FELIX NJAWALA WASAMBWANZA CHIPANI CHA MCP NDIPO WASIMIKIZADI KUTI ANATULUKA MU TONSE ALLIANCE

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 17 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 120

  • @violetpotani
    @violetpotani 2 місяці тому +14

    Munasowatu Mr Njawala.. Welcome back

  • @RafickOsama-k2r
    @RafickOsama-k2r 15 днів тому

    Your welcome to Malawi 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼 🇲🇼

  • @PatrickSomanje
    @PatrickSomanje 2 місяці тому +11

    Exactly mr njawala u ar true man osati uyu akumuti manganya

  • @deniskondani1305
    @deniskondani1305 2 місяці тому

    Felix ndi more fire

  • @afritouch4660
    @afritouch4660 2 місяці тому +3

    APA NDAWONADI KUTI UTM INAKALU YAMPHAMVU.. Ndubwera konko bola osamphwekensaso..!! More fire 🔥 UTM

  • @MuyaoComedies
    @MuyaoComedies 2 місяці тому +3

    I'm following, Salam alaikum

  • @BeatriceProfessor
    @BeatriceProfessor 2 місяці тому +1

    Tell them ❤❤❤

  • @MzikaPhiri
    @MzikaPhiri 2 місяці тому

    More fire Njawala

  • @sesfikileshop7344
    @sesfikileshop7344 2 місяці тому

    Felix Njawala my man

  • @CarolynMtegha
    @CarolynMtegha 2 місяці тому

    Good speech Felix Njawala.

  • @shayrafernandeslatif9556
    @shayrafernandeslatif9556 2 місяці тому +1

    Madam kaliyati for President ❤❤❤

  • @BrianNowa
    @BrianNowa 2 місяці тому +1

    Please akulu akulu a UTM takhaliranani pansi pasakhale kugawanika mmachitidwe together we can, pasamapezeke Ena odzipatula, pakhale mtsogoleri yemwe adzibwsletsa umodzi ngati mmene SKC amachitila, SKC adali munthu odziwa zomwe akuchita komaso zokomera aliyese, kulibwino kukhalirana pansi kukambilana kusiyana mkumanenana ku ground
    Munthu olalata kwambiri samakhala ndi mphavu, kupita pa ground mkumakalankhula za awo ndi awo sizithandiza chipani koma kuwauza wanthu pomwe muli ndi komwe mukupita ndi zomwe mukufuna kukachita, pewani a Utiko okhala pazenera ooneka ngati Ali nanu koma mkati mwawo Ali kwina, samalani ndi anthu omwe akulowa posatengera mbiri yawo,

  • @RodneySupply-tx3ul
    @RodneySupply-tx3ul 2 місяці тому +7

    Elder my brother ndi zoona zedi mwayankhula and keep it up osaopa

  • @modestamhango7737
    @modestamhango7737 2 місяці тому

    Powerful speech. 🔥🔥🔥🔥🔥

  • @MarthaMbewe-uk5nn
    @MarthaMbewe-uk5nn 2 місяці тому +3

    Njawala motooooooooo!!❤

  • @AlexManuelMisomali-sv1vn
    @AlexManuelMisomali-sv1vn 2 місяці тому +3

    Anthu ndiomwe amuphetsa Chilima chifukwa iyeyu saamafuna MCP

  • @FrancisMazamba
    @FrancisMazamba 2 місяці тому

    Njawala keep it up mulungu ankhale nawe

  • @AgnessKavalo
    @AgnessKavalo 2 місяці тому

    Kuchotsa mboraaaahhh imene ili MCP 😂😂😂😂😂😂

  • @doreendzimuuzani7180
    @doreendzimuuzani7180 2 місяці тому

    Chilima is still living through his people ❤

  • @isabelmartin7567
    @isabelmartin7567 2 місяці тому

    UTM on🔥🔥🔥🔥❤❤❤

  • @stevemtambalika
    @stevemtambalika 2 місяці тому

    Bomaw ilooo my vote

  • @CathyYobe
    @CathyYobe 2 місяці тому +1

    Utm more fire

  • @NazaniNoah
    @NazaniNoah 2 місяці тому

    Mudalitu limodzi lero muyikana poyera ok,oh!zikomo yenkhova poti inu nokha simukhumudwitsa

  • @EleniJames-rc3ot
    @EleniJames-rc3ot 2 місяці тому

    Mjawala ndimakunyadilani pamodzi mayi kaliyati ndi onse a utm mulandile ulemu wanu 2025 mavoto aku utm

  • @SamuelJoseGaviteni
    @SamuelJoseGaviteni 2 місяці тому +6

    Dr chilima wasiya chipatso ana afundo

  • @PatrickSomanje
    @PatrickSomanje 2 місяці тому +2

    I love u mr njawala

  • @jahmanmakwinja-ef7zn
    @jahmanmakwinja-ef7zn 2 місяці тому

    Words❤

  • @AlgentChilanga
    @AlgentChilanga 2 місяці тому

    Zikomo Felex njawara kumeneko ndiye kuyankhula tikuziwa zimakuwawani nafeso zimatiwawa

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 2 місяці тому +2

    Zoona zoona Mr njawala auzeniiiii

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire 2 місяці тому

    Zoona zoona

  • @HevenChiwaya
    @HevenChiwaya 2 місяці тому +5

    Felix kumeneko ndiye kubwela

  • @gracemkandawire8769
    @gracemkandawire8769 2 місяці тому +1

    Njawala ,,Fredo ndi Kaliati tikulimba mtima

  • @DynessMsiska
    @DynessMsiska 2 місяці тому

    Moto kuti 🔥🔥

  • @TiyanjaneMkwate-we8gu
    @TiyanjaneMkwate-we8gu 2 місяці тому +1

    Tinkakuuzani ife kuti sapita kawiri, inu munkachita makani lero ndi izi

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg 2 місяці тому

    Chimene ndinapeza ine ndichakut Chilima uja was bigger than UTM itself.

  • @DENSONZULU
    @DENSONZULU 2 місяці тому

    ❤❤❤ UTM 🔥

  • @nelsonkajawo5176
    @nelsonkajawo5176 2 місяці тому

    😂😂😂😂 awa palibe cha nzeru anganene ndakayikanso ngati ali ndi ma followers

  • @ewn-mc6jv
    @ewn-mc6jv 2 місяці тому +1

    UTM more fire.

  • @AlexSamalan
    @AlexSamalan 2 місяці тому

    ❤❤ one love

  • @MakawaBenjamin
    @MakawaBenjamin 2 місяці тому

    Akumanga chakwera

  • @AlgentChilanga
    @AlgentChilanga 2 місяці тому

    Mkango ukafa,ana ake sangaleledwe ndi fisi tanthauzo monga ife ana autm kholo lathu mmene lidafera (SKC)mcp singatisunge ndiye tosefe itimenza.

  • @FatimaLuwembe
    @FatimaLuwembe 2 місяці тому

    Welco😊me❤❤

  • @AlgentChilanga
    @AlgentChilanga 2 місяці тому

    Koma mwanena miyambi yamphamvu Felex chilima adakuphuzisadi eti kkkk

  • @Biath-m4b
    @Biath-m4b 2 місяці тому

    Gwilanani manja a UTM ine vote yanga ndzakupatsan, manganya ndi oipa ndpo waonekelatu kuipa kwake sakudzwika mbali

  • @AustinMhone-r3s
    @AustinMhone-r3s 2 місяці тому

    MCP Chipani chankhaza kwambiri don't make alliance with them again.

  • @StalloneButao
    @StalloneButao 2 місяці тому

    Awa ndi adolo

  • @TrizaGeorge-q8w
    @TrizaGeorge-q8w 2 місяці тому +3

    Ndipo ndizoonadi abale mulungu ativa kulila kwathu ndithu

  • @PETERSINKADZIWA
    @PETERSINKADZIWA 2 місяці тому +1

    Kuswa kuswa basi. Emusipi No chance

  • @WanangwaMfune
    @WanangwaMfune 2 місяці тому

    Mwini wake wa miyambi anapita inuyo simungaikwanitse pangani fundo zenizeni

  • @paulnyondo7572
    @paulnyondo7572 2 місяці тому

    Uku ndiye kuyankhula osaopa.chiuzeni chilungamo chipani chakupha ndi chakupha basi fisi sasintha ndi fisi basi

  • @GraceLobart
    @GraceLobart 2 місяці тому

    🎉🎉🎉🎉🎉 yomweyoooo❤

  • @blessingkamanga1781
    @blessingkamanga1781 2 місяці тому

    Ndiye mwabweretsa Kabambe kuti akupititseni ku DPP😢

  • @brownodalla
    @brownodalla 2 місяці тому

    kuthana ndi ululu wa njuchi ndikuchotsa mbola

  • @aggiemlotha1208
    @aggiemlotha1208 2 місяці тому +2

    Chipani chapa FB😂

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire 2 місяці тому

    Inde inde ichotseni mbolayo

  • @JamesChiphwanya-m4v
    @JamesChiphwanya-m4v 2 місяці тому

    Inu a UTM musafooke chifukwa a MCP nawoso anayamba pang,ono pang,ono sanafikile kutenga boma inutso pachedwe pasachedwe muzalowa boma

  • @MarthaMbewe-uk5nn
    @MarthaMbewe-uk5nn 2 місяці тому +2

    😂😂😂😂😂 koma miyambi yabwino bwanjiii?❤❤

  • @violetkamvanthupi2443
    @violetkamvanthupi2443 2 місяці тому

    Izi ndi zoona

  • @TanazioUziyele
    @TanazioUziyele 2 місяці тому +2

    Aaaa chilima kulibe pangani fundo zanu ajawala

  • @MacfelsonMunthali
    @MacfelsonMunthali 2 місяці тому

    Last kicks of the dying horse,umaliro wachipani

  • @elsontmsukwa4356
    @elsontmsukwa4356 2 місяці тому +1

    Uthenga ogwira mtima 🙏🙏

  • @Chikumbuso-l5m
    @Chikumbuso-l5m 2 місяці тому

    Wayakhula bwino tichose chakwela

  • @WhiteRichard-cw2fo
    @WhiteRichard-cw2fo 2 місяці тому

    Ndiye munalephera bwanji kumusitha chakwalawo poti mwati inu mumasitha

  • @FelistasNkasalaMakumbo
    @FelistasNkasalaMakumbo 2 місяці тому +1

    UTM in my blood

  • @MaryChipeta-y4l
    @MaryChipeta-y4l 2 місяці тому

    Mfundoles Udali kuti wabodza iwe

  • @ShurahbilMakiyi
    @ShurahbilMakiyi 2 місяці тому

    Sindimaganiza kut UTM yatha koma mmmmm❤❤

  • @SamzyTimechisaleh
    @SamzyTimechisaleh 2 місяці тому

    ❤❤

  • @AnaLourencokan
    @AnaLourencokan Місяць тому

    Mwapilila

  • @MpapiParadise
    @MpapiParadise 2 місяці тому

    Kkkk awa angomataya nthawi kachipani aka plus ka aford sazalamulilapo boma ai

  • @peterchiutsi
    @peterchiutsi 2 місяці тому

    Guys chipanichi timachikonda koma stop zomangoti chilima chilimazi Mukumatiwawisa mtima

  • @HevenChiwaya
    @HevenChiwaya 2 місяці тому +4

    Kuyankhula chilingamo kulifela dziko mulungu akutetezele

  • @IsaacAmiyele
    @IsaacAmiyele 2 місяці тому

    Kd guys manganya ndiutiyo paja😢😢😮😮

  • @elvisnjoka8428
    @elvisnjoka8428 2 місяці тому +1

    Mudyelatu dzina la malemu hahaha😅

  • @MatthewsJohn-kv8fj
    @MatthewsJohn-kv8fj 2 місяці тому +1

    Boza munali nose atose alliance mumanga nose musathawe inu a utm palibe chanzeru apo ife tikufuna Dpp ndiyimene inakwarisa zodya katatu inu alliance mwalowesa njala mziko nd umphawi oopya bon kalindo president wa Dpp

    • @AishaChibwana-b8o
      @AishaChibwana-b8o 2 місяці тому

      Mmm musova inu simumaona ndeu zimachitika zija hiyaaa fundo zanu ndi ziphwasula lembani zina ndani yemwe samaona kuti anthu sakugwirizana??

  • @MartinMajola
    @MartinMajola 10 днів тому

    Jawala moto ku buuu

  • @victorbanda9039
    @victorbanda9039 2 місяці тому

    Kutuluka m'boma kupanga campaign kufuna kulowaso m'boma mukuzitendetsa bwanji kodi ana amasiye inu kufuna undunu kokhakokhako kkkkk nkhope zake zimenezo anjawala mukhale nduna yamalawi aaas pitani ku dpp komko mwaiwalaso muja dpp onazizira chilimamu kathetseni kachipani kothaithako

  • @AlexanderYovatiKhumalo
    @AlexanderYovatiKhumalo 2 місяці тому +2

    Tiyesetse kuzolowera kulankhula zodzetsa mtendere .

  • @SafariBvumbwe
    @SafariBvumbwe 2 місяці тому

    Koma ichi chikulakhula mr njawala

  • @PatrickFicklem
    @PatrickFicklem 2 місяці тому +1

    Za ziiiiiiiii

  • @zutamgala
    @zutamgala 2 місяці тому +2

    Alibe fundo uyu

  • @TanazioUziyele
    @TanazioUziyele 2 місяці тому +1

    Mukukamba zachitukuko mwapanga zotani inu anjawala zaziiiii!!

    • @Musa1828-l5d
      @Musa1828-l5d 2 місяці тому

      Chakwera wakoyo wapanga chani sikungopha Chilima basi

  • @samuelkachimphula7278
    @samuelkachimphula7278 2 місяці тому +1

    Awa ndachitsiru

    • @Musa1828-l5d
      @Musa1828-l5d 2 місяці тому +1

      Chitsiru ndiweyo nd Chakwera okupha Chilima uja

  • @EmmanuelChirwa-z3n
    @EmmanuelChirwa-z3n 2 місяці тому

    Ana inu mwachepa MCP boma mpaka mpaka 😂😂

    • @AishaChibwana-b8o
      @AishaChibwana-b8o 2 місяці тому

      Mwana Wa njoka iwe zachikale zimenezo anthu ake anapita ndi Kamuzu

  • @kingsleyChisenga-i8g
    @kingsleyChisenga-i8g 2 місяці тому +1

    Pja zimathera pa media pompa zosaopsa ana kulira ndi mkodzo

    • @Musa1828-l5d
      @Musa1828-l5d 2 місяці тому

      Pamtumbo panu inu achitsiru mulibe mzeru mkomweso apa

  • @WitnessPhiri-zr9uf
    @WitnessPhiri-zr9uf 2 місяці тому

    Wayankhula wakuva wava mulungu aliko ayankha ma pemphelo athu

  • @ElsonNsowoya
    @ElsonNsowoya 2 місяці тому

    Mawu

  • @patricksamson4852
    @patricksamson4852 2 місяці тому +1

    Uyu akukwanira pa utsogoleri

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc 2 місяці тому

    Oh yes 😂😂😂😂, nthawi yakwana.

  • @ShillahChisi
    @ShillahChisi 2 місяці тому

    UTM moto

  • @PatrickSomanje
    @PatrickSomanje 2 місяці тому +5

    Osati 1995 yokha komaso amalawi ambili timakonda chilima

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 2 місяці тому

    MCP chipani cha Kupha aaa, Chakwera Criminal,usi Yudasi adagulisa Chilima aa, Chakwera wazi Wanda aa, Wanthu wopanda manyazi Ndi mzeru u fake pastor

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo 2 місяці тому +1

    Kodi muloza chiyani zimene mwapanga chitukuko chake chilikuti anjawala inu 😂😂😂😂😂😂

    • @temwekamlenje4358
      @temwekamlenje4358 2 місяці тому +1

      Ndalama boma lawapatsa zopangira?

    • @SafariBvumbwe
      @SafariBvumbwe 2 місяці тому +1

      Mmmmmmm inu umbuli chani utm yinalowapo m'boma kkkkkkkk uziganiza kawiri usananene

    • @IssacMateyo
      @IssacMateyo 2 місяці тому

      MBatata iwe choka apa ana ama 2000 sauzande inu sanagwinetu akufunika apiteso kwina akapangeso alayasi Ina zazi

    • @temwekamlenje4358
      @temwekamlenje4358 2 місяці тому

      @@SafariBvumbwe umbuli otengera kwa inu mmesa

  • @HopesonButao
    @HopesonButao 2 місяці тому

    Koma muli fundo umu

  • @blessingsmangulama8442
    @blessingsmangulama8442 2 місяці тому +1

    lozani zanu ife tiwone. 🤕

  • @tracybennie7783
    @tracybennie7783 2 місяці тому

    Mulungu. Ali. Ndi. Chidwi. Koma so. Akuyona

  • @SophieLupiya
    @SophieLupiya Місяць тому

    😂

  • @SamuelJoseGaviteni
    @SamuelJoseGaviteni 2 місяці тому

    Osafoka

  • @FranksonKennethChipande
    @FranksonKennethChipande 2 місяці тому

    Kodi Mr Njawala campaign yanu izikhala ya Chilima???? Pangani ndale za smart.Musiyeni Chilima apume mumntendere

  • @aggiemlotha1208
    @aggiemlotha1208 2 місяці тому

    You cannot fulfil the idea of someone... chilima was best but not you maguy

  • @stevemtambalika
    @stevemtambalika 2 місяці тому

    Bomaw ilooo my vote