Fredokiss Ndi Felix Njawala Speech ''UTM SiYaPa Facebook Mulira Nayo"'

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 5 жов 2024
  • Fredokiss Ndi Felix NjawalaPa Msokhano wautm

КОМЕНТАРІ • 30

  • @ishakatimbe7341
    @ishakatimbe7341 4 місяці тому +1

    Utm ili ngt Eff or patavuta bwanji singawine.... Adad my vote❤❤❤

  • @OliverChimsewu
    @OliverChimsewu 5 місяців тому +2

    I prefer UTM to take the charge of the country.enawo analamulirapo komanso anatiphera abale athu.kodi mukufunanso kuti azakutheni?wina adanena kale kuti amalawi samachedwa kuyiwala

  • @AishaChibwana-b8o
    @AishaChibwana-b8o 4 місяці тому +1

    SKC my vote 2025 BOMA ❤❤❤

  • @AishaChibwana-b8o
    @AishaChibwana-b8o 4 місяці тому +1

    Utm 2025 BOMA ❤❤❤❤

  • @stanleykaludzu-bm4pm
    @stanleykaludzu-bm4pm 5 місяців тому +2

    UTM bomaaaaaaa

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 5 місяців тому +2

    Zopusa zanuzo ifee ai nkhani ndi DPP

    • @EmmanuelNtago
      @EmmanuelNtago 2 місяці тому

      Kunyoza UTM is same as kunyoza DPP aise,,nd amoz awa,,,muona kusogoloku akudyera mbale imozi,,,Inu muzakhumudwa,,UTM ndi mwana wa DPP

  • @Jasonnyatwa
    @Jasonnyatwa 4 місяці тому

    MCP mukhaula sizinaoneke ndalama zanuzo tidya mwaulele, UDF my vote

  • @KondwaniLungu-x5l
    @KondwaniLungu-x5l 5 місяців тому

    Iiiii koma guys moti utm simunaiphunzilebe ? Moti mukuembekezela kuti kuipasa mpata itha kuthandiza zikoli ndikuiphula pa moto? Aaah kwa ineyo ndi kukaika kwambili anakakhala kuti azisogoleri akewa ndi okhuzika ndi kuvutikwa kwa amalawi payamba pompaja amaenela kuonesa chidwi pa kuvutika kwa amalawi osati pano achedwa . Ndi amozi utm mcp aford ndi sangathandizeso zikoli believe me guys let's wait and see.

  • @KondwaniLungu-x5l
    @KondwaniLungu-x5l 5 місяців тому

    And tonse alliance ya pangisa kuti lero tiziganiza kuti Dpp iwoneke ngati anali ma dolo pamene nawonso pa level yawo anafikaposo posakhala bwino kuwatenga amalawi for granted that's bad koma to me zinakhala bwino kuchosedwa mwina ngati angapasidweso mpata aphunzilepo kuti osauka akakwiya si zienda bwino.

  • @PatrickGonagona
    @PatrickGonagona 5 місяців тому

    APM my vote 2025

  • @SHEREEFKanthochi-ft3dm
    @SHEREEFKanthochi-ft3dm 5 місяців тому

    Komatu kuwina kulibe kaya mukudziwa?

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 4 місяці тому

    Za ziiiii kumasapotaso mbamva imeneyi odi apo DPP tiduse iya mavuto wosewa mwayiwara

  • @Zamwano
    @Zamwano 4 місяці тому

    Inu ngoimba basi zinazi mmmmm

  • @Aisha-db6ds
    @Aisha-db6ds 3 місяці тому

    Atsogoleli ake opanda mfundo

  • @SanudiMcDonald
    @SanudiMcDonald 2 місяці тому

    DPP singawine payokha popanda chipani china chothandizira 🤞

  • @kondwanimunthali7401
    @kondwanimunthali7401 5 місяців тому

    A DPP kuzikonda too much.Boma simuzatengaso

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 5 місяців тому

    APM for ever ❤❤❤❤❤

  • @chrisschikozera7271
    @chrisschikozera7271 5 місяців тому

    😂😂😂😂😂........osazivuta chilima ll never be president in this country

  • @FrancoKaunga-rq2ki
    @FrancoKaunga-rq2ki 5 місяців тому

    Unless you end chewa language in schools

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 5 місяців тому

    APM Bomaaaaaa iloooo

  • @EdwardRichman-zs5pl
    @EdwardRichman-zs5pl 5 місяців тому

    Munalamulako kd ku utm chipani ichi chinthela malangizo bas

  • @cosmasnkanda8193
    @cosmasnkanda8193 5 місяців тому

    APM my voti basi

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 5 місяців тому

    DPP pachiongolero ❤❤❤❤❤

  • @EvanceWame-v7v
    @EvanceWame-v7v 5 місяців тому

    Zowanamiza anthu zisiyike wamva ulendo uno zikuvutani

  • @jamesgama5489
    @jamesgama5489 5 місяців тому

    Mcp ulendo waku kenani kupita okha. Anzanu a UTM kuwasiya kwa pilato zaka zonsezi kumakamvera milandu, DPP tilinayo limodzi ku bagamoyo kuno.

    • @KondwaniLungu-x5l
      @KondwaniLungu-x5l 5 місяців тому +1

      Ngati Dpp ingapasidwe mwai akuenela kukonza mavuto amene anapangisa kukhala kunja kwa boma ndithu , koma ine all tonse alliance pano olo zitatani bwanji si ndingaikhulupilireso why zaonesesa kuti onse zawo ndi zimozi kuzunza ovutika basi olo kupeleka mpata kwa chilima sangasinthe chilichose azingoikilana ku mbuyo zo pusa zimene akupanga chakwela.

  • @user-lf6qf2tw5o
    @user-lf6qf2tw5o 5 місяців тому

    Mbava zachabe

  • @jamesgama5489
    @jamesgama5489 5 місяців тому

    Chipani chopanda strong hold

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 5 місяців тому

    Chipan Cha anthu a chamba