ZIKUCHITIKA - Anthu Awiri omwe anamwalira zaka zapitazo apezeka mu mb'oma la Balaka

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 1 лют 2023

КОМЕНТАРІ • 169

  • @SamsonZilikha
    @SamsonZilikha Місяць тому +3

    Seems onsewa akukamba zolondora, enawa anachita kugula mwanayo, . Mkana funso loti ndimwana wawo wachingati alephera kuyankha.

  • @markchimpeni7819
    @markchimpeni7819 Рік тому +8

    Mwanayo ndiwabambowo akufana naye awo zangolumikizana

  • @berthakambwiri6288
    @berthakambwiri6288 11 місяців тому +4

    When the manbwas asked kuti ndi mwana wao wa number chani he said ayenera kukhaka wa number 3....i can not believe this man he must have bought this girl from kwa msato

  • @GraceBanda-t4r
    @GraceBanda-t4r Місяць тому +1

    Kulibe munthu anauka kwa akufa boza mwana ndiwa abambo Zambia

  • @TadalaJenala-e1l
    @TadalaJenala-e1l Місяць тому +1

    Mene akuwonekeramo angakhale kt Ali nd mwana wa zaka 19 or Nat kt athu akubereka msanga mwanayo n wabambowo chabe muthu wamisala amawona zambili zachisis ndchofukwa amawona asatowo kmas zimay uja akt anafika n katund mujumbo ndy tizit anachoka nazo kwasatoko ay ameneyo ndwamisalad nd mwana wabamboyo

  • @bryanryankalimazeru5939
    @bryanryankalimazeru5939 Рік тому +2

    Mkafutse maneba akwabambowo ,mthu Amazika Mdela

  • @malikomubolodalakalua450
    @malikomubolodalakalua450 Рік тому +1

    Abambo awo ndititi akufuna kuti asokonedze umboni wamwanayo chifukwa mnkhani sitinamve mwana awachula dzina .Bombo uyo amadziwana ndia fiti chinsato,mtsayerekedze kumsiyi mwana akampheratu msungwana wabwino .bvomeredzani kt mwana watopa nding'mbe.

  • @JeremiahPhiri-y7h
    @JeremiahPhiri-y7h Місяць тому +1

    A chipatala ndiwo anganene zoona

  • @FocusGeorge-qz4sh
    @FocusGeorge-qz4sh 12 днів тому

    Chiphaso cha kuchipatala chigwire ntchito

  • @DanielJuwawo
    @DanielJuwawo 7 днів тому

    Achikangawa

  • @JeniferKananji
    @JeniferKananji 9 днів тому

    Mayakho Ali kuchimpatala

  • @NelsonWisedy-sy5lm
    @NelsonWisedy-sy5lm Рік тому +4

    Chofunika kupita naye ku DNA then ku church orkuma prophet like bushili I'm from Zambia

  • @FaroukPhiri
    @FaroukPhiri Місяць тому

    Ndimomwe ndikuyibverera nkhaniyi mwanayu ndi wamayiwa komano poti nkuluyu akuti ndiwakenso zosautsa mwinatu nkuluyu akudziwapo kanthu kuthetsa nkhani ndikoti apite ku hospital akayense magazi

  • @user-xf1gy9cw1d
    @user-xf1gy9cw1d 7 місяців тому +4

    Koma njira yabwino guys D N A siyimafanana angokayeza kuchipatala basi

  • @transformernadzombe
    @transformernadzombe 6 місяців тому +1

    Mwana ndiwa bamboyo , amayio akunama dzaka 18 zadutsa angawoneke choncho 😊

  • @gesinasutherland9241
    @gesinasutherland9241 Рік тому +1

    Mwanayu adamukhwimila abambo akewo akudziwapo kanthu

  • @user-fj3hz1km1r
    @user-fj3hz1km1r 9 місяців тому

    Abambo awo ndamene awasiyila zizimba zosunga anthu munyumba ndafiti iwoso mtsikanayo apasa mkakamila

  • @user-eg5zi2jk7p
    @user-eg5zi2jk7p 10 місяців тому

    Kma ndzachisoni kmaso abambowa Akuti bwerani mumutenge Munthu wanuyi akundkanda😢😢😢😢😢😢

  • @zehnqulonga
    @zehnqulonga Рік тому +2

    Mwanayo akuwaziwa abambowo ndiwawo

  • @futuremoyo5714
    @futuremoyo5714 Рік тому

    Zinthuzi Mmmmm zovuta kotheka bambowo akuziwapo kenakache km mwana ndiwa mayiwo

  • @DianaManyaupa
    @DianaManyaupa Місяць тому

    Mwana ndiwabambowo nanga akuwakakamila choncho bwanji ndekt wawaziwa abambo ake

    • @FloraBanda-w7t
      @FloraBanda-w7t 14 днів тому

      😂😂😂😂😂akukakamiladitu ndikuona kut abambowa adagula kwasato

  • @floramtiwa211
    @floramtiwa211 Рік тому +2

    Satana akufuna kutisokoneza potumiza bamboyi cholinga tisakhulupilire ndalamayu si real human being ndiongotumidwa ndi Satana.

  • @user-vz8gi8lj1b
    @user-vz8gi8lj1b 5 місяців тому

    Mibawa pankhaniyi ndiyobasa chidwi koma wapakamwela sali bwino nkhani ikamafotokozodwa akamamuloza munthu kamela iziloza pamunthuyo, monga ngati ine ndimankhala chidwi ndikuonela pa on line

  • @user-cv2jj6bj8l
    @user-cv2jj6bj8l 6 місяців тому

    Mwana ndiwambambowo adsowa loweluka wapezeka monday chilungamo chenicheni

  • @user-xl4vz3tw9j
    @user-xl4vz3tw9j 5 місяців тому

    Abambo anachita kuguladi mwanayo munthu sungayiwale mwana wako kt ndi wanambala chani

  • @ntisungekachingwe2888
    @ntisungekachingwe2888 Рік тому +1

    Afufudzidwe bwino bamboyo chilipo chilipo chomwe akudziwa za imfa ya mwanayo

  • @user-be4jt3mh9k
    @user-be4jt3mh9k 10 місяців тому

    Bamboyo watumidwa nda asato plz chonde mwanayo asiyiren amayiwo ndiwawo abambowo ndimagwala amenewo apanga kut aziwakakamila Dala plz chonde mwana ndiwamai

  • @gelandmuwowo
    @gelandmuwowo Рік тому

    Am watching from kasama zambia

  • @user-pd2jq9rx3s
    @user-pd2jq9rx3s Рік тому

    Afananadi ndamayiwo ndiwawo m'dalayo amutuma

  • @MemoryLungu-sp8eq
    @MemoryLungu-sp8eq 3 місяці тому

    Mwana ndi wabambawo mayiyo wawo anamwalira

  • @luckychimutu
    @luckychimutu 5 місяців тому

    Umfiti ulipo ndithu ndipo anthu akuikidwa mmanda amoyo

  • @elizabethphiri8486
    @elizabethphiri8486 10 місяців тому

    Amayiwo anavomeleza kale asiyireni abambowo.

  • @tamaramhango2300
    @tamaramhango2300 Рік тому +3

    Akufanana ndinthu komanso mwanayo wazindikila bambo akewo.

  • @arronlusali400
    @arronlusali400 Рік тому

    Am watching from zambia make me to understand am behind .

    • @berthakambwiri6288
      @berthakambwiri6288 11 місяців тому +1

      This is complecated but you can only understand if you learn the language

    • @ephraimphiri5789
      @ephraimphiri5789 10 місяців тому

      ​@@berthakambwiri6288He's not Chewa like me....this is also our language in the eastern part of Zambia... Chipata/Katete, etc....

  • @kingmakala3919
    @kingmakala3919 Рік тому +3

    Mwanayo ndiwa bamboyo plz give him

    • @SarahPhiri-sh4ey
      @SarahPhiri-sh4ey 5 місяців тому

      I agree with you coz akukamila and 18yrs ago mwanayo akuoneka wachichepelebe

  • @user-li4tz1sw5z
    @user-li4tz1sw5z 6 місяців тому

    Akufana ndiabambo mwana uyu

  • @mercychiba4007
    @mercychiba4007 Рік тому +4

    Apopo chofunika ndi DNA

  • @GiboRashid
    @GiboRashid Рік тому

    Anamukwimila bamboyo akudziwapo kathu

  • @SandramBetha
    @SandramBetha Рік тому

    Akufanana ndi abambowo

  • @ireennyirends-qe4ge
    @ireennyirends-qe4ge Рік тому +2

    Lord have mercy

  • @mussayassin1235
    @mussayassin1235 Рік тому +1

    Mwana WA bambo wo mayiwo siwawo ayi

  • @berthakambwiri6288
    @berthakambwiri6288 11 місяців тому +4

    If someone can help to do DNA test it will help but i am doubting the man

  • @gomzmoyo2253
    @gomzmoyo2253 Рік тому +2

    DNA TEST BASI osati kumakangana ngati a galu opanda nzeru

  • @user-xf1gb5gu3z
    @user-xf1gb5gu3z 4 місяці тому

    Mwanayo ndi wa amayiwo, 100% actual truth coz there's no way kuti mwana wako akasowe kunyumba kwako. That man he's a ritualistic, ndi a msatowo they performed rituals that's why things are like that. Komanso as you can see, mwanayo was in a bondage she needs fasting and prayers to be set free indeed.
    I am Solomon in this case, the lost son in the bible returned to his family and by the grace of God the yoke is broked and now she has returned to her family. So let her be with her family where she belongs, that's her family. If you give the child to the man, you'll kill her and fulfill the man's rituals.
    Question; how did the man knows that the girl is in that village?
    Answer; the evil spirit of sato and the man that connects the two men, that yoke has to be completely broken.
    Please, don't take the daughter away from her mother family.
    Just keep the fasting and prayers for her, God must deliver her and set her free.

  • @JuvesSovelo-sb1mh
    @JuvesSovelo-sb1mh 2 місяці тому

    mdarayo akuziwakanthu mesa

  • @user-xf1gb5gu3z
    @user-xf1gb5gu3z 4 місяці тому

    Let that man go back to his village and home to live with his life and family.
    He's a fool who even doesn't know kuti mwana wakeyo ndi number chani kubadwa and he doesn't know her. He might be sing'anga wa a Sato, just watch out.
    People are wicked nowadays, so let us keep on praying for others. Kuno ndiye tizipemphera mpaka ena anapangidwa chipongwe apezekenso.

  • @MercyMubira
    @MercyMubira 8 місяців тому

    Mfumu solomon bweran mzaveso khani yina kuno

  • @tiongesoko772
    @tiongesoko772 Рік тому

    Nkhani yi yinatha bwanji

  • @blessingsmadela4936
    @blessingsmadela4936 Рік тому

    Mwanayo ndiwabambao, kumanso akulongosola bwino kuti sikoyamba mwanayu kusowapo, kusonyoza kuti anthu ammudzi mwabamboyu akumudziwa mtsikanayu, komaso ku police akuidziwa nkhaniyi

  • @jameszulu6920
    @jameszulu6920 Рік тому

    Uyo bambo ndi mfiti Ali ndi Malaya a msipu,itanani a singanga amuone

  • @AlbertoBernardoJoão
    @AlbertoBernardoJoão Місяць тому

    É daquele senhor

  • @JuvesSovelo-sb1mh
    @JuvesSovelo-sb1mh 2 місяці тому

    mwanao ndiwamayio bamboo ndiokhwima ameneo

  • @JudithBomba
    @JudithBomba 2 місяці тому

    Mamuna sabeleka mwana, mwanayo ndi amayiwo

  • @mirriamsoko1153
    @mirriamsoko1153 11 місяців тому

    Abambowadi ndi mfitidi👹 ndiekuti amenewa amatumikira nawo zawozo

  • @user-cv8xw5zx7y
    @user-cv8xw5zx7y Рік тому

    Iburahim jumms

  • @StellahMwangonde
    @StellahMwangonde Місяць тому

    Osawafunsa kuti mayi ake a mwanayo ali kutoko? Bwanji sanabwere nawo.

  • @mirriamsoko1153
    @mirriamsoko1153 11 місяців тому

    Mwinaso zipserazo mwina ankayamwitsa ndondosha za abambowa

  • @MAPAGASTUDIOS
    @MAPAGASTUDIOS 3 місяці тому

    Bqmboyo anamugura kubanjaku mmatsenga azimayiwo sakunama😅

  • @raphaelkapamba856
    @raphaelkapamba856 10 місяців тому

    Abambowa ndiwo akuyang'anila ana ku satanism,so atumiwa kuti amufune-fune,akalephera alpha iwowa ku satanic

  • @isaiahbeaton1816
    @isaiahbeaton1816 9 місяців тому +1

    Just do DN test

  • @ThomGideon
    @ThomGideon 3 місяці тому

    Ikuveka mopusa nkhaniyi, mot ngat mwana ndi abambowo bwanji akumudzi kwawoko ayikilepo umbon chifukwa it's obvious anthu kumudziko akumudziwa

  • @DaveChirwa-s4j
    @DaveChirwa-s4j Місяць тому

    Muphen mdara ameneyo asiye soputsa kupha athu

  • @user-xc9qx9jl9s
    @user-xc9qx9jl9s Рік тому

    Zovuta kwambir eish

  • @JoyceKaliza
    @JoyceKaliza 2 місяці тому

    Bamboyo akunama

  • @SiamePhiri-kc9jy
    @SiamePhiri-kc9jy 3 місяці тому

    Sia

  • @JabesiMwanza
    @JabesiMwanza 6 місяців тому

    Jabesi

  • @GloriaPhiri-b9f
    @GloriaPhiri-b9f Місяць тому

    DNA ndiyomwe iyenela kunena zowona kuti mwana mwini wake ndindani boma lichitepo kanthu pankhani imeneyo

  • @MkaiFrancisBendera
    @MkaiFrancisBendera 4 місяці тому

    Ash koma yah

  • @joycemkupa5566
    @joycemkupa5566 6 місяців тому

    Wawo bamboyo zikavuta DNA bas

  • @user-pe7pd8bg7j
    @user-pe7pd8bg7j 11 місяців тому +1

    Pakufunika experience doctor ayeze DNA

  • @SiamePhiri-kc9jy
    @SiamePhiri-kc9jy 3 місяці тому

    Siamephiri kc9jy 10:37
    P

  • @user-oz3ks2kd9y
    @user-oz3ks2kd9y 5 місяців тому

    God protect them

  • @RachealMwale-bo8pw
    @RachealMwale-bo8pw 3 місяці тому

    Zingatheke nimadiku osiliza ano

  • @gesinasutherland9241
    @gesinasutherland9241 Рік тому +1

    zomvetsa chisoni

  • @ChikoMs
    @ChikoMs 7 місяців тому

    Bamboyo obvious mwanayo ndi wake

  • @berthakambwiri6288
    @berthakambwiri6288 11 місяців тому

    Munthu akaphedwa mwa nyanga ndiye munthu amene wamupha uja akafa nyanga zonse zimaululika komanso mankhwala onse amaululika ndiye anthu onse anaikidwa mnyumba ya a msato atulukira onse tsopano....please update what happened to those people who is their parents

  • @madalitsomofolo-ob3wy
    @madalitsomofolo-ob3wy 10 місяців тому

    Madala mwana ndwawo

  • @user-co9pg4zv2x
    @user-co9pg4zv2x 9 місяців тому

    Remember, we are in the end-time

  • @enerstAnderson
    @enerstAnderson Місяць тому

    E able zamasiku osiliza

  • @futuremoyo5714
    @futuremoyo5714 Рік тому

    Koma fuso la2 zinatha bwanji koma

  • @mathiasmajamanda5797
    @mathiasmajamanda5797 Рік тому

    Abel ulibho umatha kuitsata nkhani ndipo umatha kufunsa mafunso

  • @ayamijackson1443
    @ayamijackson1443 Рік тому

    Mmmm zovetsa chisoni koma athufe bwanji timafuna kulemela mwachidule izitu sizabwino mmmm mulungu azititeteza ndikutikhilulukila kwambili

  • @TawongaMabindi-yy1qx
    @TawongaMabindi-yy1qx 10 місяців тому

    Panopa alikt

  • @packsleysani6534
    @packsleysani6534 5 місяців тому

    Ku malawi nkokoma

  • @mustafaibrahim4504
    @mustafaibrahim4504 Рік тому +1

    DN ilowepo

  • @StellahMwangonde
    @StellahMwangonde Місяць тому

    DNA ikufunika

  • @user-xc9te6fu7d
    @user-xc9te6fu7d 5 місяців тому

    D.N.A test

  • @ShahidaIshmael
    @ShahidaIshmael 3 місяці тому

    Mawuamenewo D NA bas

  • @MiriamBenartChisale
    @MiriamBenartChisale 23 дні тому

    Where is the mother of that girl

  • @user-gg6px7rt8u
    @user-gg6px7rt8u 9 місяців тому

    Good

  • @BlessingsWakhutamoyo
    @BlessingsWakhutamoyo 2 місяці тому

    UDF

  • @harryevanceharryevancekabula
    @harryevanceharryevancekabula Рік тому +2

    Kodi eni mwana anadziwika?

  • @BrendaEnerst
    @BrendaEnerst Місяць тому

    amuwone achipatara ngati anabelekapo umbon ndiosavuta apa

  • @anniewhite3497
    @anniewhite3497 Рік тому

    Mwanayo ndi wamayiyo akufanana ndithu ,bambowo chilipo apanga mwanayo kuti adzakakamira DNA iyendepo

  • @SamuelNandolo-nc2mo
    @SamuelNandolo-nc2mo Рік тому

    Zoopsatu zimenezi mmmmmmmm

  • @MahamooduAjati
    @MahamooduAjati 8 місяців тому

    Fantastic story 😂

  • @user-tt8pr1om4t
    @user-tt8pr1om4t 10 місяців тому

    Akafukule kumanfa skawone ngati mmandamo mulibe mafupa

  • @afritouch4660
    @afritouch4660 Рік тому

    Angowafunsa kuti abambowo awawonetse picture..! Komanso kuti ali ndi dzaka zingati?

  • @AthenkosiManya
    @AthenkosiManya Рік тому

    Zoopya eti

  • @RachealKapalamula
    @RachealKapalamula 11 місяців тому

    Abambowo alindimabodxa