Це відео не доступне.
Перепрошуємо.
MICHAEL USI NDI BRIAN BANDA🙌🙌 KWATETHA.ZA TONSE ALLIANCE ZILI PATI?
- Додати в
- Мій плейлист
- Переглянути пізніше
- Поділитися
Поділитися
Вставка
Розмір відео:
- Опубліковано 22 бер 2024
КОМЕНТАРІ • 258
Наступне
Автоматичне відтворення
MICHAEL USI FIRST INTERVIEW AS A VICE PRESIDENT - UBALE WAKE NDI MALEMU SAULOS CHILIMA UNALI OTANI?Makosana
Переглядів 120 тис.
Times Exclusive featuring Bakili Muluzi - 11 May 2024Times 360 Malawi
Переглядів 223 тис.
HON ROZA MBIRIDZI KULONJEZA MWA NYOOHOT 265
Переглядів 4,8 тис.
Колишній увʼязнений - про мотивацію воюватиСуспільне Новини
Переглядів 1,2 млн
Арестович: Операция ВСУ в Курской области. @A.ShelestAlexey Arestovych
Переглядів 2,9 млн
КУРСЬКИЙ ПРОРИВ. Що ЗАДУМАЛИ у Генштабі? Нова здобич МАГУРИ. Та як вберегтись від нових аферистів?Факти тижня
Переглядів 473 тис.
Kabağ hiç böyle pişirdinizmi! İnanılmaz lezzetli #kabak #yemek #un #domates #tarif #kahvaltıGÜLSÜMÜN SARAYI TV
Переглядів 5 млн
MAFUNSO OVUTA OMWE ATOLANKHANI ANAWAPANIKIZA NAWO A BON KALINDO LERO PAMENE AMACHITITSA CONFERENCEMakosana
Переглядів 86 тис.
A SAMEER SELEMAN ATOKOTA MWA NYOO 13 August 2024HOT 265
Переглядів 28 тис.
MALAWI COURT.... TAMVANI IZI ABALE 🤔Jimmy
Переглядів 133 тис.
KAMLEPO KALUA KUYANKHULA MOSAOPA 🙌HOT 265
Переглядів 8 тис.
VICE PRESIDENT MICHAEL USI WATUTUMUSA OGWIRA NTCHTO A KU ESCOM IN BLANTYRE ATAFIKAKO MWAZIZI LEROMakosana
Переглядів 157 тис.
Enock Chihana kuulura poyela zinsisi zomwe chilima anamuuza asanamwalire zokhunza Tonse AllianceMakosana
Переглядів 232 тис.
Hilco and Ching'axy - Provoke Provoke ( Plan B Season 1 Episode 2 )Hilco
Переглядів 501 тис.
Ndege Za Shepherd Bushiri Ndi Chuma China Chodabwisa Zinapita Kuti ?Hanifa Mw
Переглядів 157 тис.
Ntanyiwa Kufotokoza Kuti Chakwera Anapha Saulos ChilimaMw Xtra
Переглядів 38 тис.
ШОК! 😱 Кадиров пішов ПРОТИ ПУТІНА | ШотамрашаOBOZ UA
Переглядів 282 тис.
«Ми так війну не закінчимо ніколи»: 22-річний морпіх про те, чому їм потрібні молоді #війна #зсуСлідство.Інфо | Розслідування, репортажі, викриття
Переглядів 606 тис.
Get 10 Mega Boxes OR 60 Starr Drops!!Brawl Stars
Переглядів 8 млн
ЕЛІАС #8. НАСТЯ ТКАЧЕНКО х ВЛАД СТЕБЛІВСЬКИЙ х КУРАН х ВЕНЯ | Ветерани космічних військВетерани космічних військ
Переглядів 528 тис.
Шеф, все пропало. У пропагандистів РФ істерика через F-16Факти тижня
Переглядів 567 тис.
Replacing a valve on a full water tank! 🫣💦 - 🎥 the_ladyplumberUNILAD
Переглядів 119 млн
🤯 ЗДУРІТИ!🔺КУРСЬК: куди дійшли ЗСУ? 🦾 Наступ на Росію ЗВІЛЬНИТЬ Донбас? Новини від ЯніниYanina Sokolova
Переглядів 567 тис.
Удар по російській колоні в Курській області #shorts #війна #курськ #арміярфBBC News Україна
Переглядів 801 тис.
Malawians let us not be polotical in everything . Before you judge others ask yourself a question what am I doing towards the development of my country ? Not just faulting people as many Malawians have chosen to do
Ndpo live
Manganya ayambitsa chipani chake
Mr Usi can not be defined as to which party is he, such a leader shouldn't be trusted. A leader should be straight forward osat kumabweletsa mafunso osowa yankho
Aliyense Ali Ku Tonse akumakhala confused kwambiri, Usi is becoming one of the stupid politicians these days. Palibe chomwe walankhulapo chanzeru apa .
Ndipo lyv ❤watha kuyinvesesa conversation iyi umakwana
There is wisdom in Michael Usi.what I have learnt is 3 perspectives/ dynamics of human being- cultural, political , environmental .Ambiri pa social media phokoso la ndale basi.
Some questions deserve to be answered in a straight way rather than running here and there .😅😅😅
Brian has met his match.,......
.
You are not Brian Banda's fan
Michael Usi katundu wa boma, chilungamo umachikwanisa. Continue work hard.
Chilungamo chake Chiti,,
Genius man Michael USI umakwana
This man is very clever ,usi
Chamukwaana chibamzi uyu Sangayakhul zothandiz amalaawi aaa
Mmmm Usi vomelezani kuti mwalowa mcp chifukwa chauduna dyela ndindlama iwe
Usi has matured politically and MCP muzamumva kuwawa 2025 mukaphwanya pangano
Uyu ndi Chilima a MCP achenjele naye.
Koma alibo mtakhala cheteee ndikumvesera ma fact akeee
Chamba Michael Usi ukuganiza kuvuta kwa dziko la Malawi tikaone mmipingo dziko lolamulidwa ndi ana anjoka tikaphatikize Mulungu mwaona lero kuti Mulungu alipo iweyo Amanganya ndi mbuzi kwabasi wadziwa liti kuti onse asamapange zandale mbapako
Banzi yafinya pakhosi a usi akukanika kuyakha mafuso iwe ife si ana usi tangoyakhula kuti ndiwe member wa mcp bas.mukuyakhatu za nonsense a usi sali limozi ameneo asazembeso pamenepo nkuluyo ndi ochenjera akumuyenda pasi chilima chinanga nae paja akuti ndi wa look sharp
Adha akuthawathawa kma chilungamo choti amangodziwa kulakhula chilungamo ndi za nzelu ali ku adra kuja kma paground zikuwavuta
The guy is not calm to asked questions fully from Brian.
He should be calm and explain well
Michael Usi ndi munthu wandale komanso woyanjanitsa ndiwokonda dziko lake
Sakuziwa pomwe Ali mr usi
This guy is not a politician
He is dramatist 😂😂😂😂
Usi has to follow mcp so that he can be financially balanced,
A hot ...musamaike nkhope Pa screen
Mbutuma iyi
ndi kape ameneyo 😂
Ndi kape😂😂
Atha kuika sakutukwana si mnutumba ayi
Chisilu yudasi sikaliyoti ameneyo amene anampereka chilima maliro achima samamukhuza nawo anali busy ndi chakwera ngati ali wa utm asiye vp yo ngati sasiya ndi wamcp
Usi ndi wamzeru kwambiri ndipo amapanga zinthu moganiza bwino.I printed my t-shirt friend's of usi with my own money just love for him.
Shame,,look at the question and see How do we define politicians,,answer should be yes or no inafe sitinawonepo iyeyo akuvala zovalazo Ngati wachipani komaso misonkhano,,akuchulutsa zolankhula
m0000000000000⁰mi
He is not a UTM he answer in crooks style
A MALAWI AMBIRI TIMAFUNA MUNTHU ADZICHITA ZOMWE TIKUGANIZA KUTI NDI ZOLONDOLA, ZOMWE NDIZOSATHEKA
Zoona bro ndizomwe zikuvuta kwambiri zimenezo, politics everything
Uyu amationa kupusa amalawi koma adakati asasithe mmene analili Ali ku adra kuja mwina ndibwezi tikut tizakhala ndi tsogoleri oganiza boh koma ah manyaka amuthu uyu Chilima zawo ndizimodzi
Sali ku UTM uyu komanso sanakhalepo ku UTM Ali after ndalama basi
Funso limodzi mpaka 15 minutes 😂
Dr akulephera kuyankha
Ndipo lyv iweyo you know what is happening to this conversation ❤
utambwali weniweni
I've been ask this to people kuti Kodi ausiii alivhipani chiti,chifukwa chifweeni or saulosi sinaonepo atalakhula Kaya zamaliro zakufa Kwa bwana sao aliziiiiiii mayakho simdimawapeza kuti Kodi alimbali itiiii sinawaonepo or ndi mai anga Patricia or ena a utm even chisakhidwireni sindimamvesa ndipo sinamve ataima kumulira kupereka speech za saulosi ineyo simavesesa wat kind of quite is this one i don't get it
Usi you're genius❤
Utsi musana wanyokooo, paribee chadzeruu chimene ukunena sichikuvekaaaa , pita ku mcp ukoooo , mwatiphera chilimaaa inu cnyapapi achabe chabe inuu
Excellent Mr Usi ❤
Never kukhulupiliranso andale ndipo sindingachitenso zovota ndinasiya 1994 that's wall
Usi is sitting at a crossroads...he doesn't know what to do...
He is not coming out exclusively as a UTM member because he doesn't want to disappoint President Chakwera..
He is trying to preserve his ministerial position ...
How can a Vice President of a party desist from wearing his own party regalia openly??
Nthawi ya DPP ija amkapangitsa Tikuferanji nkumati bwanji chimanga chafika pa k12 000?Lero ali mubomamo koma dzimene akulankhula dzosamveka..Usi is corrupted by Chakwera
Koma uyu dzeru apapa ndiye palibe guys😂😂😂😂😂
Nanga inu ndi nzeru zanuzo mwapangapo chani?
Komanso malemu saulosi chilima anaganiza bwanji kuwasakha AWA asawerowa? Wadzeru anali malemu😢
Koma ndiposo
Usii ndiosalakwa guys as vp WA utm wayenelansoo Kukhala vp WA mcp
Usi be straight forward
He is a political guys
Awawa anakomedwa ku UTM just replace this guy ndi Fredo mafana osatengeka ndi zinthu
Ndabodza awa akupembedza chakwera chifukwa akudziwa kuti akaonetsa mbali sazidya nawo ndalama mukatuluka boma ndipamene mudziwe kuti nyimbo ya fuko anthu ilibe video 🎺🎺🤣🤣🤣🤣🤣 ndikweze voliyomu 😂😂😂😂😂😂🎷🎷
Last actor usi my Vote
Aaaaah mulibe nkhani a usi mmutu mwadzadza ndale basi
Pali zina zomwe akuluakulu amadziwa 😂😂😂 oookha kuti alowa MCP 😂😂
Brian is very knowledgeable than stupid usi, just beating about the bush he dont even know chomwe wafusidwa komaso kuti ali pati
Usi zero pa 10,leadership mulibemo n u are at a give way .
Usazembe Michael usi pakuti Uli Mbali ziwili that's why sumavala makaka umasowa Choti uchite
Anchor wangoti ziiii no more noise
Kkkkkk ndikuonela Tikufelanji ndithu kkk😂😂😂😂
Lowani pa mpando basi ❤❤
Yudas uyu wampereka SKC ku imfa
Usi is a dramatically higher comedian person so anything he can say dramatic thing guys
Ameneyo ndi njoka
Kunena moona mtima,akulu awa ndi a Mcp
Uyo zomwe amayankha ineyo sizikundimvekera bwino
Sungamuvese ndiolozedwa uyo😊
Mafuso safusana mr Brian akufusa inuyo muyankhe osafunsaso pafunika yankho basi.
Siyani bwana mmozi kuti mukomze zinthu
Koma zinazi zikumawawisako mmutu anthu awa atikwana eeesh
Michael usi is really a politician
Ango yamika usi kuti kufa kwamzao apeza mwai basi don't talk a lot of under of this interview
mmmm anachenjeresa awa
vuto la umbuli you expect Usi kut azinyoza president ngat bulutu uja amene mmamuonera patali.Usi is a gentleman who knows what he is doing.Sukulu ikumuthandidza,munthu sukhala stupid and foolish at the same time so its only those who think Usi is confused but those are the ones who more confused than Usi himself.
Wayesa drama eti? Za zii
Ndimuthu wankulu akuziwa zomwe akupanga
Michael Usi analowa MCP kalekale malemu Chilima alimoyo asatinamizepo apa
Dr usi keep it up onetsan umunthu wanu
But I'm warning him be careful if he decides to stand with MCP PATY
Ma Sikono adakuuzani Bambo Sikono. Kt anthu akalowa mmboma, amaiwala zonse zomwe adalonjedza kkkkkkkkk
Brian banda muwaona posachedwapa akudya chibanzi chachikulu pano muwasiyanise mene amagwilila ntchito poyamba
Chitsilu Michelle Usi ndipo sakutha kuyankha mafunso Ali kumbali ya boma
Akulephera kuyankh fuso loti bwato satsotsirana panjira yet analankhura yekha
Uyutso ndigalu kwambil
Usi wakula nukambelembere don't 4get Galu akaluma fupa sauwa
Michael usi wapeleka fuso apa akuti munamuwonapo munthu akukodza akuthamanga? Michael usi ndi nkhani zina.
Congratulations Mr usi
Shame,,mumango kumupanga support munthu according to his fame
Nde a mcp alozedwe aphwanye lonjezo nd bambo skono yhoo azaona nyenkhe 😂😂 usi sapanganika
Anduna inu munabweletsa anthu akulilongwe kuno ku Blantyre kuti azizalanda makala koma katangale wawo akudula kwambili mpaka 1000000 galimoto imodzi
Brian Banda anagulidwa kalekale ndipo ndi galu WA MCP
He is brilliant Michael Usi and you have my support
Not brilliant he runs away to answer direct questions
Izi ndizopusa,, because akuzungulira mayankhidwe ,, the truth is sinawonepo akuvala zovalazo komaso misonkhano zomwe aliyese wa chipani amawonetsera poyera
That's why you are not at a position where you can address people 😢it looks so simple zikakhala sizili Kwa iwe 😂 you can say he is stupid but I guess he knows what he is doing 😊
Interview yangothela mwa TIKUFELANJI palibepo chikumveka
Amakhala pankhate sapheka Khoswe. Situluma Chala chokudyetsa phala. Now Michael Ussi has has come to his normal senses he has seen how tough is to run government , he has been criticize the previous government but now he don't want to be criticized whilst in government😅😅😅😅😅😅
Eeee koma ndi fumbi kuti kobo😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Unali munthu kale nthawi ya DPP ukulimbana ndi boma. Panopa mmmmmmm mwakhutha ndalama Inu.
He knows what he is doing
Opusa uyu anayamba zibwana kwambiri
Ndi opusa uyu
Manganya usachenjere mopusa wamva
Mmmm koma zizati vutadi kuiwala
Tikufuna tsogoleri ife oganiza boh not achakwela kapena Chilima ayi we need guys amene azasithe mmalawi kod MDF kulibe Traole wakumalawin😅
MDF inagulidwatu ku Malawi 🇲🇼 panopa ndi ya mcp
Manganya uchenjere bwinu to iwe
Mmmm awa asatisekese koma ku Malawi kwatha basi
A WISE NEW THINKER WILL GOVERN OUR LAND SO HELP ME GOD AM GOING TO END ALL THIS NONSENSE GARBAGE FOOLISHNESS HAPPENING TO OUR LAND SO HELP ME GOD
Uyuyu ndi kape sangathandize
Timuwona chaka chamawa ma plan ake koma panopo mmmmm ndikathyali 😅
Usi kuvara makaka kulibe tchito zonse zotsara zachabe zimenezo
It doesn't make any sense,akukonda kuyankhula zinsanzo zosagwirizana ndi nkhani,shame on him
Micheal Usi, is failing and is down now. Nothing He can give us his no longer a productive person
Kma malawi afika powawa
Palibe chanzeru alakhula akuluwa.