Це відео не доступне.
Перепрошуємо.

kangaude

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 15 лип 2023

КОМЕНТАРІ • 159

  • @marynkhata9707
    @marynkhata9707 Рік тому +5

    Chisiru ndi bambo wa mwanayo zosenzi zikuchitika chifukwa cha iye ndi abale ake afitiwo mulungu amukhuze mwanayo ndi machiritso 🙏

  • @mphatsosadiki4983
    @mphatsosadiki4983 5 днів тому

    Kungoyambila Dam lomwe anapanga mamunayo liphwele asowe podalira ndipo amve kuwawa Ngat mmene akumvera mwanayo mu dzina la Yesu.... chemwali wa mamunayo tikupemphera kusauka kuti aziwe za ukulu wa Yesu...OC and corrupt officers ku police imeneyoyo i speak kuchosedwa ntchito kuti aziwe kuwawa kobeleka in Jesus name...I can feel the pain that this family is passing through,this is temporary life tikayankha pa maso pa Mulungu zosezi.

  • @mordecaikachale2497
    @mordecaikachale2497 Рік тому +7

    Anthu mwapasa bail wina akubwera kuzaseketsa mlandu koma opasidwa bail osauzidwa kuti mlandu uja watha 😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @user-qq6dv2up3w
    @user-qq6dv2up3w 10 місяців тому +1

    Zkundinvekera mwachinyengo choncho aaa koma dzikoli

  • @mordecaikachale2497
    @mordecaikachale2497 Рік тому +7

    Wapolisi uyuyu ngati ntchito akugwira chonchi ndiye kuti akuononga dziko basi

  • @gladyschisomo4324
    @gladyschisomo4324 Рік тому +5

    Bwana Abel tafufuzani akuluakulu alowelelepo anthu osaukafetu tilibe voice mwawamva a OC akuti kaya anthu akumudziwo kusonyeza kuti akumudzi ife tilibe mphamvu a original OC akudziwa ndithu pomwe inayambila ndipomwe inathela zose akuzidziwa koma akubisa

  • @user-di4om7sh8w
    @user-di4om7sh8w Рік тому +2

    Ndikumufunila🎉 kuchila mwa nsanga Mwana ameyu

  • @kofibist6845
    @kofibist6845 Рік тому +7

    A police achinyengo palibe chanzeru chomwe ayankhulapo andinyasa kobasi anthu anji opanda chisoni ndimomwe akuonekera mwanayo 😢

  • @BlessingsNyirenda-ru7ss
    @BlessingsNyirenda-ru7ss Рік тому +2

    Apolice a police pena muzikhala ngat tonse ndife anthu mukuyankha mozemba zemba pomwe mukuziwa chowona mulungu akukantheni

  • @mordecaikachale2497
    @mordecaikachale2497 Рік тому +3

    Abel u must no urself that Ur putting urself on the map of the country we need this issue until the end ...Ur doing the GRT job ...I like that question chifukwa chani apolice ndi atolakhani safuna kugwilizana keep it up bro❤

  • @lytonmaseko4534
    @lytonmaseko4534 Рік тому +6

    Wa police uyo ali ndi vuto akubisa kuyikira ku mbuyo a police ena

  • @user-yp3um6mf8d
    @user-yp3um6mf8d Рік тому +5

    This is a sad development Abel.Please pull up your strings until the end of this case.Both the Officer In charge and the police officer have to be fired and save a curruption case.And unlawful arrest of those victims.When the complainant closed the case the police didn't bother to inform the defendants.Please Malawian Lawyers take this case to court on probno there is money here.The case can be seen that it is on the defendants' side.

  • @costerrobert1519
    @costerrobert1519 Рік тому +5

    Wapolice uyu ndi mbudzi yeniyeni ndithu

  • @YusufWanck
    @YusufWanck Рік тому +3

    Ku police kulibe chilungamo too much kubelekana kma pa chichewa pali mawu "Chaona nzako chapita mawa chili kwa iwe" Ndipo Galu aliyense ali ndi tsiku lake.

  • @victoriawilliam4490
    @victoriawilliam4490 Рік тому +4

    Alibe mfundo a OCwo
    Akuti anthu akumudzi iye ndiwakuti ? Palibe chomwe anganene ndimbava zokhazokha zonsezo

  • @shabaniphiri7261
    @shabaniphiri7261 Рік тому +2

    Kodi bambo a Gracious alikuti Albel tawafufuzani abwere azalankhule mbali yake

  • @reginamichael7664
    @reginamichael7664 Рік тому +2

    Chilungamo chioneke chifukwa wina aliyense ngat wachoka pantchito kaya wapita ku holiday kukapuma aliyense amamuziwa yemwe wamusiya pa mpando.

  • @user-hg9ye9ux1v
    @user-hg9ye9ux1v Рік тому +2

    Kunyasa mawu ngati mamuna ukuwoneka kuti ndiwe oyipa gaku

    • @user-tg1tg8wt8f
      @user-tg1tg8wt8f Рік тому

      Mayi oyipa uyu mayi zimbili ndikumuziwa anandimanga ine ndisanalakwe ndizamupeza ubwino wake Ali kwathu tizakupezani komweko

    • @user-yk6qn3hg5i
      @user-yk6qn3hg5i 10 місяців тому

      Ndipo live

  • @HellenKanyemba
    @HellenKanyemba 2 місяці тому

    Awa akanazisiya apange focus zamwanayo komanso anthu awaonetsa chikondi iwonso mwachikondi akhululuke

  • @user-ek3tm3su3g
    @user-ek3tm3su3g 2 місяці тому

    Apolice akumalawi ntchito yomwe amagwila siyidziwika mwana momwe akuwonekelamo moti chisoni alibe😢😢😢 kmaso akufuna kwabwino angothandiza mwanayo bola zinazo angozisiya kuweluza ndikwamunuwake mulungu and awakanthila pansi pompano

  • @reginamichael7664
    @reginamichael7664 Рік тому +3

    Pagona chinyengo apaaa. Koma chilungamo chioneke bac

  • @user-oq1pz6cv1y
    @user-oq1pz6cv1y Місяць тому

    Ndikuva kuti ndiwachinyengi OC

  • @user-xf1gb5gu3z
    @user-xf1gb5gu3z 4 місяці тому

    Officer in charge, "she is even failing to explain of the case, oh my!" she had the mother's file but hear what she's saying 😮😢 oh my!
    Good job Abel, I salute you. This is perfect, keep on doing this good job. We need to correct where things are going wrong by giving out our overviews of what is going on.
    Choonadi sichiola, chilungamo sichimatayika, so watch out when you're doing a bad thing. It comes back to you, from God. There's no secret under Heavens, under the clouds and under the sky.
    Those police are insane, not helping.

  • @user-ws4ue7tf6j
    @user-ws4ue7tf6j 11 місяців тому +1

    Mmmmmm koma nzimayi oti kuwawa kwa uchembele ukukudziwa sunga pondeleze khani chonchi kodi police yakwathu kumalawi mumachulutsa kupanga ziphuphu bwanji koma ??? Mulibe manyazi ??? Inetu ndinkayesa kuti
    Police imathandiza komano apapo ndatsimikiza kuti police ndimbava eniyake ziphuphu mudziweni mulungu

  • @ErickDzicco
    @ErickDzicco 2 місяці тому

    Ndikumufunira chithenda chapadera dera wa police ameneyi😢😢

  • @chifunirosaka9077
    @chifunirosaka9077 Рік тому +1

    Mum'dzina la Yesu chilichose chobisika pankhaniyi chibwela poyela ndipo mulungu awapatsa chilango pompano padziko lapasi anthu akumuona amen

  • @user-xf1gb5gu3z
    @user-xf1gb5gu3z 4 місяці тому

    I believe the women, they are saying the truth. Apolisi akuno it's there habit, amatenga aliyense accused or locked in behind the bars is a criminal without proper investigations and arrogations.
    Another thing is this, ufiti and satanism here in Malawi zikuchuluka and with those coordinates and networks amongst them when they are together, no truth comes out. They backside each other.
    I can encourage them to do fasting and praying for a breakthrough, there's a living God in Heaven. I am testifying, that's why I am awake by this time. Let's keep on praying everyday, every time and live a Holy life.

  • @abdulkha7810
    @abdulkha7810 Рік тому +4

    Ku malawi wachuluka katangale please 🙏🙏 boma tinthandizeni

  • @user-yk6qn3hg5i
    @user-yk6qn3hg5i 10 місяців тому

    Km mamuna aneneyo komaso ccter wakeyo mulungu awakanthe mu dzina la yesu amen

  • @user-lr7ux2ok4t
    @user-lr7ux2ok4t Рік тому +3

    Chulungamo chiziwike Ambuye atichitile chisoni

  • @user-di4om7sh8w
    @user-di4om7sh8w Рік тому +3

    Km ndikanakonda bamboo oyipayi mutacheza naye onse Ali limodzi

  • @ericchilinjala481
    @ericchilinjala481 3 місяці тому

    9:27 kunkhozomolaku..tubecho nthawi zina chimasuntha..nkonanso akubanika..ndiofunika chest x ray ..kuti aone ngati tube chili mmalo.

  • @user-od9wh3iu9w
    @user-od9wh3iu9w 4 місяці тому

    Kt apeleke galimoto yokagwilila muthu wa police kumatelo aaaaa

  • @BdhfbHdhe-pd7nh
    @BdhfbHdhe-pd7nh Рік тому +3

    Abel undipezele bambo amwanayu ndimenyane nawo 1_1

  • @faithmtika6121
    @faithmtika6121 Рік тому +1

    Mulungu amuchitire chifundo mwanayo

  • @user-xn6yp2nj8t
    @user-xn6yp2nj8t 7 місяців тому

    Galu oc ameneyo chinyengo kwambili...mbuzi

  • @brighttomakamanga5370
    @brighttomakamanga5370 Рік тому +2

    please amabungwe lowelelanipo mayankhowa sizowona ayi apolice tiyeni tigwire ntchito yathu mowopa mulungu umphawi chisakhale chitozo

  • @user-od9wh3iu9w
    @user-od9wh3iu9w 4 місяці тому

    Tili pano kuonesetsa khan imeneyi iyende mopanda chinyengo

  • @hucklyrajabu7137
    @hucklyrajabu7137 Рік тому +1

    Sambi abale Mmmmmm ai ndithu Allah akhale nanu sister

  • @user-fd7wj3mg2i
    @user-fd7wj3mg2i Рік тому +2

    Moyo uno sukufunika kukhala odekha,sukufunika kukhala opusa,sukufunika kumazionela pansi kuti ndine wamkazi,pompo munamuona uyo amadzintcura kuti OC yo mukanapatsa makofi yobu 13 :13 ndipomwe pakanayambika kuoneka cilungamo

  • @mrsnsuzilenardil4827
    @mrsnsuzilenardil4827 Рік тому +2

    Mmmmmm Sambi chinyengo

  • @herbartkaphamthengo9978
    @herbartkaphamthengo9978 Рік тому +1

    Apolice ambiri kumalawi akufunika zaichosedwa ntchito akapanga zinthu zophera anthu ufulu chifukwa akumazuza anthu ambiri.

  • @user-rf7qu1gb3f
    @user-rf7qu1gb3f 6 місяців тому

    Amene angakwanitse kuwathandiza anthuwa kut nkhan ipite chitsogolo pliz do so amene muli ndikuthekera Sizoona zikuchitikazi

  • @user-hc6rc7yr8y
    @user-hc6rc7yr8y 6 місяців тому

    Wapolice oyo malankhulidwe ake akuchita kuoneka mmalankhulidwe ake kuti pali chinyengo

  • @yassinjanna9564
    @yassinjanna9564 Рік тому +1

    Wa police yi ndiwamwano

  • @namondwejohn9354
    @namondwejohn9354 3 місяці тому

    Mmmm koma amayi awa mulungu awaone mai odziwa ululu pobereka kukhara satana chonchi,atolankhan musaisiye panjila mkhan kufikira chilungamo chiyende ngati madzi,kuti ena atengerepo phuzilo

  • @shabanitendo4781
    @shabanitendo4781 Рік тому

    Maiwa ndi hule komaso mfiti khope yakeyo ngt buluz

  • @gesinasutherland9241
    @gesinasutherland9241 Рік тому

    Ambuye alowelerepo..ndipo awochetse ntchito...komanso wa 70 uja alondoledwe basi..

  • @user-hw8ds8oy6i
    @user-hw8ds8oy6i 7 місяців тому

    Chili chose Mulungu akuwona

  • @user-oq1pz6cv1y
    @user-oq1pz6cv1y Місяць тому

    Kodi anawamanga chifukwa chani😢

  • @user-ws4ue7tf6j
    @user-ws4ue7tf6j 11 місяців тому

    Timadziwatu kuti eniyake ogulitsa chamba ndinu a police ziphuphu ngati mukuyamba inuyo ana anu mungawala ngize bwanji zigawenga zachabechabe

  • @user-mk8cn2no3o
    @user-mk8cn2no3o 4 місяці тому

    Apolice amangofuna ndalama nda mbava zikuluzikulu koma chilungamo chioneke

  • @thokochilimba-bs2mm
    @thokochilimba-bs2mm Рік тому +1

    This woman chilungamo akuchidziwa

  • @saukophiri4535
    @saukophiri4535 11 місяців тому

    A police ndi atolankhani zikuoneka kuti sadzagwirizana olo pang'ono chifukwa atolankhani amalondoloza nkhani mpaka olokwa apezeke pamene kumbali ya police amabisana .Zikuonekeratu kuti a oc wo akudziwapo kanthu and vuto ndi iwowo

  • @AkimNyimba
    @AkimNyimba 10 місяців тому

    Mwamuna oyipa mulungu amene analenga iyeyo ndi mwana yo amupase chilango mwamuna yo nkhaza kwamwana

  • @FosterCement-yn4cj
    @FosterCement-yn4cj Рік тому

    Atseka bwanji nkhani abale pangani zoti chilungamo chioneke amaseka bwanji mulandu

  • @mkhokholasamuzonda5094
    @mkhokholasamuzonda5094 Рік тому

    kodi iwe wa camera osamujambula wapolisi wopusayo bwa timuone

  • @omarlux3434
    @omarlux3434 Рік тому +1

    muzayimalize tizave kuti zili pati?

  • @chikonjiwe007
    @chikonjiwe007 Місяць тому

    A police aku Malawi too much corruption fosteki

  • @joicemartin-ji5zu
    @joicemartin-ji5zu Рік тому +1

    Ndi cisiru ameneyo wachinyengo ameneyo

  • @victorbanda9039
    @victorbanda9039 Рік тому

    Azimai ndinu anthu oipa kwambiri mukangoyerekeza kuidwa paudindo mumazuza kwambiri azanu zoona mulibe chisoni ndimwana wanzanu momwe akuvutikira mmm Oc oipa kwambiri mulungu akulange sure

  • @user-hn7sc3ft1f
    @user-hn7sc3ft1f 7 місяців тому

    That case need justice up to the end of story please Abell go ahead on that case may good Lord be with the concerned family

  • @ErickDzicco
    @ErickDzicco 2 місяці тому

    Koma mfiti wa police iweyo ndwe onyatsa ndi mtima omwe

  • @siskanyirenda
    @siskanyirenda Рік тому +1

    Nkhaniyi siingathe choncho apange apilu police Ina iyendeposo apo bii police ilibe ntchito ndi mbava zikuluzikulu zobela anthu akuona

  • @monicabanda7322
    @monicabanda7322 6 місяців тому

    How is the baby now asking from Washington DC.

  • @towellabanda2218
    @towellabanda2218 Рік тому

    Ndi Ameyo mayiyo 😂😂😂😂😂
    Wazomera kale

  • @sharrifgwape7169
    @sharrifgwape7169 Рік тому +1

    Zovuta ndithu

  • @user-nf2fh2zr8u
    @user-nf2fh2zr8u 9 місяців тому

    Apolice akusogoza ndalama Koma Mmmmm zosayenda😢😢😢

  • @jennifermbewe9684
    @jennifermbewe9684 Рік тому

    Ndipo azibambo sazindikira ndithu Nkazi okongora bwino Ngati ameneyo kumamuzuza ndithu ayi zikomo murungu akuyendere bambo iwe pomuchita chipongwe Nkazi ndimwana murungu ngwama chiritso achira mwanayo osadandaura

    • @user-rh3ts4yh4z
      @user-rh3ts4yh4z 10 місяців тому

      Ndipo mmene wakongolera nkaziyo ndikuzifunsa Kuti bwanji mulungu sanatikumanise ndi mayi odekha ngati uyu 😢akuchita kuoneka kuti ndiolifuna banja ndipo alindichikondi mayi uyu ❤..anyway ambuye achitepo kanthu ndithu

  • @peterchunga8990
    @peterchunga8990 7 місяців тому

    Iyi ndinkhani yomvetsa chisoni kwambili koma OC wapa luchenza wachulukitsa katangale and nkhani ngati izi ndizija apolice amapezelapo mavuto chifukwa chamchitidwe waukatangale koma ine zitandichitikila zimene wayankha OC ameneyu straight mpakana ndimpanga chiwembu kuti ena atengelepo phunzilo mmayi opusa kwambili.

  • @FlyingSquadz-nz5cl
    @FlyingSquadz-nz5cl Рік тому +1

    For just my opinion u can go whatever you can if you have no money or if you're poor 😭 big problem and behind bars is for the people who doesn't have money

  • @AishaPanjira-od9hg
    @AishaPanjira-od9hg Рік тому +1

    Apolisi akumalawi ndi zisilu

  • @giftphiri1533
    @giftphiri1533 Рік тому

    Aaaaa inu bwanj chilungamo mukuchibitsa apa osawapanikiza mafuso iwowo akuoneka akuziwa chilungamo

  • @esteryndau8546
    @esteryndau8546 Рік тому +1

    Zikhala bwanji za mkati mwanu poti mwana anamuyika ku cell mayi khalani ndi mtima wachikondi inu m' mene mwafotokozera tanziwano kuti mkuziwapo kanthu

  • @chikonjiwe007
    @chikonjiwe007 Місяць тому

    Lucheza police has messed up big time kodi munthu osauka usakhale ndi voice why Malawi..the child is so innocent muzikhala ndi mzimu. Azimai kodi bwanji mumakhala olimba mtima. Ndi dzikotu ili..God will punish you. Stop oppressing the voiceless..A Police munakhala njibwa kukonda ndalama..bambo wa mwana ndi sister wake muli kuti..could you please come out in the open we need to hear your side of a story..Dam la nsomba.mwayambalo will soon dry up and you will suffer for the rest of your life.

  • @leonardkaumphawi2858
    @leonardkaumphawi2858 Рік тому

    Apolice akumalawi amakhala ndimwano .and akakumanga omangidwa umakhala ngati chitsiru and ngati opanda ntchito kuziko..the way mmene amakulankhulira.

  • @berthakambwiri6288
    @berthakambwiri6288 11 місяців тому

    Shoooo😮😮😮 if mwana analowa mu cell, thats criminal offence...instead of releasing the mother of the child

  • @user-yk6qn3hg5i
    @user-yk6qn3hg5i 10 місяців тому

    Mayi oyipa iwe mulungu akukanthe galu wamayi ngati subeleka

  • @towellabanda2218
    @towellabanda2218 Рік тому

    Wabodza mayiyo 😮😮😮😮
    Sikuona magalasiwo
    Bushing around 😢😢😢

  • @user-wg5lp9zt2w
    @user-wg5lp9zt2w 5 місяців тому

    Kurakwa koma😢

  • @FosterCement-yn4cj
    @FosterCement-yn4cj Рік тому

    Kumwamba zikaoneka Mai Ngati kumapemphera APA mukutero Koma kumwamba mukazivera chisoni Mai mulingalire muli inu mungatani mwana Ali wanu

    • @FaithKasonjola-dj4qx
      @FaithKasonjola-dj4qx Рік тому

      Mayi wopanda mzelu ngobeleka koma ameneyi Mulungu adzakukatha zimayi iwe phaka kunena kuti athu akumudzi iwe ndewakutawn

  • @user-ch2kq4th5j
    @user-ch2kq4th5j Рік тому +1

    AC Odyssey Samantha Road indore

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 Рік тому +2

    Mu katundu munali katundu ooopsya koma ziliko ku Malawi

  • @user-fg5iw1qy1k
    @user-fg5iw1qy1k Рік тому

    A ocwotu aziwapo Kathu koma akuopa akuziwa kuti zavuta mulungu akukhululukireni pakuti chimene mukuchita simukuziwa

  • @herbartkaphamthengo9978
    @herbartkaphamthengo9978 Рік тому +1

    Koma Aubrey umatha kufusa mafuso komaso wapolice sakuyankha moveka

  • @giftblack7690
    @giftblack7690 Рік тому +1

    Apolice akumalawi ndi amphawi nde sangalondoloze nkhani opanda dziphuphu anthu inu mulungu adzakulangeni kwambili ndipo inu a oc ntchito yanu simumayidziwa koma dyela kukonda ndalama mudzafa mumphawi ndinu otembeleledwa

  • @LuciasZepete
    @LuciasZepete 4 місяці тому

    Apolice ambiri vuto lake ndi mburi

  • @brasiobrasio2113
    @brasiobrasio2113 Рік тому

    Wankulu wapolisi openda nzeru ameneyo corruption inawawapweteka kuyankha mopanda nzeru ngati si mmayi

  • @user-di4om7sh8w
    @user-di4om7sh8w Рік тому +1

    Chitsilu wa police uyu amayikilana kumbuyo anyani awa

  • @user-cs5ss4rj7g
    @user-cs5ss4rj7g Рік тому

    Mwaonatu amalawi tipepha mulungu alowelelepo

  • @user-nx7yz4qo8f
    @user-nx7yz4qo8f Рік тому

    Oc yo sangalephere kudziwa yemwe amkagwila ntchito nthaw yomwe iyeyo anali pa holiday,nanga anafufuza bwanji kudziwa za omwe anasekedwawo mayina awo akuwantchula bwa?

  • @jennifermbewe9684
    @jennifermbewe9684 Рік тому

    Murungu adzaurura zisisi zose zobisika murungu ndiwo Oshwa kwambiri

  • @chikuchimbatata3169
    @chikuchimbatata3169 9 місяців тому

    The officer palibe chomwe wayakha chazeru ... i wish khaniyi itatsatiridwa to the end

  • @user-tg1tg8wt8f
    @user-tg1tg8wt8f Рік тому

    Mayi oyipa uyu mayi zimbili ndizakupezani wasala pang'ono

  • @herbartkaphamthengo9978
    @herbartkaphamthengo9978 Рік тому +2

    Nkhani imeneyi ilondolezeni please izikike pothera

  • @user-rd4lf2gg7g
    @user-rd4lf2gg7g Рік тому

    OC omvetsa chisoni mulungu ndi omwe akuziwa
    Mtola nkhani timakunyadila zed

  • @user-cs5ss4rj7g
    @user-cs5ss4rj7g Рік тому

    Yes mayio akunena zoona apoliceo ndiooputsa anawapasa ndalama a .o.c

  • @user-uf2rv3kh2j
    @user-uf2rv3kh2j Рік тому

    Mmmmm kod chomwe amakuitanilan ndizopusa ngat zimenezo km apolice ena ndinu zitsilu kwambiri kuyakhula ngat uchembere sukuwuziwa zandiwawa kwambiri nkhani iyi isathere apa please albel, zandikhuza kwambiri 😢😢

  • @FosterCement-yn4cj
    @FosterCement-yn4cj Рік тому

    Akambirana bwanji kumbali Palibe zimenezo

  • @jamesmakawa-hl6gf
    @jamesmakawa-hl6gf Рік тому

    Mmmm koma a Police athu alibe chilungamo ,koma ambuye kumwambako alowelelepo pa nkhaniyi