Kangawude Amuna folo

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 4 бер 2023

КОМЕНТАРІ • 37

  • @shabanitendo4781
    @shabanitendo4781 Рік тому +1

    Abelo pls tikufuna nkhan yasikaana anasekeledwa aja pamodz ndimwana pls part 3

  • @dn30972
    @dn30972 Рік тому +4

    mumatha kufufuza nkhani zabwino but full episode is needed

  • @mordecaikachale2497
    @mordecaikachale2497 Рік тому +2

    Mumaba ???ayi koma ndimalanda ma fon ndi ndalama 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x 4 місяці тому

    Ine kwathu ndikwa Bvumbwe koma sindikuwadziwayi ataaah, kwathu kwa William kufupi ndiku research station

  • @aleksawilliams710
    @aleksawilliams710 Рік тому +1

    Kkkkk ayambe ubusa SInanga akulapa

  • @GiftChadika-he7nd
    @GiftChadika-he7nd Рік тому

    Abel zulanga Abella zulanga ulemu wako umafufuza nkhan bwno pitilizan 😂😂😂

  • @peterbanda7003
    @peterbanda7003 Рік тому +1

    Kkkkkkk ndakuziwa iwe wa kwathu Kwa bvumbwe

  • @charityamos2183
    @charityamos2183 4 місяці тому

    Anakwatira nkazi ofatsa

  • @isaacmussa2942
    @isaacmussa2942 Рік тому

    😃😄😄koma Abello utionetsa zinthu

  • @MAPAGASTUDIOS
    @MAPAGASTUDIOS 3 місяці тому

    Ameneyo 11bongoz akuluwa ankangoitsata ine ndnakulila mu36 mwakatantha 11bongoz ndmaidziwa ine ndiya achina amoni tiyende achina never anaokwiya amungwenya munanjilimu ndmwachisapo awa anali mbava zomwe zimaba kuyuza dzina LA 11bongoz 11bongoz inaridi ya ku36 mudzi mwakafula not munthu wakumwera dzinalake fula wabodza uyu afumu akafula kwaphwetekere kuseri kwa mashop a pakandikole mukatsikila pa centjoze muzinamiza Ena ifeyayi

  • @florencebonga3211
    @florencebonga3211 Рік тому +1

    11 bongozi mmm anatchukadi ai mumatha kufufuza

  • @idrissahyunus7650
    @idrissahyunus7650 Рік тому +2

    please imalizitsen nkhaniyo ifike pa mapeto

  • @nophiimadalitso4655
    @nophiimadalitso4655 10 місяців тому

    Kodi part two yijayo yilikuti Mr Zulanga?

  • @mussaabass925
    @mussaabass925 Рік тому

    Ndimachotsa nyama 😂😂

  • @mathewsscotch2105
    @mathewsscotch2105 Рік тому

    Koma iweyo umatha, umaisatila Khan bwino ndithu ayi timakunyadira

  • @AugustineIshmael
    @AugustineIshmael 9 місяців тому

    Following

  • @user-ki9kk5lv5n
    @user-ki9kk5lv5n 6 місяців тому

    Bro tandize komwe munapita

  • @collinschipala611
    @collinschipala611 9 місяців тому

    Mafunso,o sali in good order. !!!

  • @mbawabuliyan9704
    @mbawabuliyan9704 Рік тому

    Adali oopsa kwambiri akuluwa

  • @dalisoulphiri3094
    @dalisoulphiri3094 3 місяці тому

    Kodi part two nde ilipati?

  • @rabisonpias5131
    @rabisonpias5131 Рік тому

    Program yafupikaa.
    Where is part 2.?

  • @hawkinstikatika7785
    @hawkinstikatika7785 10 місяців тому

    Part 2 pliz

  • @user-rn9cd3be6k
    @user-rn9cd3be6k 5 місяців тому

    Kkkk Anali van Damme 😂

  • @aleksawilliams710
    @aleksawilliams710 Рік тому

    Kod nkhani yamwana ija ilipati?( Yakuchikwawa )

  • @KayiweMatama-wk1xn
    @KayiweMatama-wk1xn 9 місяців тому

    Part 2 plix🙏🙏🙏

  • @kondwaninyangulu5563
    @kondwaninyangulu5563 Рік тому

    Mumatha kufufuza man

    • @mercychiba4007
      @mercychiba4007 Рік тому

      Abelo umatha utolankhani iweyo

    • @sheenahmwalabu
      @sheenahmwalabu Рік тому

      More nkhani Abel, love your program and mudziika # yaku mibawako kuti zikachitika nkhani kuno tidzikuimbilani mudzidzajambula.

  • @De86666
    @De86666 Рік тому

    Alomwe alomwe 🤣🤣🤣

  • @isabelmartin7567
    @isabelmartin7567 Рік тому

    Part 2 please

  • @patricknzima3053
    @patricknzima3053 Рік тому +1

    parts 2 please

  • @isabelmartin7567
    @isabelmartin7567 Рік тому

    Tikudikilabetu

  • @schaumer
    @schaumer Рік тому +1

    Pisitole 🤣🤣🤣

  • @romsa4590
    @romsa4590 Рік тому

    Mlibho

  • @isabelmartin7567
    @isabelmartin7567 Рік тому

    Please part 2