AMUKWENYA PETER MUTHARIKA KOMASO ATUPELE MULUZI KUTI NDI OLAKWA

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 6 вер 2024

КОМЕНТАРІ • 197

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg Місяць тому +25

    Inuyo anthu a ku Mangochi ndinu adyera, mwagulisa vote yanu ndi ndalama. Ndipo olo mutati musazavoterenso DPP kapena UDF, Apm ndi Atupele sangavutike muzivutika nokha ndi nkhanza za MCP.

    • @AngolanChinga
      @AngolanChinga Місяць тому +1

      Ndiponso kwambili zitsilu za kumangochi akuona ngat anthu amene aja angavutik ovutik ndi omweo mahule

    • @JonesChingaya-yf4gg
      @JonesChingaya-yf4gg Місяць тому

      @@AngolanChinga Ndipo anthu ofooira zedi, ndalama alandira okha adyanso okha lero akulimbana ndi APM ndi Atupele.

    • @AngolanChinga
      @AngolanChinga Місяць тому

      @@JonesChingaya-yf4gg mahule akumangochi ka mitu yao sigwila

    • @user-pe8uh6oq8q
      @user-pe8uh6oq8q Місяць тому

      Ayao ife sitimawawerengeratu kuti kuli anthu kumalawi kuno 😅

    • @spargomw
      @spargomw Місяць тому

      ​@@user-pe8uh6oq8qkkkkkkkkkkkkkkk Koma ndaseka🤭🤭🤭

  • @duncainjimmy
    @duncainjimmy Місяць тому +5

    Awa adya za MCP .
    Kodi Atupele mmene anaigwilira ntchito yokopa anthu muja koma bwanji anthube tisankha MCP ?
    Kodi APM ndi Atupele ngati satiuza kuti zinthu zavuta mdziko muko ndie kuti nafe sitingadziwe tokha kuti zinthu sizikuyenda mdzikoli ?

  • @sungananigondwe2807
    @sungananigondwe2807 Місяць тому +7

    Ayawo ndiokonda ndalama kuyambila kale

  • @YamikaniMwale-bo7cv
    @YamikaniMwale-bo7cv Місяць тому +1

    Kuwina wa mcp ku mangochi sizikutanthauza kut kumangochiko anthu ndi a mcp,,,kumeneko ndikwa DPP NDI UDF BASI, musamunyoze peter ndi atupele chifukwa cha chisankho cha counsellor,,MUSIILETU ZOMAMUNYOZA PETER KUTI WAKALAMBA,,IFE ACHINYAMATA ZIMATINYASA,,,APM MY VOTE 2025 ISHAALA

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms Місяць тому +2

    Anthu mu kuposita zabodza izi, uyu wa mcp akuyakhulayu panyapako iwe

  • @CassimRasheed
    @CassimRasheed Місяць тому +2

    Choka apa iweyo chisiru palibe chomwe mungatiuze choka choka

  • @mkhokholasamuzonda5094
    @mkhokholasamuzonda5094 Місяць тому +4

    Akudyesa banzi galu iwe

  • @yakiduidi5752
    @yakiduidi5752 Місяць тому +2

    Koma a kumangochi ngati mukufuna kuti azikupasani ndalama a DPP ndi UDF simuzatukuka ndipo iweyo amene ukuyakhula ulibe nzeru ngati MCP umayikonda usamayakhule zopusa

  • @PatrickMakina-c2w
    @PatrickMakina-c2w Місяць тому +1

    Komanso we have to learn a Malawi pazomwe tinachita poika m'boma mimbulu yomwe ikutiluma leloyi. Chakwera ankachita kusasa mau poyankhula asanalowe m'boma, koma now alind soft voice poyankhula. But I hope will not Rpt this anymore

  • @akudo7819
    @akudo7819 Місяць тому

    Ndagwilizana nanu amayi inu . A Chakwera anabwera kudzapanga kampeni ku Mangochi kumene kunali kumuthandiza kansala wawo pomwe APM and Atupele sanachite. Zotsatila anawina kansala wa MCP. China ndichakuti Mangochi ndi ya UDF and DPP muulamuliro wawo wonse sanasankheko nduna from Mangochi pomwe MCP inasankha nduna ku Mangochi (Ibrahim Matola). Chonde konzani khalidwe timakonda UDF komanso DPP kuno ku Mangochi. Zikomo

  • @ElvisKanyenda
    @ElvisKanyenda Місяць тому +1

    Sakunama munthuyu and Chakwera tidzamuvoteraso akapanda kusamala

  • @LindiweMoloi-wn5qo
    @LindiweMoloi-wn5qo Місяць тому +2

    Mai mwalankhulatu, ayi ndizoona mukunenazo peter ndi atupele akugona,sanazukebe

  • @BensonAbdul-li1bc
    @BensonAbdul-li1bc Місяць тому +1

    Mayi uyu watumidwa ndi MCP iwe mangochi yake umakhala kut mdikukuziwa ine wakwagona ngati iwe

  • @JamesSinyolo
    @JamesSinyolo Місяць тому +2

    Sakunama ayi Peter angoti phwiiii mnyumba kenako kumati i will win

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 Місяць тому +2

    Vuto rako ndi chani muzimayi iwe ngakhare murandire ndarama tose tipitiliza kuzuzika ndi MCP

  • @MaxwellChiwaya-tv7kn
    @MaxwellChiwaya-tv7kn Місяць тому +2

    Mwadya ndalama za mcp ndiye mudzitokota

    • @eliaskhofielias8152
      @eliaskhofielias8152 Місяць тому

      Ayi sikut wadya koma ntima ukumuwawa kut anthuwa osakampangila bwanji kampeni mwanayi bwanji.zowawa palibe as dpp ndi as udf osakampanga support Bwanji?sanapange bwino iye sakufuna kut mcp isakhale ndi room ku southerner.koma akuipasa mpata akut aaah zaukhansalazi zopanda ntchito pomwe anzawo zomwezo ndipomwe akuziona zofunika kwambili.adzazindikila atagwa a dpp ndi udf 2025 chifukwa chonyozera zinthu zomwe zisali zosafunikila.so zomwe akutanthauza azikhala busy ndizilizonse a wiliwa.zaukhansala,za u mayor,mp ndi u prezident zomwe.mphwayi ndi tsoka ndipomwe aona izi mcp izilowa chonchi.

  • @YanjananiChayenda
    @YanjananiChayenda Місяць тому

    Sakunama ngati atopa apume basiii , a mcp akangowina vuto sikubela koma kuzikonda kwa MA oppositions leaders awo, palibe kutosya chala munthu, zikhalani mphwiiiiyo choncho kumadya MA sausage wo

  • @user-zl9vj6hc6y
    @user-zl9vj6hc6y Місяць тому +1

    Kodi ndindani namachende ameneyu... ??? Walandila zingat Ku MCP??

  • @BradahzMajawa
    @BradahzMajawa Місяць тому

    Ayao ufulu wawo samauziwa. Koma ndalama basi. Peter ndiwachikulire, anakapedza wina oimira Dpp. Tupere ndiozikonda, uzimva ndalama

  • @hawardwilliams9704
    @hawardwilliams9704 Місяць тому

    Muluzi ndiworakwa anatenga arendo chipani cha UDF kusogoza arendo rero mwawonatu

  • @ziyamporoma377
    @ziyamporoma377 Місяць тому

    Akunena zoona ameneyu ngakhale mukumutukwana....APM & Atupele were supposed to campaign for their candidates....chisankho chinali mkhonde mwawo why they didn't show up?

  • @FaidaKuntiya
    @FaidaKuntiya Місяць тому +2

    Koma 3 kwacha inampelekaadi yesu 😂😂 Awatu zilipo alandila

    • @user-ky4ce9gb6j
      @user-ky4ce9gb6j Місяць тому

      Ndipo kwambiri tu mmm

    • @patriciacraiton-sf5vu
      @patriciacraiton-sf5vu Місяць тому

      😂😂😂😂😂😂😂

    • @ModicaiChirwa
      @ModicaiChirwa Місяць тому

      Nanyongo wako Uona chomwe chidameta nkhanga mpala siudya bwino ka 2kwacha akupatsako anzakoo akuba zochuluka tikulira limodzi ndiiwe wemwe nanyongo wako

  • @user-og4oe5yp4w
    @user-og4oe5yp4w Місяць тому +3

    Kalindo anayamba kale akukutakatani koma inu dyooooooo ngati akukumetani

  • @JosephMoyo-k2h
    @JosephMoyo-k2h Місяць тому

    Akutuma iwe, olo president akanabwera ndiye akadavotera councillor? Inu ndi ofoila

  • @ishmaelbonomali7303
    @ishmaelbonomali7303 Місяць тому +2

    Wachita kuinekelatu kuti akutuma

  • @AmosScott-z9x
    @AmosScott-z9x Місяць тому +2

    Mwadya zingati bwana

  • @user-ym2bu3cx3k
    @user-ym2bu3cx3k Місяць тому

    Ndiye osangovotela MCP yo bwanji chosokosela ndichani

  • @PatrickMakina-c2w
    @PatrickMakina-c2w Місяць тому

    I'm a gree with this guy cuz chiyembekezo cha a Malawi nd Dpp koma kuiyonaso Dpp yakeyo siyoifela ayi anthu akulila koma iwo szikuwakhuzaso ayi

  • @GeorgeKapito-um2wl
    @GeorgeKapito-um2wl Місяць тому

    Iwe usalire.zimthu zili bwino.ngati umachikonda chipani cha DPP dziwa zilibwino.

  • @EbenezerSaidChikumbu-w7i
    @EbenezerSaidChikumbu-w7i Місяць тому

    Inenso mjomba zandinyasatu kwambiri.Mwambi uwu upite kwacha dpp ndi dug
    Chete chete sausa nyama komatu hoi hoi.uyoo uyoo.kapena kuti ndakuona ndakuona

  • @user-wn3mu3cx6z
    @user-wn3mu3cx6z Місяць тому

    Chilungamo icho mzowonadi ineso ndakwiya nazo ,kumangochi Pana mcp Aaaaaaaaaaaaa chitaponi khanthu mabwana a DPP komaso mcp please please, zikomo.

  • @TwayazAbdul
    @TwayazAbdul Місяць тому

    Kunena chilungamo munthuyu akukamba zoona Amuthalika ndi Atupele mukupanga zithu zauchisilu kwambiri ndalama muli nazo koma kuumila ndi kusathandiza kupanga Campaign basi

  • @Chiso2019
    @Chiso2019 Місяць тому

    That's why analandidwa boma....kupepera too much....mmene imachedwera milandu kut akagamule kuma courtko akufuna azizapitisa nkhani ya ma I'd mu august chaka chamawa, kulemphera kuwaunikila komabe sakuonapo vuto...ndaikonda mcp kwambili

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms Місяць тому +1

    Don't trust who's talking this nonsense

  • @AllieKaisi-je6rm
    @AllieKaisi-je6rm Місяць тому

    Ndipotu muzawina inuyo mwadya chim'basi cha mcp or mwanyoze bwanji a opposition inuyo nde adyerawo

  • @user-lr5bz7qk2d
    @user-lr5bz7qk2d Місяць тому +2

    Tiye uko kape tizingodyani zimene akupasa zo chikwela

  • @MeriaMasinga
    @MeriaMasinga Місяць тому

    Kugulitsa vote chifukwa cha ya singachite

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm Місяць тому +1

    Zoooonaaa auzeniiii afasa mopusa kwambiri

  • @HappyAutumnTrees-cd9ye
    @HappyAutumnTrees-cd9ye Місяць тому

    Mukufuna mumuphenso chifukwa chaukhansala udikire ukuona September ino iwe khala ndi chakwerayo,,

  • @JamesLongwe-qz9fd
    @JamesLongwe-qz9fd Місяць тому +1

    Akutumani mwina

    • @IssacMateyo
      @IssacMateyo Місяць тому

      Sanatubwe koma akunena zoona kwambili akuluwatu

  • @DennisKachele-z7b
    @DennisKachele-z7b Місяць тому

    Ukufuna upusise ndani badyerera paja anakupangirani sadakatu inu---- kukonda kusheta

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo Місяць тому

    Kulakhula kwambili mwalakhula bwino kwambili muthu wamkulu otsutsa boma palibepo akupanga athu akungodikila kuti akhale president akhala bwanji ngati makhasala akuluza chamba basi

  • @JosephMoyo-k2h
    @JosephMoyo-k2h Місяць тому

    Olo ikhazikike MCP ndiye mumpuza ndani

  • @Randy-er2xo
    @Randy-er2xo Місяць тому +1

    Achituma ichi😂😂😂😂 adad okalambawo 2025 akudzakulamula pusi iwe

  • @FrancisDay-br7xb
    @FrancisDay-br7xb Місяць тому

    Palibe chomwe ulankhula chakwera agula mavoti koma come 2025 sadzakwanitsa Malawi onse. Iwe galu anthu safuna afuna ulamuliro okomela onse

  • @Blessings-td4cr
    @Blessings-td4cr Місяць тому

    Akutumani ndi ayaniso inu musatinyasepo? Ingopephani inu,,iwe usatinyasepo wamva ifeyo tili kuno kulilongwe komwe kuli azako a MCP ukunenawo,,wadya zambiri za MCP anakupezawo.

  • @YaqoobStandwell
    @YaqoobStandwell Місяць тому

    Kod mcp kumwaza ndalama zosez akufunabe kuyimila ziko kumachita kut amalawi sakwafuna bas kufuna azingokubabe

  • @AustinChiyembekezo-cx4mz
    @AustinChiyembekezo-cx4mz Місяць тому +3

    Nanyongo wako mai iwe ...oipa anthu akumangochi dyela ....akalamba amako

  • @user-pe4ym8gm5s
    @user-pe4ym8gm5s Місяць тому

    DPP inapita ndimwini wache Bingu...

  • @BarwickSalanje
    @BarwickSalanje Місяць тому

    Inuso nanu mukulankhula zopanda nzeru mukuona ngati mukulankhula zanzeru

  • @Jordan-d5z
    @Jordan-d5z Місяць тому

    Uko ndiyekuyankhula anthu awa sakudziwa zomwe akupanga amangofuna azilemela okha

  • @AstrolManando-x6o
    @AstrolManando-x6o Місяць тому

    Zoonadi atsongoleli apngeni athunu saport

  • @Chiso2019
    @Chiso2019 Місяць тому

    Zikugonadi kwambili mbuzi zimenez...anthu kuyeseera kuwakonda but they are too selfish....chilichose kumangoti ku page house,akufuna misonkhano azikapangila ku page house komweko.....yachita bwn mcp ndipo tiyivotera...awa even akazalowaso mboma kupepera kwake kudzakhala komweku...

  • @AllieKaisi-je6rm
    @AllieKaisi-je6rm Місяць тому

    Awa sakuliziwa boma lolamula kodi saziwa kut boma lolamula limakhala ndikuthekera kowina mmene akufunira

  • @ShaliBasket
    @ShaliBasket Місяць тому

    Audio iyiyi ndiyowona anthuwa ifewo timawakonda koma za Ife saziwelengela popeza ndi anthu a ndalama zawo it's okay ifewo tifeyo tizivutika mene tililimu kaya azatiponya mu damu la ng'ona وا الله يعلم و احكم

  • @youmad9087
    @youmad9087 Місяць тому

    Peter wakalamba , chifukwa chache chisale azingomudyera mkazi wakeyo

  • @JamaniNyirongo
    @JamaniNyirongo Місяць тому

    Akutumani a mcp kuti muyankhule izi.
    Moti khansala ameneyo alamulira mpaka 2030? Nde mmene mwavotera mcp kudela limenero katundu watsika ntengo kumeneko?
    Manyaka amzimayi osavinidwa iwe.

  • @BwanaGD
    @BwanaGD Місяць тому

    Mwapaga nonkja dyera chifukwa Cha ufa ndi 5000 yochokera kugulu la chikagawa anthuwatu malamulo akuwadziwa musayelekeze ndi buli yachikagawayo akayayendaso tiyamba kunena kuti mwalawira kuyamba ka mpeni tinkhala tikulubwa zabili ndiye siku zipanizi sizikudziwa lamulo komano opupwa ndamalawi aku magochiwo komaso zoberazo

  • @ClementinaViola
    @ClementinaViola Місяць тому

    Mpaka kupanika kukhosi, 😂😂 bwanji osangonena kut mwamva kukoma chifukwa chot khansala wa MCP wawina, za ziii

  • @JohnGreen-v8f
    @JohnGreen-v8f Місяць тому

    Choka iwe usapusise anthu. Ndiwe wa mcp. Pasanapakoso

  • @ZioneMandala-n7h
    @ZioneMandala-n7h Місяць тому

    Nsalu zikutandizani chani moti muzimuuza chakwera wanuyo kuti asise zinthu bwanji

  • @KasimuKachingwe
    @KasimuKachingwe Місяць тому

    Simukunama mjomba ichi NDI chilungamo

  • @MercyGopani
    @MercyGopani Місяць тому

    Ndiiwe chitsiru aise. Ulibe nzeru

  • @KeffaBeseni
    @KeffaBeseni Місяць тому +1

    Fada iponde

  • @edsonphangula5817
    @edsonphangula5817 Місяць тому

    Amazipasa udindo
    Every time same leader the mtalika
    And the muluzi boring

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 Місяць тому +1

    Kkkk ayi mvuto ndinu anthu akumangochi nokha sikudziwa kuyipa komvotela mcp mene wawonenfila chakwela paka kupasa khasala nde mumafuna a dpp ndi udf akuwuni kuyipa kwa mcp aaa pena anthu akumangochi mumawoneka ngati ochenjela kuma ayi tulo basi mafumu dzisilu nde mumati udf olo dpp adzikuwudzani dzochita kkkk khasalayo wachitawo wangalusa apa kulusati aku paka mcp amangochi kukodze nyumba ayu dyela kwambili nde mcp akusangalala ndi uchisilu wanu achiyawo dzikani dzukani

  • @user-yu4np2wq4s
    @user-yu4np2wq4s Місяць тому

    Galu wamunthu wadya ndalama Za amcp

  • @user-gs7wc3nx3q
    @user-gs7wc3nx3q Місяць тому

    Basi tiyeni tizingovotera mcp iyo tizivutika tose tizifa tose chocho

  • @user-tb6yh1kx3o
    @user-tb6yh1kx3o Місяць тому

    DPP ikugonadi kalindo amayankhula kale

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl Місяць тому

    Machende anu mwadya za mcp ayao wophusa adyela

  • @user-xd6hq1pp4d
    @user-xd6hq1pp4d Місяць тому

    Mbuzi yamuthu palibe nzelu kd ndimamuna nkaz sindikumvesa

  • @user-cf9yz3ei5o
    @user-cf9yz3ei5o Місяць тому

    Peter mutharika is too old we have said. this several times

  • @NtakumbaNtara
    @NtakumbaNtara Місяць тому

    Wayankhulayu akundinyasa ngati manyi ake

  • @FrankKambwani
    @FrankKambwani Місяць тому

    Opepera ndinu ayao akugulitsani fertilizer k110 000

  • @JohnAsendi
    @JohnAsendi Місяць тому

    Inu ndi zisiru izi zakalamba sizikufuna tikungozikakamila tizijowa zikungotimanisa zabwino palibe zoti atibela tulo takale ndiye akundinyasa pomwe ndikuwaonapo

  • @user-og4oe5yp4w
    @user-og4oe5yp4w Місяць тому +2

    Zoona peter ndi atupele atilakwira komanso atikhumudwitsa 2025 atisamalenso tikonza kugulitsa mavote athu.ku MCP komweko anthu amenewo angokhala duuuuuuuu

  • @MussaMasuku
    @MussaMasuku Місяць тому

    You're alright my friend

  • @mcsellahntv6896
    @mcsellahntv6896 Місяць тому

    Nde nchawadi, kulalata choncho, wakwiya.

  • @martinnyirongo2892
    @martinnyirongo2892 Місяць тому

    Zamwanyazi kwambiri, umbombo zipani izi, akati tiyeni tikamwe tea ku page house eee amayenda chothamanga

  • @JamesChimera-hw1nv
    @JamesChimera-hw1nv Місяць тому

    Mumadana ndichilungamo

  • @JulietKapata
    @JulietKapata Місяць тому

    Tiyeniko inu akutumani inu munganene chani choti mungafokese anthu za ziiiiii.wakula chani

  • @user-vm7iz6oz6r
    @user-vm7iz6oz6r Місяць тому

    Aaa mayi inu mwadya zambili mufuna mumupheso

  • @ishmaelbonomali7303
    @ishmaelbonomali7303 Місяць тому

    Iweyo ukunenawe akutuma Iweyo udali kuti?

  • @PempheroMoleni
    @PempheroMoleni Місяць тому

    Mbuzi iwe wadya ndalama za mcp

  • @LindaTebulo-k4w
    @LindaTebulo-k4w Місяць тому

    Vote ili mumtima hiyaaaaaa

  • @NicholasMackinnah
    @NicholasMackinnah Місяць тому +1

    Zopusa basi zangondionongela bandle

  • @ModicaiChirwa
    @ModicaiChirwa Місяць тому

    Komatu atupeletu samakakamiratu izi komanso kuyankhula koteroko mbali ina siukuyankhula bwino wadyera ndiwe anthu samapanga ndalama ndicholinga Choti azikupatsani zaulele ayi nawo alindimavuto awo komanso kuyankhula kopusa ukuayi anzanu amafuna kuona kuti kubera kwao kuzayambapati ndiye paoneka iweyo ngati wapatsidwa ndalama galu iwe uona kuti anakutumawo akuonedi

  • @AiwaMedia-sh6vx
    @AiwaMedia-sh6vx Місяць тому

    Amayiiiineeeeee!!!!
    Palibe angati NYO-NYO-NYO pazimene mai ayankhulazi. Opposition you are very pan'yeroful. Simuyitha MCP mungovomeleza you are useless. Ife aMalawi obsauka ndiimene tikuvulala. You are stupid the Opposition,

  • @SumanPhunzirod
    @SumanPhunzirod Місяць тому

    Wasowa zochita zandalama funsa chakwara hule tsek

  • @MussaSamuel-vm5ry
    @MussaSamuel-vm5ry Місяць тому

    Chakwera anakupatsan ufa watha apa mwayamba kuliraso chokan agalu inu mukusokosa mesa mwavota kale pasana pako

  • @Freedomchennl47
    @Freedomchennl47 Місяць тому

    Izo ndizoona agalu awa ndiokwana ine nde anandibhowa kale

  • @GoodsonLindani-gf8pn
    @GoodsonLindani-gf8pn Місяць тому

    Kodi kudula kwa zinthu akukuona ndi APM ndi ATUPELE Masa ndianthu njala, kusowa mankhwala, ana kulephela kupeza school fees, akuona ndiamene ukuwanenawo.muziganiza pofuna kulankhula,dyera anthu akumangochi.

  • @CarolineMukhova
    @CarolineMukhova Місяць тому

    Chomwe akuyankhula sakuziwa Chakwera adaononga almost 5million kuhonga wanthu koma MCP no more 2025

  • @GiftSoko-w4h
    @GiftSoko-w4h Місяць тому

    Vuto ndinu Anthu Akumangachi osavotela Adadi bwanji uligalu kwabasi inu simumaziwa kuti mukuvotela MCP dyela mangochi

  • @saidiwilliam9832
    @saidiwilliam9832 Місяць тому

    Umphawi wamukwana uyu zisiyeni inu azelunu bapangani kampeniyo

  • @SueWahna
    @SueWahna Місяць тому

    Inu kuvutika ukuku mkofuna kuteroko adad akusekan paja mumkat mukufuna kusitha pitilizan kusithako atifinyadi ana osamva inu

  • @joaquegerman2250
    @joaquegerman2250 Місяць тому

    Koma. Munthuyu akuyankhula chilungamo

  • @RAJABSTYLESTYLE-yi1el
    @RAJABSTYLESTYLE-yi1el Місяць тому

    kusonyeza kuti nonkha simukuwona mumafuna akupangileni kapeni

  • @RamadanShafisha
    @RamadanShafisha Місяць тому

    Ndiye vuto la zipani za pamtundu kkkkkk

  • @arafatMtyala-bo8ev
    @arafatMtyala-bo8ev Місяць тому

    Alakwa ndinuyo achina kinka makoloni