SYMON AND KENDALL ALOWA CHIPANI CHA MCP NDIPO AIMBA NYIMBO IYI KU NSONKHANO WA MCP LERO LIVE LIVE

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 29 гру 2024

КОМЕНТАРІ •

  • @HopeKeyz-pr5pw
    @HopeKeyz-pr5pw 2 місяці тому +6

    Mkasa ndi zanyimbo iiiii kuswakuswa.koma Dpp my vote💙💙

  • @EmelesiyaYohane
    @EmelesiyaYohane 22 дні тому

    Tiona 2025

  • @Jane-qb5qf
    @Jane-qb5qf 2 місяці тому +11

    Amalawi osadandaula kumwamba kuli mulungu pomwe lafika dziko lamalawi mkumayimbira mmanja izizi aaaa chizaziwe ndichipande poomola

  • @DavieChamasowa-p1g
    @DavieChamasowa-p1g 2 місяці тому +7

    Zikafika apa umangodziwa kuti ndalama za satanic zaphweka. Dear Grace Chinga. May Your Saul Keep Resting. Still Love You.

    • @EdsonChikanga
      @EdsonChikanga 12 днів тому

      Koma ñdiye cadet ukumva kuwawa kwambiri

  • @LekeleniWilfred
    @LekeleniWilfred Місяць тому +3

    Boma ndilomweli km tingositha president bass APM my vote❤❤

    • @ChipiliroSemu
      @ChipiliroSemu Місяць тому

      Nde apart from chakwela kulinso wina??? Nde mbola zeni zeni

  • @annievitumbikonkhoswe770
    @annievitumbikonkhoswe770 10 днів тому

    Symon mwanenepa tu. MCP yomweyo 🎉

  • @KondwaniKazako-m3d
    @KondwaniKazako-m3d 2 місяці тому +3

    My message Is vote ndi mtima 😂😂😂😂

    • @TsArKhaii
      @TsArKhaii 29 днів тому

      Tell them, ife phee😂

  • @DorothyZimba-s2x
    @DorothyZimba-s2x 10 днів тому

    Boma ndilomweli sitikusintha❤❤

  • @PeterPhiri-nd6op
    @PeterPhiri-nd6op Місяць тому +2

    Ndalama ndi satana koma ine my vote dpp❤🎉

  • @EasternMusango
    @EasternMusango 2 місяці тому +2

    Nyimbozi nthawi ina zizakulilitsani,,,

  • @RichardKuden
    @RichardKuden 18 днів тому

    Ndalama ndizowopsa kwambili😢😢😢😢

  • @PiliraniChalamanda65
    @PiliraniChalamanda65 2 місяці тому +2

    Kuli oyimba osangalasa koma athu sakuwoneka kt akusangalala zomwe zikungowonesa kt athu MCP sakuyifuna nokha mukawona misokhano ya DPP sikukumakhala oyimba koma athu kuzaza kusangalala

    • @TsArKhaii
      @TsArKhaii 29 днів тому

      Anthu atopa ase😂

  • @AnthroGondwe
    @AnthroGondwe День тому

    Chakwera arolela kare khondo iye akuopa ifa za achilima akuziwa kut akaferuka alimumazi so akupanga zoti zichitike zichitike

  • @nathannyirenda1477
    @nathannyirenda1477 17 днів тому

    Boma ndilomweli 🔥 ❤❤❤❤❤❤

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete 7 днів тому

    UDF 😂😂❤❤❤ manganje akwathu ku zomba awa ngwesile ja atupele 🇲🇼

  • @Bless-ws6rf
    @Bless-ws6rf Місяць тому +1

    Nkasa unakanisisa kuti suzayimbaso zachipani nanga lelo bwanji ukuyimbaso unanena pamaso pa joab chakhaza cruise 5

  • @DeborahEfudala
    @DeborahEfudala 16 днів тому

    Chakwera emweyo akupitiliza my vote mcp

  • @IbrahimIsmael-h2w
    @IbrahimIsmael-h2w 27 днів тому +1

    Kwakakamiza anthu😂😂boma lakupha ili

  • @nathannyirenda1477
    @nathannyirenda1477 17 днів тому

    Boma ndilomweli 🔥

  • @nathannyirenda1477
    @nathannyirenda1477 17 днів тому

    Boma ndililomweli ❤❤❤❤❤❤

  • @NoelNthala-d6b
    @NoelNthala-d6b 28 днів тому

    Chakwera 2030 woooooo

  • @SteveSpeack-u2s
    @SteveSpeack-u2s Місяць тому +1

    2025 APM my vote

  • @ShamaxNyirenda
    @ShamaxNyirenda 2 місяці тому +1

    Mwakonda ndalama za anthu mulibe nazo ntchito vote Dpp

  • @IsaacWilliam-y8d
    @IsaacWilliam-y8d 20 днів тому

    Waitha kwambili nyimboyi ili very hot amenyele kampeni adadi

  • @asantemkwinda6658
    @asantemkwinda6658 28 днів тому

    Mukuwauuza anthu aziyankha zopusazi zoti akachoka pamenepo akukagona osadya simukudziwa? KABAMBE MY VOTE

  • @AnusaMponda
    @AnusaMponda 2 місяці тому +1

    U president ndi business guys no one can come and mkutivetsa kukoma ndipo zomangosintha zipanizii ndiye dziko tizingoononga basiii nkhani ndiyomwe ija chipani chimodzi kumangosintha atsogoleri koma zathuziii mmmm aliyense angosiya ngongole kuti nzawo anve kuwawa komwe kuli. Kupweteketsa amalawi kum'bwezelera ngongole wina siii easy apa tili nyengo zovuta basi 😢😢

  • @GabrielJosua-r2y
    @GabrielJosua-r2y 2 місяці тому +1

    Kukwera yakumpwa uchitsiru suuntha ndi xchool ndi xoona

  • @IdirissaCharles-s8g
    @IdirissaCharles-s8g 2 місяці тому +7

    Dpp my vote ❤❤❤❤

  • @AuphieBannet
    @AuphieBannet Місяць тому

    DPP woyeeeeeeee ❤

  • @EnerstMwitha
    @EnerstMwitha 6 днів тому

    Mugwela limodzi chakwela wanuyo chifukwa chakwela salamulila dzikuli ndithu

  • @LicksonKandiero-nf7wl
    @LicksonKandiero-nf7wl 13 днів тому

    Dpp woyeee bt nyau mayazi

  • @BashiruKatuli
    @BashiruKatuli 2 місяці тому

    Dpp woyeeee🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @masingatichilumba8263
    @masingatichilumba8263 Місяць тому

    Aganyu amakometsera kuti zawo alandire, ndikutha kuonanso kuti tsiku lokavota mcp azaivungira kumbali😂😂

  • @LazarusMkandapachuma
    @LazarusMkandapachuma 24 дні тому

    Ovota ndife

  • @JamboJambo-y6c
    @JamboJambo-y6c 11 днів тому

    D Dp oye

  • @HanifComzy
    @HanifComzy 2 місяці тому +1

    Adadi ndiye vote yanga

  • @FlorenceDouglas-x5c
    @FlorenceDouglas-x5c 2 місяці тому

    Chipani cha magazi grace Chinga zimu wake uziusa mutendere, DPP my vote 👌

  • @SliviaJosephy
    @SliviaJosephy Місяць тому +1

    Anthu olo kuvina njala yawapola sanadye,,,

  • @SaulosMsimuko-q1v
    @SaulosMsimuko-q1v Місяць тому

    Saima ndi ndichakwera abanyoza Basi azowo akupita

  • @fulbertkalongonda5171
    @fulbertkalongonda5171 Місяць тому

    Ma disc onse a symon ndi Kendall ndikukaotcha

  • @MoosaSame
    @MoosaSame Місяць тому +1

    Anatha awa angulukunyinda

  • @LajabuSamson
    @LajabuSamson Місяць тому

    Awaso ndiye makape enieni mafuta mmene akuvulamu zimitu zikuluzikuluzo

  • @BrownMaseko-f2h
    @BrownMaseko-f2h 2 місяці тому +1

    Simusokhano koma show

  • @SusanaMakanga
    @SusanaMakanga 2 місяці тому

    Ku opposition kuja kuri dzuwa🤣🤣🤣🤣🤣🤣🔥🔥Kwa bwana wabwino sitisiya tchito 💃

  • @GeorgeJeremia-dv1sv
    @GeorgeJeremia-dv1sv 2 місяці тому

    Otsutsa ndiomwewa😂😂😂😂😂😂😂🤣🤣🤣🤣🤣

  • @PaulChafikirah
    @PaulChafikirah 2 місяці тому +1

    Nkasa ndikaswili iyi sinyimbo kkkkkk amatha makape awa agalu awa

  • @PeterManyamba-cp4sb
    @PeterManyamba-cp4sb 20 днів тому

    mmene zinthu zikuvutiramu ndiye anthu a ooneka ngati anzeru mkumakayimba zimenezo
    kumawuza anthu oti thumba la CHIMANGA pano sakukwanitsanso kugula

  • @dorothymosimbwa3638
    @dorothymosimbwa3638 Місяць тому

    Kuba ma tune aeniwake

  • @supa4dupa
    @supa4dupa 2 місяці тому

    More Fire 🔥 Free Mai Kaliati ,powerful song

  • @GetrudeJailos
    @GetrudeJailos Місяць тому

    Za ziiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii kaye iweeeeee

  • @moureenmolesi
    @moureenmolesi Місяць тому

    dpp my vote heeeee

  • @MussahLazack
    @MussahLazack 7 днів тому

    APM DPP 🔥🔥🔥🔥

  • @chipilirombengo4813
    @chipilirombengo4813 2 місяці тому +2

    Nsonkhano ngati ali kumaliro

  • @HafizahHarack-bn3bf
    @HafizahHarack-bn3bf Місяць тому

    Mavuto in top of pamavuto

  • @InkosiKatengeza
    @InkosiKatengeza 7 днів тому

    Mcp my vote !!

  • @yasitafuphiri-nw2he
    @yasitafuphiri-nw2he 2 місяці тому +1

    Kendal my next mp umakwana ,kuli dzuwa ukoko kkkkk

  • @LatifahShaffie
    @LatifahShaffie Місяць тому

    Ndipo mmm angofunako ndalama agalu awa

  • @JosephMpamila
    @JosephMpamila Місяць тому

    Map my vote

  • @AdisonYoswa-i8w
    @AdisonYoswa-i8w Місяць тому

    Peter akapangira kwao chilima nyungwi adatsogola wakhala ndi chisale utsogola

  • @Faithmoto-j3x
    @Faithmoto-j3x Місяць тому

    Dpp my vot

  • @WilliamNhlane-fd9hi
    @WilliamNhlane-fd9hi 28 днів тому

    Kodi oimba inu mukuganiza ?

  • @ClementKapalamula-n6e
    @ClementKapalamula-n6e Місяць тому

    Kumapwala kwawo ana machende amenewa mxieew

  • @JosephJuice
    @JosephJuice Місяць тому

    Kumwamba kuli yawe amene amaona ndipo sangalole ana ake azidzuzika ayi

  • @LouisGwinya
    @LouisGwinya Місяць тому

    ❤❤❤❤❤

  • @HevenChiwaya
    @HevenChiwaya 2 місяці тому +1

    Simon and kendo nkhale akuimaba Mimbazawozo zinaphwelatu panopa ndi njala enawo ngati akudwalatu 😂😂😂

  • @KestenNakhawonga
    @KestenNakhawonga Місяць тому

    Anthu owonelawo sakusangalala bwanji? Zosakoma

  • @gabrielkapiza4059
    @gabrielkapiza4059 Місяць тому

    Mkasa akati asapote amasapota 100% kukwapura cadet ndi nyimbo akulira mobangula chifukwa Ali kunja kwa boma😂😂😂😂😂😂😂

  • @DesmondNelson-f5p
    @DesmondNelson-f5p Місяць тому

    Mulandle thembelelo guyz kma muli nd abale ku dzko kuno inuyo mmmh

  • @PhilominaAustin
    @PhilominaAustin 2 місяці тому

    Dpp woyeee

  • @FracksonMadani
    @FracksonMadani Місяць тому

    Ambenjere, ai zikomooooo

  • @WhiteSera
    @WhiteSera Місяць тому

    After votes blv me mkasa adzayimba nyimbo ya DPP

  • @MaxwellChiwaya-i8q
    @MaxwellChiwaya-i8q Місяць тому

    Hahahaha koma kumalawi

  • @LukasKalele
    @LukasKalele Місяць тому

    Dzisilu inu dzopepera bas

  • @MtamboNthala
    @MtamboNthala Місяць тому

    Dpp oooye!

  • @GenitojosebingalaJosebingala
    @GenitojosebingalaJosebingala 2 місяці тому

    Zinali ku Mozambique afelelimo agwa chatenga ndi chipani changoyamba chaka chomwechino awuzen achakwela akudziwa salu zake zamagazi zomwezo

  • @robertchidzaye5015
    @robertchidzaye5015 Місяць тому

    Nkasa wafupidwa ngati Makanja woChakwera 😂

  • @IssackCassimu
    @IssackCassimu 2 місяці тому +1

    Dpp my vote iwe achimwendo mapwala anu🙄🙄🙄🙄

    • @peterkamwaza8863
      @peterkamwaza8863 2 місяці тому

      Aaaaaaaa, choncho

    • @SliviaJosephy
      @SliviaJosephy Місяць тому

      ​@@peterkamwaza8863iwe umati chani machende ake pamodzi ndi chakwera ukamuuze

  • @FolamiTowing24
    @FolamiTowing24 Місяць тому

    Chipani cha nyimbo

  • @yusuffatch4146
    @yusuffatch4146 29 днів тому

    Or Mkasa amadziwa kuti vote ndi mu mtima

  • @ChristopherJumu
    @ChristopherJumu Місяць тому

    Amasikini awa nyimbo zawo ndi matope satha kuimba koma kuchemelela chakwela pamene anthu akufa ndinjala mbuzi za anthu izi

  • @beinhardkausiwa7107
    @beinhardkausiwa7107 2 місяці тому

    Dpp❤

  • @PatreckInussa
    @PatreckInussa 2 місяці тому +1

    Mbuzi zaanthu iziii

    • @CorneliusSande
      @CorneliusSande 2 місяці тому

      Mbuzi ndiwe omako bambo Ako gogo wako nkhope ngati bwetete.

    • @TsArKhaii
      @TsArKhaii 29 днів тому

      ​@@CorneliusSandezotukwana zachimidzi boss

  • @LukeBiscuit-x2u
    @LukeBiscuit-x2u Місяць тому

    APM vote

  • @LameckBanda-gk6ri
    @LameckBanda-gk6ri 2 місяці тому +5

    MCP ndi malonda osavuta kuguritsa kusiyana ndi zakubanjazi ,mutukwana mutopa koma boma ndi lomweri basi

    • @SliviaJosephy
      @SliviaJosephy Місяць тому

      Iwe mapwala pako ndi chakwera wakoyo

  • @MorganNyirenda-w7c
    @MorganNyirenda-w7c 2 місяці тому +1

    Akumafuna kudya ndarama bas oimbawa nangasi boma ndichisimi chandarama aaaaa musatinamize

  • @danielzitande5231
    @danielzitande5231 4 дні тому

    Iwe lindo ndi mzako ndine mbudzu za anthu

  • @RuthMsosa-c4r
    @RuthMsosa-c4r Місяць тому

    Mukatha kudya chumacho mudzatipezq tilipo kuma stand kuonerere

  • @GSMxTEAMRepair-q3j
    @GSMxTEAMRepair-q3j Місяць тому

    Ngat kuli oimba mitu Yao sigwira ndi awa, ikantha campaign, akakwerelo mungolo azikadandaula

  • @Enocent-k8k
    @Enocent-k8k Місяць тому

    Mcp ndiya center region yokha bas, but but but DPP ndiya dziko lose malawi Yosemite Nsanje mpak chitipa nkhotakota mpak mnjinjiiiiiiiiiii!! Mcp kwake nkupha kuba ndikoononga, mazila anu noseeeeee!!

  • @HacksonRuReKabwitama-s6v
    @HacksonRuReKabwitama-s6v Місяць тому

    Chisankho ndikamodzi basi kupanda kuvotera mcp kulibwino kungokhala pheeeeeee

  • @NdaonaSandifolo
    @NdaonaSandifolo 2 місяці тому +1

    Koma kendo ndi sayi eee ndinu madolo

  • @EdwardAllie-s4m
    @EdwardAllie-s4m 2 місяці тому

    Dpp boma 2025🔥🔥🔥🔥🔥

  • @robertchidzaye5015
    @robertchidzaye5015 Місяць тому

    Presidential candidate ndi Chakwera yemweyu

  • @DamsonUsanje
    @DamsonUsanje Місяць тому

    Mcp my vote

  • @EustaNjikho
    @EustaNjikho Місяць тому

    Vote is confidential

  • @DamianoGabriel-sh2mf
    @DamianoGabriel-sh2mf 2 місяці тому +1

    Mesa anali a mcp kale awa alowaso kangati

  • @JohnBanda-ux9fy
    @JohnBanda-ux9fy 2 місяці тому

    Oyimba nokha nokha mukapanda kulodzana urendo uno ndakaika

  • @AliNtolera
    @AliNtolera 2 місяці тому

    Anne matumbi amanena zowona kuti eyi ndi mkhatheya nyakwawa nanga Ragga yafika pa m'nganda munatha inu dyera inakuchulukilani ndi ndalama zamagazi atumbuka ambiri ndi mbuli zasukulu sangatukule ziko chifukwa cha dyera chisanzo ma judge athu mwamva kale sayimoni ndi kandulo mvisiru

  • @AuphieBannet
    @AuphieBannet Місяць тому

    Tazingodyani ndalama za magazizo
    DPP woyeeeeeee
    2025 Boma

  • @OsmanChisi
    @OsmanChisi 2 місяці тому

    Oyimba a Ku Malawi Ngati simulemera ndi MCP plane crush