CRUISE 5 WITH MOSE WA PA PHIRI LA BUNDA
Вставка
- Опубліковано 10 вер 2024
- Mose wa pa Phiri la Bunda (Radford Kamwendo) adakwela pa phiri kuti akapemphere, ali pomwepo adalandira ulosi kuchokela kwa ma Prophet kuti akuyenela kukhala pamwamba pomwepo kuti azisamalire malowo. Pano wakhala pa phiri lo kwa zaka zitatu.
Mose adakula moyo ovutika, kulekela sukulu pa Standard 8, kugwila ntchito ngati lebala, kenako ngati msilikali kwa zaka 6, kenako ngati truck driver. Mose ndiokwatila ndipo ali ndi ana akulu akulu. Atazindikila kuti akukhala moyo wosokonekela adaganiza zoyamba kusala komanso kupemphera. Ndipamene adakapezeka pamwamba pa phiri la Bunda.
❤❤Thank GOD this man has accepted GOD call.
I crealy know him worked same department,(at Lulongwe Regional Engineer Roads Department ) i am based in South Africa now but still remember him.
I really believe GOD has a big meaning with him.
Keep it up big brother.❤❤
God is good all the time, God bless you joab and that Mr
I love the way he described the route to to mamba mine to collect coal his been there it's true
Koma mose wapaphiri eishiii God is Good kwandisangalasa komwe akukhala mose ndikanakonda takhalako naneso ndikuona ngat ndi life yabhoooo
Wow . This is wonderful. Mr Chakhaza you think outside the box. Keep it up. Mose wa phiri la Bunda. Ambuye apitilize kuchita nanu.
I like Mose koma. Interesting life story
this is such a hiden testimony and mavuto azitipatsa chiyembekezo wow wow wow
I like this program...komaso mose wake omasuka...zimafunika chonchi ukazindikira uchimo wako...suchita manyazi kulapa pa maso pa mzako.
I love this it sounds crazy but to those who fell in the hands of God and rise they will understand. That's what we call Grace
This Joab guy knows how to do interviews. Big up Bro
For sure, is an expert, and Jovial
This man is really man of God
One Joab and Cruise 5 ni zi zi ziiiii Mr. Joab keep it up please. Watching from Chipata Zambia
🤣🤣🤣 Joab, Cruise 5 is always entertaining.
Hallelujah
Iyi ndi intervew vs intervew may God bless u man of God
This is funniest 😂 chakhaza,one my number one watching you from zambia 🤣🤣🤣🤣🤣🤣 you have made my day
Ntchito za pick ndi fosholo.Mmmmmm sizinthu. Ndilibenazo mau. Kuchedza KWA bhoooo guys. Thanks.
Joab amatha,,,,,God bless you both
Love the hill. Ndizakikwela basi.
Umayenda m'mbali joab wakumana Nazo...kkkk I like this guy...mwandimvetsa kukoma guys👏👏👏👏
Kkkkkkkkk koma joab kkkkkkkkk. Ati iyi nde misala kkkkkkkk. That's amazing interview. Thanks for loading it
A Chakhaza Mafunsafunsa, kkkkkkkkkkk. Mudzatemedwatu. I could tell from the beginning kuti Interview siitha bwino iyi. Kkkkk, Anyway, that was a good work Joab.
I like your t-shirt man
Kkkk akuti akadakhala kuti Mulungu anakuyankhulani mukadabweretsa biscuit 😆😆
😆😆😆😆😆😆
God is great #my saviour.
Joab ur number 1
Mabvuto akabwera zambiri zimayenda bwino...Mose wa pa Phiri
Nice, phiri silifunika ma Vuvu kkkkk
Joab wang'ambang'amba Tshirts kumpalapata Mulungu mmmh😂😂
Ajoab mulungu sanakulankhuleni kuti muguleko Ka biscuit
This is best interview I like the way amayankhira mafunso, Joab wakumana ndi mtumiki wa Mulungu😂😂😂
Big up moses
Ndasangalala ndi program imeneyi kwambiri. Ambuye ndi wabwino. Mulungu ndiye mwini zonse kopambana zonse.
Ndamuyankhira joab.
Mn of God
There is something in him..I feel Amen
Joab God installed fun softwares un your head. This one with Mose wa Pa phiri la bunda was woow. Excellent throughout. I cant say keep it up since you are already up. I love your work bro
KKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKK
That's incredible wiew right there. Koma Mose osamutenngerako chakudya kkk.
Hàhahaha
Joab Ndiwe Chidilu😊
Bwana Joabe you really inspire us
Joab answer the simple question yesu ndi boma wankulu ndindan 🤣🤣🤣🤣
This program makes me happy
I love this program honestly. More especially this segment kkkkkkkk
❤❤❤❤ yoooh since I had left my Bunda cumps zaka zingapo zapitaza anyway am watching you All the way from Cape Town
I love Joab too much
Program iyi imandisangalasa
Joab is a top-notch interviewer
Ineyo koma shirt yavala Joab yandibanda. Funny interview loved it, the guy can tell endless stories
Amazing
Chakhaza plz nkufuna interview unapanga ndi namajekete winawake amene anakufunsa mafunso monga okut ndiwe okwatila or share Link
Joab u r the best. Umaitha keep up bro. Nkhope yako ndiyansangala nthawi zonse
Zoonadi
This is too powerful this is what people want to know
Ndizowona zimenezo kulibe kusuta chamba ku trying
Mulungu akudalitsen
Joab ur the best! Ma shows ako satopetsa
Now this what we call grace
mose wapa phiri etii
Zamphavu 😂 we enjoy ur interviews
🤣🤣🤣ati musati ndwiii baba🤣
Destiny is a #mystery . This has to be understood.....in life of every man on the earth. when God speaks , be privileged to hear.......#am blessed with your amazing work Joab you are performing.
😢😮😅😅😂🎉❤
Mose mkuyigwira ntchito
Kkkk km nd shashaaa😂
Joab nzako watchena bwinobwino iwe basi busy kut simisala imeneyi kkkk
this is just wow 😍😍😍😍😍😍
Man chakhadza mmakwana❤
Kkkkkk komatu agwira ntchito yabwino yokopa alendo kuposa ku unduna apitenso ku mulanje akakonze mseu kkkkkkkk
Thanks Joab I love this
Mose ndiye pick and fosholo simunaisiyebe. Kkkkkkk
Good interview
Mosses ameneyi ndambuye adamutuma coz wachitazithu padziko😊
Kjkkkkk boma ndi Mulungu wankuru ndani? Mumaopa ndani?😂😂😂
👍👍👍👍👍💖💖
Amen
koma Joab, umawapeza kuti anthu ngati awa?
Musati Ndwiii Baba,😹😹😹 can't stop laughing
Mwachitatu zinthu a mose
Reminds me of TB Joshua
Kkkkk koma mose and joab kkkkkk Boma ndi yesu wankulu ndani ???? Kkkkk
YOU ARE THE BEST JOAB. ENTERTAINING AND ALWAYS INFORMATIVE
Following
Mumakwana wakulu ndidzapanga nthawi ndidzafika ku phuriko
ATI chipisi
Tsono ajoab Mulungu sanakuyankhuleni zoti mose afuna kudya??😂
Koma joab 😅😅mafuso ena kkk
🤣🤣🤣🤣 mpaka chamba udasutapo
Uhmmmm
Kkkkk Joab wakumana naye mose
Kkkk boma ndimulugu wamkulu ndan😂😂
😂😂koma chakhaza anakumana nazo apa.
Angelo 1million chamba sichabwino kwabas kkkkkk
Tathokoza kwambiri taziwa nawo abambo Mose apa phiri la Bunda
Umakwana joab.
Kkkkkkk a Joab munapita mutakonzekatu kwa Mose, wakuyamikilani Mose kuti zonse zilibwino dressing & your hair style
Koma Mose T shirt ya Joab sanaione bwino
Joab suzatheka kkkkkk , koma timakunyadilan , ulemu wanu
Wa mkulu ndi Mulungu
Koma mafunso a Yoab kkkkkkkkkkkk muzasutako chamba? Chitamera apapa simungasute kkkkkkkkkk
He is crazy
Kkkkkkk he does not smoke at all mose wa phiri la Bunda
Kkkk mlungu alemekezeke.boma ndi mlungu waphamvu ndana
Joab anthu adzakutibula🤣🤣🤣🤣
Patricia kamwendo ndi Winnie kamwendo Kani awa ndi bambo anu?this is good ending
He doesn't know that mose walelo ndimuthalika😂😂😂