#PROFESSOR_HASSAN_SAID_ZAMBIA

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 14 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 204

  • @MoosaSame
    @MoosaSame 2 місяці тому +7

    I am proud from Christian to be Muslim ☪️ ❤❤❤

  • @GoldenBarnet-hv3wj
    @GoldenBarnet-hv3wj 3 місяці тому +7

    Am proud to be a Muslim,Allah is great

  • @GiftBonomali
    @GiftBonomali 3 місяці тому +5

    Allah bless you professor mashalah❤❤❤

  • @BysonBanda-z8q
    @BysonBanda-z8q 2 місяці тому +2

    I am proud to be a Muslim

  • @MtengowaPadambo-ub4ji
    @MtengowaPadambo-ub4ji 27 днів тому

    Please upload another episode

  • @idreesahjafari5093
    @idreesahjafari5093 26 днів тому

    I am proud to be a Muslim Alhamdulillah ❤❤❤

  • @FayazNhlema
    @FayazNhlema 2 місяці тому +4

    Ndinali msilamu koma ndinasiya Chisilamu nditazindikira kuti YESU ndiye njira yowonadi.

    • @EdwardZuze-r7w
      @EdwardZuze-r7w 2 місяці тому

      Mulungu akudalitseni kwambiri, munapanga chisankho chabwino.

    • @HakeemJossam
      @HakeemJossam 2 місяці тому

      munali msilamu koma Osazindikila kungopitako poti makolo Anu amkapita kumeneko

    • @EdwardZuze-r7w
      @EdwardZuze-r7w 2 місяці тому

      Ambuye akudalitseni chifukwa ndi ochepa amene akumaona patali mu uzimu, ambiri ali komweko chifukwa anabadwila momwemo kapena makolo awo anawasiya mzikiti omwe anamanga,
      ambuye akuthandizeni in everything especially moyo wanu wa uzimu

    • @felixsaidi6715
      @felixsaidi6715 Місяць тому

      Dzivere chisoni m'bale wangaa. Akati Islam mean, kuchita chifunilo cha Mulungu. Ndemukamati munatuluka chisilam, mudziwe kuti munasiya kumugonjera Mulungu. Tsopano mukutsatira satana yemwe wasochoretsa anthu ambiri padziko lonse lapasi

  • @clesheinvestments
    @clesheinvestments 3 місяці тому +6

    Alhamdulillah kuti ndine Msilamu.
    Ma videos ngati awa adzipezeka ndithu pa UA-cam.
    In so doing zithandizira uthenga wa Allah kufikira ena omwe ali kutali mosavuta

  • @SUWEDSHAMWKUPE
    @SUWEDSHAMWKUPE 2 місяці тому

    Allihamdulilah to be a Muslim my dad please protect pokhala slamu paka ifa

  • @MussaMalon
    @MussaMalon 2 місяці тому +1

    Mashallaah Sheikh mulungu akudalitseni ❤.

    • @blessingsdouglas3
      @blessingsdouglas3 2 місяці тому

      Aaaaaaa ine saidi Zambia nakhala nayepo ndi tambwali uyu

  • @mickchiliko2796
    @mickchiliko2796 3 місяці тому +2

    Alhamdulillah am proud to be Muslim. May Allah guide me and protect me In shaa Allah.

  • @TennisMatandika
    @TennisMatandika 22 дні тому

    I'm proud to be a Muslim

  • @ChrispinLunda
    @ChrispinLunda 2 місяці тому +2

    Zamasiku otsiliza amenewa ndiwo omkana yesu aja zimene munthu udakhazikikamo sikopheka kukusutha amenewa simungawauze za mzimu oyela sangave ndiwo umaulula umazindikilitsa umaphuzitsa ngat ulibe mzimu oyela ungalive baibulo ukamaliva kuthupi mzimenezo zovetsa chison ambuye akuzindikilitsen amen

    • @tauhidtimba
      @tauhidtimba 2 місяці тому

      Kumva chichewa umafunikira kukhala ndi Zimu oyera kod?

    • @chiogamata2560
      @chiogamata2560 2 місяці тому

      Ine anthu inu mmandiwaza apapa
      Kumva language yako yomwe zufunaso nzimu oyela??
      Kukuuza kut iyo ndi kapu yomwela madzi, sumva coz ulibe nzimu oyera??
      This thing of nzimu oyera, koma mmaudziwa, mungaufotokoze ndi malemba maumboni??
      Concept iyiyi eeeeti eeeeeeish mumadyera guys 🤣🤣🤣🤣🤣

    • @sharifhenderson6982
      @sharifhenderson6982 2 місяці тому

      Mzimu oyelawo anaulenga ndan??? 😂😂😂

    • @sharifhenderson6982
      @sharifhenderson6982 2 місяці тому

      ​@@tauhidtimbakayatu 😂

    • @ALICKMASANGANO
      @ALICKMASANGANO 2 місяці тому

      Mmm baba moti ma verse akupereka muthuyu si amu bible

  • @EmmanuelstoneyJere
    @EmmanuelstoneyJere Місяць тому +2

    Afarisi a lero ndamenewa ntchito yao nkuphwekesa Yesu basi

  • @MpondaBanda
    @MpondaBanda 2 місяці тому +1

    Alhamdu lillah proud to be one hu follows Allah's submission

  • @SuperSave-r8u
    @SuperSave-r8u Місяць тому +1

    Allah akbar

  • @EdwardZuze-r7w
    @EdwardZuze-r7w 2 місяці тому +1

    Hohn 14 v 6, Yesu anati ine ndine njira choonadi ndi moyo.
    palibe munthu adza kwa atate koma mwa ine.
    Most of theses things brings conflicts among peoople, Palibe mpikitsano pa mawu a mulungu

  • @KassimIssa-bn3od
    @KassimIssa-bn3od 2 місяці тому

    Mashalla Allah ndi silamu ndipo tikuphemba kwa Allah ndizafe ndi silamu

  • @ghadaffmoosa7535
    @ghadaffmoosa7535 2 місяці тому

    Ma sha Allah may Allah bless u sheikh SAID HASSAN ZAMBIA

  • @HarleemahJamesMatolah
    @HarleemahJamesMatolah 16 днів тому

    ❤❤❤Mashallah

  • @swalienkhumbwa7338
    @swalienkhumbwa7338 19 годин тому

    I am proud to be Muslim

  • @KhadijaJambo
    @KhadijaJambo 2 дні тому

    Proud to be a muslim❤❤❤

  • @BesterMagetsi
    @BesterMagetsi 25 днів тому

    Alihamudulilah ine kukhala msilamu

  • @UmarAjussu
    @UmarAjussu 3 місяці тому +3

    Allah akudaliseni ma sheikh nonse

  • @ishmaelmadalet2591
    @ishmaelmadalet2591 2 місяці тому

    When was this debate held

  • @RedsonRichard
    @RedsonRichard 3 місяці тому +7

    Nthawi yatha amsilamu inu musasokoneze choonadi

  • @promisemakawa1556
    @promisemakawa1556 3 місяці тому +2

    Im proud to b Muslim, mpaka imfa idzanditenge ndili msilamu

  • @FathimaMa2
    @FathimaMa2 3 місяці тому +1

    Alihamudulilahi kwaine mpakana kwa asilamu ose pano pa dhunia mashaalhaa

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 3 місяці тому +1

    I am proud to be a muslim ,
    Komafunso langandiloti ,
    Ndichifukwachani Muhammad timamupemphela chikhululuko komanso madaliso kwa mulungu ?
    Kodi Muhammad ndi azibale athu omwe anamwalila oyenela kuwafunila zabwino kwa mulungu ndindani ?

    • @JohnstoneMwandira
      @JohnstoneMwandira 3 місяці тому

      Dzina la mtumiki Muhammed likatchulidwa timanena kuti swalalah alaih wasalamah,( meaning , mtendere ndi madalitso amulungu apite kwa iye).
      Zimenezi even zimachitikaso kwa Azitumiki ena onse . Issah(Yesu) ndiye timati Alaih Salam Wasalatuh(Meaning, madalitso amulungu apite kwa iye).
      Nde zimenezi zimanenedwa kwa mtumiki winaaliyese akatchulidwa dzina.

    • @rashidadan2533
      @rashidadan2533 3 місяці тому

      @@JohnstoneMwandira ok , ndichifukwa chani okhala atumiki a mulungu timawafunila mtendele ndi madaliso , chikhalilenicho anapanga ntchitoya mulungu .

    • @JohnstoneMwandira
      @JohnstoneMwandira 3 місяці тому

      @@rashidadan2533 Zimenezi akulamula ndi Mulungu akuti mfunireni zabwino mtumiki wanu. Nde Ife ndindani kukanira.

    • @AndersonBishop-i2t
      @AndersonBishop-i2t 3 місяці тому

      Iweso sisilamu tachoka apa

  • @HarnetJauma
    @HarnetJauma 2 місяці тому

    Am proud to be a Muslim ❤

  • @Chayibujackison
    @Chayibujackison 2 місяці тому

    Mashah allah sheikh awuzen ndithu❤❤❤

  • @JUBRANBULAYHl-yb4ke
    @JUBRANBULAYHl-yb4ke 3 місяці тому

    Mwenyezi Mungu, hapana mungu ila Yeye, Aliye hai, Msimamizi wa milele, Amekuteremshieni Kitabu kwa haki, kinachosadikisha yaliyokuwa kabla yake, na ameteremsha Taurati na Injili kabla yake kuwa ni uwongofu kwa watu. Na akateremsha upambanuzi: Hakika walio kufuru Ishara za Mwenyezi Mungu watapata adhabu kali, na Mwenyezi Mungu ni Mwenye nguvu, Mwenye kulipiza kisasi wewe katika Mwingi wa rehema, vipi hakuna mungu ila yeye ni mpendwa, Mwenye hikima ni yule aliyeteremshiwa kwako Ama waliomo nyoyoni mwao wanafuatwa Hawakusema kuwa kila mmoja Kwa Mola wetu Mlezi. na hawakumbuki ila wenye akili, tusipotoke nyoyo zetu baada ya kutuongoza bila shaka Mwenyezi Mungu hatavunja ahadi yake, mojawapo ya makusudio ya surah.
    Kudumu katika Uislamu baada ya ukamilifu na ubainifu wake, na kukanusha shaka za Watu wa Kitabu, hususan Wakristo
    Ni surah ya Madina iliitwa Surah Al Imran kwa sababu familia ya Imran imetajwa ndani yake katika aya ya surah.
    Herufi hizi zilizotengana zimemtangulia mwenzao katika Sura Al-Baqarah, na zinaonyesha kutoweza kwa Waarabu kutoa Qur’ani kama hiyo ingawa inaundwa na herufi ambazo Sura ilianza nazo, na kutoka kwao wanatunga hotuba yao.
    Mwenyezi Mungu ndiye ambaye hana mungu wa kuabudiwa kwa haki isipokuwa Yeye pekee na hakuna mwingine aliye hai ni maisha makamilifu yasiyo na kifo au upungufu.

  • @dennismachemba9514
    @dennismachemba9514 2 місяці тому

    Masha Allah may Allah Grant him jannat firdaus

  • @IbrasyaicheWizyx
    @IbrasyaicheWizyx 3 місяці тому

    Alhamdulillah for choosing me to be a Muslim❤

  • @Lionelmosse
    @Lionelmosse 2 місяці тому

    Allahmdulillah ❤❤❤❤❤❤

  • @YusufuYunusuSavielMakey
    @YusufuYunusuSavielMakey 2 місяці тому +1

    Masha Allah pondipanga kukhara msilam ❤

  • @mariamhassan6788
    @mariamhassan6788 3 місяці тому

    Proud to be a Muslim Alhamdulilah ❤

  • @frankkasamala6956
    @frankkasamala6956 2 місяці тому

    We need you here at ntonda in ntcheu

  • @muhammadisaid3968
    @muhammadisaid3968 Місяць тому

    Mashallah

  • @cassimmeleka40
    @cassimmeleka40 2 місяці тому

    ان الدين عند الله الإسلام

  • @raphicallan5331
    @raphicallan5331 2 місяці тому

    Proud to be a Muslim

  • @LUCKYM4787
    @LUCKYM4787 3 місяці тому

    Manshaallah brother

  • @GiftSinalo-ku6zb
    @GiftSinalo-ku6zb 2 місяці тому

    Alhamudulillah to be a Muslim

  • @JohnAsendi
    @JohnAsendi 3 місяці тому

    Dawa koma imeneyo osati zakuti Achibeketi adali mfiti adakuphera agogo ako muzichita Dawa yolimbana ndi amene Sali Asilam timakunyadiran big kep it up

  • @tomthompson4429
    @tomthompson4429 2 місяці тому

    Where is the other part of Seventh Day part? Let's PRAY that each one of us here on Earth meets GOD's Grace and know the truth, I Pray for you my muslim brothers. Amen

  • @JazraJeffm
    @JazraJeffm 2 місяці тому

    I'm proud to be a musilim

  • @BindulaMtambo
    @BindulaMtambo 3 місяці тому

    Mashallah, please upload some more

  • @AfredMbeta-pk1cn
    @AfredMbeta-pk1cn 3 місяці тому +2

    Ndizomwe timadikilira,go ahead

  • @UlandaHarjisonstone
    @UlandaHarjisonstone 2 місяці тому

    Allihamdulillah pokhala msilam chonde Allah muzanditenge ndili msilam

  • @YAZIDU-l9s
    @YAZIDU-l9s 2 місяці тому

    Allahu Akbar. Ma sha Allah. Na am ❤❤😂

  • @BornwellOtala-dm1zm
    @BornwellOtala-dm1zm 3 місяці тому

    ❤Ma shaaAllah

  • @JafaliChiwimbi
    @JafaliChiwimbi 21 день тому

    Marshall

  • @UmariBashiri
    @UmariBashiri 3 місяці тому

    Ma Sha AllAh Amee

  • @martinchimwala
    @martinchimwala 2 місяці тому

    Proud to be Muslim

  • @AnthonyLushu
    @AnthonyLushu Місяць тому

    Komatu a seneth day mwapanga zopoira mwaganiza ngat nkhuku pomunyozensa yesu mulungu akukanthen inu pamozi ndi a siramu anuo sipangakhare ntendere pakat pa asiramu ndi khrisitu

  • @omarmanduwa4127
    @omarmanduwa4127 3 місяці тому

    MAA SHAA ALLAH

  • @YatoRoy-kt4lh
    @YatoRoy-kt4lh 3 місяці тому

    I once met this Saidi Zambia for almost 8 hrs.
    Anafika pokwiya titamufotokozera zinthu zomwe iye samadziwa za chiyambi chachisilamu ndipo anakwiya heavy.
    Amene mumamudziwa ask him za anyamata omwe anakumana nawo usiku mnyumba ina ku mangochi.
    He ended up a failure on that meeting.

    • @GiftStephano
      @GiftStephano 2 місяці тому

      Chinayamba bwanji tiziwe nao

  • @mramir.s.smkubwa3985
    @mramir.s.smkubwa3985 2 місяці тому

    Komano kunena chilungamo Alhamdulillah asilamu mulungu anawapasa mzelu ndithu

  • @SaymonMawaya
    @SaymonMawaya 2 місяці тому

    Maashallah

  • @AshrafSaidi
    @AshrafSaidi 3 місяці тому

    Jazakum llah khaira

  • @AsanteBilly
    @AsanteBilly 2 місяці тому

    MashaAllah ❤❤

  • @khadijailiyasa5315
    @khadijailiyasa5315 3 місяці тому +2

    Kodi simungayike apapa dawa yonse please tikuyifuna

  • @ElickBanda
    @ElickBanda 2 місяці тому

    Ma shaallah

  • @Shelifibraheem
    @Shelifibraheem 3 місяці тому

    Ameen thummah Ameen

  • @AbgirlChinheya
    @AbgirlChinheya 2 місяці тому

    Alihamudulilah❤

  • @peterkinsLekera
    @peterkinsLekera 3 місяці тому +1

    Kwamuthu yemwe sawerenga ndikutsata za zipembedzo adupha nkhani zonse ndikumangosankha momwe akufuna pokwanilitsa zolinga zanu koma choonadi mukuchidziwa

    • @AustinManes-m3w
      @AustinManes-m3w 3 місяці тому

      Pelekan lemba nanu

    • @chiogamata2560
      @chiogamata2560 2 місяці тому

      Pelekani zomwe mmawelenga inuzooo
      Ndanga izi zikuchoka mmitu mwao ngat?? 🤣🤣🤣🤣🤣

  • @Chayibujackison
    @Chayibujackison 2 місяці тому

    Mashah allah ❤ ♥ 🙏

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp 3 місяці тому

    Macha hallah ❤❤

  • @OmrahGeraldOmrahGerald
    @OmrahGeraldOmrahGerald 3 місяці тому

    MASHA ALLAH MASHA ALLAH MASHA ALLAH

  • @JummahbinhoPartison
    @JummahbinhoPartison 3 місяці тому

    Salaam aleykum...video muzimalidza osamayidula

  • @danielmangalisobanda8356
    @danielmangalisobanda8356 2 місяці тому

    Mr Hassan munaphunzira koma ndinu mbuli yothelatu kuuzimu ndichifukwa chake mukupembedza wovumbulutsa Quran naganiza ndikukhulupilila kuti mukupembedza Mulungu wamoyo, chonsecho ndiSATANA weniweni adamunamidza muhammad kuti ndiiyeyo adili kuvumbulitsila aneneneli amuBible

  • @MariamJaffali
    @MariamJaffali 3 місяці тому

    Ma shaa Allah

  • @SulaimanaKanot
    @SulaimanaKanot 2 місяці тому

    Allah Akbar

    • @hermesmbendera9860
      @hermesmbendera9860 2 місяці тому

      Pliz pliz fellow Christians, don't be deceived nor mislead with these anti Christs. Jesus dead upon the cross to save mankind from the wrath of sin. He was crucified for our sins and resurrected for our justification.

  • @ElizabethKazambwe
    @ElizabethKazambwe 3 місяці тому +1

    Chiweluzo chidzapelkedwa chifukwa Cha zintchito zarhu osati proud to be a Moslem or proud to be a chriastian nzopanda pake

  • @AbdullahRight-ld2vv
    @AbdullahRight-ld2vv 3 місяці тому

    Ma sha Allah ❤❤

  • @ShaibuJackson
    @ShaibuJackson 2 місяці тому

    Mashaalla

  • @abhentomwcmwanjeza5771
    @abhentomwcmwanjeza5771 3 місяці тому

    MaShaallah

  • @HarryChindiwo
    @HarryChindiwo 2 місяці тому

    Nawe hule Zambia ukuziona ngati ndi mngero

  • @RashowLajabuh
    @RashowLajabuh 2 місяці тому

    ❤❤❤❤❤❤

  • @AbdurashidAhmad
    @AbdurashidAhmad Місяць тому

    Tiyeni tafunile zabwino zonse makolo athu omwe anayima pakati pachowonadi chisilamu omwe alimoyo mpakana omwe anasogolera kale kumanda mulungu awapatse jan'na please

  • @ThokozaniChadza
    @ThokozaniChadza 3 місяці тому

    Mashaa llah

  • @IssahNgalinje
    @IssahNgalinje 3 місяці тому

    Mashaa Allah sheikh ❤❤

  • @GiftTwaya
    @GiftTwaya 3 місяці тому

    Allah akbr

  • @KassimShaibu-f6h
    @KassimShaibu-f6h 3 місяці тому

    Machalawu

  • @UseniMailosi
    @UseniMailosi 3 місяці тому

    Mashaah Allah

  • @MussaLameck
    @MussaLameck 2 місяці тому

    Alihamdulilahi

  • @JafaBulhm
    @JafaBulhm 3 місяці тому

    Masha Allah Allah Akibari

  • @HalimTalim
    @HalimTalim 3 місяці тому

    Alhamdulillah

  • @masebermsanga7623
    @masebermsanga7623 3 місяці тому

    Masha Allah ❤

  • @YusufAdam-n8z
    @YusufAdam-n8z 3 місяці тому

    Masha Allah

  • @SwaibaMussah
    @SwaibaMussah 2 місяці тому

    Mashaallah

  • @IssahNgalinje
    @IssahNgalinje 3 місяці тому

    Sheikh musiponya zambili kuti tizinva zambari chonde chonde ❤❤

  • @MathpeterLemon-ls1ns
    @MathpeterLemon-ls1ns 2 місяці тому

    Asilamu olambila mwala wa ku arabia saudi dzipumi biii ngati zoona

  • @HaliJana
    @HaliJana 2 місяці тому

    MULUNGU AKUONJEZELENI MASIKU AMOYO WANU ADALISESO MU MZELU ZANU

  • @DIMZYRECORDS
    @DIMZYRECORDS 2 місяці тому

    Minika ❤❤❤❤

  • @SABITISABITI-yv9jq
    @SABITISABITI-yv9jq 3 місяці тому +1

    🕋🕋🕋🕋🕋☝️☝️

  • @AustinManes-m3w
    @AustinManes-m3w 3 місяці тому

    Mashaalah

  • @MadalitsoWillson
    @MadalitsoWillson 3 місяці тому

    ❤ mashaallah

  • @EdwardZuze-r7w
    @EdwardZuze-r7w 2 місяці тому

    Anthu timasokoneza pakati pa Mulungu ndi Alla, palitu kusiyana kwakukulu, ndipo mudzadzindikira koma mochedwa kusiyana kwa awiriwa

  • @LacksonLungu-e2q
    @LacksonLungu-e2q 3 місяці тому

    Kampen kumphatsa koma mmm pot mwati yesu ndee yesu basi Kaya silam Kaya Christi ndi yesu basi.