Surprisingly, it is the rich that go for family planning and yet those who are struggling keep on having more children without following kulera. Look now, 7 children without a father, this should change. Tisalemetse anthu oti sizikuwakhuza
Samazuzula munthu Ali mu coffin it's like kuyimba nthungululu pa maliro zikatere timangopepesa ndikupereka thandizo ngati lilipo kenako uphungu ine ndinu anzeru ndi ozindikira komano mudzidziwa kuti ena amaphunzira atalakwisa ofcoz am not intending to jump your point mukanalangiza izi zisanachitike osati zitachitika muzikhala ndi chisoni ndemanga mwapelekayo palibe kusiyana ndi. Kumapasa mbama munthu amene Ali pa oxygen
Congratulations to you mr good job mulungu azikudslitsani kwambiri dziko lino munakakhala anthu ngati inu zinali bwino iwe ndithu utankhala president dziko lintha kusintha
Man mulungu akudalitsen mwawonetsa mtima wacikond km kwaenafe likhale phuzilo zobeleka ana ambirimbiri ndizakale ndibwin kukhalanawo awiri or modzi bas
Ambuye chifukwa chan ndimalephera ndikukuthokozan komwe pazochepa zomwe mwandipasa ,,,😢😢😢😢😢😢 ndisithen ambuye ndikuziwen inu muzimu ndimuchonad mayi ineee😢😢😢😢😢😢😢😢
Ndipo inu ,Ambuye atithandize ndithu
@@AngellaZawanda 🙏🙏🌹
Surprisingly, it is the rich that go for family planning and yet those who are struggling keep on having more children without following kulera. Look now, 7 children without a father, this should change. Tisalemetse anthu oti sizikuwakhuza
Muziyankhula bwino plz
Sakunama..nanga munthu ulibe thandizo ana onseo uzitani nao.
Samazuzula munthu Ali mu coffin it's like kuyimba nthungululu pa maliro zikatere timangopepesa ndikupereka thandizo ngati lilipo kenako uphungu ine ndinu anzeru ndi ozindikira komano mudzidziwa kuti ena amaphunzira atalakwisa ofcoz am not intending to jump your point mukanalangiza izi zisanachitike osati zitachitika muzikhala ndi chisoni ndemanga mwapelekayo palibe kusiyana ndi. Kumapasa mbama munthu amene Ali pa oxygen
Azlimayi timakumana ndi zinthu zowawa koma eish timapilira munyengo zowawawisa mulungu adalise azimayi onse pachisaliro chomwe amapereka kwa ana awo 😢😢
Kma Rodwell Lumbe Mulungu adzikudalitsa kwambiri 🙏
Kumalawi kuno kuli umphawi wadzaoneni,God bless you rodwell
Choyamba mayiwo akaseketse Kaye ana achuluka
Ndipo inu eish
Akatseke bwanji?sabelekanso mesa amuna anamwalira.
@@SinyoroMoyosakwatiwaso?
kkkkkkk
Zikomo ambuye chifukwa chazabwino zomwemumatipangil adalisen Bambo alordiwel
May God continue blessing you Mr Rodwell for reaching out and the hand given
Congratulations to you mr good job mulungu azikudslitsani kwambiri dziko lino munakakhala anthu ngati inu zinali bwino iwe ndithu utankhala president dziko lintha kusintha
Rodwell My God bless you keep it up
Komatu mayiyu ngosamalila ana ndiovutika koma ana akuoneka osambako
Ndithu kukuuzan,zovalaso zowoneka 😢😢😢😢😢😢😢
Ndipo akuoneka ana health mulungu ndiwodabwisa samana zonse
Eshii ambuye sithani nyengo zamai yu ndiinu osamala ambuye
Inuyo ntchito mumaigwira mulungu azikusogolelani Lodwell❤❤❤❤
Linyangwa that's my home village and I was working at Linyangwa health centre from 2010 to 2014 before posted to Dedza DHO in November 20214
Uncle aRodwell Ambuye akulitse malire anu ndipo Ambuye akudalitse afikire zokhumba zanu komanso kukutetezerani pa ntchito yotamandika yomwe mukuyigwira 🙏🙏 Almighty GOD bless uncle Rodwell 🙌🙌
Keep it up my brother may god bless you ❤❤
Koma Rodwell mulungu akudalitse pofika police kutumiza anthu kwaiwe dziko likukudalira ndithu mulungu akuze malire ako❤❤❤
Mulungu akudalitsen rodwell
You are doing a wonderful job
Mmmm mulungu zikomo pa zinthu zomwe mmatipangera mulungu inu mkule ine ndichepe nthawi zonse😢😢😢😢😢😢😢😢
Big Up brother ❤❤❤
Ambuye achitilen chifundo amai awo ndi banja lawo chitilan chifundo moyo wanga ambuye ndichikhumbo khumbo changa kut mutandidalitsa kut naneso ndizadalitseso athu ena monga momwe akuchitila mr Rodwell
Bwana wazolengedwa zonse mudzimusamalira Rodwell mkupatsa moyo wautali
Kumwamba kulandile ulemu🙏🙏 mwagwira tchito yaikulu
Big man mulungu adzikudalitsa ndipo akupatseni moyo wautali
Zikomo ambuye 🙏 pachilichose chomwe mumandi pasa ngakhale yena amatichochepa km kwaine chokwanila kwambili ndithu 😢😢😢😢
Ngakhale sindikukuziwani koma mulungu aonjezele ppamene mwachosapo ❤🎉 achimwene
God 🙏 bless you bro work hard on ❤❤
Eshiiii kma ambuye😭😭😭😭😭 anthu kunjaku akuvutika ndithu! Ayendereni ndipo muwakhuze ndizanja lanu lamadalitso monga mnachitira pa tenafe posintha nyengo zathu😭😭😭😭😭
Ambuye azikudalitsani thawi zonse pa tchito yomwe mukuigwira achimwene
Rodwell 🙌🙌🙌 may God bless you more.
zomvetsa chisoni anthu akwanthu ku Dedza kwa chidewere..kwa kanyenzi ku chikoma😢😢😢
Wawo kanyezi lknow the placr
Mul utumiki mwa inu
Tiyeni tigwirane manja powathandiza mayiwa Kuti mwina angayambeko business Kuti azipeza thandizo latsikundiku komaso tithokoze Mr Rodwell APA zaonetsad Kuti iwowa ndimzika yeniyeni yaMalawi yosadzikonda ambuye azikudalitsani malume
Esh god continue to bless you brother
God bless you more and more blessings to you brother
Ndakumbukila masiku omwe ndinkadwa feya ndidabwerela kwamayi 😢😢😢
May God bless you for helping people.
I wish nditazakumana nawe Lodwel... May God bless you
mulungu inuyo adzikudaritsani bro
Ambuye ndikozeni ine
Komatu pena umphawi timachita kuusaka pa Ana 4 okhawo amenewo ndimavuta kale.ndiye nkuonjezeranso atatu ? Pena pake kungosakha kuzuzitsa Ana...
Rodwell mulungu akudalisani
Rodwell God bless you, all the time 🙏
Pepani kwambiri Mulungu akutsogolerenizabwino zonse,komadi anthufe tiri pamabvuto owopsya zedi.
Rodwell mulungu akuwonjezere masiku ambiri.usazafe
Only God know
Eishiiii Koma Rodwel iweyoooo???? 😢mulungu akupatse moyo ,mphavu ,zelu zochuluka .komaso akuze malile amoyo wako ngat momwe anamuchitila yabesi.chifukwa Anthu tikuthandizika .mulungu akudalitse ndithu
Imfai 🙌
Ambuye daritsani banja limeneri kopotsa Amen 🙏🏽
nde who's feared dead apapa im lost
Eish koma abale tiyen tidzilela plz izizi tu sizabwino eish mukuzutsa ana taonan iii asabelekeso yi
Gus job , be blessed
Mulungu awonjezere pomwe mukuchotsapo Mr ..
Komaso penapake tiziti kupolice or kuwagulilako gwaladi anthuwo inde sindikukana anawathandiza komabe
Eeeish ndalira kobas,, koma ambuye awalitse maso ake pa inu asinthe nyengo zanu kut anawa aphunzire,,,
Koma pali ana mmmn, God have mercy 😢
Big up Rodwell❤❤
Mulungu ndiwazatheka bwanji
God bless you Rodwell
😢😢😢 chonena ndilibe
Mulungu akudalitsen
May God Bless you Rodwell
Ambuye mupaseni Rodwell moyo wautali
Rodwell Ambuye akuze malire ako
Ambuye azikudalitsani ndikuchulukitsa pazomwe mumachotsa pakuthandiza kwanu
Nanuso my kumangobereka ana choncho lero taonani
You should be our president buddy
Mayi woziwa kusamala ana ,ana sakuwoneka kuthimbilila
Akuru Mulungu apitilize kukuza malire anu God bless you
Man mulungu akudalitsen mwawonetsa mtima wacikond km kwaenafe likhale phuzilo zobeleka ana ambirimbiri ndizakale ndibwin kukhalanawo awiri or modzi bas
God bless you bro and Citizen
Ambuye akuze malire anu pa ntchito yambwino yomwe mukugwira
Mayiyu ndiokonda ana ake
Koma Rodwell usazafe iweyo God bless you 😢
Allah bres you
Amuna anu kumwalila osawauxa akuchimuna zoona ?
Komanso mwini farm akuyenela kufikilidwa atiuze chifukwa chani sanadziwitse achibale za imfa ya tenant wawo
Koma bambo ameneyo/malemuwo amampanikiza mkaziyo samapumayi, zaka zomwe anakwatilirana nzochepa koma ana mpweche iiiìì chisoni.
May God bless you rodwel.
Km moyo uuu ndi ozunza mmm rodwell mulungu azikudalisa ukugwira ntchito yotamandika ambuye akuze malire amoyo wako
God bless you Rodwell❤❤
Mulungu azikudalitsa Rodwell Lumbe Mmmmm anthu akunvutika
Komano bwenzi akulera😢
Anthu akuvutika awa Koma president maulendo achuluka bwana tawathandizeni Mai awa pls kubomako
God bless you alot Mr
Mulungu tsegulani khomo la Make Ndaziona
Zosayenda
Eeeeeeeee😭😭😭😭😭😭
May God keep on blessing u
God bless you Mr lumbe 😢🙏🙏
God help people through people we thank God
Ambuye ngati sindimayamika ine muzindikhilulukira😢
May almighty God bless you rodwell
God bless you 🙏 mr
Komatu nkhani yokhudza kwabasi
Zoonadi Allah azikuwonjezerani
Eee zithusizilibwino
Ambuye azikuzabe malile anu Mr Rodwell ntchito mukuigwila kuposa apresident
Km abale dzikoli anthu akuvutika ambuye chonde tichitileni chifundo ,, ndipomwe chakwela president opanda nzeru akungoyendayenda kuononga ndalama pomwe anthu akuvutika chomchi ambuye mumuchitile chifundo chakwela sakudziwa chomwe akuchita
Ambuye 😢😢😢
Eish koma dzikoli anthu akuzuzikatu
God bless you Rodwell eee