NKHANGA ZAONA ANTHUWA AKUCHITA NGATI MAWAYA ADUKA MMUTU CHIFUKWA CHA MZIMA WA BHIYENI

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 15 вер 2024

КОМЕНТАРІ • 92

  • @NizigiyimanaChantal-c2p
    @NizigiyimanaChantal-c2p 9 днів тому +16

    Yesu wandigometsa ine amadziwa mawa langa akudziwa dzulo lathu more fire❤❤❤❤❤

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b 9 днів тому +10

    😂😂😂😂😂 Ulemu wanu abusa pemphero lamphambvu Mulungu akudalitseni ndipo Mulungu ayankhe pempherori

  • @daviskamonde4882
    @daviskamonde4882 9 днів тому +8

    Your journalism is so sweet and professional!!

  • @cynthiandekhakatundu6890
    @cynthiandekhakatundu6890 9 днів тому +17

    Akataya black box Timanga Kunkuyu chifukwa tili ndi umboni woti black box ilipo ndipo yasungidwa pa malo abwino . Ndiye akungozivuta akayankha ku Court

    • @AngolanChinga
      @AngolanChinga 9 днів тому +1

      Thank u brother kumenek nde kuyankhula ndithu

    • @SydneyMwale-u9w
      @SydneyMwale-u9w 4 дні тому

      Kunkuyu ali nayo black box umboni tili nawo mokwana ndipo akataye aona ndithu

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b 9 днів тому +7

    God is watching agwidwanso kokataya black box ko yakwiya ndi mizimu palibe chinsisi pa dziko lapansi, chilichonse Mulungu akuchiyika poyera

  • @OssmanAbubaker-y3z
    @OssmanAbubaker-y3z 9 днів тому +10

    Ulemu wanu Mr Ntanyiwa zoonadi MCP ndi anthu oipa tinapanga mistake povotera MCP

  • @DalitsoMatope
    @DalitsoMatope 9 днів тому +6

    Mtengo otchedwa Malawi congress party uwume ndinthu chipani chimenechi chife tisazachiwonenso mudziko lanthu lino

  • @esaMoha-dm4kj
    @esaMoha-dm4kj 9 днів тому +6

    Mr president mtanyiwwa tinankusowat mulipo kd ngat mulipo ulemu wanuw osawopha osavowonka amalawi 2025 mcp nkulibe osasiyya mpanka 2025 Mr mtanyiwwa yendani limodsi mpanka 2025 osaphasa mphata ameneyyo

  • @DavidMbewe-v1r
    @DavidMbewe-v1r 9 днів тому +5

    Adad pali ka coffee ☕ tu apa ❤❤

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 9 днів тому +4

    Koma pemphero ili ndiakatundu 😂😂😂😅😅😅😅😅😅😅😅😂😂🎉mtengo wanji umeneu kodi unauzala ndiwe Chikangawa,Silimangeni,😅😅😅😅😂😂😂amayo kotoooTobiyasi 😅😅😅😅😅😅😂😂😂😅

  • @TopoTopo-bm4vw
    @TopoTopo-bm4vw 9 днів тому +5

    Kkkkkk😂 agwanayo a MCP sichipani

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 5 днів тому

    Koma Ntanyiiiiiii iwe aaaaaaa ndagoma nawe iwe ndi more🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥❤️❤️❤️❤️❤️❤️😊

  • @scoltenroma6240
    @scoltenroma6240 9 днів тому +4

    MCP chipani chosavuka kwambiri,they don't know what's all about politics in the world of Democracy

  • @ChimwemweLiwonde
    @ChimwemweLiwonde 9 днів тому +10

    Angwa nayo bas asomva

  • @MangaDamiano
    @MangaDamiano 9 днів тому +4

    Yahweh tetezani ziko lamalawi

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 5 днів тому

    Ulemu wanu Abusa pemphero ili wina akupsa nalo mdipo miseru nthawi zonse akamva pemphero ili iiiii Mulungu si Jems ai aimilira nyengo zonse zimasintha akatsegura palibe amatseka akaseka palibe otsegura uyo ndiye Yehova amapanga zake popanda opikitsana nae Ulemu wanu Ntanyiwa 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @RoseChimbwefu
    @RoseChimbwefu 6 днів тому

    Ulemu wanu Mr ntanyiwa umatiyimira more 🔥

  • @user-ky4ce9gb6j
    @user-ky4ce9gb6j 5 днів тому

    Limpopo fm ndi best mmm oyes

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 9 днів тому +2

    😂😂😂 pemphelo la mtengo opangitsa ngozi kumalawi

  • @MariamJaffali
    @MariamJaffali 9 днів тому +4

    🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥ntanyiwa mumakwana kkkkkkkk kuyaluka basi chikangawa ❤❤❤❤❤❤❤

  • @louismagongwa
    @louismagongwa 9 днів тому +3

    😂😂😂😂😂 mzimu wa chilima uziusabe mu mtendele ndithu thawi zina mulungu amalolela kut zithu zichitik cholinga tidziwe ukulu wake apatu mcp ikuyaluk wez wez akuzikola okha okha mwaona mwazi wa muthu sungapit pachabe chilima anapangilidwa misa 11 mukuona ngat zingapit pachabe zimenez😢😢

  • @VincentMagriva
    @VincentMagriva 9 днів тому +1

    Mntanyiwa ndipo iweyo nd one kulibenso kumalawi we love you ❤❤❤ and we like you ifeyo tikhala tikupenphela kuno mpaka chilungamo chiziwike

  • @OsmanMasamba-ck4mo
    @OsmanMasamba-ck4mo 9 днів тому +2

    Muwauze kuti simataika chifukwa olo m, madzi samaiononga BLACK Box

  • @lyiemax
    @lyiemax 9 днів тому +1

    Proud of you comrade 🔥🔥🔥

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire 9 днів тому +2

    Kumangidwa basi ,amphasi anagwidwa NDI kokeni mesa amanangidwa lamulo NDI lamulo basi kumangidwa basi

  • @SydneyMwale-u9w
    @SydneyMwale-u9w 4 дні тому

    Lakatula mntanyiwa osaopa osafok a 😅😅😅😅😅❤❤

  • @AnaLourencokan
    @AnaLourencokan 9 днів тому +3

    Allah...bless .you.....we .Love...you❤

  • @IdahBanda-z8u
    @IdahBanda-z8u 4 дні тому

    Amen

  • @BigBangalala
    @BigBangalala 9 днів тому +2

    Big huzihu ndinamunguridza garimoto audi Q5 yawayinti panopo ayizinda ndi antira penti waredi zanandi pase ndara yanga ntingwizana pantengo mk 10 million anapeleka mk 8 million kuzala mk 2 million ndimanti munditandise big ntanyiwa plus

  • @AnaffSayamika-uh6vg
    @AnaffSayamika-uh6vg 9 днів тому +2

    Aziwona amenewoooo

  • @DigleDafter
    @DigleDafter 9 днів тому +1

    Chikangawa yo mweyo bas😂😂

  • @MussahWilliam-py1ff
    @MussahWilliam-py1ff 9 днів тому +2

    Pemphero lanji ili kkkkkkkk😂😂😂

    • @OsbertMwanyali
      @OsbertMwanyali 9 днів тому +1

      Ati mtengo ovula anthu nsapato ndi nsokosi

  • @KondaniPhiri
    @KondaniPhiri 7 днів тому

    😂😂😂😂😂. Inuyo. Bwana. Mumakwana. Kkkkk. ❤

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 9 днів тому +1

    Kkkk Ntanyiwa we need to talk,I like that

  • @KelvinJpchimphepo-sh6nc
    @KelvinJpchimphepo-sh6nc 7 днів тому +1

    Kusava achewa ndinu osava kwabasi, ndinava kut mkamapita kokavota mpaka mmatenga ndi ana omwe kukavota, bakili muluz ananena msavotere kokoliko lero ndiiz wina so ananenapo kut msavotere mcp mmmm vuto ndinu achigawo chapakat mmanena kut chigawo chapakat sipanakhare president lero ndiiz, sonu mtivere ife akumpoto nchifukwa ndinu anthu osava kwabasi, ndipo nonse vot yanu muugwire kaye msavote ulendo uno tikusakhiren oti mmuvotere mwalephera kusakha bwino, zikoli atisogolere ankaz kaye

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire 9 днів тому +2

    Mtengo womwewo unakhoma ma 6 inches achina Gadama kkkkkk Mtengo Iwo Mtengo Iwo kkkkkkkl,abare kambitseni mbutsayo ungasowetse Mtengo 🙄🤣lol🦎🦎🦎🦎🦎idzo

  • @TressLuka
    @TressLuka 9 днів тому +1

    Game on Mtanyiwaa 😅

  • @user-je8jm5uy1q
    @user-je8jm5uy1q 6 днів тому

    Mwazi wa anthu 9 sungapite pa chabe yudasi ndi anzake onse akhala pa ntunda

  • @HastingsKambalame
    @HastingsKambalame 6 днів тому

    More fire mr ntanyiwa

  • @RonaldodalitigerSpencerDaliRic
    @RonaldodalitigerSpencerDaliRic 8 днів тому

    kkkkkk iweyo comrade ,unabwera kudzakhalad

  • @user-pk6vq1cr1b
    @user-pk6vq1cr1b 9 днів тому +1

    Kodi anali angati ma Blackbox?mesa kunkuyu akuti ilipo ili malo abwino,nsono imene ikukatayidwayi ndiyiti imeneyi

  • @ThomasMlowoka
    @ThomasMlowoka 8 днів тому

    More fire 🔥🔥 Limpopo 💪💪

  • @Linda-r6w
    @Linda-r6w 9 днів тому +1

    Ma plan awo ndiokataya usiku anthu atagona anyani amenewa atikwana bwanji???Mtanyiwa keep it up ayaluke amenewa

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire 9 днів тому

    Amen Amen abusa moto Kuti bhu!omweuja wa MCP mtengowache🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🤸🤸🤸🤸🤸🤸🤸☑️

  • @JulietKapata
    @JulietKapata 9 днів тому +1

    Ndipo mtengo umenewo mmmmh 😢😢😢

  • @cynthiakananji1608
    @cynthiakananji1608 4 дні тому

    Akangoitaya pa nthaka yamalawi black box izapezeka

  • @AuphieBannet
    @AuphieBannet 8 днів тому

    MULUNGU ayakhe pephelo limeneli 🤲

  • @ChisomoBanda-g5s
    @ChisomoBanda-g5s 8 днів тому +1

    🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤❤

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire 9 днів тому +1

    Atate chotsani chakwera ndipo tikudziwa imfa dzikuchitikadzi tsidzikutsangalstani,

  • @BettieNickson
    @BettieNickson 6 днів тому

    Ana achepa 😂😂😂

  • @KelvinJpchimphepo-sh6nc
    @KelvinJpchimphepo-sh6nc 7 днів тому

    Anthuwa ndi wopanda nzeru kwambili

  • @KINGSLEYDINIWA
    @KINGSLEYDINIWA 9 днів тому

    Koma Ntanyiwa we need to talk I like that by the way, we remember very well with Mr kumkuyu by saying that Bkackbox ilipo yasungidwa pabwino ndie akataya chifukwa chani,, kumkuyu udzayankha mulandu oopsya.

  • @user-zk7jw9up6m
    @user-zk7jw9up6m 9 днів тому +1

    Umakwana mtanyiwa

  • @Mphangala
    @Mphangala 8 днів тому

    Palibe kubisala pa dziko lapansi

  • @MiracleMalichi
    @MiracleMalichi 8 днів тому

    Mzimu umodzi umakuzunza kulili mizimu 9 yosalakwa ingalephere kukuzunzunza chakwera ndi bushiri wakoyo

  • @ChifundoNkhoma-x7p
    @ChifundoNkhoma-x7p 9 днів тому +1

    Ntanyiwa ndi kawawa

  • @NgeyasjuWadeya
    @NgeyasjuWadeya 6 днів тому

    Kungosintha boma mbuzi zonse pachingwe

  • @user-hs2dw7ly2c
    @user-hs2dw7ly2c 8 днів тому

    Please Ntanyiwa we love you without you we are nothing

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon3429 9 днів тому

    More 🔥 tanyiwa

  • @MustapherDavie-su3nk
    @MustapherDavie-su3nk 9 днів тому +1

    Mcp the killer party

  • @MerryWayson
    @MerryWayson 9 днів тому +1

    ❤❤❤❤❤

  • @BlessingsMakalani
    @BlessingsMakalani 9 днів тому +1

    Apa anaganiza ngat ana kuchosa black box

    • @KawawaIbrahim
      @KawawaIbrahim 9 днів тому

      Ndipo inu bolanso mwanayo mwamva,imene ija ili ngati track olo kukwirira pansi imaonesa mu system kuti ilipakuti

  • @Alice-z7t4z
    @Alice-z7t4z 9 днів тому

    Amen ❤❤❤

  • @AbelKaunda
    @AbelKaunda День тому

    chakwela wanyanya

  • @AlickAlfred
    @AlickAlfred 9 днів тому

    I❤ you Jesus

  • @MayinatuBrown
    @MayinatuBrown 8 днів тому

    Mulungu akuziwa zose zimene zinachitika ndipo muluwangu wanthu ndiwamoyo achitapo kanthu

  • @user-cp4qt9hs8w
    @user-cp4qt9hs8w 9 днів тому +1

    Mcp atsogoleli ake dzinkhope ngati nyau

  • @user-lc3sw8iz2g
    @user-lc3sw8iz2g 8 днів тому

    Tipange ma Demo basi

  • @SamuelLiwonde
    @SamuelLiwonde 9 днів тому

    Nkhanga ndye zaonatu kkkk agwaaa nayo

  • @ChawingaMwaseteza
    @ChawingaMwaseteza 8 днів тому

    Chimene tikudziwa ife mdichokuti black box ilipo,and yasungidwa potetezeka,,kumkuyu anawuza dziko lonse la malawi,

  • @edwinnyasulu2088
    @edwinnyasulu2088 9 днів тому

    🔥🔥

  • @MussaChilembwe
    @MussaChilembwe 9 днів тому

    Zoonadi amene angamangidwe ndi Moses kunkuyu akasever ngati atataya black box for show

  • @KawawaIbrahim
    @KawawaIbrahim 9 днів тому

    Ndipo mtanyiwa iwe umatiimirira kupanda iwe tinasekeredwa m'bokosi,ambuye akuyang'anire

  • @ThokohPrescotKalonga
    @ThokohPrescotKalonga 9 днів тому

    More fire 🔥🔥🔥🔥

  • @inessliundi4347
    @inessliundi4347 9 днів тому

    🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @GeoffreyMangame
    @GeoffreyMangame 8 днів тому

    Tonde wapenga mutu sukugwira

  • @IanAllstal
    @IanAllstal 9 днів тому

    Kodi # ya chakwera ndichani mmafuna Akanamvako uthengau

  • @ZakifuMajasa
    @ZakifuMajasa 9 днів тому

    Anyani awa atikwana

  • @ZinawZinawmulu
    @ZinawZinawmulu 9 днів тому

    Mthengo wanji umagwesa ndichipani chimozi chamcp zipani zina mthengou sauwona

  • @BwanaGD
    @BwanaGD 8 днів тому

    Zafikapa tigoti neba mutu sukugwira

  • @MemoryKamanga-jv4jh
    @MemoryKamanga-jv4jh 9 днів тому

    😭😭😭

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 5 днів тому

    Anyaaaaa basi

  • @JosephHill-fy1bb
    @JosephHill-fy1bb 9 днів тому +1

    Fire mabomba 🔥

  • @DangerDanish-db1lg
    @DangerDanish-db1lg 8 днів тому

    Amen

  • @JamesKalasa-s6s
    @JamesKalasa-s6s 9 днів тому +2

    Amen