OKASIYA REPORT AJA AKUMANA NDI MAI CHILIMA LIVE EEEH ~ KOMA AKU UTM NDE AWABWEZA NALO REPORT LAWO

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 31 січ 2025

КОМЕНТАРІ • 220

  • @SteveKamwendo-wi8to
    @SteveKamwendo-wi8to Місяць тому +5

    Amene anayimisa kusaka NDENGE ndani.
    MKULU Wa aisirikali ayankhe

  • @Lazarus-qo1sl
    @Lazarus-qo1sl Місяць тому +17

    Adayichotsa black box ndindani tipemphere kwambri zidziwika in name of Jesus🙏🙏

  • @AdamJames-x7x
    @AdamJames-x7x Місяць тому +14

    Manyi a report awa , tizapanga inquiry MCP ikazachoka m'boma Chaka cha mawa, onse okhudzidwa azamangidwa including amene anapanga kafukufuku ameneyu.

  • @GuejendraMk
    @GuejendraMk Місяць тому +3

    Ndikukhulupira kut Mr President wakhutisidwa ndiripotiyi. Koma ndinakakhala ine ndikanafuna mudziwa
    1. Anapopa magazi mkodzo ndi màlovui awanthuwa ndani and why
    2.kodi ànaendesa ndege kukasia thupi 17:10 ku nkhatabay y a kasambala ndi ndan

  • @waniamwale
    @waniamwale Місяць тому +12

    Nanu tangopelekani black box bsi

  • @StarchJonas
    @StarchJonas Місяць тому +17

    Kafukufuku wa ndege popanda black box palibe chimene chingadziwike. Uku ndi kupusisana chabe. The whole inquiry report tikumva kuti palibe olo point imodzi yokhuza black box why?

  • @chifundobuledi
    @chifundobuledi Місяць тому +7

    Inenso sindikukhutira za report yi! Mumufune oti muzimunamizayo anthu akupha inu!!!

  • @BenjaminKapale-k1f
    @BenjaminKapale-k1f Місяць тому +5

    tikufuna black box basi palibe zoyakhula apa zonse zomwe mukuyakhula APA ndi zamanyi

  • @MphatsoBanda-c9c
    @MphatsoBanda-c9c Місяць тому +3

    Inu ndege munthu kugwa ingamuvule munthu zovala ?? Aaaaaaa guys mudzikhala serious

  • @TrizaGeorge-q8w
    @TrizaGeorge-q8w Місяць тому +5

    Chakwela chimwendo kukuyu zikhale ng,oma ndinu afiti koma mulungu akukathani posachedwa

    • @kingsleyhopematchaya5184
      @kingsleyhopematchaya5184 Місяць тому

      @@TrizaGeorge-q8w mukuwapatsa mwayi kod ndichifukwa chiyani a kubanja kwa kasambala amati sakweraso ndege pobwerera mesa anaona kt sanayende bwinobwino inu kakaka kupambana a kubanja amalawi koma

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe Місяць тому +5

    AND LIMPOPO FM WITH COMRAD NTANYIWA HAS DISCLOSED THAT @ BLACK BOX A CHAKWERA NDI NDUNA ZAO AKALISUNGAKU KASÙNGU .KU NYUMBA YA KAMUZU .YA NGULI YA NAWAMBE*** PAMODZI NDI MAVOTE OMWE A MCP ABERA KALE AJA NDI MEC NDI NRB

  • @timothynkhata4012
    @timothynkhata4012 Місяць тому +1

    Nthawi zonse timaganiza kuti imfa ikachitika wina alowesapo zanja lake awa ndimabvuto kwathu kumalawi

  • @KelvinJpchimphepo-sh6nc
    @KelvinJpchimphepo-sh6nc Місяць тому +3

    Kod ndege yo imayenda pansi mwina bwanji mkut nyengo siinalibwino mkhalango, itafika mkhalangomo inasikira pansi, ngat nyengo siinali bwino bwanji anakakamira kupita

    • @GilibetaMbewe
      @GilibetaMbewe Місяць тому

      Tien tizilankhula zomveka coz ndege siyingaende bwino pamene mphepo silibwino pamalopo ai Tien tiwamvetsele chilungamo chioneka

  • @isabelmartin7567
    @isabelmartin7567 Місяць тому +1

    Ndege yanji yochosa magazi awathu 💔😭😭😭😭

  • @Enock-gu5ff
    @Enock-gu5ff Місяць тому +1

    Apapa ife ngati amarawi tikusogoreredwa ndi mbusa amene usogoreriwo muribemo tsoka rarikuru romwe tiri naro ngati amarawi

  • @ZikaniJere
    @ZikaniJere Місяць тому +1

    Eish

  • @mussakapalamula1990
    @mussakapalamula1990 Місяць тому +1

    Nonse amene mukupelekera umboni wa report la bodzali mudziwe kuti muli gulu la anthu omwe anapha Chilima ndi anthu 8 ku Chikangawa ndipo Mulungu achita nanu kanthu. Nthawi yanu izakwana popeza iye Mulungu sachedwa komanso safulumira la 40 lizakwana.

  • @ELLENZAPS
    @ELLENZAPS Місяць тому +2

    Ndimakhara ine bare wanga ndingawsthsmangitse kusekerera zopusaxo

  • @LizqBakali
    @LizqBakali Місяць тому +2

    Ngt akwawo alola ndizazizi ndeine mkachaniso anthu andalama salilana coz amaona thumba landalama

    • @SheenahMwalabu-iz3pr
      @SheenahMwalabu-iz3pr Місяць тому +1

      Ayi osanyanyala they know better kuti olo akane zomwe aboma akupanga or kupereka palibe chomwe angaphule cz boma ndiboma and sakufuna kuwonetsera mkwiyo wao but let's wait tikasintha boma 2025 September adzawaonetsa awa 😅😅

  • @LeoChimaliro
    @LeoChimaliro Місяць тому +4

    So black box ilikut

  • @Nelsonmatenda
    @Nelsonmatenda Місяць тому

    Kodi a chakwera chikuvuta ndichani kungotula pansi udindo? Feteleza k108,000, chimanga thumba k50,000, report ya covid 19 6 billion simunamange munthu, ma xul fees kudula, ma passport afegi, mec yafeg, NRB ya feg, No smartmatik 2025 let's count one by one.finally this is one of the worst goverment than ever

  • @IvyZinjani
    @IvyZinjani Місяць тому

    Kwinako tiyeni timusiyire Yehova, Mulungu wathu okhala kumwamba, zikomo.

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i Місяць тому +2

    Za zii apanga bwanji kafukufuku wa ndege popanda black box? Ndinakakhala ine ndikanangoling'amba cifukwa ndiyabodza.

  • @NearBanda
    @NearBanda Місяць тому +12

    Mmmmmmmm chilungamo akuchiziwa ndi mulungu

  • @LastonMmanga-r2u
    @LastonMmanga-r2u Місяць тому +2

    Zonsezi ndi chabe cz mukunena umboni akumva, black box ili kuti Mr kumkuyu???? Black box ndiyokhayo yomwe anganene zenizeni. 😢😢😢

    • @LinlyMathewe
      @LinlyMathewe Місяць тому

      Zoona uyu anayankhula kale kuti ilipo ikusungidwa

  • @FridayKabade-t7x
    @FridayKabade-t7x Місяць тому

    Ngat president zisakumukhuza za ngozi apeleke black box basi ndizomwe amalawi akufuna kuti tiziwe chilubgamochake cha ngoziyi

  • @JoyceKasongo-s8k
    @JoyceKasongo-s8k Місяць тому +3

    Tikufuna black box nkhaniyatha

  • @JamesYusufu-l6d
    @JamesYusufu-l6d Місяць тому

    komaso. ifengati amalawi lipoti limenelo sitingave. ndege. akuvule.munthu sapato. komaso. inutu munena bwino sitikusiyani. lipoti limenelo abesele. makafe ndichimwenda zachambazo usatiuza zopusazo .anthu munapha.bass.zopusazo..ndege paka imaba ndalama paka kuba bulaki box. inu. zisilu .anthu sakusiyani munya ..anthu okuba ndipha

  • @KhirChisale
    @KhirChisale Місяць тому +1

    Iwowo chilungamo achitenga kuti popanda blackbox zaufiti mukhale tu muli inu achakwera akwanu tiziwanamiza choncho

  • @PeterNgola-i1v
    @PeterNgola-i1v Місяць тому +3

    Ikufunika black box ituluke please kumpando

  • @georgeraphael8198
    @georgeraphael8198 Місяць тому +1

    Chomwe munabisila Black Box ndi chiyani?
    Ndipo akusunga black box ndi ndani?

  • @RosinaPatel
    @RosinaPatel Місяць тому +3

    Report it nde ayi..bwanji simunalole kuti ma banja oferedwa onse akhalepo

    • @Eliezer-vg1nx
      @Eliezer-vg1nx Місяць тому

      Umbuli kuuika poyela, mu commission of inquiry simakhala achibale aokhudzidwa , vuto umbuli😏

    • @SliviaJosephy
      @SliviaJosephy Місяць тому

      Tachokani apa nanu​@@Eliezer-vg1nx

    • @rodrickphiri
      @rodrickphiri Місяць тому +1

      Komanso senior chief Makwangwala wa kwao kwa malemu anali konko mumafuna kuti mkazi wake akakhale kumeneko. Imfa mumaidziwa chotsani umbuli

  • @TachikoMwanamanga
    @TachikoMwanamanga Місяць тому

    Apo amafunika aku MDF ena achosedwe tchito or amangidwe anakanika kugwila tchito yawo, komaso president anatipasa report yabodza ngozi itangochitina kumene, komaso atipase evidence yomwe wako airport amayakhulana ndiwamu ndege powafusa zanjila yomwe adusa, n why anayamba kufufuza mochedwa n anaima kaye kufufuza. They told us kut black box ilipo zonse tinva kma pano anatiuza kut inali yoonongeka. Mafuso ndiambili coz sitikuonapo research yanzelu apa. Timaona ma report amzathu mmene amakhalila osati zathuzi

  • @JamesRoben-dy7bx
    @JamesRoben-dy7bx Місяць тому

    Mcp sizava koma dpp ndi Bomba likafun kulowa bama wina amagulisa chithu joice amagulisa ndege naye chakwela wagulisa lake ndiye dpp ikulowaso

  • @LindaBuleya
    @LindaBuleya Місяць тому

    Like a dream when you say chilima died

  • @PatrickSomanje
    @PatrickSomanje Місяць тому +1

    Iwe kunkuyu don't think that is 1950

  • @TriciaMalikebu
    @TriciaMalikebu Місяць тому

    Mafunso adakali, black box ili kuti, anthu onse ofunika kufunsidwa did they give evidence ie the president & his team? If not, this investigation is yet to start

  • @Extratremendouszeus
    @Extratremendouszeus Місяць тому

    ZBS yafika pa manyaka...mpaka kulephera kuwerenga nkhan😅

  • @KondwaniNedi
    @KondwaniNedi Місяць тому

    Mulungu akuoneni akuluakulu ndiboza limene mwanamiza amalawi.

  • @LameckGamah
    @LameckGamah Місяць тому

    Report li muli be umboni wenwen wapa ground kod black box inja akati idasungidwa bwanji sadakambeko?

  • @masterchitabwino898
    @masterchitabwino898 Місяць тому

    Koma dziko ili zoona akatiuze kuti oyendesa ndege analekerera mmmm kulakwira mizimu, achibare ndi a Malawi. Atiuze chomwe chimazunguza ndikupotoza ndege mmwamba

  • @joebrown1158
    @joebrown1158 26 днів тому

    Kodi iwe George chaponda vuto lako ndi chiyani palibe chimene wukuchita ku parliament ko angakhale kwanu kumene wukuchokera ukukanika kumanga mulatho kwanuko you're not fit to be opposition leader.

  • @GraceShaibu-i9d
    @GraceShaibu-i9d Місяць тому +1

    Brack box ilikuti?

  • @chrisschikozera7271
    @chrisschikozera7271 Місяць тому

    Opanda black box we ll not agree with inquiry

  • @AlihIbrahim-s7v
    @AlihIbrahim-s7v Місяць тому

    Koma guys ku Malawi ndiye basi sikuzathekasoyi ndithu palibe obwela poyela mkulifusa or Boma ngati akhuthila ndi report lomwe lapangidwa popanda Black Box,,,kodi zoti oyendetsa ndegeyo analephela kuyendatsa bwino anadziwa bwanji popanda Black Box,,,,koma ndithu basi zatha izi eeee komaso malawi

  • @masterchitabwino898
    @masterchitabwino898 Місяць тому

    Tili munyengo ya Kunkuyu ndi Alide referee wake Chimwendo

  • @LuciusKhudze
    @LuciusKhudze Місяць тому

    Nchifukwa CHANI nthawizonse pakachitikazinthu zipani zotsutsa zimakonda kugwiritsa ntchito MAU oti A MALAWI AMBIRI akuti. Bwanji osanena zayiweyo ngati munthu ?

  • @mylifeisbette2345
    @mylifeisbette2345 Місяць тому

    China AID kumafotokozera

  • @SadrackTseka
    @SadrackTseka 19 днів тому

    Asazivute ndi kufufuza mitima yathu idafufuza kale okhudzidwa tikunziwa chigamulo pa 16 september nyengo yoipa kkkkkk km yaaah mukusewera ndi mulungu muziona

  • @celinephuka4961
    @celinephuka4961 Місяць тому

    Who did they consult? Nanga mlonda uja adatinji

  • @SteveNdhlovu-r2x
    @SteveNdhlovu-r2x Місяць тому

    Ni chifukwa chiyani mundege munalibe wa mcp

  • @ZamuChizamba
    @ZamuChizamba Місяць тому

    Kodi nyengo yoyipayo idanena ndi black box nanga mukuti panali kulekelela analekelela bwanji

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick Місяць тому

    amene,munkadziwa,box,simunapite,komweko,lelp,mukutsutsa,pa,4nzitanthauza,chiyani,musati,pusise,

  • @SteveKamwendo-wi8to
    @SteveKamwendo-wi8to Місяць тому

    Anthu woyipa inu ndipo nonse mwafufuza muzayankhanso, ngati sipansi pano kapena kwa Mulungu.

  • @WanangwaMfune
    @WanangwaMfune Місяць тому

    Vuto la mafuta simungalithe inu, mesa nthawi ya PM linalipo kare?

  • @franciskampandira7698
    @franciskampandira7698 Місяць тому

    Umboni uli mu black box. Where is the black box?

  • @mabvutomichaelpanagona1949
    @mabvutomichaelpanagona1949 Місяць тому

    Kodi papita dzaka dzingati nkhalangoyi ilipo ndege sizimadutsa dela limeneli? koma Black box anachotsa ndindani pakuti munalibe ndipo mpaka pano Black box mulibe mu ndegemo

  • @timothynkhata4012
    @timothynkhata4012 Місяць тому

    Bvuto lathu ndilakuti timadziwa kuyankhula kwambiri kuganiza pang'ono ili ndi buto ku dziko lathu.

  • @EmmanuelHarrisonTembo-k4t
    @EmmanuelHarrisonTembo-k4t Місяць тому

    Report imeneyi,ine sindikugwirizana nalo,ndi report yabodza yokomera chitsirucho

  • @johnmsona8845
    @johnmsona8845 Місяць тому

    Liport la manyi lmeneyi report lenileni likubwela next year 2025

  • @stevenmwamadi3035
    @stevenmwamadi3035 Місяць тому +2

    Thawi ndi nyengo ikwana

  • @MussaZimba
    @MussaZimba Місяць тому

    Kodi agalu amenewa akuziwa bwanji kuti woyendesa ndegeyo adatayilila zamanyi bc tangopelekani black bokos

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick Місяць тому

    ife,sitikufuna,kupenpha,mavoti,paifa,yachilima,ingoliuzani,dziko,umboni,wanuwo,,ndikunena,tsogolo,yamilanduyi,kt,iyenda,bwanji,osamango,tsutsa,zipindula,chiyani,

  • @AlfredJuliusTemboh
    @AlfredJuliusTemboh Місяць тому

    Kutseka pakamwa Kwa Amalawi sikuti ndi anthu osaganiza ayi koma kuganiza mozama monga anthu oganiza bwino

  • @BrightChiphaka-w2d
    @BrightChiphaka-w2d Місяць тому

    Black box mudakasungabe? Nanga mlonda uja anasowanso?

  • @MayamikoJeke-d5m
    @MayamikoJeke-d5m Місяць тому +1

    Zanziiiiii report yabodza ngati imeneyo

  • @NoelKanyoni
    @NoelKanyoni Місяць тому

    Bwanji utm ipangiseso wao kafukufuku popeza akafukufuku enawa sakukwanira kwa iwowa

  • @UlemuAkimu
    @UlemuAkimu Місяць тому

    Amene watulusa report limeneli ndi mbuli kwambili komanso samapemphela ndikukhulupililanso kuti kwao kulibeko anthu oti azafa

  • @HamuzahBamusi
    @HamuzahBamusi Місяць тому

    Izi nde zapatumbo izi nde munena bwanji zimenezo pomwe black box palibe muzanya mukachopa boma

  • @bliksempiemoerdyk6605
    @bliksempiemoerdyk6605 14 днів тому

    Black box basitu ndiye chida chokhazikitsa bata

  • @SelinaGamaliyere-q8v
    @SelinaGamaliyere-q8v Місяць тому

    Mufufuza bwanji opanda black box mcp chikangawa party

  • @SherifaG.Mlelemba
    @SherifaG.Mlelemba Місяць тому

    Dziko ndi anthu akee.....
    Nkhani iyi,siyoitengela maso m'mwamba,...Zufunika olimba mtima ndi oopadi Mulungu

  • @RodgersMwanakhu
    @RodgersMwanakhu Місяць тому

    Kunkuyu naye sangatiuze zopoila ,report lakwawo limenelo

  • @masianobrighton
    @masianobrighton Місяць тому

    Abale maganizo anthu siomwe ali mulipotilo ifeyo tisunge maganizo anthuwa bcoz mwai oti tipite tikapereke maganizo anthu unalipo palibe anaipitako kukanena zomwe ifeyo timafuna kuti zikhale mu repotilo kuti likhale loona sibwino amalawi tiphunzire kugwiritsa ntchito mwai omwe tapasaidwa ndipo amachita kunenesa kuti amene akuziwapo zangoziyo apite akafotokoze koma inuyo ndi ine sitinapiteko it will be of no use kumalubwanso apapa imfa ija inatililisa ambiri bcoz its first of this kind mu democracy ndiye otsutsa olamula aliyense zinamukhuza ndithu

    • @TrizaGeorge-q8w
      @TrizaGeorge-q8w Місяць тому

      Mumafuna muthu akapita kukanena chilungamo akamuphe uweso kapena eti ndati nose mumaikila kumbuyo boma lakuphali muli ndi tsoka lalikulu kwambili ndipo simuzapeza m, tendele

  • @Dayanschirwa
    @Dayanschirwa Місяць тому

    Amalaw mulipavuto president wanu sakunena zoveka

  • @BILALAJASIMVERANI
    @BILALAJASIMVERANI Місяць тому

    Inu mmafunsa okhao amene amaikira kumbuyo MCP komanso inu munadya zophuphu

  • @Bonfacempokosa
    @Bonfacempokosa Місяць тому

    Ndipo simmayenela kuitanitsa anthu pa umboni koma chidule black box ibwele ituudza yokha mmene zinayendela

  • @kingsleyhopematchaya5184
    @kingsleyhopematchaya5184 Місяць тому

    Ajawala atiuze paja god papa analipo ndi gawo mwina atiuza ndi a utm

    • @LinlyMathewe
      @LinlyMathewe Місяць тому

      Zaziii ana anjoka dziko ndi laling'ono zizatuluka mulungu simunrhu musathe mau

  • @moosakananji1879
    @moosakananji1879 Місяць тому

    Komano nanu muzilembe bwino eee okapeleka report la ndege zomwe akumana nazo ndi mai chilima panja peni peni

    • @bs-malawi
      @bs-malawi  Місяць тому

      Yaa, tamuwuza munthu amene anapangayo kuti azikhala serious. tikonza kusogoloku

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick Місяць тому

    akhala,akufufuza,,zandege,masiku,ambili,km,inuyo,,osakapeleka,zomwe,mukuzidziwazo,bwanji,lelo,nkumatsutsa,,amalawi,aveziti,

  • @lacksonmanyewu3615
    @lacksonmanyewu3615 Місяць тому

    Ikanakhala nthawi ya nyasaland anthu akanakhulupilira koma ma last Born sangakhulupilire

  • @RodgersMwanakhu
    @RodgersMwanakhu Місяць тому

    Tikudikila clip yomwe inajambulidwa

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick Місяць тому

    amalawi,akudikila,inu,amene,mukutsutsa,kt,mukalengezetse,pawayilesi,ndipamene,timava,zowona,zenizeni,osati,pa,4n,ayi

  • @TamikaKaponya
    @TamikaKaponya Місяць тому

    Nde akumabanjawo alandira nyasizo?ngati ndicomco tu n ndekuti akuvomerezano nazo za report yo cos sanayenereka kutero

  • @MariaNkhata-i9q
    @MariaNkhata-i9q Місяць тому

    Uku nkupepela kwambili kuona amalawi uchitsilu za ziiiiiiiiii

  • @AllanChabwela
    @AllanChabwela Місяць тому +1

    chaka cha mawa sikale choona tizaziwa @fter votes

  • @FelixKChisale
    @FelixKChisale Місяць тому

    Kodi inu a utm simukunvetsa pati nanga inu a utm za abuleya lure mukutinazo bwanji tiwuzeni a njawala

  • @Joe-h9v
    @Joe-h9v Місяць тому

    Nyasi zanu za report fusek nonse munalo mu report limeneli tidzava black boxs ikabwela poyela komwe mudakabisako agalu inu

  • @EdwardMorris-pf3ue
    @EdwardMorris-pf3ue Місяць тому +1

    kafukufuku wa mkabudura zachamba

  • @MolosoniKachikumba
    @MolosoniKachikumba Місяць тому

    Mitumbo yanu nose bwanji simutulutsa black box mubisilanji

  • @paulpaseli6310
    @paulpaseli6310 Місяць тому

    Zaugalu basi kd iwe nkukuyu mesa ukt black box ili Malo abwino tabwelesano ikufunika

  • @StellaChiudzu
    @StellaChiudzu 26 днів тому

    Mukaba tiziwa ine chiudzu ema@dontcome

  • @LevisoniBandawe
    @LevisoniBandawe Місяць тому +1

    Tikufuna black box

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 Місяць тому

    Ngozi ya ndenge amafufuza kopanda black box kondowe ndiwe mutumbu opanda nzeru

  • @madakabichi2251
    @madakabichi2251 Місяць тому

    Chakwera wa kupha uyu uzampeza nzako

  • @EleazarSimwanga
    @EleazarSimwanga Місяць тому

    Why do you use strange voice instead literal human voice?

  • @RoseMkandawire-e2g
    @RoseMkandawire-e2g Місяць тому

    Ok nyanja mwagurisa ku songeya ija mdarama zake nizimene mukupangira zopusazo

  • @LawrenceNdala
    @LawrenceNdala Місяць тому

    Let Njawala commission his party's Commission of Inquiry for the plane tragedy. He seemingly has some special interest apart from what we as Malawians have been informed on the catastrophe.

  • @LashidBenardi
    @LashidBenardi Місяць тому

    Km mene inarili ngodzi ija mayakho ake akukhara amenewa mulungu Ali nafe😢😢

  • @JumaEriya
    @JumaEriya Місяць тому

    Akuntundu abwenze mapepara amenewo.akasumire amapanga kafukufukuyo