Msika Wa Ziwalo part 2...

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 10 вер 2024

КОМЕНТАРІ • 56

  • @lawrencemsefula5108
    @lawrencemsefula5108 6 місяців тому +1

    Great work Abel God bless you..

  • @bobchola5083
    @bobchola5083 Рік тому +1

    Nice one Mr Abel

  • @abdulkatopola3612
    @abdulkatopola3612 Рік тому +3

    Tapezani camera yabwino pls ndinu wailesi yaikulu pls

  • @aleksawilliams710
    @aleksawilliams710 Рік тому +2

    Tikuyisatatu nkhaniyi,,,momwe amkakambilana ndi Mr manjolo ndi Enest yo timazimva ndipo akut wakhala business akupanga wagwidwa nayeyu ndiwanambala 5,,,ntchito yake ndi yomweyo koma samagwidwa ,makolowo akungodandaula Poti kubeleka koma nanga akanakhala kut wagwidwa Mathews yo atamupaha kale zikanakhala bwanji? Tiunikepo pamenepo a Abel,from Balaka thank u

    • @victoriawilliam4490
      @victoriawilliam4490 Рік тому

      Ine kuona kwanga ndikuona ngati mkulu waku Thyoloyi ndiamene amamukocha mwanayi kuti azilankhula zimenezi cholinga ogulawo amukhulupilire msanga

  • @arnoldtem4
    @arnoldtem4 Рік тому +1

    Mr well done

  • @graceelias7381
    @graceelias7381 Рік тому +1

    Good work Abel

  • @user-eo7om7vj8e
    @user-eo7om7vj8e Рік тому

    Big up manjolo God bless you

  • @charlurquhart5788
    @charlurquhart5788 10 місяців тому +1

    Mwanayinso ndi opusa bwanji samakana

  • @lewisbonongwe8518
    @lewisbonongwe8518 Рік тому +2

    Mwana okongola Mathews

  • @user-fe6pp9gc6u
    @user-fe6pp9gc6u 8 місяців тому

    Good job Mr Aber

  • @burnnetsikwese
    @burnnetsikwese Місяць тому

    Mulungu ndi mwini chuma

  • @medsonkapondera5836
    @medsonkapondera5836 Рік тому

    Zandikhuza bravo kwa a TA ndi majolo

  • @janemvubu7750
    @janemvubu7750 Рік тому

    Good work mr Abel

  • @BdhfbHdhe-pd7nh
    @BdhfbHdhe-pd7nh Рік тому +1

    Grory to be God

  • @standykuchaga5355
    @standykuchaga5355 Рік тому

    Nice continue Abel

  • @user-sl6ty4dv6n
    @user-sl6ty4dv6n 9 місяців тому

    Good boi, God is with us all, be well my boi

  • @maxwellmustafa3078
    @maxwellmustafa3078 Рік тому

    God bless you Mr Abel

  • @alexgweje8610
    @alexgweje8610 Рік тому +1

    Anthu amene mumachita mchitidwe uwu wonyansawu Mulungu azikukanthani ndithu

  • @giftdulamkalenga7344
    @giftdulamkalenga7344 Рік тому

    The boy is genius than Chakwera wa monika ..Akadakhala chakwera bwez akungot sindikudziwa ... kufuso lililose

    • @cliftonmsowoya
      @cliftonmsowoya Рік тому

      Ndipo sukunama aise chakwela chilichonse samachidziwa 😂😂😂😂😂😂

  • @aleksawilliams710
    @aleksawilliams710 Рік тому +2

    Tikudikilirabe part 3 ngati mkotheka Mr Abel🤗

  • @lilianchikondi195
    @lilianchikondi195 Рік тому

    Bomanso limaziwapo kanthu zazimenezi, that's why sapanga kanthu akamvesedwa zaizi,we thank mibawa tv potulusa poyera nkhani zi

    • @cliftonmsowoya
      @cliftonmsowoya Рік тому

      Kunakakhala kuti ndiku south zitha kale kale izi

  • @gesinasutherland9241
    @gesinasutherland9241 Рік тому

    Makolo amwanawo asabakile mwana wawo..ndipo mwana ameneyo a langidwe basi ..iyeyo analora bwanji nanga anthu four aja ..alangidwe basi

  • @Malani41
    @Malani41 Рік тому +4

    Thanks for continuing this story! I feel it for the poor boy! I’m glad that he is saved. His fate was about to be gruesome!!! Kudos to the two people who saved this kid. It hurts to even imagine how traumatizing this is going to be for this kid for the rest of his life. We all need to be following up on him. Just sad. Wish the perpetrators got the death penalty for this.

  • @josephybenjamin3877
    @josephybenjamin3877 Рік тому

    Tendai Mezzan akuti2 mwana wa afiniyasih

  • @elizabethziba1652
    @elizabethziba1652 Рік тому

    Eshiiiii koma the trauma amupatsa mwanayi eeee God have mercy on us

  • @user-eg5zi2jk7p
    @user-eg5zi2jk7p 10 місяців тому

    😢😢😢😢nkhondodi ndianasi kuti muivetsetse nkhaniyi anthu wa ndpachibare kufuna kugulitsa mwana wa m'bare wawo

  • @chifunirosaka9077
    @chifunirosaka9077 Рік тому

    Achinyamata osamatengeka ndizinthu zachabe chabe zopandatsogolo taonani mnyamata uyu akufela zaeni chifukwa pakhomo pake pakuoneka povetsa chisoni kwambili

  • @geniuskamwanje
    @geniuskamwanje Рік тому

    Manjolo thank you

  • @tingamasi106
    @tingamasi106 Рік тому +1

    Tikudikira part 3 yaku police

  • @victorauwana7258
    @victorauwana7258 Рік тому +2

    Handsome kid

  • @gesinasutherland9241
    @gesinasutherland9241 Рік тому

    AMalawi mphada amene mukupangayo muzitenga anu ana..mudzafa manja ali kumbuyo...

  • @ambuyampundubanda9419
    @ambuyampundubanda9419 Рік тому

    Good job, but when you say that hidden part do so. We can see the gentleman. Edit the video.

  • @mordecaikachale2497
    @mordecaikachale2497 Рік тому

    Akanakhla majolo kunena kuti abwere munthu wamoyo Kodi Elosoni akanatha kumupha mwanayo ndikupitisa ziwalo??? Nkhani yovuta iyi

  • @cliftonmsowoya
    @cliftonmsowoya Рік тому

    Komanthu eeeeeee

  • @isaacmussa2942
    @isaacmussa2942 Рік тому

    Umphawi okha okha chosecho mukupanga business yoopsa achita bwino kukumangani agaru

  • @rabisonpias5131
    @rabisonpias5131 Рік тому

    Nkhnai Zomvuta, Mwanayu Kodi ali ndi Dzaka zingati..!?
    I mean mwana emwe adatenga mwana mzakeyuu..!?

  • @pauldaka7966
    @pauldaka7966 Рік тому +1

    Tikudikirabe zakukhoti zinayenda motani?

  • @tshepangmatebele7822
    @tshepangmatebele7822 Рік тому

    Nkhani yomvetsa chisoni komanso yoopsa

  • @mbawabuliyan9704
    @mbawabuliyan9704 Рік тому

    Zachisoni kwambiri Mwana wa bwino bwino

  • @gracechiumia7103
    @gracechiumia7103 Рік тому

    Munthu ameneyo chilango chikharepo basi nanga akanati apitise ziwalo simwanayo akanampha basi?chilango chikharepo kuti anthu ena atolepo mphuzilo

  • @janetmanda6412
    @janetmanda6412 Рік тому +1

    Umphawi wasanduka nyambo pamalawi ya anthu achuma, someone big behind the scene

  • @pauldaka7966
    @pauldaka7966 Рік тому

    Tikusatira mwachidwi

  • @mathewsscotch2105
    @mathewsscotch2105 Рік тому

    Aaaa ndimadabwatu kuti ithera pompaja

  • @user-vx4gu4fs9s
    @user-vx4gu4fs9s Рік тому

    Mulungu nd wamkulu basi

  • @TheVizionet
    @TheVizionet Рік тому

    Manjolo ndi a TA ndiofunika kuwafufuza

  • @omarlux3434
    @omarlux3434 Рік тому

    Zachisoni

  • @ellenjulius-jk3jb
    @ellenjulius-jk3jb Рік тому

    A mfumu kuyakhula kwake kumeneko angaweluze khani bwinobwino koma

    • @rosebanda3613
      @rosebanda3613 Рік тому

      😂😅😂😅😂

    • @thokokawaza
      @thokokawaza 7 місяців тому

      Amfumu wopusa awa, seems akudziwapo kenakake! Akuikira kumbuyo chigawenga