Це відео не доступне.
Перепрошуємо.

MTAMBO WAYAMBA KUNG'ALURA ZA INFA YA ACHILIMA KU MSONKHANO KU MZUZU |

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 12 лип 2024

КОМЕНТАРІ • 67

  • @TiyanjaneMkwate-we8gu
    @TiyanjaneMkwate-we8gu Місяць тому +3

    Opusa uyu, mavuto tikuwaonawa anatipalia ndi iyeyo. May GOD punish him.

  • @amoschataika7440
    @amoschataika7440 Місяць тому +3

    Ntambo thanks my Brother for your bravest speech.

  • @Nganya96
    @Nganya96 Місяць тому +1

    Talk is free, mvura ikagwa kumachuluka zolilalira😂😂😂😂😂😊

  • @JacksonKanjanga
    @JacksonKanjanga 22 дні тому

    Thanks for powerful speach

  • @user-un8yq1gg2i
    @user-un8yq1gg2i Місяць тому +1

    Fetilizer yo ayi, tikufuna biochar ife zinthu zotchipa zosavuta kupeza komanso zogwira ntchito nthawi yayitari, komanso biogas, gas wachilengedwe ndicholinga chofuna kuteteza mitengo yathu,

  • @Marymahendra
    @Marymahendra Місяць тому +2

    I want to see Malawi and change the present state like Chikwara is not doing well enough in four years time he killed 18people so please don’t be chose him may god bless Malawi xx

  • @JamesChiphwanya-tb3tq
    @JamesChiphwanya-tb3tq Місяць тому +2

    I wish to see change for Malawian with alliance for democracy god bless you

  • @user-bd5kw8oq1r
    @user-bd5kw8oq1r Місяць тому

    Chomwe chinapha chilima ndi opposition yonse because ndi amene akudziwa zonse kuposa boma ndiye akudziwapo kanthu amenewa kuphatikizapo mtambo

  • @DevisonHala
    @DevisonHala Місяць тому +2

    Adapha chilima nayeso aphedwe osamunyengelera ameneyo ndale zophana zinatha

  • @user-ve4zn2ne1k
    @user-ve4zn2ne1k Місяць тому

    Big up bro mumakwana ndinu big wa ma biggy ife tilindi inu even wina afune asafune munthu wakulu kwambiri mutambo❤❤❤❤

  • @jestinanamkonda1495
    @jestinanamkonda1495 28 днів тому

    Afford = Chakufwas son
    UDF = Muluzis son
    DPP = Bingus Brother
    PP = JB
    MCP = LMC
    Where is Makawi heading? Dyela too much

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon Місяць тому

    IMPHAWI ONSEU , MAVUTO ONSEWA , KUZUNZIKA KONSEKU AMALAWI AKUVUTIKA NDI WEYO GALU MTAMBO USAPUSITSE ANTHU NDIWE UNAPANGITSA ZONSEZI STUPIT NDIWE GALU KWABASI

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Місяць тому +1

    Good Messnge ❤

  • @FrankMkandawire-tl8gf
    @FrankMkandawire-tl8gf Місяць тому

    Only Jesus is honest

  • @Faithnsini
    @Faithnsini Місяць тому +1

    Bilimangwe pa malo oyela amakhala oyela 😂

    • @joebrown1158
      @joebrown1158 Місяць тому

      Kodi iweyo wutawona mzako amene wukuyenda naye akupanga zoipa kodi wungapitilizebe kumayenda naye?bilimamkhwe ndi iwe.

  • @McphersonMsulira-zx2lj
    @McphersonMsulira-zx2lj 27 днів тому

    Chipani chimombole malawi

  • @AminaPhiri-pp9tw
    @AminaPhiri-pp9tw 28 днів тому

    Mawu anu bwana chakwera achoke

  • @ellennchambalinja484
    @ellennchambalinja484 Місяць тому

    Aaaa uyu nde pomukhulupililq panadutsa 2019 tinkaipatsa moto

  • @ChifundoChiwanda-ru3pg
    @ChifundoChiwanda-ru3pg Місяць тому +2

    Osaopa! Mtambo kuti moto buuuuuu

  • @EdwardKachinjika-c8q
    @EdwardKachinjika-c8q Місяць тому

    Mose wake uti naweso usanamize wanthu iweyo

  • @user-zr7wk4oq2x
    @user-zr7wk4oq2x Місяць тому

    Katundu 🔥🔥
    Confidence 🎯

  • @FaraiMatandika
    @FaraiMatandika Місяць тому +1

    Mtambo ndikamamuona mtima umandisiya siya munthu oipa uyu

    • @joebrown1158
      @joebrown1158 Місяць тому

      Kodi iweyo wutawona mzako amene wukuyenda naye akupanga zoipa kodi wungapitilizebe kumayenda naye? Woyipa mtima ndiwe osati mtambo

  • @JohnJohn-og8rt
    @JohnJohn-og8rt Місяць тому +1

    Nkondo ilipo apa ukuvunika dpp kapena UDF afodi tikwavuna koma apapa ayi sangate

    • @masalinodovu1705
      @masalinodovu1705 Місяць тому

      😂😂😂😂😂😂 koma yaaaa anthu mumath

    • @actuarialscience2283
      @actuarialscience2283 Місяць тому

      Silipo sindu sambiri somwe mwanena. Soninso inkuwechetayo isyesyene.

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg Місяць тому +2

    Tiyen nazo mtambo osaopa

  • @CharityGondwe-bw9gs
    @CharityGondwe-bw9gs Місяць тому +1

    Unapanga khaza adadi iwe oipa iwe tambo😢

    • @FrancisNyayi
      @FrancisNyayi Місяць тому

      Ndipo live ine nnakaponya pompa ine coz of izi adadie abale

  • @AshimayeGama
    @AshimayeGama Місяць тому

    Ife sitidza khululupilaso andale ayi Bola dpp sina gwetsepo ndalama ayi

  • @JohnFrank-cg1yh
    @JohnFrank-cg1yh Місяць тому

    Izi ndi zoona anthu akale andale must go chifukwa ambiliwa ali ndi magazi m'mazi ndie zazitukuko sizingatheke, koma azingoganiza zothana ndi ana asogoleri am'mawa

  • @user-jw2vy8sr7i
    @user-jw2vy8sr7i Місяць тому

    Kugwa Kwa ndege jekete,lamba,sapato ,kolona mpaka miyendo mmapaxi kuthyoka,ma phone kupangika wipe 😂? Aaaaaa guys ambuye akukamtheni

  • @MayorKachali
    @MayorKachali Місяць тому

    Mwasowa
    Cholakhula
    Fundo
    Zatha
    Mukangoyamba
    Kumpha
    Mbewa
    Komaso
    Satanic
    Yakoyo
    Ife
    Ayi

  • @VacksonPhiri
    @VacksonPhiri Місяць тому

    Musapuse naye Mtambo ndi nazikambe kapena kuti bilimankhwe

  • @OliviaFour-rk9ir
    @OliviaFour-rk9ir Місяць тому

    Unatipussa iwe MTAMBO chikkhulupililo paiwe tinataya

  • @SaulosKacheche
    @SaulosKacheche Місяць тому

    Mtambo ndiwe galu kwabasi, chibilimangwe

  • @Shelifibraheem
    @Shelifibraheem Місяць тому

    Bilimangwe Ali pa mpando wa blue tsopano

  • @MsaMtonga-wo1nb
    @MsaMtonga-wo1nb Місяць тому

    Very stupid info iyeyu analiko komwe ngoziyo ikachitikira matako ake

  • @temwarachaelkhonje3733
    @temwarachaelkhonje3733 Місяць тому

    Bravoooooo

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 Місяць тому

    Unalipilidwa kale mtambo wadyera

  • @VacksonPhiri
    @VacksonPhiri Місяць тому

    Ndi ndege

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 Місяць тому

    Aford 💙💙💙

  • @GraciousFrank
    @GraciousFrank Місяць тому

    Nde kuli gulu la anthu ngati ine a duuuuuu nobody knows which side we are vote ndi mu ntima

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 Місяць тому

    Maloto achumba antambo kkkkkkdpp woyeeeeee

  • @kensonmbewe6692
    @kensonmbewe6692 Місяць тому

    We Malawians are tired of you people, mukametana kuseriko mumabwera poyera kudzapangana black mail, timakidziwani ma politicians a Ku Malawi. Now we need a new blood, a new gene, we want someone selfless and bold to help Malawians not you people

  • @GLABELMW
    @GLABELMW Місяць тому

    Ndizoonadi kafukufuka achitikedi tive zoona zake

  • @MosesMsiska-x2n
    @MosesMsiska-x2n Місяць тому

    Chihana and his fellow are the one Who made all these messes we are in deed

  • @JuuuKomba
    @JuuuKomba Місяць тому

    😂 koma awa unduna mmesa anaulawa madyela bas 😂😂😂

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 Місяць тому

    Mtambo mbuzi

  • @tuzijachaba-zl6pm
    @tuzijachaba-zl6pm Місяць тому

    Tikawina akale wonse azatuluke ziko litha kukhala bwino

  • @CharlotteMushimiyimana-g6b
    @CharlotteMushimiyimana-g6b Місяць тому

    Zona

  • @SusanaMakanga
    @SusanaMakanga Місяць тому

    Zazii bilimankhwe weniweni iwee

  • @GeraldGunde
    @GeraldGunde Місяць тому

    Aaaaaaa! Zabwino sayitanira

  • @zolozaifilipe5940
    @zolozaifilipe5940 Місяць тому

    Wamasukat ntambo

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj Місяць тому

    Kodi Chilima ndi chida choyakhulira zandale kodi abale

    • @johnbullyohanittokasikizim7127
      @johnbullyohanittokasikizim7127 Місяць тому

      Kodi munamupha ndinu?

    • @joebrown1158
      @joebrown1158 Місяць тому

      Iwe mwana wanjoka

    • @inessmsiyambiri8517
      @inessmsiyambiri8517 Місяць тому

      Simwamupha dala cholinga tikhale mchonena

    • @joebrown1158
      @joebrown1158 Місяць тому

      @@inessmsiyambiri8517 you need someone to interpret for you people will not gonna stop to speak about chilima until the truth must prevail ngati wuli mvali yomweyo ya kupha nawo ndiwe watsoka

  • @FridayKasto
    @FridayKasto Місяць тому

    U was bigy at first
    But now mmm little trust 😢

  • @AminaPhiri-pp9tw
    @AminaPhiri-pp9tw 28 днів тому

    Mawu anu bwana chakwera achoke