Since democracy came in I have never heard anything good from the people about ours leaders leaders here in malawi and Africa as a continent. The main reasons are regionalism, tribalism and favoritism. Kalindo has one or two of these effects that is why noising much .
A Malawi, chomwe mumafuna sichidziwika, mumatangwanidwa ndi kuchitira m'sanje president ndi chipani cholamula, presidente akakwera udindo amakhala oyipa kwayinu, Kodi mumafuna president otani?
Bon kalindo akutiyankhulila anthu osawukafe we love you❤
Our own president kalindo you stand with poor people
Mmakwa boss
Bon keep on fighting for the good of Malawians imagine ku Queens zoyezera malungo kulibe at 60years please
Since democracy came in I have never heard anything good from the people about ours leaders leaders here in malawi and Africa as a continent.
The main reasons are regionalism, tribalism and favoritism.
Kalindo has one or two of these effects that is why noising much .
Bon kalindo amakwanila kwambili ❤❤❤
Thank you so much Mr Bon kalindo for your information ❤❤
From njeza village T/A mabuka central Africa malawi mwana woopya kwambiri ndipo sindiopa
Wisely spoken
Big up Mr kalindo
Powerful massage massage
Apa president wa anthu osauka wayooya eeeee
koma tu zinganizo znazitu president i hope sakuzwa ai
Mumakwana bg 💪
tikuyamikileni potitsegula mitu
Pano ndifuna ndikuyamike
Bone ungoyambisa chako ife tikisata
Makolo ankatiuza kuti mcp ndiyoophya now pano tawonano
Kell kay nanja lake lasokonekela
Dc
😂😂 komalizako eee sikusinja ndi gwenembe
Kkkkk kkkk koma The DC
Anapha m'bale wake chifukwa chofuna kulamula Malawi mpaka 2060 akuti hehehe yomweyo chikangawa
Sure
Opoila uyu
Vuto ndife amalawi kupusa zinthu ziku onongeka wanthu ali mphee.
Km ineyo bone kalindoyi ineyo ndimamuda km nkhani akukambayi ndiyoona tizichita kugula Kaye kuboma nchenga 😂😂😂 kenaka kwamavenda noo this is not fair
Koma kalindo ndi 1 kkkkkkkk
Agalu achabe chabe awa ndipo anthu atope naye chakwera
Kalondo ndi mbuzi yamunthu. Amandinyasa. Ameneyu sakudziwa kuti akubzala mbewu yachabe.
Iwe mutu uwumawo do you think zikutisangalasa ifeyo nkhope yonyasayo
Ngat kalindo ali mbuzi yamunthu iweyo ukhala ndani?
Gwenembe😂
Boma ili ndilopenga misara pompano ananena Kuti tisiye kudya nsima yoyera panopa akuti anthu asiye kuvuwura chenga pokhapokha atenge chilolezo Kodi ndarama zamisokho zachepa panopa mukufuna zamuchenga shame on you MCP
Ya komadi e
Ayamba kulimbana ndi anthu osauka ndipo ziwanda zimenezi zalitenga dziko ngati ndi lao, zikanthidwa ndi zanja la Mulungu pompano
Adapenga uyu kuchita kunenerela kut kufuna kumangidwa ndiye tinene kut akamatuluka kupolisi amalandila ndalama eti
Mpaka ntchenga koma eish
Akuonjeza tsopano
chakwera ndi chigawenga boma la mbava ili boma la zitsiru zokha zokha chakwera pantumbo pa make chitsiru mbava
Km aonjeza achoke mbomamo palibe akupanga km ukakwatila umadalila makolo kd
Koma mumapitadi ku vep bwana
Chifukwa chadyera 😂😂
A Malawi, chomwe mumafuna sichidziwika, mumatangwanidwa ndi kuchitira m'sanje president ndi chipani cholamula, presidente akakwera udindo amakhala oyipa kwayinu, Kodi mumafuna president otani?
Aside kuba ndalama zamalawi
Inu dzimvereni chisoni inuyo.Mukamawona usi mukumamva bwanji.Inuyo akalindo ngati achibale anu ngati ali anzeru bwanji osakutengani akakuwoneni kaganizidwe sikalibwino
Utsi watani munthu oipa mtima umapereka chilima mmanja mwa cakwera kuti amuphe ukuona ngati amalawi sitikudziwa bon kalindo sanaphapo munthu alibe magazi mmanja sanalowepo satanic ndipo usanalakhule udziganiza wamva anthu ambiri timamukonda kalindo ndi munthu yekhayo yemwe amatitothonza udzikamuudza
Bon kalindo musamamufanizile ndi usi chifukwa kalindo alibe dyera koma awo mukuti awusiwo ndi adyera
Mbuzi iwe usi Nd chigananga
Galu iwe ungafanizile Bon Kalindo ndi utsi what kind of you human being are you?
The DDDDDDDDDCCCCCCCCCCCC 🤔 🤔
😂
Kodi amwene simukutopa mene munayambira aanzako Ali phee kuyendesa ziko
Adzatopa cakwera akadzacoka kapema kusitha maganizidwe ace onyasa chifukwa anthu ambiri itikuona ubwino wachakwera chimene tikuona mwacakwera ndi kupha kuononga ndi kusakadza mmm cakwera munthu oipa ukamuudze wamva ndi iweyo
Sangatope ameneyi chifukwa dzikoli eliyense akusata chamba atsogoleli akasiya kusuta nayeso asiya
Akulimbana ndi inuyo a mcp kut musiye kuzunza amasiyewo
Pamene ndimapemphera kupempherera dziko la Malawi ndinaona thambo la ziwanda. Tsiku lililonse limene Chakwera akilamula zithu ziwanda zikulowa m'Malawi. Mupemphere kuti Chakwera asadzawine. Chakwera ndi wa satanic.
Tingomenyana yamanja basi
Shitombo shag'wako bon mathanyula
Matlamela a ng'uako nawenawe Robson nyompfi wako
@@reggieanthony7508 hunro nayar
Dangerous Child
Komatu chakwela wafika pauchitsilu
NDIMAGANIZA KUTI MWINA INU A UTM KUTI MAGANIZA NGATI ANTHU INU CHAKWERA ANAPHA CHILIMA LERO MUPANGASO ZAMGWILIZANO NDI SATANA MUGANIZA KUTI ASIYA KUPHA NOSE AKUPHA INUYO A UTM MUTHA
Mfundo za boma zikakhale za nchenga koma mcp mwasowa zokambilana