Patricia Malawi beloved teacher keep it up standing firm for as utm leader for Malawi nation.. One day you shall become Malawi nations presidents president..May God bless you in Jesus name amen
Unduna si u president ai ndiye muzitosa Chala amene anali president panthawi yomwe iyeyo anali nduna, Komaso nthawi ya DPP zinthu zimaenda bwino komaso dziko limakoma unali okanika ndiiweyo.
Chitsiru iwe wakutuma ndani ajutukwanitsa galu iwe mbuzi ya munthu iwe,iwe umapanga chani ku mtundu was kwanu chule iwe ndiwe uja unapha nawo chirima ND chitsiru chinzacho chichakwera eti ???? Mfiti gologolo ,nyani bakha uzikawanyoza amako
Yes, you're 100% right, malawi needs anew breed of politicians, we're super tired of change golo politicians, they're a stumbling block to our country.
I will never ever trust you ,,just imagine how many political parties have you run as a ministry what have you help to the country since from UDF,dpp until now but still saying the same tune aaa Chamba eti..😊
Nthawi zina mavuto amamupanga munthu kukhwima ndikubwera mzeru zina. Ndaphunzira kwa ana amasiye maka ma first born omwe amatenga udindo olera young siblings though anali achibwana makolo alipo. Just look at how people have flocked to UTM after Chilima's death? I did not follow politics until I was aroused with that painful death. Tiyeni tiwapatse mwayi tione zomwe Mulungu atichitire kupyolera mwa iwo koma chikangawa party takana.
Thank you so much ho patrisha your message is really good unity for Malawi God bless you madam and one more thing chilima mzimu wake uwuse m,muntendele ndiumene ukutsogolera chipani chathu cha utm
UTM chipani cha social media kkkkkk. MCP ndi akatundu Baba sichipangana zawo za pa social media. Za ana izi, come pa ground inu a UTM ndinu mafana heavy. Zisokosani pa social media basi
U ar true leader and God must continue to be with u , u ar strong woman l love u mah
Inu mayi kaliat ineyo ngat munthu pandenkha ndinu mzimayi olimba mtima panzabwino, God bless you mama
I am truthfully and 100% utm ..we are winners and we are doing it again in 2025!!!!!
God bless you your excellency Hon KALIATI 🙏
Awawa ndi machine
Long luve UTM ❤
This is indeed an idea and it shall always be.....
Osawopa, osafooka, osatopa 😊 51:58 51:58 51:58 51:58
Patricia Malawi beloved teacher keep it up standing firm for as utm leader for Malawi nation.. One day you shall become Malawi nations presidents president..May God bless you in Jesus name amen
UTM for ever ,, tipatseko ena ulamuliro ,, Osaopa Osafiooka osabwekera mmbuyo ,,, tikufuna New way of doing rhings UTM my vote
🎉 iron lady we support you
Akweni the master teacher,ndimakuyamikani mai.posunga dzina la afana Sau Chilima. Mulungu adzikudalitsani
Mai Patricia Kaliati we love you so much in our party
Our SG kweni osaopa osafooka 🔥🔥🔥
Bravo mai we are behind you ,May God bless you.
Master performance By Iron Woman Kaliati❤❤
Uyu Mai Ali ndibodza how many years akukhala pa udindo wa unduna since nthawi ya UDF amalepherelanji kuthandiza kut dziko litukuke.
Pali unduna omwe unamkanikapo?
Unduna si u president ai ndiye muzitosa Chala amene anali president panthawi yomwe iyeyo anali nduna, Komaso nthawi ya DPP zinthu zimaenda bwino komaso dziko limakoma unali okanika ndiiweyo.
Chitsiru iwe wakutuma ndani ajutukwanitsa galu iwe mbuzi ya munthu iwe,iwe umapanga chani ku mtundu was kwanu chule iwe ndiwe uja unapha nawo chirima ND chitsiru chinzacho chichakwera eti ???? Mfiti gologolo ,nyani bakha uzikawanyoza amako
Koma ndipo inu. Amalawi ndi zitsiru. I won’t be surprised when the next president will be the worst as compared to Chakwera
Take the leadership nw kaliyati. Utm needs you
Nice speaking Mother Malawi, Mr Chili's soul may him rest in peace, God is good all the time.
Respect to you Mama ❤
Action is needed. Don't be fooled by Social media, not all of them will vote. Establish tap roots. Time Will Tell. All the best UTM
Yes, you're 100% right, malawi needs anew breed of politicians, we're super tired of change golo politicians, they're a stumbling block to our country.
Akatundu utm yeniyeni
UTM my vote 🔥
Utm my vote🔥🔥
😮😮
Strong woman ever 🔥 and our best SG 🔥💪 i love you so much
Za ziiii
Tirinanu mai we are with u
Lea Malekano come in and invite Kaliati again for interviews pls
That's why we stand for utm ❤❤❤
Patricia, the real colour of UTM ❤
Akweni ndinu ulimba mtima. Keep strong, Mulungu alinafe
Kupanga peace kuja kunawononga zinthu kwabasi, koma fine I like ur speech
🔥🔥🔥 keep it up UTM
Always mayi Patricia kaliati stands by true
God bless you mam
Muma we are with you always God bless you
Well spoken Mrs P Kaliati
Ofusa mafuso satha, Kaliati yu amafunika Lea Malekano uyu, akanalira, Lea where are you?
Then u dnt knw who kaliati is ask Brian akuuza😂😂😂😂😂iwe akweni sapanganawo
Aaaaaaa amathawa ma interview kwa anthu okutha uyu amakana ,,,amangonamizira busy kkkkkkk
Pakhala azanu ambiri uprezidenti nde Inu mudzaposa osewo?
May kaliyati bwanji osatsekula kampani mudayamba liti ndale mayi wagwilo
We love you mama 😘
Ur a true leader mai😢
Brave kailiat
Powerful massage mama
Koma inu amalawi mukagona ndi kutsuka malawi mumaifunira sabwino ndanena isi chifukwa ndi ma comment amene mukulemba
Eti wayakhula chani Kaliyatiyu ,zomvetsa chisoni ndithu aaaaaa
Kuno ku mpoto utm timaikonda kwambiri koma no offices ku Mzuzu imene ili regional headquarters.ikaniko office please.
More love mamie ❤❤
Vuto la ndale atsigoleri amatha kulonjedza zambiri mbiri kuti tiwavotele.Komano tikawasankha amasintha zochitika nkuyambanso ena kumasankha mitundu pofuna kuchita zinthu
Zoona bale
Chakwera anapha m'busa nzake kulibwanji chilima 😢😢😢 kupha m'busa Kuti akhale mkulu wa mpingo
Galu uyu Ambuye amkanthe
Ndinu mfumukazi mumakwana mama from Mangochi
We love you 💜 mum stay blessed
She can be as a President in future
No deal. Crushing
Mai kaliat nonsense you said government is using utm manifesto so what do you want in alliance?
A Malawi tisamangonyoza, mayi Kaliati ndi mayi wolimbika komanso kulimba mtima ndi nzeru zomwe....
Muzalowa boma lake liti chifukwa pompano mukhalaso munkhwapa za dpp
Wakuuzani ndani kuti utm ikupita ku DPP sitikupanga nawo za agogo akowo ife
You are the best akweni
UTM 🔥💯
Akaliati kulongolola, Inu mwakhala minister zakazambiri mwapangapo chiyani? Olo mutakhala president mungatani? Kodi Inu ndazeru kwambiri? Sukulu munaphuzila kuti: secondary, college? Bodza siyani?
😂 ndiwe mbuli ase
Nanuso mesa nde ndalezo umati atani mzimayi or inu mungapange chani
@@user-sc7ih4op3lbapusitsanani
Ife ndi ma die hard forward ever
Wabodza amalawi tinasukusula sungati namiza
Mbambande mama akaliat
Loved party is UTM osati enawa ayi more fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
God bless our madam S G
❤❤ moto buu anatitaya kare zawayendera ati phera wathu zianthu zompha anthu zimenezo ndiye akhare nawo alliance ndiye nawoso ndi chipani chakumpha anthu chimene ndiye azamumphaso ndiye ndiwoputsa tu
Boss andale musamawakhulupirire zitsiru izi or atasina amenewa palibeso cazeru cingaoneke in short tiyen tizingolimbikra patokha bas
@@kingsleyChisenga-i8ginu ndiye mwalasa,andalewa amadziwa kuti a Malawi ambiri school ndi kaganizidwe ndi vuto.Taonani akuti Chilima anaphedwa Koma kuti uwafunse kuti fotokozelani ngati anamupha anamupha bwanji,zingakhale kuti anapanga bwanji?,sangayankhe koma aMalawi akukhulupiliradi mapeto ake asankhanso anthu okuba ena,akabenso m'boma,zonse ndi mbava or m'mayi uyuyu wapeza danga pa kufa kwa Chilima,muntimamo akusangalara chifukwa akuona kuti Usi anthu sakumukonda potsalira m'boma ndiye kuti atenga malo aChilima,dyera.
UTM is an idea ✊🔥🔥
UTM nde deal
Yaa zoona
But action also has to be conveyed to pple thr media evev other parties
utm moto olo anthu anyonze tili mbuyo mwanu
Together we can stand
🔥🔥🔥
Mayi kaliyati inuyo ndinu 1 ndipo tili pa mbuyo panu komanso pambu pa utm
May God, bless you Mamie Dr Kaliati, your courage and confidence
Mwatenga chipani mwawapatsa agogo anu aja Apm ndiye umuvotela wekha Chimutu chako
UTM, my vote. Mum be as strong as you have always been.
Powerful lady
I will never ever trust you ,,just imagine how many political parties have you run as a ministry what have you help to the country since from UDF,dpp until now but still saying the same tune aaa Chamba eti..😊
Mai Kaliyati 👏 nkatundu 💪💪💪💪
being a minister for so long period of time and now ur talking of developing a country eeeeeiash malawian politics
Nthawi zina mavuto amamupanga munthu kukhwima ndikubwera mzeru zina. Ndaphunzira kwa ana amasiye maka ma first born omwe amatenga udindo olera young siblings though anali achibwana makolo alipo. Just look at how people have flocked to UTM after Chilima's death? I did not follow politics until I was aroused with that painful death. Tiyeni tiwapatse mwayi tione zomwe Mulungu atichitire kupyolera mwa iwo koma chikangawa party takana.
Who told you a minister runs the affairs of a government?
understand the reason of having a parliament and its compostion, from there u wu appreciate that development starts within u.
@@JamesIngeni-ku3qjso what was her job?? Kupusa amalawi
Amayi ovuta awa akangokhala kuti alibe udindo m'boma amalalata kuona ngati alipo okha m'Malawi muno
Mayi wodziwa kugwira ntchito not ukulankhulazo.
@@williamswira2693aaah tizaona. Amalawi ambirinu kusachangamuka
Thank you so much ho patrisha your message is really good unity for Malawi God bless you madam and one more thing chilima mzimu wake uwuse m,muntendele ndiumene ukutsogolera chipani chathu cha utm
😎🤏,,,,, Ulemu wanu mai P Kaliyati
❤
UTM my vote
I like u mum❤
Mayi Kaliati muli ndi fundo zabwino Ambuye akusongoleleni❤️
UTM chipani cha social media kkkkkk. MCP ndi akatundu Baba sichipangana zawo za pa social media. Za ana izi, come pa ground inu a UTM ndinu mafana heavy. Zisokosani pa social media basi
Tionana 2025 akulu inu pheeeee utm boma
Akulu mumatha kuwongolora akamaona noise pa social amaona ngati alindi fans ibwele vote ndiye pamene amadziwa kuti MCP simasewela😂adikile 2025 adzawona landslide yake mpamene adzadziwe kuti MCP simasewela.Imabeledwa apapa ndiye on the driving seat adikile Kaye zaka 40 zikubwelazi 🎉
Munali ndani inu popanda UTM, tangothokozani kuti inakulawitsani mpando, anthu opanda zikomo inu, Mulungu akuoneni September 2025
Aaaaa koma iwe ukunena mani ali okwana munali ndani inu kupanda SKC kuzipeleka mpando mukanaunuknkha inu??
@@user-qp8kh2hj9o you can say that again
Powerful God bless you more ❤
My vote
Akweni woyeee osaopa, osatopa, osafoka
Akweni timakunyadilani kuno kwa muliya be strong
kod even muli ku out of gvt cant u start kupanga zomwe munenazo kaya ma tooth stick munenawo...if u want to help malawi to develop inuso kazipangan ka
Great woman
Zodiac may you give your presenter a tablet, look how mayi Kaliyati wakunyuzerani.
Kadeti uyu ngolongolora
Utm my vote
Akufunsidwa zina akuyankha zina. Hungry for power.
SKC my vote
My vote Utm basi
Tili kumbuyo kwanu Mama osafooka, osatopa, osaopa
UTM movement please don't alliance with any party
More fire Mai kaliyati.
God bless you Dr Patricia Kaliati.Mwathandiza anthu ambiri,mwayankhula mfundo zabwino kwambiri.
Kulibenso kumalawi e kaliati
Akungofuna kukhutitsa mimbayake uyu wakhala nduna mbuyomu kwathawiyayitar wapangapo can cotukura dziko cimene angaloze kkkkk
Osaopa mama,pitilozan kutsata mapazi a chilima
Mmm yakhani mafuso mum , utm ISANTHE mum gonjeranani
Amugonjere ndan?
❤❤