Indeed the Vice President, you are a brilliant, humble and wise person. As you help our President in governing Malawi, may the Almighty God help you and give you all the desires of your heart.
One wise statement that caught my attention " ine ndinalowa mmalo mwa a Chilima...when he died, was he out or inside Alliance? " Wakumva wamva...yankho la straight 🔥 👌 💯
Chilima anakukondani a Usi ndi mtima wake onse, koma inuyo chikondi chanu chinali cha mitala, that's why nzanu uja atafa mumapanga ma celebration ndi Chakwera wanuyo ku state house, olakwa ndi Chilima mwina pokukondani 😢 still in our heart SKC 😭😭😭😭😭
I have learned something from Michael usi akuti ukakhala tsogoleri don't rush kuyankhula because as being a leader you need kukonza ma speech olakwakika kwa okutsatira
Vuto la a Malawi ndiloti when it comes to Presidency, we always miss the right person to be the President guys Micheal Usi hes has the characters of a right president and he can deliver the gest kungoti a Malawi timangomuona pa angle yolakwika munthuyi sinthila kuwili guys ndimunthu oyenela uyuyu Lets believe him and give him a chance
Bwana vice president pempho langa lakuti pitirizani kupanga zabwino ndi maganizo okonda anthu osati wina akusokonezeni kaamba ka udindo wanu please try to do good things koma moopa Mulungu poti iye ndiye mwini zonse. ❤ Love your country ❤❤❤❤ monga tonse ndife anthu amodzi posayang'ana mbali kapena mtundu wa anthu kuti uyu ndiwakumpoto kapena chigawo chapakati kapenaso uyu ndiwakumwera ai, inu ndinu kholo la a Malawi wonse ndipo mukhale ngati m'mayi amene adabala ana amapasa amagona pakati chagada kuti mwana wina akafuna kuyamwa ayamwe osagonera mbali imodzimodzi ai kumbukirani kuti odyetsa anthu wonse ndinu ndipo tikunena panopa Thiko ulindiinu.
I loved so much Usi when he was abambo a Sikono in ADRA Koma pano mmmmmmm ayi, I can't take him on board as the VP of Malawi! Zinthuzi aliyense amakhala ndi malo ake choondeee!
Brian Banda ake aja adalephela kwa fusa ma a m'sonda........ Amwene kwa onse panopa amene akumafusa ma funso omvekandiwa nkazi uja amene amampanga interview Winiko uja
Now I love this guy he is doing anything for malawians achakwela aziyamiza ma vp awoo ndi a nzelu koma achakwela musamavele mafana anu akuchipani kwanu plz ma members aku mcp ndi nsanje kwambili komanso amadalila kwambili zaufiti but good job Mr usi under the president chakwela
But this guy is trying to cover himself in terms of answering questions.😢 My point of view this Usi is an Mcp member not Utm🤞powers can make people completely change. Let's meet next year bwana Usi mulungu akuona chilichose atimenyera nkhondo🙏 muzaululika.....
Dr Usi is unifying leader who don't want to injure the divided party. His agenda is to bring unity In the party. UTM should nurture the wisdom in their Leader.
Ndalamazo zikupelekedwa lelo nthawi yonseyi mmene Malawi wakhala aku kulukutika ndi umphawi zidali kuti Don't play with our mind,we need serious leaders and leadership So Michael wayamba bwino do not change,please we recognize you
Indeed the Vice President, you are a brilliant, humble and wise person. As you help our President in governing Malawi, may the Almighty God help you and give you all the desires of your heart.
One wise statement that caught my attention " ine ndinalowa mmalo mwa a Chilima...when he died, was he out or inside Alliance? " Wakumva wamva...yankho la straight 🔥 👌 💯
Msiska interview yakukulira iyi....bravo Dr usi
Brilliant Usi
🔥🔥🔥🔥🔥
Very familiar with people, may god bless you Dr usi
Good interview and we learnt a lot
DR Michael Usi is a man with wisdom and a philosopher.proud of you VP
Wise and humble leader. God bless you.
Chilima anakukondani a Usi ndi mtima wake onse, koma inuyo chikondi chanu chinali cha mitala, that's why nzanu uja atafa mumapanga ma celebration ndi Chakwera wanuyo ku state house, olakwa ndi Chilima mwina pokukondani 😢 still in our heart SKC 😭😭😭😭😭
Two mistakes made by chilima
1. Making alliance with MCP
2. Trusting Michael Usi
@@DanielKaombe-im3pr ndipo that's a big mistake
Ur seeing this in a small minded point of view
Ndipo udindowu ankausakasaka ndipo zikuoneka kuti njira ayisaka kuti afikepo basi ndipo panopo is happy
Mwanena chilungamo
Brilliant Dr Usi, am encouraged with your sentments
I have learned something from Michael usi akuti ukakhala tsogoleri don't rush kuyankhula because as being a leader you need kukonza ma speech olakwakika kwa okutsatira
Facts
Keep it up sir.Mulungu amadziwa zonse,
Dr. I sulute you 💯
Ngat yudasi adapheleka yesu kulibwanji Dr usi
Of course I don't underate Wonder Msiska in this interview! He is also very challenging and well composed!! Bravo Mr Msiska!
Bravo wander msisha olive you big
Woow Manga you are blessed ,wishing to learn more from you.very good answers with examples without any complications
Vuto la a Malawi ndiloti when it comes to Presidency, we always miss the right person to be the President guys Micheal Usi hes has the characters of a right president and he can deliver the gest kungoti a Malawi timangomuona pa angle yolakwika munthuyi sinthila kuwili guys ndimunthu oyenela uyuyu Lets believe him and give him a chance
Young talent vp i salute you kuyankha mopanda mantha komanso chimene mukudziwa odya zake alibe mulandu
Am getting your points mr vp and you are a wise person big up mr usi❤❤❤❤❤
Ndinu 1 , munthu wa mzeru our VP🎉
Watching from Rosenberg Germany
Onaa nzeruu 🎉!!
Bwana vice president pempho langa lakuti pitirizani kupanga zabwino ndi maganizo okonda anthu osati wina akusokonezeni kaamba ka udindo wanu please try to do good things koma moopa Mulungu poti iye ndiye mwini zonse. ❤ Love your country ❤❤❤❤ monga tonse ndife anthu amodzi posayang'ana mbali kapena mtundu wa anthu kuti uyu ndiwakumpoto kapena chigawo chapakati kapenaso uyu ndiwakumwera ai, inu ndinu kholo la a Malawi wonse ndipo mukhale ngati m'mayi amene adabala ana amapasa amagona pakati chagada kuti mwana wina akafuna kuyamwa ayamwe osagonera mbali imodzimodzi ai kumbukirani kuti odyetsa anthu wonse ndinu ndipo tikunena panopa Thiko ulindiinu.
Don't forget that UTM wants to be independent
Michael Usi. you are number 1,ndiwe ochenjera kwambiri
Akatundu
❤❤ our new virce president Dr micheal Usi......😊😊
Kma ndfe anthu anu bwana mukanamatiyankha kut tidxiwe
Wonder sangamukwanitse Dr Usi.
Olo Brian Banda amanama koma Britain banda amayesesa
Uyuyu simbuli chomwe amapanga amachidziwa 🙌
Thanks Mr VP for your clarification
rsz
Uyu amafunika Brain banda sanyengerela mafunso.usi adamupeleka skc.wamagazi mmanja iwe
Bravo hon usi
Genius Michael usi bravo
I loved so much Usi when he was abambo a Sikono in ADRA Koma pano mmmmmmm ayi, I can't take him on board as the VP of Malawi! Zinthuzi aliyense amakhala ndi malo ake choondeee!
Wonder you should have given this interview Brian banda
Izi akadakhala Brian ❤
High time to hear that
Watching from south Africa
Exclusive iyi imafunika Bryan Banda uyu akanaithawa interview imeneyi ndithu
Anakanika kale adamawa nda nzeru osat masewela
Brian Banda ake aja adalephela kwa fusa ma a m'sonda........
Amwene kwa onse panopa amene akumafusa ma funso omvekandiwa nkazi uja amene amampanga interview
Winiko uja
Now I love this guy he is doing anything for malawians achakwela aziyamiza ma vp awoo ndi a nzelu koma achakwela musamavele mafana anu akuchipani kwanu plz ma members aku mcp ndi nsanje kwambili komanso amadalila kwambili zaufiti but good job Mr usi under the president chakwela
@@StevenMjMbama bwana opoila ndi Chakwerayo he don't have leadership
Wonder kuyang'ana kwake ngati ungomewamenya khofii
Watching from Vietnam ..Ooh my beloved Malawi
how are you there bra
But this guy is trying to cover himself in terms of answering questions.😢 My point of view this Usi is an Mcp member not Utm🤞powers can make people completely change. Let's meet next year bwana Usi mulungu akuona chilichose atimenyera nkhondo🙏 muzaululika.....
Amen. Zoona.
yankha bwino fuso iwe wunapereka chilima ndiweyo
Ndinu abonza
Dr Usi is unifying leader who don't want to injure the divided party. His agenda is to bring unity In the party. UTM should nurture the wisdom in their Leader.
God bless Mr Vp
Apa, UTM ikungonamiza Anthu ndiyekuti...😅😅😅😅😅😅 ,
Sorry Osangalala popanda Phinduuuuuutu Apa
Politician is not a person that will give u a direct response in most cases...
Udasi miss Usi Munthu Oipa zedi 😢😢😢
This man has very clear points and feelings before towards his country.
He has points step by step well analysised
You deserve Michael,let's hold hands malawians let's support Michael
Kupusa kwako nyau iwe
Awa ndebolaso kalindo straight to the point osati kulambalalaso apa.
Genius Usi
Usi Ali ngati Judahs skaliyoti adamupereka SKC koma anva ululu owopsa
I think it is you bra uli judahs
Komatu mmayankhula ngati muli ndi umboni.Just guessing but kuyankhula as of you have concrete evidence
Concrete evidence iposele SKC adamwalila😂😂😂😂
Watching form Lusaka Zambia 🇿🇲 big up vp of Malawi 🇲🇼
U r true veep in mw
Munapereka bwana wanu Dr utsi, nkulakwa kodi kutero, akanakhala Brian Banda tu akanafutsa limenelo
🎉
Very Interesting. Sitinati
Big up bwana vp
Or ka minute of silence in honour of Chief odya naye mtedza, taaaa!
Leading between the lines, and ofcoarse without forgetting about the plane crush... Usi is with MCP
Well-done Mr VP wonderful speach keep it up
Usi ndi machine
Usi mulungu akuone😭😭😭😭😭😭
❤
This guy is in Very Serious Situation. If he won't reveal his Intentions avutika Mumtima hvy
I repeat, Dr Usi ndakunyadirani, ufulu tilinawo koma tsopano what remains now - is the battle against disease, poverty and discipline.
He should not confuse utm people he is mcp member for long time. People will meet him at utm convetion leave him adzatha ngati curtain
VIVA USSI
Usi you're moving computer, l salute 👏 👌
Wander wachepa nayotchitiyi Brian banda is very capable
Olo mutapeleka ngongole yopanda chikole koma palibe chomwe tingachite ife anthu osauka chifukwa nima ndiodula sitikudya ndalamayo izingothela madeya ndiposo deyayo kupezeka nd mwayi ingotsisani zinthu ife osauka tizikalima ganyu bas palibe chanzelu chomwe mukupangapo apa ngongole ndiye chan mukuganiza kut munthu wagona ndinjala masiku atatu mumpase ndalama imeneyo bizinesi itheka inutu mutokhuta
Dr Usi mukumubalalisa Wonder
Ndipo nde wabalalikiratu😂
@@quincyswart1884wabalarika kale koyambilirako ine zandimvekera mokolana kolana 🙌🏻🙌🏻🙌🏻😳
Aliyese mayankho aziwapeza yekha apo sanamvetse 🤣🤣
My VP
Usi ur brilliant but don't be deceived with this so called position..... build ur own party aise
Michael your number one, mupitilize because anthu ena akumakudelerani dada
Usi just do your job but don't forget where you come from
Chief _--_Chief 😅😅😅😅😅😅
Kalulu uyu sazatheka 😂😂
God is the best judge all the best bwana vp we have to move on as a country
Dr Usi is wise lets give him support 🙏
You may have full support if you just play ur cards well Mr VP....
The best person who answers interview without any force is only born kalindo not awa iyayi
I would feel gud if Wander ask him about v investigation about v crash of Airplane VT MW we ready to hear
Musiye manganya asakukulakwise ameneo ndiwa mcp ameneyo akugulisa utm ndimwana pandale kutha kwamanyanya
Brian Banda would have been the best host in this Times Exclusive interview!
This man is indecisive, wadziika pa mpani sakudziwa kuti aliku UTM or MCP .
Chief emweyo sizikumveka akurankhurazo
😂😂😂manganya chilungamo alibe according the way he is swaying the straight simple question
Micheal Usi ndi dolo. Atukula dziko.
Kkkkkkkkkkk bwana usi akuti uziti ndatuluka osati tatuluka 😂😂😂😂😂😂
Koma ichichi 😅 chimafunika Brian Banda,,, ndi ship iyiyi siyokoka ndi boat ikawonongeka
😂
Bwana you is brave enough,bweresani UTM pamodzi
Usi your number One
Ndalamazo zikupelekedwa lelo nthawi yonseyi mmene Malawi wakhala aku kulukutika ndi umphawi zidali kuti
Don't play with our mind,we need serious leaders and leadership
So Michael wayamba bwino do not change,please we recognize you
Ife talandira kale
Koma nzeru zilimo
APM my vote
Tathokoza kuti mwanva pempholathu kuti muzichosa sound yomwe imanveka pansi.
He is wise
I can hear beautiful Adhan maashaa allah
mr vice president and mr president himself all the best God help you