КОМЕНТАРІ •

  • @amunaachisale6120
    @amunaachisale6120 7 місяців тому +127

    😂😂😂😂 Fanz yaching'axy ibwele pano tipatse moto🔥🔥🔥👍

  • @AlfredMwenyali
    @AlfredMwenyali 7 місяців тому +12

    Ine ngat ndingalembedwe ntchito tuu kumeneko ndiyonkhala ndi Hilco yooo 😂😂😂😂😂 ching'axy fire 🔥🔥🔥🔥

  • @amunaachisale6120
    @amunaachisale6120 7 місяців тому +56

    Fans ya Hillco bwelan pano tiipatse moto pa modzi ❤🎉

    • @jamestewesa1046
      @jamestewesa1046 7 місяців тому

      Ife ai😂😂

    • @nelsontembo8036
      @nelsontembo8036 7 місяців тому

      Tilipo tiyipasa moto

    • @yamikanikaunda7443
      @yamikanikaunda7443 7 місяців тому +1

      mkazi winayo ..amanga hilco kumutu she is too emotional ...akufunika traning yabwino ...

  • @princemtuwa8468
    @princemtuwa8468 7 місяців тому +21

    Hahahahahahaha kofunsira banja kuja akufunsirakonso ntchito ,mpaka kulira.

  • @davisnyole3655
    @davisnyole3655 7 місяців тому +15

    Kufunsira kuja ndikovutaa😂😂😂😂Ine umbon ndili nawoooo😂😂😂

  • @yesayamalunga-eo5wj
    @yesayamalunga-eo5wj 7 місяців тому +11

    Koma Ng'axy😂😂😂😂😂😂😂 Hilco keep the fire burning, I have laughed today lol😅😅😅😅😅😅😅😅

  • @AlickGobede-qx8wd
    @AlickGobede-qx8wd 7 місяців тому +13

    Eeeh komano ching'axy amatha ma guy eeeh 😂😂 🔥 🔥
    Next plz

  • @True-worshipper
    @True-worshipper 7 місяців тому +2

    Ching'axy matama onse aja mwafunsilako ntchito 😂😂 zoti akulolani zikukaikitsa

  • @LewisKazembe-1405
    @LewisKazembe-1405 7 місяців тому +17

    Ching'axy ma award onse mpaseni 😂😂😂

  • @RichardKachingwe-p8h
    @RichardKachingwe-p8h 7 місяців тому +2

    Paliponse pakungosekesa ndiye nkuyambila pati kusekako 😂😂😂 ching'axy anaza 😂😂😂😂

  • @thokobanda4483
    @thokobanda4483 7 місяців тому +6

    Ati " look at Mr spider 🕸 " koma @ching'aning'an you are the best Comedian in Malawi 🇲🇼.

  • @Dianabanda902
    @Dianabanda902 5 місяців тому +1

    The prove mode.😅😅🔥
    Was everything

  • @ChinsisiKananga
    @ChinsisiKananga 7 місяців тому +22

    Ati look at Mr Spider 🤣🤣🤣

  • @MirrieMw
    @MirrieMw 7 місяців тому +2

    Wangoyamba kulira chingaxy po mmene ndasekera ine😂😂😂😂komatu mwaikometsa musachedwe ina changu❤❤

  • @Watson265
    @Watson265 7 місяців тому +27

    If you see this comment in 2063 know that I was watching this in 2024 while smiling 😀

  • @maxyfreeman9691
    @maxyfreeman9691 6 місяців тому +1

    I love this...mayi ching'axy

  • @RamusiJames
    @RamusiJames 7 місяців тому +3

    Umakwana ching'axy ati muzipempha appointment 😂😂😂

    • @AungunKadzinja-wv2uc
      @AungunKadzinja-wv2uc 7 місяців тому

      Kkkkkkk Mmmm chinga`aning`ani unapitililila pokwana I can't wait for episode 3 Guys chonde pasamatenge nyengo yaitsli musanatuluse kena mix mukutisiyila nmalere anyway more fire

    • @abduhrwahmaansilverbanda4908
      @abduhrwahmaansilverbanda4908 6 місяців тому

      @@AungunKadzinja-wv2uc kod part 3 sibwela

  • @eltonmsuku8287
    @eltonmsuku8287 7 місяців тому +1

    Adha awowo operekeza ching'axy, a very good actor

  • @HilcoMw
    @HilcoMw 7 місяців тому +6

    Thanks for the feedback

  • @halimasauzande2514
    @halimasauzande2514 7 місяців тому

    😂😂😂Ayi ndithu. Zoti kufunsila kumavuta Ndaonela pa ching'axy😂🤣 Ayi ndithu. May God be with you and Gate be with me😂😅🤣

  • @MHG__BeatS
    @MHG__BeatS 7 місяців тому +5

    Ili fire mwala mwala ching'axy ndi gate man 😂😂

  • @SusannaSibongire
    @SusannaSibongire 6 місяців тому

    bwana ching''axy kkkkkk nice one

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 7 місяців тому +1

    😂😂😂😂😂Atii muzibukatu ma pointment 😂😂😂 ndie dzakeyo atii ndikukupatsatu 10 minutes ndikuonera😂😂😂😂😂

  • @alickka
    @alickka 7 місяців тому

    Ili mushe episodiyi, Malawood is on the rise 😂😂 mukadye lunch, osati za nandolo 😂😂

  • @alexngomola3654
    @alexngomola3654 7 місяців тому

    Following live from cape Town ...kazitalikako koma pleas ili bho kwambiri
    Komanso ampwanuwo aphunzile acting..
    Koma so far ili bwino hvyy🇲🇼🔥❤

  • @cassimyusuf6683
    @cassimyusuf6683 7 місяців тому +2

    Ching'axy welephera kufusira nkazi 😂😂😂😂

  • @mortonnyasulu3282
    @mortonnyasulu3282 7 місяців тому +1

    God be with you & Hilco be with me... koma ching'axy 😀😀😀

  • @thokobanda4483
    @thokobanda4483 7 місяців тому +1

    Koma zimati aluminum onse ndasiya kucheza nawo 🤣 ai zikomo mudzatifuna zidzakqvutqko kumeneko🤣🤣🙌

  • @AyrooRajab-ls3om
    @AyrooRajab-ls3om 7 місяців тому

    Kkkkkkkkkkk uyu akufuna akuti yaUlonda after kusoowa mbalume Chingaxy Fanz muli kuti✍️✍️🤸🤸🤸🤸

  • @blessingsmwenela1308
    @blessingsmwenela1308 7 місяців тому

    Aaaaa Kodi mau a Hilco amamveka chonchi ngat kamwana 😅🤣😅🤗timangomva mnyimbo muja koma omwe akutuluka apapa enatu

  • @EsnartPhiri-c2m
    @EsnartPhiri-c2m 2 місяці тому

    Love you guys from Zambia 🌺

  • @KajawoAdamBlessings
    @KajawoAdamBlessings 7 місяців тому

    Ching'azy tsopano wabwera ndi fire 🔥🔥🔥💚 ipitilize mission ilibwino hvy

  • @Navy-ps9hx
    @Navy-ps9hx 5 місяців тому

    This guy is something else

  • @KondwanMakhaza-yc2md
    @KondwanMakhaza-yc2md 7 місяців тому

    Kkkkkkkkkkkkk ati walowadi uchenjeletu asakulande ameneyo utha kungoona hilco wayamba mwano😂😂😂😂 kkkk koma mubebesa

  • @ChifundohMitulo-bg2lv
    @ChifundohMitulo-bg2lv 6 місяців тому

    Vuto la ching'ax ndilimenelo osangopita pa mfundo bwanji😅😅😅😅😅😅😅

  • @BillyMbwandira
    @BillyMbwandira 7 місяців тому

    Kikkkk,, ati mukhala pa pay slit 😂😂😂 Ching'axy 🔥🔥🔥🔥

  • @SundayScova
    @SundayScova 4 місяці тому

    Makina pa macheza ❤😂😂😅😅

  • @blissvevo2003
    @blissvevo2003 7 місяців тому

    kkkkkkkkkkk koma yeeeeeeeh apa wabwera hilco ndi nzako ching'axy

  • @pemphelobendela5375
    @pemphelobendela5375 7 місяців тому

    Hiliko wachichewa Ching'aning'ani iweyo unabwera kuzakhal aaaaa🤣🤣🙌

  • @SdjcNgophiShadreck
    @SdjcNgophiShadreck 7 місяців тому

    Kkkkkkk satanayo ndi balé wa hilco hahaha , ndimakufilani ku kumozambiki

  • @ChikumbusoSingano
    @ChikumbusoSingano 6 місяців тому +1

    Akuti kusakhulupilira ngati Thomas didimu kuti misomali inayenda bwanji 😂😂😂😂

  • @oswardmbewe
    @oswardmbewe 2 місяці тому

    I love your patience hilco

  • @ToptikBanda-gp1cd
    @ToptikBanda-gp1cd 7 місяців тому +2

    Satana amatha kukhara Nanu pafupi Koma inu simudziwa😂😂😂

  • @YaasirMdoka
    @YaasirMdoka 7 місяців тому

    Masha Allah ching'ni x
    Allah Akupatseni zonse zabwino ❤❤❤😂😂

  • @kondwanchigwenembe3183
    @kondwanchigwenembe3183 7 місяців тому

    😅😅😅😅 bwana ching'axy ati mkazi uja ndagwira.... My me

  • @Patricknelson710
    @Patricknelson710 7 місяців тому +1

    Kkkk kuyambira lero alimi ndasiya kucheza nawo 🤣🤣🤣🤣

  • @cloy28eyemark
    @cloy28eyemark 7 місяців тому

    Kkkkkk aaaa zee mfundo zeee nothing Koma ching'axy 🤣🤣🤣🤣🤣 ayi senks 🔥 🔥

  • @yohdizzy3526
    @yohdizzy3526 7 місяців тому

    Ngt ndukaba nde kt ndi hilco yooo kkkkkk
    Amene unja I'll marry me

  • @Hanna-gr5il
    @Hanna-gr5il 6 місяців тому

    God be with you Hiloc be with me 😂😂😂🔥🔥🔥😊

  • @Jusper998
    @Jusper998 6 місяців тому

    💥💥💥💥💥 Umakwana m'dara wazimagwelu 😂😂👏😂😂

  • @joycetembwe
    @joycetembwe 6 місяців тому

    I love seriousness in all the actors 😂
    Mabwera ngati coming

  • @OsmanS.Songwe
    @OsmanS.Songwe 7 днів тому

    😂😂😂😂Koma munthu uyu ndigalu kwa basi 😂😂😂

  • @CharleyItcan
    @CharleyItcan 7 місяців тому +1

    Kkkkk ching'axy @ wasiya kucheza ndi alimi

  • @Denze265
    @Denze265 5 місяців тому

    😂😂😂😂 Ching'axy ati munthu osekesa ngat iwe sindinamuwone chonsecho osekesa ali iyeyo 😂🙌🙌🙌

  • @JumahKanjombi
    @JumahKanjombi 7 місяців тому

    Kkkkkk😂😂😂😂😂 uyu ndigalu kwabasi nde akunyadila ngati wafusila bwanji

  • @andrewchikafa7322
    @andrewchikafa7322 7 місяців тому

    Ati sinanga ndikasanzike mai kunyumbaku koma chonsecho chikufunaso abwana 😂

  • @ArthurMtokoma-rt7yr
    @ArthurMtokoma-rt7yr 7 місяців тому

    😂😂😂😂😂 Ati apa ndy provoke provoke zikomooooo gugugugu zikomoooooo

  • @EnerstMzuza
    @EnerstMzuza 7 місяців тому

    Kofusira hilco chibwez wakafusira tchito 😂😂😂😂Kom ching'ax

  • @McdonaldBandah
    @McdonaldBandah 7 місяців тому

    Ching'axy ndi hustler guys Hilco akungoyenera kugwa naye nchikondi for so long😂😂😂

  • @WilliamPhiri-s4w
    @WilliamPhiri-s4w 7 місяців тому

    Koma ching.aning.an 2024 award utengaso ndipo ndiwedi spider wasiya kucheza ndi alimi iweyo wayamba gusegulila gate madamu uwo

  • @louiskagona
    @louiskagona 6 місяців тому

    Eeeeeee! Must watch serie ine pheeeee! Kudikira next episode

  • @HappyflexaChiraq-cl2ip
    @HappyflexaChiraq-cl2ip 7 місяців тому +1

    Ine ndikubwera kuzakufunsira kwanu konko sister wako alikonkoso🥰🥰🥲🥰

  • @aaminangelez2320
    @aaminangelez2320 7 місяців тому +1

    ching'anxy kkkkkk ugalu wako manthano🤣🤣🤣🤣🤣

  • @BensonLitta
    @BensonLitta 7 місяців тому

    Kkkkkkkk km Mr spider anabwera km likumachedwa km 😂😂😂😂😂😂

  • @MussaJohn-gt8ep
    @MussaJohn-gt8ep 7 місяців тому +2

    ching_axy his always make crazy....... big up to hilco and them

  • @JoãoChirwa
    @JoãoChirwa 7 місяців тому

    Mmmmm ndimachedwa yatuluka❤❤❤❤ imandiwaza azibwelabe

  • @BrianSimfukwe-eg1vr
    @BrianSimfukwe-eg1vr 7 місяців тому

    Ndungoseka ine kuno iiih. Ching'aning'ani ndi dolo eeeesh 😂😂😂🙌🙌🙌🙌

  • @HEZEKIAHCHUNGA-ib2hi
    @HEZEKIAHCHUNGA-ib2hi 7 місяців тому

    😂😂😂😂😂Ching'axy wasiya kucheza ndi alimi 😅😊

  • @PatumaLabson
    @PatumaLabson Місяць тому

    Nice 😮😊🎉❤❤

  • @hendersonbendes903
    @hendersonbendes903 7 місяців тому

    😂😂Koma a ching'axy kumuwalira mzanu choncho ngt wagwiraditu🙌

  • @VeronicaKataya
    @VeronicaKataya 5 місяців тому

    Adona atsegula gate wa nde mmmmm Ali serious 😅😅😅ngat afuna iwowo bwa

  • @alinafemakwinja
    @alinafemakwinja 7 місяців тому

    😂😂😂😂😂😂😂 mesa amadzafunsila Kodi kkkkk game changer

  • @giftwanya7901
    @giftwanya7901 7 місяців тому +1

    Imene ingandikhale ine ... Ndiyokhala mamuna wake wa Hilco

  • @AnnieBanda-rb2dk
    @AnnieBanda-rb2dk 7 місяців тому

    Koma ching'aning'ani sazatheka mwava iyaa kkkkkkķkkk koma iwe sunachenjere bwino eti... kkkkkk mumatisekesa madala

  • @shamranabdullah3004
    @shamranabdullah3004 7 місяців тому

    😂😂😂😂 ching'axy ulibe mfundo ase Mesa umapita kokafunsira 😅😅😅😅

  • @TheboZilinde-tq1gf
    @TheboZilinde-tq1gf 7 місяців тому +2

    Provoke provoke 🤣🤣🤣🤣🤣 kma yeah 🙌

  • @jamesnixonMw
    @jamesnixonMw 7 місяців тому

    Nyamata ching'axy suzatheka uli ndi khofidesi ya nyooo😂😂

  • @jameslifah7909
    @jameslifah7909 7 місяців тому

    Ka low ka low move daddy kupita ndi confidence 😂😂😂

  • @HanifahSaiti
    @HanifahSaiti 7 місяців тому

    🎉🎉😅😅 kma mumativetsa kukoma MR ching'aning'ani 😂😂😂

  • @RachealNyirenda-s1z
    @RachealNyirenda-s1z 7 місяців тому

    Kkkkkkkkkkk koma kukafunsira ntchito mumalo mwa bebi kkkkk

  • @adamslabanah504
    @adamslabanah504 6 місяців тому

    Ching'asy aise 🔥

  • @hawamavule
    @hawamavule 7 місяців тому

    😂😂😂😂😂😂 kom iyiyi yandiwaza shaaaaaa plan B ilimwala

  • @GindiYagamba
    @GindiYagamba 7 місяців тому

    Kkkkkk mwagwila ntchito mwina ntchito ching'axy kkkkk😅😅

  • @ackileogaya9768
    @ackileogaya9768 18 днів тому +1

    Provoke provoke 😂😂😂

  • @kingsleymsampha2260
    @kingsleymsampha2260 7 місяців тому

    Koma guys eeeeeh....mwabweratu, big up.

  • @BealiniaLangultone-jk5nj
    @BealiniaLangultone-jk5nj 7 місяців тому

    Kaya atuluka kya satuluka ineyo ndy ndikhalapo kwa 3 dayz😂😂😂😂😂

  • @RuthTembo-id2wi
    @RuthTembo-id2wi 6 місяців тому

    Wow that's great 🎉

  • @daviekachigunda6682
    @daviekachigunda6682 6 місяців тому

    Kokafusira, mwayamba kufusira ntchito 🤣😂

  • @Dickiez99
    @Dickiez99 7 місяців тому

    Wow! I've enjoyed it. Can't wait for the next episode. 🥳😋
    Ndi Ambuye indeed 🔥 from the song in the background.

  • @thimaschilombo794
    @thimaschilombo794 5 місяців тому

    This is great

  • @ChisomChikaiko
    @ChisomChikaiko 6 місяців тому

    This machinjiri Fede kwabanyira guys et ? Amene akudziwa andiuze

  • @LindaMuyaya
    @LindaMuyaya 5 місяців тому

    Kodi zimatheka kupanga download mavideo pano? Ngati ndichoncho umatani? Ine zikukanika

  • @christopherpetro-pen3678
    @christopherpetro-pen3678 7 місяців тому

    Komatu chiphwanya ndi za look at Mr spider wakoyooooo😅

  • @IreenBauleni
    @IreenBauleni 7 місяців тому

    😂😂 km yeah kofunsira ukwati kuja kwafunsilidwa ntchito

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 7 місяців тому +2

    Hilco n Ng'axy + Adha enawo ndi Sister inayo guys muli fireeeeeee😂😂😂😂😃😃😃😃😃😃🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @LovelyBassGuitar-rq4wf
    @LovelyBassGuitar-rq4wf 7 місяців тому

    LOL😂😂😂😂😂 ching'axy uzatipha ndi pwete

  • @lusungugondwethebulu2947
    @lusungugondwethebulu2947 7 місяців тому

    Koma Masamu awa azatheka poti chikondi sichiona nkhope😅😅😅😅 koma chilungamo Inu Hilco Si type yanu

  • @felixphiri2465
    @felixphiri2465 7 місяців тому

    Koma ching'axy mutu wako sumagwira,, kokafunsila mkazi mkukafunsira ulondo😂😂😂😂😂😂

    • @happyk449
      @happyk449 7 місяців тому

      Khulupililan musanawone ...koma kamdala aka

  • @mphatsondalama1111
    @mphatsondalama1111 7 місяців тому

    At least being a get man azimuonera pafupi hilco😂😂

  • @robertmwambazi3524
    @robertmwambazi3524 7 місяців тому

    Hahahahahaha kufusira ndi kovuta ndithu 😂😂😂😂