziJames День тому +2

    Atule pansi udindo mr chikangawa

  • @HestingsEdward
    @HestingsEdward День тому +1

    Kodi ndizoona kuti sitima ija idari juice wa shuga votiyanga yasintha ilimbana ndi mashin aja akuti ndi obera zisankho tikungofunako tsikulo bwana

  • @mcdonaldnkhwazi1982
    @mcdonaldnkhwazi1982 День тому +1

    Mukumakhala ndima dolas ochepa koma daily kumayenda kupita kunja pali nzeru

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule День тому +1

    Kkkķkk Mavuto❤

  • @BlessingsKachokola
    @BlessingsKachokola День тому

    Moses kunkuyu ndiwe chitsilu kwabasii aseee AAAA umatiwona ngatii ndife ana mudziko Muno kapena dzikoli umalitenga ngatii ndila amako iwe pa nyelo pa mako wavaa mbuzi yamunthuu iwe bola mayako akanapita pa chabe kusiyana ndikukubeleka iweyo

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 День тому +1

    Uyu ndinamandwa alibe muzake

  • @AubreyChiyaya-ty8ge
    @AubreyChiyaya-ty8ge День тому

    Denis tiomboleni please

  • @ShayibuJames-xc8il
    @ShayibuJames-xc8il День тому +1

    kaganizidwe kamahata andale sanaganizeko ngakhale dontho

  • @AlihIbrahim-s7v
    @AlihIbrahim-s7v День тому +1

    Komano akuluwa nwanji sakunwelano poyela kuti mwina Amalawi amudziwe mwina mkuzamusankha

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera  День тому

      Anabwera kale poyera km akuluakulu akumupondereza komaso achinyamata we need to support him

  • @MadalitsoChinkhonyo
    @MadalitsoChinkhonyo День тому +1

    Munja anayendela chikwangawa munja ndalama amazitenga kuti amukuuzani kuti chepetsani maulendo koma kusava

  • @fanuelbinde
    @fanuelbinde День тому +1

    Popita ku unga kuamerica anthuwa amalipira ma kwachaaa kapena ma dollars?

  • @Lizzie-h1k
    @Lizzie-h1k День тому

    Mwachidule, tinene kuti zomangongola dzindalama zambirimbiri zija mukupitilizabe???

  • @AllanWyson
    @AllanWyson День тому

    Ma dollars analipo koma Chikangawa anatenga onse mkumayendayenda nawo mkumapita kokwera njinga plus kutenga anthu 150 kumapita nawo ku UNGA

  • @andiwochishadreck3753
    @andiwochishadreck3753 День тому

    This government is gone

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete День тому

    Denis mahata my vote ❤❤😂😂

  • @AdamJames-x7x
    @AdamJames-x7x День тому

    kumkuyu ku Malawi kulibe president iwee , machende Ako

  • @JohnWame-u3l
    @JohnWame-u3l День тому +1

    Kumvatu timanva,koma timanva monvenura

  • @AdamJames-x7x
    @AdamJames-x7x День тому

    ukatero ukuganiza zokabwerek a ndalama ku ma bank akunja then mugulure mafuta , kumkuyu ma battery Ako komanso mutu ngati choswera malambe galu.

  • @ThokozaniPiyo
    @ThokozaniPiyo 11 годин тому

    Kod malaw imaendetsedwa ndi ngongole kapena economic activity yake

  • @IsaqueFernandoAntônioAntônio

    Ndintunda zedi umeneyu

  • @joshuaagabu3032
    @joshuaagabu3032 21 годину тому

    APM mmene amachoka dziko la Malawi linalindi three months import cover. Kuthauza kuti ku Malawi kuno tinali ndi ndalama zakunja zoti tikanatha kugula zinthu zakunja ngati mafuta kwa miyezi itatu mosavutikila. Mfunso ndi kumati Olemekezeka A Nduna A Kumkuyu ka three month import cover anasiya big man ndi team yake ku mpingo wa mtambo mtambo kaja kanayenda bwanji?

  • @AdamSteven-ne9hg
    @AdamSteven-ne9hg 15 годин тому

    🔥 bakili muluzi tv 📺 😂

  • @StewartGoma
    @StewartGoma День тому +1

    Chakwela akanabo mqondo

  • @thokozanindalama
    @thokozanindalama День тому +1

    😮😮😮😮😮

  • @StellaCharmer
    @StellaCharmer День тому

    Funso la nzeru America ma dollar amatenga kuti

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg День тому +1

    Kunkuyu plus yr boss dzimachende dzanu bwanji simukuva chisoni ndi anthu tikuopeni poti ndinu satanic mukaudzane nose nyini dzamanu

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 День тому

    Komatu bwezi akunena mayi uja wa nkhope ngati ine uja

  • @Moses51
    @Moses51 День тому

    Chakwela ndamene adaongonga madollas ndikuyenda yenda ndiye Kaya ayenda liti

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 День тому

    Koma fuso chakwela akamayenda amalipila makwacha?

  • @WysonSadiki
    @WysonSadiki 10 годин тому

    Komano mutachepetsa kuyenda yendako mwina zinthu zambiri zilongosokako

  • @yunuschiutula
    @yunuschiutula 8 годин тому

    Maulendo opanda pake achuluka

  • @TendaiMerisha-eh3gn
    @TendaiMerisha-eh3gn День тому

    Kod mesa munati mafuta azibwera pa train not pa truck?

  • @martinnyirongo2892
    @martinnyirongo2892 16 годин тому

    Mafuna avuta kwambiri 4yrs yanu iyi, komaso maulendo akuchuluka kwambiri akuwononga ma dollars ankhani ankhani mdziko muno, tafika moti mpka kuchita kuwenga truck amene kubwela alimnjila 😂😂😂 ai boma ili salendi izi ndi mbuzi za anthu.

  • @ZayaweStone
    @ZayaweStone 16 годин тому

    Uyu simunthu wamba

  • @BawulenLuka
    @BawulenLuka 22 години тому

    Nkhani ya mafuta yomweyi mpaka zidodo...ngati mwagwesa ndege ina....mmmhhhh

  • @Bonisiwentamo
    @Bonisiwentamo 23 години тому

    Afanawk ndi katundu osati akukuyu angoba

  • @ChikondiChimwaza-i8l
    @ChikondiChimwaza-i8l День тому

    Kukuyu ndiwe galu wamva eti

  • @RacsonKundambo
    @RacsonKundambo День тому

    Avutikadi chifukwa chopanda nzeru za chipani cha mcp munangobwera kudzaba basi agalu inu anyapapi

  • @AdamJames-x7x
    @AdamJames-x7x День тому

    iwe kumkuyu pamtumbo pako , forex munakathera ku UNGA , pano ukufuna kumanamiza anthu , zopusa basi , tchende lako kumkuyu

  • @JamesRoben-dy7bx
    @JamesRoben-dy7bx День тому

    Kukuyu ndimakukonda koma zomwe wayamba kukamba zopanda dzelu mwachidule Mafuta asowa chifukwa sanapeleke ngongole fuso ndalama zinaononga chakwela Kunja zinja bwanji osabweza ngongole

  • @papelariareis.e.
    @papelariareis.e. День тому

    Kunyamura anthu 300 kupita nawo kunja ma allowance in usd 😂😂😂 ine sindidzabweranso kumeneko😂

  • @SimonBanda-b1f
    @SimonBanda-b1f 18 годин тому

    Akamakuwuzani kuti chepetsani zoyenda yenda NDI chigulu KU maiko akunja simumamva apatu mwamaliza ma dollars.
    Komanso mwabitsa ma dollars ena KU mayiko akunja

  • @Moses51
    @Moses51 День тому

    Chulungamo chibwele poyela

  • @Mickeykasambula265
    @Mickeykasambula265 День тому

    Tikamavutika padziko pano zimangokhala nkhanza zanthu ena

  • @AdamJames-x7x
    @AdamJames-x7x День тому

    kod mesa 2 weeks yapitayi mumayakhula monyera kuti mumakalandila mafuta through pa njanji ndi nzako wakupha uja , nde pano mafutawo Ali kuti ? agalu inu mu 2025, muchoka m'boma