Atupele Muluzi; Munamulakwira lenala kumpatsa Bus kuti ayendetse."

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 15 вер 2024

КОМЕНТАРІ • 54

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 7 місяців тому +5

    Atupele umaona patali brother vuto amalawi kusanva mmmm lelo ndizi chigoba chamadeya 4500 kkkkkk

  • @JohnConar-kq4hi
    @JohnConar-kq4hi 7 місяців тому +1

    Muthalika ndimachini big up bakili muluzi tv📺

  • @jacobranuga
    @jacobranuga 7 місяців тому +3

    The only our last hope of Malawi

  • @lyiemax
    @lyiemax 7 місяців тому +1

    Powerful speech, the only hope for malawians

  • @kennethmakweya3561
    @kennethmakweya3561 7 місяців тому

    Prophet speech..
    Apm my vote

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 7 місяців тому +3

    Kusamva A Malawi Lero chakwera wagwetsa bus wánthu a vulala

    • @MahometAli-e8w
      @MahometAli-e8w Місяць тому

      Kma Atupele ni munthu amalosera kma vuto ni anthufe timati azapanga zimene anapanga abambo ake kma sizili choncho onani peter mene anayendetsera dziko kuposa bingu zinthu zimasintha

  • @christophermkhize1991
    @christophermkhize1991 7 місяців тому +2

    Koma ndiye ankanena zowonaditu amalawi tinalakwitsa kumpatsa lenala

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 7 місяців тому +3

    APM my vote ❤❤❤❤❤❤❤

    • @MahometAli-e8w
      @MahometAli-e8w Місяць тому

      Naa Chakwera nde bola Atupele

    • @MahometAli-e8w
      @MahometAli-e8w Місяць тому

      Even Mutharika Atupele ali ndi experience to think fast

    • @RiteRoderick
      @RiteRoderick Місяць тому

      @@MahometAli-e8w Zoonad kwambiri ndithu brother

    • @RiteRoderick
      @RiteRoderick Місяць тому

      @@MahometAli-e8w Zoonad kwambiri eishiiii Chakwera mfitiyi mm

  • @chipiliromalola6380
    @chipiliromalola6380 7 місяців тому +1

    That's fact

  • @emmanuelmpenda2673
    @emmanuelmpenda2673 7 місяців тому

    Prophetic

  • @JohnJohn-og8rt
    @JohnJohn-og8rt Місяць тому

    Aliyese awona tiwonaso 2025inshall allah tupere ulamulire

  • @VicterSparter-uu7ej
    @VicterSparter-uu7ej 7 місяців тому +1

    Zooona😊

  • @ConfusedFlamingos-rz9hw
    @ConfusedFlamingos-rz9hw 7 місяців тому +1

    Uku ndiye kuyankhula kogwila mtima, kuyankhula kwachikoka kwa usogoleli sizina.mmmmm koma kugula mafumu ma venda.heeee waiona yekhweeee

  • @kubengovender6996
    @kubengovender6996 7 місяців тому

    Big up brother man!!

  • @LotiMilanzie-qj7ek
    @LotiMilanzie-qj7ek 7 місяців тому +1

    Nkhalamba ndi nkhalamba basi singasinthe kukhala mnyamata, ndi chimodzimodzi ndi MCP

  • @EmmanuelGordon-q9s
    @EmmanuelGordon-q9s 7 місяців тому

    Koma nawo angoyankhula.. politicians are just the same

  • @ChristopherKabanga
    @ChristopherKabanga 7 місяців тому +1

    Adali ndi fundo ndi bambo awo awazonena alibeso athawira ku dpp

  • @asiyatujuma5507
    @asiyatujuma5507 7 місяців тому +1

    Kkkķkkk zoyonadi ❤❤

  • @longimtimabii1017
    @longimtimabii1017 7 місяців тому +1

    Amanena zoona ndithu

  • @robsontyg3928
    @robsontyg3928 7 місяців тому

    Dzimachende dzanu achawa, chomwe mmadzi ndikuchapa kumatako

  • @user-pi8gu3zw4f
    @user-pi8gu3zw4f 7 місяців тому

    Ndkuonamo tsogolo mwaiwe atupele,ndpo chikhulupililo chathu amalaw chomaliza taika mwaiwe.ndie usazatikhumudwitse mfundo zako zogwila mtma zed

  • @greychizaka4088
    @greychizaka4088 7 місяців тому +1

    Uyuyu koma samandiwaza wakhala chete malawi ikuvutika nde lero ukutulukano.. atupere ekha nde ai

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 7 місяців тому

    Mudakali mukulira mpaka 2035 woo chakwera akulamulira zanu izo zi fit inu

  • @ConlardNkhoma
    @ConlardNkhoma 7 місяців тому

    Cholinga ukufuna pitala ankadzawina uzabwerepo ndimwe ndi yellow yako

  • @albertbello8067
    @albertbello8067 7 місяців тому +1

    Tsono yemwe sanali lenala ndiye anamuchotseranji anthu?😅😅😅😅

    • @sheikhjaffarwhyte2688
      @sheikhjaffarwhyte2688 7 місяців тому +2

      Umbuli wa anthuwo dyera ndi nkhwidzi... Lero siizi Chakwera angowowozedwa ngati chitsiru

    • @ephraimchigamba
      @ephraimchigamba 7 місяців тому +1

      MCP inaberekedwa ndi Akhothi..

  • @user-mz8nw6nx6p
    @user-mz8nw6nx6p 7 місяців тому

    Tipaseni update ya South Africa ICJ ndi Israel

  • @AustinHamisi
    @AustinHamisi 7 місяців тому

    😮L

  • @collennyadile8179
    @collennyadile8179 7 місяців тому

    mcp singasinthe or zitavuta maka nkhanza zoyamwira APM ndikaswiri pa utsogoleri

  • @VICTORKANYENDA-gf9xt
    @VICTORKANYENDA-gf9xt 7 місяців тому

    How to be an experienced person, m'mesa umayamba ndi ulenalawo,iwe atupele,Malawi is not ur father's Farm,of course ur was the president of Malawi, ndiye iwe ukufunaso upresident, Malawians have opened their maso ndi makutu,Malawi isn't ur farm

  • @johnw.posomanchanel4023
    @johnw.posomanchanel4023 7 місяців тому

    mcp ndi chipani choipa

  • @memorygondwe1635
    @memorygondwe1635 7 місяців тому

    Anatiwonongela ufumu wanthu WA Kwa chikulamayembe

  • @Moses51
    @Moses51 7 місяців тому

    🎉🎉🎉🎉

  • @user-dq9pz1nv2x
    @user-dq9pz1nv2x 7 місяців тому

    🎉

  • @harrymicah6140
    @harrymicah6140 7 місяців тому

    😂😂😂😂 eee zamuvutati

  • @BkZikawe
    @BkZikawe 7 місяців тому

    Muluzi anapatsa Bingu lenala

  • @Alabu-g6i
    @Alabu-g6i 7 місяців тому

    Apm boma

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj 7 місяців тому

    Zandale izi anthu awa sungawakhulupirire

  • @MuhammadBAKILI-kl2mj
    @MuhammadBAKILI-kl2mj 7 місяців тому

    Mbambande bwana

  • @harrispheleni2205
    @harrispheleni2205 7 місяців тому

    Cadet Yako ija uchira

    • @ephraimchigamba
      @ephraimchigamba 7 місяців тому

      Utachile ndiweyo mbuzi yako ingowowozedwa ikamayenda😂😂😂

  • @user-xc1xt2qd7t
    @user-xc1xt2qd7t 7 місяців тому

    Zoonad

  • @OFG-th3st
    @OFG-th3st 7 місяців тому

    Best TV🔥🎮

  • @MjombaMjuba
    @MjombaMjuba 7 місяців тому

    Za manyi

  • @LotiMilanzie-qj7ek
    @LotiMilanzie-qj7ek 7 місяців тому

    Nkhalamba ndi nkhalamba basi singasinthe kukhala mnyamata, ndi chimodzimodzi ndi MCP